Leader of Opposition Lazarus Chakwera has this afternoon walked out of Parliament due to government’s reluctance to table the Electoral Reforms Bills.
Reports say Chakwera and other opposition legislators walked out to express their anger.
Speaker of Parliament Richard Msowoya did not stop the Members of Parliament from leaving the house saying it is their right.
Chakwera and the Malawi Congress Party (MCP) want government to table the six Electoral Reforms Bills which if passed will among other things change the system of electing president from the current first past the post to the 50+1 percent system.
Before the current sitting of Parliament started, Chakwera threatened to boycott Parliament if government will not include the Electoral Reforms Bills on list of bills to be discussed.
voting for chakwera wl b the worst thng mmmmm wanyanya man of God yu
Bwana chakwela munakangodikila a dpp akakana inu mukazatenga boma bill yoyamba ndi ndiimeneyo kungolamula basi mwinanso no bill abwana alamula.koma zonyanyalazo mmmmmmmmmmmm
Masiku omaliza…chikondi chapa abale..chidzazilala…anthu adzakhala odzikonda okha…osati okonda Mulungu !!!
ngati ali owina akukakamira chani ku 50+1, we don’t need dictators in this country, ngati sakumva za anzake while in opposition, adzamva za anthu akalowa mboma? God never chooses anybody with selfish motives
hahaha a pioneer inu mukuti chani, 50+1 izakupatsani chani? you people need extra education osati nyau zanuzo, running a country ndi ng’oma ndizosiyana mwamva?
Chakwera is gt characteristics of a bad leader….he z a nytmare
Kkkkkkk
They will solve, coz they know what they doing, any way check me at here
what next, atatuluka iyeyo ndi anyamata akeo was Parliament disrupted or business continued as usual
Ife tufuna Dr Chakwera. Osat zakarezo tufuna tioneko kusintha .mwina tingabwerere kumudziko
DPP for life…..
Weak decision from the weakest leader of opposition
Good
Kodi inu who can 4 chakwera?
ambilinu ndinu a DPP mukudana ndi chakwela cholinga APM adziwona ngati zili bwino pamene sizilichoncho koma pempho langa kwa a APM ndikuti asankhe njila yoyenela osati kutengeka ndizongolembazi chisankho chimakhala muntima
ambilinu ndinu a DPP mukudana ndi chakwela cholinga APM adziwona ngati zili bwino pamene sizilichoncho koma pempho langa kwa a APM ndikuti asankhe njila yoyenela osati kutengeka ndizongolembazi chisankho chimakhala muntima
Do U Think Guyz This Man Can Lead Us On Better Development, If He Can Win 2 Be The President Of This Nation??
Some fights are not worth it…if a goat is bleating non stop its better to go away coz simungamvane zilankhulo
I Dont Lik Ths Man #chakwera
I Dont Lik Ths Man #chakwera
Alibe ulemu
dont take nonsense mr President in waiting
M’mene dziko la Malawi lafikirapa munthu wina wa nzeru mkumasangala kuti zinthu zikuyenda bwino? A Malawi, tidalakwanji? Dziko latha apa ndipo latsala nsanza zokha-zokha. Magetsi ndi chinthu chofunikira zedi mu dziko. No electricity, No development
Ndiye nanji kuti chakwera watenga udindo kuzakhala kulira
Big up Dr Chakwera , we should stop clapping hands on stupid excuses. Malawi belongs to us all not to these princes and princess of thieves. They always bring the bill in Parliament that is in their interest , they don’t even care about the future of this nation.
So if he choose to walk out of parliament will it change anything?….. the sessions will continue…. we as a nation can’t rush to make a decision like that….. ask yourself how many Malawians know what 50+1 is.. the challenges… people need to be educated first…. kupewa pa mawa…. zisankho zomwe timadalira ndalama zopempha zomwezi….
It’s a good development yes… but needs time
Muntha kulankhulana mmene mungalankhulire but chimene achita Dr Lazarus chakwera is good because nthawiyoseyi zaka zonsezi otsutsa amangowombera mmanja ndi zopusa zomwe what is that? Pitilizani Dr Lazarus chakwera anthu wa adziwe ndale
A president amenewaaaaaa? kkkkkkkkk
Chakwela is premature in politics
Mutukwana angati
This is what we call regionalism.
TIME
Rubish
When you can not stand the heat umanyanyala kumene
Not chakwera alone but members of the parliament walks out even for the ruling also walks out
zachabechabe zithu zosezi zongosautsa mtima atelo mlaliki musazitsatile just focus onto Jesus son of living God yemwe akut idzan kwaine nonse olema ndiothodwa sezani goli langa lomwe silolelemela koma lopepuka munthu amakhumudwitsa bt Jesus Will never ever dissapointed you,we ar in last dyz guyz let us repent our sins zotukwananazi sizabwino be holly as de one who creat us iz holly
Kumayimba bwino ng’oma zanuzo.Dance the way u have heard it pple.
Chitsiru chosapola pa mchombo,, uzalamula dziko la ambwiyako.
Utsiru wa zitsiru zadziko lino they think this bill will remove Dpp and APM from power Only.. This will come to stay, and will even kill all other parties because expect coalitions after coalitions.
mcp will never rule this country,
foolish pac, foolish catholic priest, amsembe ake ati angobala ana mmidzimu, zopepera basi,,
mr chasika mwayamba mantha mumaona ngati ndi za mmbale pelekanipelekani izi ndi zandale zimafuna anthu olimba mitima. osati ngati azimayi ngati inu ai
Ndale siphada be strong mr man.Malawi mpovuta kuti dziko lizalongosoke.
hahahahaha koma.galu ameneyi kkkkk
Politics ni deal kkkkkkkkk
Ndiofoila chakwera,mamuna sanyanyala ndiponso sangawine,aziwina pa Facebook pomwepa basi
Yah that’s being a man don’t just smile at shit ……mcp siya dzibwana
Chakwera ndi dihlu alibe dzibwana ngati enawa ogwa podZala mtengowa
Zinyanyalani
Thanks to Dr.momoh who saved and cured me from hepatitis B.. virus.with his herb medicine you can also reached him for similar issue on…you can add him on WhatsApp +2349068579672
Simudati! Mutsegula naye mmimba
aaaaaaasati ntero ochakwe kunyanyala kkkkkkkkkk.
Some people like to comment because people are commenting. That way he protested showing disagreement. Its part of democracy. Some think protesting is walking in roads with cards. Know your rights than fwe fwe fwe. Even in court you have a right to remain silent. Its a way of protesting. And whatever they discussed the record is he was not with them. Don’t forget its not time of aSamunda. If he criticise the speaker say its disrespecting the President. This is not time for yes yes bwana. At least he protested in a peaceful way. One day you will remember him. Instead of discussing important issues. They want to talk unnecessary things. Why they don’t want to talk about it? That reason is the one cause Chakwera to walk away. I salute him like it or not
In politics, action is valued than merely words
Childish…
Chakwera Has 2 Show Qualities Of Being A Good Leader.
Kkkkk !
Amalawi opusa mukufusa chitukuko chomwe wapanga Chakwera osafusa chomwe wapanga namachende pitara wanuyo bwanji nyini za amanu
He won while out of government and he is now in the system. Is he going to fail, while running the machine? ??
What is harsh action here than being stupid only?
The dumbest opposition leader malawi has ever produced.
DPP cadets sisowa. We kill a snake the way it deserves. Some things needs hash actions.
Tembo Jzu Sanapangepo Zimene Akuchita Bakha Uyu Mukuti Chakwerayu!Mpaka Kutuluka Mu Parliament Kamba Kankhani Yopusayi?Munthu Ameneyu Atakhala Mtsogoleri Wadziko Lino Zinthu Zidzafika Pati?Munthuyu Simunthu Wabwino Waonetseratu!
Kumatsatila Lazalo Nde Bolaso Kumavina Nyimbo Ya #MAHEPE.
What happen that he should walkl out
manwatu sizikuwayendela analakwisa kusiya zamulungu mkujoina ndale petro atasiyana ndiyesu mkubweleramso kokasoza plibe chimayenda yohane 21-3 ndiye auzeni aganize mofasa kupambana kwa ma MP aMCP siachakwera ma mp amakhala ku maconstituency anthu akwao amawadziwa na achakwelawo kukula kwake mtima kumeneku angasogolere mitundu ya mmalawi Idont believe mkuona anasiya za ambuye amakanganila chopeleka ndi asogoleri ndiye afuna kundale azikabako chenjela nayeni ameneyo he is not there to lead people but to encourage cashgate scandle beware of him.
Politics needs mature pipo not makanda ngati ochina ochakwera,mpaka leader opposition ndiamene alimalingaliro olamula dxiko lino kufika ponyanyala aaaaah awa tikawaninkha mpandowu adzatinyanyalanso very childish
#Malematype’ it has just become a trend now ‘ i saw the other day in Gambia, chairs were frying all over parliament
komaso
hahaha leader of opposition? aphunzire kwa achina Malema akupanga fight until justice prevail osati za chakwela alibe nzeru
Ndiwamwano basi akhaula sangakhale president
Boma limafunika kufotokoza osati masanje amenewo akuona ngati anthu ndiopusa tikuona.
Kkkkkk amayesa kuti amunyengelera
Yes, Malawi is in a bad shape and a leadership refresh is long past due coupled with these reforms which are needed post haste, but Chakwera is not the answer. That man cannot be trusted. A Chakwera presidency would be the worse thing to ever happen to our country.
Kkkkkk abusaaaaaa ndichani kod? Kapena munalandila call kwa akazi anu kut kunja kuli ziii mukabenso madzi kkkkkkkk i dont havb much to say about chatsika i think he must join wandale at zomba
Iye ngati ali wachilungamo bwanji anachita illegal water conection ku Mcp hq?this guy is sick
Chakuba ichi ineyo ndilibe nawe mawu anaba chopereka ndi kulowera ndale andibwedzere changacho
Kkkkkkkkkkkkk apa madzi achita katondo kulibe mvula nankha mvula ikangwa kukhala bwaa kkkkkkkkk
Yes!!!!! My president!!! We need that bill!!!!!!!!!!!!!! Hey !! You DPP!! We need that billllllllllllllll
Sanalakwitse ndi boma la bwampini akamba chiyani chanzeru naye,magetsi on and off,katundu kudula,simalawinso amene ndi mamudziwa,bwanji osangofa basi tione zina
Uyambe iweyo kufa,we all malawians osamafika pofunira imfa zako,kunjaku kuli Mulungu amene amasunga mpweya wawina aliyense osamatero bale amene ukuona ngati adzapanga zabwinoyo ukhoza kudzakhumudwa naye
Kodi mukudandaula chiani apa,munaona dziko lomazima magetsi,ife taluza azibale ku hospital,who are u to judge me
Pakholo pamako
Nawense pamako,pantupako,posaseta anyaza onunkha manyi
In a standoff like this between the so called PAC and the government the best what PAC could have done was to challenge the government to call for a referendum if it feels that this is what people in Malawi want. This us what PAC in 1992 did to challenge Dr Banda. Vuto lomachita zinthu muli ndi munthu mmaganizo ndi limenelo
Ndiye mwati abusawa ananyayala paka kutuluka chifukwa ma MPs amawazuzula chifukwa chokuba madzi kwa zaka zingapo ? inetu chizuguchi sindinachimve . or he want to be like Julius malema ? zikanakhala kuti ndi Ku football ndiye kuti Mr chakwela akuyenela kubwelela Ku division because he is not well qualified to be President and still poor minded and to say de fact this issue singamupangise muthu kuti atuluke. and to come out of the house isn’t a substitute to solve this problem so called 50+1. anyway palibe vuto pakuti ukayenda ndi mwana ndi chimozi mozi kuyenda wenkha.
Kodi a Chakwera akuganiza kuti azalamula dziko lino. Akuzinamiza munthu onyanyala angamuvotere ndani ndipo ife Kuno ku South sitingavotere Chakwera azingozitaisa Nthawi yake pachabe.
Ineso ndikudabwa who can vote 4 him?
Kkkkkkkkkkkkk
Congras
Kkkk komanso awa kuchoka ku meneko kupita ku chibwezi chisilu cha munthu so ndi phindu lanji lomwe walipeza shame on u
Replication of DNA …section 65 number one budget number two.
Koma zowona DPP boma likukutererani lili mmanja mwanu chifukwa cha makani ngati ofula agalu. Kulibe wanzeru Ku DPP? Who can advice bwana to do the will of Malawians
Izi zimachitika mumaiko ambili ndipo inu amene mukungoyakhula apa simukuziwa chifukwa chake watuluka muzivesa khani musanayike ndamanga sizonse zomwe amakambilana ndizothandiza anthu ayi
You are duck too
This man he’s not feet to be a prasident
Hehehe chizungu cha dpp cadet icho!
Kkkkk kukhala cadet ndi chizindikiro cha umbuli.
He is a man who doesn’t like no sense, He couldn’t do otherwise bt walking out.
…mun2 waphonkho abale samanyanyala nkhani..amakhara pompo,kukambirana zimatha…#(soldier)
Do even Know what your talking about?
I was saying that new Mcp carries the dna of old mcp, what has happened now? M’busa uyu sangatumikile dziko wachepa nazo,even the Bible says “a person who does not control his anger is like a fortless city, ndiye mwamuwona mtsogoleri wanuyi za malemu a chakuamba izi
true man
Akagwere uko fisi wachabechabe
Abusa tsopano leaving the a sheep’s behind? Ha ha
Kkkk abusa akubweleranso ku Saul
akuti awa anali abusa kkkkkkk
Eeee!
He’s a coward why can’t he keep fighting?
walk out to urinate or what malizisani nkhaniyo
komaso2 achakwera sakupeleka chilimbikitso.. aaaa simagulu aka cash gate awa akalowa muboma??? hahaha ndalama zochepa zija zidzabedwaso ndithu… how can tis man behaving like achild chonchi full of pompus, selfish ndizina zambiri ine apa nde bolaso mugabe ndithu
this is why politics need men not children…
Kkkk zoonadi man
Kkkkkk yeah
MWATI SAZIZANYANYALA DZIKO UYU?amalawi samalani. As leader of opposition samayenera kukapanga zachibwana akupangazi
Kkkkkkk good comment sistez
Hahahahahhaha amayesa ndale ndi masewera lero siiizi kutenga boma sizibwanatu
This man
Its now too much
Enough of chakwera chakwera thing
Is he Jesus or what
I don’t trust him.he should be a dictator in making, the way he take Malawi as if every one is in his control but he is yet to be the nation president ,so if he becomes one , how will he be?????
My #opinion
Zako zimenezo,behind him!
I doubt if you are part of the many suffering Malawians, Chakwera is the hope for Malawians so stop this nonsense
If you don’t trust chakwela, you are nothing in Malawi.
What makes you think that Chakwera is the hope for Malawi? As a reader of Opposition chaphindu chomwe wachita ndi chiyani chomwe ungatose? In his Constituance ndi Chitukuko chanji chomwe CHAKWELA wachita?
Apange chitukuko ngat akulamura ndi iyeyo?
If you are DPP just remain so. Don’t force others to follow you to your zikwanje party. Chakwera is in opposition and a leader yes, what has your papa who is in government now done?
inuso ngat muli a mcp musakope anzanu kt azisatila zopepela
Koma zoona alipobe oganiza bwino bwino omwe akuyimabe mbali ya Blue Camp?
Comment from an independent observer
Juma wa mpokosa jr,funso lomwe wafusa rodrick kapasule ine ndlimvetsa koma iwe wangoyakha usanalimvetse ndikuliwerenga.akufusa kuti kudera lake ndichitukuko chanji wapanga? Ndie iwe ukuyakha ngati kuti ofusayu wafusa as if chakwera is a president.muzionetsetsa ndikumayakhano bwino kk
I trust him
Chitukuko chakudera ndicha ma mps
ONLY GOD IS OUR HOPE………
Brothers kipa,ine siwa chipani cha blue koma ndizomwe chakwera akuonetsa panopa pple yayamba kuganiza kwambiri kuti 2019 akazawina azatisungadi,sitizampanga criticise atalephera nae kupanga zina zomwe akuzinena panozi zomwe zikutipangitsa kuti timukondezi?titha kumaoneka ngati a mcp tilipo ambiri koma zamumtima tisakuziwana
Kkkkk aaaaa chabwino awowo ali mu government, what have they done since 2014?
wazikwanje fc Linda wukukana chani
Specimen of goods train
Chakwera is our last hope don’t be stupid we are tired of these dpp thugs, Prince of thieves
Chakwera will be more worse than this regime. azakhalangati Mugabe uyu, I dnt think ngati akuziwa chomwe akuchita
Last hope my …s
mmmm mpaka last hope kkkkkkkk ndakomoka amalawi awooooo
Ife nde chakwela yemweyo nanga tngakondeso ndan pot atupele ali darkside …chakwela yemweyo bas zkazamukanika tzasnthaso.,.
Apapa zikuonesa kuti omwe akuti chakwera is our last hope
Alibe ma options hence they see chakwera as the only possible candidate who can take Malawi to another level not that they are confident he can do so but because they are out of options.
Am not a DPP fan but I see what is happening.
Rachel Bema,iwe siungachione coz moyo wako ndiotsutsa basi,koma ena akuchiona chitukukocho,zilipodi zina zomwe sakukwanitsa sindikukana koma nayeso ndimunthu amene sangakhoze chinachilichonse coz iye si Mulungu,as i said b4 am not a dpp cardet koma chachikulu ndinachiona kumalawi kuno ndichakuti,timayakhula zithu ngati kuti malo omwe tikuwanyozawo tinakhalapo ndikuona mene zithu zimayendedwetsera(moyo wa nsanje basi )limbikirani mukalowe mundale mukakhale president tione ngati mawa sitizakutukwanani kamba kakulephera kwanu kuyendetsa dziko
Siine wa DPP komanso nane chitukukocho ndikuchiona munthu ndani angakhonze dziko pa zaka5? More over adapeza mavuto a cash gate kuti alongosole mukuona kuti ndalama akadadzitenga kuti? Mpatseni mpata munthu zomukokakoka chepetsani musiyeni munthuyu nayenso ndi munthu inde amalakwitsa zina munthu sakhala 100% nanunso a mipingo awuzeni anthu za kubweranso kwa mpulumutsi wathu YESU mkhristu osati zimene mwayambazo mwanva!
ndale m’kachisi wamulungu eti eti
koma ndiye zafikapo ku malawi kkkk
Nde yake ana achepa MCP more fire
Ochakwerawo soonadye ndiye onakumbukira mkute osati othawa,kkkk munthu wamphongo anzanga samanyanyala nkhani,amakhala pomwepo, kukambirana zimatha(lucius banda on repeat).
Kkkk Omakadya Mkute Wa Therere
Ochakwera siozatheka dala,kkk komatu okuti okufuna mpando ononawu 2019 ndi kunyanyala nyanyala oli kuchitaku kaya ozalimba kaya.
Mmmmm ibra ndizabwino zimene wachita chakwerayo kodi dpp ikuopa chiani kubweretsa bilu imenei.ndizofunika kukambirana ndikuwaphunzitsa anthu ubwino wake wabilu imenei.ine ngati wachigawo chapakati sitilora kutiberanso tione zina bg
Kkk ndiye kuthawako ndi solution?patatu sindisapota dpp or mcp ine koma kuthawa sikuthandidza anthu.
Kuthawa nkupusa ……kuchenjera nkulimba mtima …….munthu wankulu waonesa kupoira apa
Ndukaika ngati ochakwerawa ozatithandize okazawina. Kunyanyala kwa iwo ndi solution
Ochakwerawo olusonyeza kusakhwima munzeru anga ngokazi iwowo????
Ochakwera ngolaikitsa odala
Ndakuenyani guyz Kkkkkkk ochakwera woyeeeee
Odala! Ochakwela alupanga za madzera mphuno, nkhasako Vincent Wandale
Kkkkkkk mulunenetsa inu o Alex
KK ZOVUTA
Kodi Imeneyi Amaziwona Ngati Ndani.?
Ndakhala ndikunena kuti Chakwera ndi wamisala,tifunanso umboni wina pamenepa
Kumalawi tsopano.kkkkkk
What really happened? please tell us.
Ndizopanda ntchito izi palibeso chomwe chingatithandizepo apa anthu opanda mayinafe….
Sanalakwitse zibwana zikuchuluka
Good Mr Chakwera I Was On Hunger Strike I Did Not Want Munthu Wotukwana Komanso Wa Usilu Mu Nyumba Ya Malamulo.Its Time For Me To Eat.Just Know That Ukazawina Ndi 38% Tizavotaso Kaya Kazakhala Katatu
No work no pay.
bring,back electrol bil other wise muonongetsa zithu
Zithu Zake Ziti, Munakanka Sec 65 Kamenekaso Ndikachan!!
iwe uona ngat chan?
Mani musanamepo APA palibe kugwedezeka pitani Ku msewu kuno tikaonana komweko
zoti adali m’busa ndimaakaiķa mwina adali mkulu wagulewamkulu kuķasiya
KKKKJKKK
the duty of the pastor is to protect and prepare the flock from the devil n chakwera is duin so
Kkkkkkkkkkkkkk uh? Gulewankulu? Ndakomoka
Kkkk mesa kod mutchalichi anatulukanso chonyanyala nkukayamba ndale then what gud do u espect from a cursed dull
Kkkkkk.nyau party iyoooo!!
I see no problem…no one is tied to the chair
Kkkkk good comment ???
A SOTHINI Banda ndi imeneyi timanena ija”MCP cannot be trusted, this new Mcp carries dna of old mcp “inuyo nkumati ineyo ndizimvere chisoni, look at honourable Chakwela’s guesture resembles to Late chakuamba, ndale za pa malawi its part of our blood from makolo athu adali ma diehards to this brutal Mcp mpaka anadzitaya, ndikupatse clue ina, “Catholic letter yowerengedwa ndi bwana vp,there is amotive behind mchifukwa mukuwona CCAP n Anglican adzizimuka kodi kunjaku kuli izinso ie political science yayaka kuti buu
Chakwera leaving the house i see no problem because we all know a dpp safuna kumva za anzawo. If i was him i would leave too because it was a waste of time participating with those who dont wana get help. If you fight with a fool you also become a fool so i salute mr chikwara on his good decision. And that has nothing to do with old politics, thats history . Learn to appreciate good things for once. Anyway you think peter munthalika is fit , that’s how you view things at your own prospective way and i view mr chakwera in my own way too. Za chilima trust me ulibe umboni. Your only assuming things
Ndiye kuputsako think first ulindiana ndiye wayambana ndi amunako ndiye ana asowe mntendere bcoz of that nonsense
What? I was waiting for this kkkkkkkk
Not dramatic but ndi wamisala busa yo……wat kind of man is this?chakwera
wise people don’t take nonsense big up Mr Osamatayisa tym kumeneko
Nde Atule Pansi Udindo Nanga
Atula pansi adamuvotera namako?
only cowards run away from war but real men do fight to the last drop of their blood……!!!!!!
True David
True
True
Words of wisdom
True boss,awa awonetseratu kuti mphatso yautsogoleri mulibe adzatinyanyalanso ndithu
Wisdom will tell you that not all battles are worthy your struggle. Select your battles wisely. Ask King David he wud have ended on a sad note after he went back to finish off the remnants of Goliath family.
Very true
Watch your mouth mboba we don’t smile at shit at mcp
Well said
What has happened?