Abambo ku Kenya akumatsuka makondomu ndikugwiritsaso ntchito
Abambo m’dziko la Kenya akugwiritsa ntchito makondomu ogwiritsidwa ntchito kale. Malingana ndizomwe yalemba nyuzipepala ya Daily Nation, izi ndimalingana ndi kusowa kwa makondomu ozitetezera ku mimba zosakozekera komaso matenda komwe kwafika pa mponda chimera mbali… ...