Khoti la Euthini, m'boma la Mzimba lagamula Martha Chaula wa zaka 47, kukakhala kundende kwa miyezi 18 popezeka wolakwa pa mulandu wofuna kuba khanda. Bwaloli linamva kuti mayiyu anachita izi pofuna kusangalatsa mamuna wake, yemwe… ...
Articles By Ephraim Mkali Banda
Police in Mzimba have arrested an intern at M'mbelwa District Council who is suspected of stealing tablet phones and reams of paper in offices at the council. Our reporter witnessed the arrest of the intern… ...
Two officers at M'mbelwa District Council who were recently posted to new working places are defying orders to relocate to their new duty stations. According to the documents that Malawi24 has in hand, Chigonjetso Chiromo,… ...
Chipatala cha Mzimba chikumagwiritsa ntchito ndalama zosachepera K800,00 pa tsiku kugula mafuta a jenereta kamba ka vuto la kuthimathima kwa magetsi pachipatalachi. Malawi24 yapeza kuti chipatala cha chachikulu cha boma la Mzimba chikumagula malita a… ...
Wapampando wa mabungwe omwe asali aboma ku Mzimba a Christopher Melele ati ndiwokhuzidwa kwambiri kuti adindo ena akulephera ntchito m'bomali. Iwo adzudzula zomwe zikuchitika kuti apolisi ya Jenda akukanika kukwizinga mwana wa Inkhosi Khosolo wazaka… ...