Flames
Timu ya mpira wa miyendo ya anyamata ya dziko lino 'The Flames' yafika tsopano mdziko muno kuchoka ku ulendo wake omwe inapita ku Tunisia kukasewera ndi timu ya dzikolo Lolemba komwe yakaswedwako 2-0. Osewerawa afika… ...
Mithi
"Khaaa kuti khaaa.."Julius Mithi apata shuwa pomwe ma loya odziwika bwino mdziko muno a Silvester Ayuba James ndi a Khwima Mchizi ati akayimilira mwa ulele a Mithi omwe awamanga dzulo mu mzinda wa Mzuzu. A… ...