Kukolora madzi amvula, yankho lakusowa kwa madzi
Pamene dziko la Malawi chaka ndi chaka likupitilirabe kumakhala likukumana ndi vuto lakusowa kwa madzi m’madera a ku midzi komaso mu matauni, katswiri wina wati kuvutikaku ndikochita kufuna. Anthu ambiri mdziko muno amakhala akulilira kuutsi… ...