Pali chiyembekezo chachikulu kuti ntchito za umoyo m'boma la Balaka zipita patsogolo kutsatira thandizo la galimoto za ambulansi ziwiri zomwe phungu wa dera la kumpoto m'boma la Balaka, Tony Ngalande, wapeleka pa chipatala chachikulu cha… ...
Articles By Macdonald Kaleso
Khonsolo ya Balaka yatsutsa mphekesera zomwe zakhala zikuzungulira m'masamba a mchezo osiyanasiyana apa makina a intaneti onena kuti boma latseka sukulu ya pulaimale ya Naliswe yomwe ili m'bomali kamba ka njala yomwe akuti yafika posauzana… ...
Mkulu wa bungwe lolimbana ndi kuthana ndi mchitidwe wa ziphuphu komanso katangale la Anti-corruption Bureau, mai Martha Chizuma, ati ndi kofunika kugwirana manja kuti dziko lino lipambane pa nkhondo yolimbana ndi mchitidwe oipawu. A Chizuma… ...
Nkhadze Alive Youth Organization (Nayorg) in partnership with Giving Tuesday Malawi on Tuesday joined the rest of the world in commemorating the National Day of Giving. The National Day of Giving is dedicated to giving… ...
Dzuka Africa Organization in partnership with Zantchito Entrepreneurship and Access to Finance has launched the Zantchito program in Balaka with a call for young entrepreneurs and graduates to be innovative and not rely on job… ...
Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chati kuchoka kwa mamembala a zipani zina omwe akuti alowa mu chipani cha DPP ndi chitsimikizo chakuti nzika zambiri za dziko lino zili ndi chikhulupiriro ndi chipani cha DPP. Gavanala… ...
Bishop Andrew Mankhanamba, Principal for Destiny College of Leadership and Development Studies in Blaaka, has highlighted on the need for graduates at the college to be job creators rather than job seekers. The college in… ...