The outspoken Salima North West Parliamentarian Jessie Kabwila has claimed that she is still Malawi Congress Party (MCP) spokesperson despite being fired from the party.
Kabwila explained that the party has not communicated officially to her on its resolution to fire her from the MCP.
“A Malawi kumudziko dziwani kuti okuyakhulilani ine ndilipo “machine” (Malawians must know that I am still spokesperson for the party),” said Kabwila.
She added that the party is ready to be the ruling political party with Richard Msowoya as vice president of the party, General Secretary Gustave Kaliwo and Lazarus Chakwera as the leader of MCP.
The MCP National Executive Committee (NEC) on Sunday resolved to fire Kabwila and suspend Msowoya and Kaliwo for opposing Chakwera’s leadership.
The party has since replaced Kabwira with Ezekiel Ching’oma as publicity secretary for the party while second deputy secretary general Eisenhower Mkaka has taken up the position of secretary general.
Cling cling cling cling osangopeza chipani choti mulowe bwanji mayi mcp sifuna avundula madzi
Tsonotu muvale zilimbe ndithu coz amene mudzapikisane naye pa ma primary a Congress hoping akubwezeretsani mu Congress ali ndi mtundu!! Kwayambira po Khombedza pamene, Chitala plus Kasonda mtundu wake okhaokha!! Omake ndi otatake onse kwao T/ A Khombedza so play ur cards very well!! Munthu akaluza u MP political career sioneka bwino!! Anga mmalangizo coz mmayenda maliro koma moto wapadzanja souzana!! Zikomo
MCP virus
Mudzidekha enao ndikale adakhala mmipando akupweteketsa mcp imakukondani km inu kudziva
End of the road
Kwathu timati mtengo woongoka umalimbana nkhwangwa! Mwina nkutheka zina olunena o yemupi wathu zoona koma O Chakwera wathu timokonda ndiye mtangu zintha chipani mwasemphana ndi mavoti a ko Khombedza apo nde neneletu! Zikomo
Kungochoka kapena kuchotsedwa Malawi Congress Party kwathu ko Khombedza sungawine!
Kkkkk
Kkkkkk I don’t think chakwera can defeat this lady
Kabwila ngati anakutuma ukanangodya akupasazo osasokoneza popezera khobidi iyai
Wayamba misala
well oiled machine of Mcp….. Mo fire Kabwila
Gologolo wakakamila.akuona kt zolinga zomwe anamutumira aDPP sizinakwanilitsidwe. ulendo wake ndi inu unya uwona
Inde Mayi Auzeni Kuti Mcp Ine Ndimobadwira Simunachite Kulowa Ayi Nde Palibe Ondichotsa
Kabwila with all due respect to you and the whole party sit down and solve your peronal issues inside the house. This the reason I say Malawi has parties but no democracy.
Samalani onsewo Ali ndi voti komanso Ali ndi anthu awo owakonda
Chibwana mama timakukonda koma Aaaaa mavelavela
Welcome to DPP Kabwila. You will be a cornerstone.
As from the beginning
kabwila tsopano kkkk, asewere ana osapola pa nchombowa kuti azidziwe bwino ndale zapa nyasa kkkkk, sizoti wangochoka uko ku ubusako unvekele ndilamula dziko la malawi walemba mmadzi ameneyi, kabwila ukasokoneza sokoneza iwe basi bwelera kuchipani chako.
msowoya kaliwo kabwila mwati onse mngoipa mmmm amcp mukapanda kusamala chaka chamawa muthalika azawina nd mavot ambir
we need courageous women
Kabwira unagudwaso bwanji mpakana kupangisa press Conference yawekhawekha.Samalanawo anzakowo akuwonongera tsogoro lako.
Jessie kabwira ,,don’t cling onto this cursed party. U want achieve anything in your political career ,
Wanya nazo galu iwe.
Thats acomplete fallancy she has fired,she has fired thats all nobody can reverse nec^s decission.she will cries and cry thinking of her constituency. she will never come again in parliament even if she joins another party
Hahaha boss munena ngati mumamuvotera nokhatu
let’s hope the MCP NEC is following all the procedures to fire Kabwila
Mamuna Akati Banja Latha Umakakamira? Ndiye Chilipo Ufuna, U Hule Basi
Kkkkkkkkkkk.
Mwinatu Malume Che Mpando Ankanena Zoona Kt MCP !!!! Sidzatenga Boma Mpaka Muyaya ,mwinatu Nchifukwa Alimkati Momwaza Mmalo Motolelatu Eeetiii Choncho Mukwanitsa Kuwachotsa A……….Wa
msonba ikavundila mmanja sitimasunga pofuna kuchulukitsa nambala ayi yaola yaola timataya poti inu mumatola zoola tolani
Haaahaaa i do like this woman she doesn’t want to be among the political prostitutes like what most of men are doing wondering here there, keep it up j kabwila YOU will win the race.
Mama,musalimbane Nao Anthu Awa Amafuna Anthu Opepela Omangovomeleza Zopanda Pake Adzazindikila Patsogolo Kt Jessie ndi Mwala Wapangodya (kulephela Kukonzekela Ndikukonzela Kulephela) 2019 Yayandikila Mmalo Motolera Mwakangalika Kumwaza M C P Chipan Chonvetsa Chison MUKADZALUZA MUDZIDZALIRA ,atibela!!!! Zaziiii!!!!!
Chiyambi choluza mmalo momanga chipani mukuphwasu adani anu apedzelapo mmpata pamenepo.
Azimai ake amenewa kkkkkkkkkk
Koma kabwira
Mutu ukugwira bwino umeneu musasokoneze chipani kapumeni or else join Akweni ku DPP
makani ake amenewa wina nde aziti votelani mzimayi
MCP always number one pa nkhani zolimbanirana ma udindo malo mokozekera chisakho .
Ayayaya, Iwe #Jessy, Uzithokoza Kt Simuli Boma, Mukanakhala Kt Lazalo Ndi Presd, Bwezi Pano Utakacheza Ndi Ng’ona
Ngati akungochosa Enii Khomo kuli bwanji Enafe
Koma chaka chimene azalowe Bomacho Ng’ona zizanenepa kkkkk
Hahahahahaha #Ramzy, Gat A Youth Amafuna Mutu Wa #Msowoya, Kaliwo Nde Enafe Tigalimbe, Congoles Sidzava
kd mai uyu akufun chan kd? mesa tava zot analandla ndalam kuchkela ku dpp apte bas
Openga ameneyu apite Ku dpp
no comment
U are almost welcom once again mama
Yes we kno she wil bounce bac in there…
Thats Great Kumalimba Mtima
“Educated savage”, sorry that I have used that word please!! But truth preveils
I understand she has eyes & ears she knows what she’s talking & she knows what she’s fighting for. Who’ll be the winner & loser in this game
NDIYE WINA AMATI KABWILA WAGULIDWA KU DPP UJA ALIKUTI ATALANKHULASOTU. DZIKO LIMADANA NDI CHILUNGAMO. MMAI UYU AMADZUDZULA PA CHILUNGAMO NDIYE WANTHU AMADANA NDI CHILUNGAMOCHO. NDINAONELA YESU KUPACHIKA YESU KUPASULA BALABASI. MIA NDI BALABASI KAVUWE VUWE AKUKONDEDWA CHIFUKWA ABWELA NDI KAISALA. AKUBALALITSA NKHOSA ZA CHILUNGAMO.
Kodi muli ntulo che Jafali?
Osat Inu Man #Frank, Nda Mene Mukusiza, Chikhala Kt Munali M Boma, Bwezi Onse Ataona Ya China Gadama, Kma Awa Adzatheka Kma?????
nosenu ndnu ana mai uyu analandla ndalam kuchokel ku dpp kmas anagulilidw galimot yodul ndcholinga kt asokonez chpan
Magongwa sukunamadi man
kkkkkkkkkkk mmayi ameneyu osazisiya bwanj
Kod akukakamila bwanji osapita mbali inayo bwanji?
Inu Osamuuza Mia Kt Ayambise Chake Chipan Bwaaaa?? Mmensa Ali Ndi Cash, Panja Mcp
MCP has no money. And they’ll perpetually lose their members who, as we approach elections will be there to make political business using their prowess. Kabwira has been fired. MCP’s constitution has four corner stones. If one violates those corner stones, he/she is drowned. Kicks of a dying horse is what Kabwira is doing. What she needs to do now is to reposition herself for next elections. She’ll win her seat back in 2019.
If she wants to win then she should strive to become the Mia’s of this world,I mean the financial muscle to sway the masses in her constituency. Mind you he’s coming from a constituency where MCP is in the blood.Furthermore the leadership of MCP is a darling to all the constituents therefore I doubt if such people can put in office somebody who’s construed to be fighting their loved party and its leadership.The more she fights MCP the more she is subtracting her votes.This is plain truth ,mark my words this woman is engaging in a self destruction affair unless she has a very fat wallet to bribe everyone
LET THEM GO WHERE THEY BELONG.
Mmmmm tili pa mbuyo pako ase
Sokonezani mmene mungathele mama ndi ufulu wa azimayi umenewo
Machine For Real
Chakwera wayamba kumene ndale asamangochotsa anzake omwe adamva kuwawa ndi chipanichi kumeneko ndikupusa jessy ndiolimba mtima amufunse Bingu Mmai uyuyu siopangira naye zibwana chenjerani
Kusokoneza sikulimba mtima baba
Tanenakale Kt Inu Mukulota, #Jessy, Pandale Samatekeseka
Iweyo uzikawakulira mtima bwana wako tione ngati sakuchotsa ntchito..
kkkk nde muona ngat atan apte bas tilibe naye tchito
Jessie Kabwila a fine tuned MCP machine…keep the grip Mama.politics is your trade.
Kicks of a dying horse
Kkkkkkkk wavakale dzuwa thawiyomwe kabwila uwauze azako umapanganao zauhuleo kuti musama sazile modyelamo zitsilu inu ,chipanichinakhala pa opposition kalekale chifukwa cha mahule inu kkkkkk ulila sunati
Kikikikiki Masiku omaliza anthu azayamba kuwukirana pa chiweniweni
ndeno ngat sadzigwiritsidwa ntchito pindu lake nd chani? atadzapta ku convetion atadzavotera ena udindo wakeo adzapanga chani?KKK
I think wapasidwa ndalama kuti azibweresa chisokonezo.
anapatsidwa kale kmaso anamugulir galimot yodula hevy
Akudziwa kuti kungoti atuluke Mcp niye kuti za kunyumba ya malamulo ayiwale coz komwe iyeyu akuchokela phungu wachipani china sadapambaneko ndi Mcp palipose kumeneko
true salima north west ndya M.C.P bas
More fire kabwira mcp ndi deal
KKKKKKKK MAYI UYUU SANGAMUTHE NDIPO NDIYEMWE MCP WAYIMVERA KUWAWA
Akudziwana iyeyu ndi chakwela ndale ndi chonchotu
Go deeper
But Hw?? Sound awkward …. Anyway thats politics @ its best
ZOONA 2019 boma u and chakwera timakukondani