Chakwera walks out of Parliament

Advertisement
Parliament

Leader of Opposition Lazarus Chakwera has this afternoon walked out of Parliament due to government’s reluctance to table the Electoral Reforms Bills.

Reports say Chakwera and other opposition legislators walked out to express their anger.

Lazarus Chakwera
Chakwera has walked ou

Speaker of Parliament Richard Msowoya did not stop the Members of Parliament from leaving the house saying it is their right.

Chakwera and the Malawi Congress Party (MCP) want government to table the six Electoral Reforms Bills which if passed will among other things change the system of electing president from the current first past the post to the 50+1 percent system.

Before the current sitting of Parliament started, Chakwera threatened to boycott Parliament if government will not include the Electoral Reforms Bills on list of bills to be discussed.

 

Advertisement

192 Comments

 1. Bwana chakwela munakangodikila a dpp akakana inu mukazatenga boma bill yoyamba ndi ndiimeneyo kungolamula basi mwinanso no bill abwana alamula.koma zonyanyalazo mmmmmmmmmmmm

 2. ngati ali owina akukakamira chani ku 50+1, we don’t need dictators in this country, ngati sakumva za anzake while in opposition, adzamva za anthu akalowa mboma? God never chooses anybody with selfish motives

 3. hahaha a pioneer inu mukuti chani, 50+1 izakupatsani chani? you people need extra education osati nyau zanuzo, running a country ndi ng’oma ndizosiyana mwamva?

 4. ambilinu ndinu a DPP mukudana ndi chakwela cholinga APM adziwona ngati zili bwino pamene sizilichoncho koma pempho langa kwa a APM ndikuti asankhe njila yoyenela osati kutengeka ndizongolembazi chisankho chimakhala muntima

 5. ambilinu ndinu a DPP mukudana ndi chakwela cholinga APM adziwona ngati zili bwino pamene sizilichoncho koma pempho langa kwa a APM ndikuti asankhe njila yoyenela osati kutengeka ndizongolembazi chisankho chimakhala muntima

 6. Do U Think Guyz This Man Can Lead Us On Better Development, If He Can Win 2 Be The President Of This Nation??

 7. Some fights are not worth it…if a goat is bleating non stop its better to go away coz simungamvane zilankhulo

 8. M’mene dziko la Malawi lafikirapa munthu wina wa nzeru mkumasangala kuti zinthu zikuyenda bwino? A Malawi, tidalakwanji? Dziko latha apa ndipo latsala nsanza zokha-zokha. Magetsi ndi chinthu chofunikira zedi mu dziko. No electricity, No development

 9. Big up Dr Chakwera , we should stop clapping hands on stupid excuses. Malawi belongs to us all not to these princes and princess of thieves. They always bring the bill in Parliament that is in their interest , they don’t even care about the future of this nation.

  1. So if he choose to walk out of parliament will it change anything?….. the sessions will continue…. we as a nation can’t rush to make a decision like that….. ask yourself how many Malawians know what 50+1 is.. the challenges… people need to be educated first…. kupewa pa mawa…. zisankho zomwe timadalira ndalama zopempha zomwezi….
   It’s a good development yes… but needs time

 10. Muntha kulankhulana mmene mungalankhulire but chimene achita Dr Lazarus chakwera is good because nthawiyoseyi zaka zonsezi otsutsa amangowombera mmanja ndi zopusa zomwe what is that? Pitilizani Dr Lazarus chakwera anthu wa adziwe ndale

 11. zachabechabe zithu zosezi zongosautsa mtima atelo mlaliki musazitsatile just focus onto Jesus son of living God yemwe akut idzan kwaine nonse olema ndiothodwa sezani goli langa lomwe silolelemela koma lopepuka munthu amakhumudwitsa bt Jesus Will never ever dissapointed you,we ar in last dyz guyz let us repent our sins zotukwananazi sizabwino be holly as de one who creat us iz holly

 12. Chitsiru chosapola pa mchombo,, uzalamula dziko la ambwiyako.
  Utsiru wa zitsiru zadziko lino they think this bill will remove Dpp and APM from power Only.. This will come to stay, and will even kill all other parties because expect coalitions after coalitions.

  mcp will never rule this country,
  foolish pac, foolish catholic priest, amsembe ake ati angobala ana mmidzimu, zopepera basi,,

 13. mr chasika mwayamba mantha mumaona ngati ndi za mmbale pelekanipelekani izi ndi zandale zimafuna anthu olimba mitima. osati ngati azimayi ngati inu ai

 14. Thanks to Dr.momoh who saved and cured me from hepatitis B.. virus.with his herb medicine you can also reached him for similar issue on…you can add him on WhatsApp +2349068579672

 15. Some people like to comment because people are commenting. That way he protested showing disagreement. Its part of democracy. Some think protesting is walking in roads with cards. Know your rights than fwe fwe fwe. Even in court you have a right to remain silent. Its a way of protesting. And whatever they discussed the record is he was not with them. Don’t forget its not time of aSamunda. If he criticise the speaker say its disrespecting the President. This is not time for yes yes bwana. At least he protested in a peaceful way. One day you will remember him. Instead of discussing important issues. They want to talk unnecessary things. Why they don’t want to talk about it? That reason is the one cause Chakwera to walk away. I salute him like it or not

 16. Amalawi opusa mukufusa chitukuko chomwe wapanga Chakwera osafusa chomwe wapanga namachende pitara wanuyo bwanji nyini za amanu

 17. Tembo Jzu Sanapangepo Zimene Akuchita Bakha Uyu Mukuti Chakwerayu!Mpaka Kutuluka Mu Parliament Kamba Kankhani Yopusayi?Munthu Ameneyu Atakhala Mtsogoleri Wadziko Lino Zinthu Zidzafika Pati?Munthuyu Simunthu Wabwino Waonetseratu!

 18. manwatu sizikuwayendela analakwisa kusiya zamulungu mkujoina ndale petro atasiyana ndiyesu mkubweleramso kokasoza plibe chimayenda yohane 21-3 ndiye auzeni aganize mofasa kupambana kwa ma MP aMCP siachakwera ma mp amakhala ku maconstituency anthu akwao amawadziwa na achakwelawo kukula kwake mtima kumeneku angasogolere mitundu ya mmalawi Idont believe mkuona anasiya za ambuye amakanganila chopeleka ndi asogoleri ndiye afuna kundale azikabako chenjela nayeni ameneyo he is not there to lead people but to encourage cashgate scandle beware of him.

 19. Politics needs mature pipo not makanda ngati ochina ochakwera,mpaka leader opposition ndiamene alimalingaliro olamula dxiko lino kufika ponyanyala aaaaah awa tikawaninkha mpandowu adzatinyanyalanso very childish

 20. hahaha leader of opposition? aphunzire kwa achina Malema akupanga fight until justice prevail osati za chakwela alibe nzeru

 21. Ndiwamwano basi akhaula sangakhale president
  Boma limafunika kufotokoza osati masanje amenewo akuona ngati anthu ndiopusa tikuona.

 22. Yes, Malawi is in a bad shape and a leadership refresh is long past due coupled with these reforms which are needed post haste, but Chakwera is not the answer. That man cannot be trusted. A Chakwera presidency would be the worse thing to ever happen to our country.

 23. Kkkkkk abusaaaaaa ndichani kod? Kapena munalandila call kwa akazi anu kut kunja kuli ziii mukabenso madzi kkkkkkkk i dont havb much to say about chatsika i think he must join wandale at zomba

 24. Sanalakwitse ndi boma la bwampini akamba chiyani chanzeru naye,magetsi on and off,katundu kudula,simalawinso amene ndi mamudziwa,bwanji osangofa basi tione zina

  1. Uyambe iweyo kufa,we all malawians osamafika pofunira imfa zako,kunjaku kuli Mulungu amene amasunga mpweya wawina aliyense osamatero bale amene ukuona ngati adzapanga zabwinoyo ukhoza kudzakhumudwa naye

 25. In a standoff like this between the so called PAC and the government the best what PAC could have done was to challenge the government to call for a referendum if it feels that this is what people in Malawi want. This us what PAC in 1992 did to challenge Dr Banda. Vuto lomachita zinthu muli ndi munthu mmaganizo ndi limenelo

 26. Ndiye mwati abusawa ananyayala paka kutuluka chifukwa ma MPs amawazuzula chifukwa chokuba madzi kwa zaka zingapo ? inetu chizuguchi sindinachimve . or he want to be like Julius malema ? zikanakhala kuti ndi Ku football ndiye kuti Mr chakwela akuyenela kubwelela Ku division because he is not well qualified to be President and still poor minded and to say de fact this issue singamupangise muthu kuti atuluke. and to come out of the house isn’t a substitute to solve this problem so called 50+1. anyway palibe vuto pakuti ukayenda ndi mwana ndi chimozi mozi kuyenda wenkha.

 27. Kodi a Chakwera akuganiza kuti azalamula dziko lino. Akuzinamiza munthu onyanyala angamuvotere ndani ndipo ife Kuno ku South sitingavotere Chakwera azingozitaisa Nthawi yake pachabe.

 28. Kkkk komanso awa kuchoka ku meneko kupita ku chibwezi chisilu cha munthu so ndi phindu lanji lomwe walipeza shame on u

 29. Koma zowona DPP boma likukutererani lili mmanja mwanu chifukwa cha makani ngati ofula agalu. Kulibe wanzeru Ku DPP? Who can advice bwana to do the will of Malawians

 30. Izi zimachitika mumaiko ambili ndipo inu amene mukungoyakhula apa simukuziwa chifukwa chake watuluka muzivesa khani musanayike ndamanga sizonse zomwe amakambilana ndizothandiza anthu ayi

 31. I was saying that new Mcp carries the dna of old mcp, what has happened now? M’busa uyu sangatumikile dziko wachepa nazo,even the Bible says “a person who does not control his anger is like a fortless city, ndiye mwamuwona mtsogoleri wanuyi za malemu a chakuamba izi

 32. komaso2 achakwera sakupeleka chilimbikitso.. aaaa simagulu aka cash gate awa akalowa muboma??? hahaha ndalama zochepa zija zidzabedwaso ndithu… how can tis man behaving like achild chonchi full of pompus, selfish ndizina zambiri ine apa nde bolaso mugabe ndithu

 33. This man

  Its now too much
  Enough of chakwera chakwera thing
  Is he Jesus or what

  I don’t trust him.he should be a dictator in making, the way he take Malawi as if every one is in his control but he is yet to be the nation president ,so if he becomes one , how will he be?????
  My #opinion

  1. What makes you think that Chakwera is the hope for Malawi? As a reader of Opposition chaphindu chomwe wachita ndi chiyani chomwe ungatose? In his Constituance ndi Chitukuko chanji chomwe CHAKWELA wachita?

  2. If you are DPP just remain so. Don’t force others to follow you to your zikwanje party. Chakwera is in opposition and a leader yes, what has your papa who is in government now done?

  3. Juma wa mpokosa jr,funso lomwe wafusa rodrick kapasule ine ndlimvetsa koma iwe wangoyakha usanalimvetse ndikuliwerenga.akufusa kuti kudera lake ndichitukuko chanji wapanga? Ndie iwe ukuyakha ngati kuti ofusayu wafusa as if chakwera is a president.muzionetsetsa ndikumayakhano bwino kk

  4. Brothers kipa,ine siwa chipani cha blue koma ndizomwe chakwera akuonetsa panopa pple yayamba kuganiza kwambiri kuti 2019 akazawina azatisungadi,sitizampanga criticise atalephera nae kupanga zina zomwe akuzinena panozi zomwe zikutipangitsa kuti timukondezi?titha kumaoneka ngati a mcp tilipo ambiri koma zamumtima tisakuziwana

  5. Apapa zikuonesa kuti omwe akuti chakwera is our last hope
   Alibe ma options hence they see chakwera as the only possible candidate who can take Malawi to another level not that they are confident he can do so but because they are out of options.

   Am not a DPP fan but I see what is happening.

  6. Rachel Bema,iwe siungachione coz moyo wako ndiotsutsa basi,koma ena akuchiona chitukukocho,zilipodi zina zomwe sakukwanitsa sindikukana koma nayeso ndimunthu amene sangakhoze chinachilichonse coz iye si Mulungu,as i said b4 am not a dpp cardet koma chachikulu ndinachiona kumalawi kuno ndichakuti,timayakhula zithu ngati kuti malo omwe tikuwanyozawo tinakhalapo ndikuona mene zithu zimayendedwetsera(moyo wa nsanje basi )limbikirani mukalowe mundale mukakhale president tione ngati mawa sitizakutukwanani kamba kakulephera kwanu kuyendetsa dziko

  7. Siine wa DPP komanso nane chitukukocho ndikuchiona munthu ndani angakhonze dziko pa zaka5? More over adapeza mavuto a cash gate kuti alongosole mukuona kuti ndalama akadadzitenga kuti? Mpatseni mpata munthu zomukokakoka chepetsani musiyeni munthuyu nayenso ndi munthu inde amalakwitsa zina munthu sakhala 100% nanunso a mipingo awuzeni anthu za kubweranso kwa mpulumutsi wathu YESU mkhristu osati zimene mwayambazo mwanva!

 34. Ochakwerawo soonadye ndiye onakumbukira mkute osati othawa,kkkk munthu wamphongo anzanga samanyanyala nkhani,amakhala pomwepo, kukambirana zimatha(lucius banda on repeat).

  1. Ochakwera siozatheka dala,kkk komatu okuti okufuna mpando ononawu 2019 ndi kunyanyala nyanyala oli kuchitaku kaya ozalimba kaya.

  2. Mmmmm ibra ndizabwino zimene wachita chakwerayo kodi dpp ikuopa chiani kubweretsa bilu imenei.ndizofunika kukambirana ndikuwaphunzitsa anthu ubwino wake wabilu imenei.ine ngati wachigawo chapakati sitilora kutiberanso tione zina bg

 35. Good Mr Chakwera I Was On Hunger Strike I Did Not Want Munthu Wotukwana Komanso Wa Usilu Mu Nyumba Ya Malamulo.Its Time For Me To Eat.Just Know That Ukazawina Ndi 38% Tizavotaso Kaya Kazakhala Katatu

  1. A SOTHINI Banda ndi imeneyi timanena ija”MCP cannot be trusted, this new Mcp carries dna of old mcp “inuyo nkumati ineyo ndizimvere chisoni, look at honourable Chakwela’s guesture resembles to Late chakuamba, ndale za pa malawi its part of our blood from makolo athu adali ma diehards to this brutal Mcp mpaka anadzitaya, ndikupatse clue ina, “Catholic letter yowerengedwa ndi bwana vp,there is amotive behind mchifukwa mukuwona CCAP n Anglican adzizimuka kodi kunjaku kuli izinso ie political science yayaka kuti buu

  2. Chakwera leaving the house i see no problem because we all know a dpp safuna kumva za anzawo. If i was him i would leave too because it was a waste of time participating with those who dont wana get help. If you fight with a fool you also become a fool so i salute mr chikwara on his good decision. And that has nothing to do with old politics, thats history . Learn to appreciate good things for once. Anyway you think peter munthalika is fit , that’s how you view things at your own prospective way and i view mr chakwera in my own way too. Za chilima trust me ulibe umboni. Your only assuming things

  1. Wisdom will tell you that not all battles are worthy your struggle. Select your battles wisely. Ask King David he wud have ended on a sad note after he went back to finish off the remnants of Goliath family.

Comments are closed.