
Anyamata anu mwawatuma ku Tunisia aja afikako koma kwatsala ndikubweletsa zotsatira tsopano. Timu ya dziko lino yampira wamiyendo yatera mdziko la Tunisia lero kudzera pa bwalo la Ndege la Tunis-Carthage International, pomwe ikuchalira kuvungumulana ndi… ...