Tamwapo zithaphwi. Kukakhala Lilongwe kuno, ndiye tinanyambitilapo madzi a manyi khathikhathi anga tikubwira mahewu kapena yogati wa Kombedza. Ku Kabula kuja mbiri ndiye inatifika ndi ija yoti anapeza chitanda. Koma kwa amene amawona ngati izi… ...