
Atapulumuka kwa kanthawi, tsopano wagwa chagada George Chaponda. Chikalata chochoka ku nyumba ya boma chimene wasayinila mneneri wa a President chalengeza kuti a President a Peter Mutharika amuchotsa Chaponda pa unduna. Malinga ndi chikalatachi chimene… ...