A 57-year-old man has died after drinking locally brewed beer called Kachasu without taking food.
The deceased Macford Matemba is reported to have drunk Kachasu at Manyenga village in Nkhotakota and he was later found dead at a house.
Confirming the incident to Malawi24, Nkhunga Police Spokesperson Ignatius Esau in Nkhotakota district said Matemba was taken to hospital where post-mortem revealed that death was due to low sugar.
Esau has since appealed to community members to desist from drinking beer without food in their stomach.
Kachasu is one of the local beers with highest alcohol percentage.
Matemba was from Chimbudzi village, Traditional Authority (TA) Wimbe in Kasungu district.
Heavy dose… big surprise.. kkk
RIP
Eat & drink. .dats de only rule to drunkards
Waku chipinda umafuna kudyera
Kkkkkkkkkk
wafa ndi njala osati mowa
Wafa ndi njala not bedroom iyaa!!
True man , Wafa ndi njara
Sinyaupe zithuzi
Kkkkkkkkkk tisanamwe timaphika kaye chakulamba
Kkkkkkkkkkkk amango thila basi kuti rambaaaaaaaaaa
Mwalo mwa nsima iye anadya nyaupe then hedeck kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkk amawona ngati nfata eti
Imeneneyo Ndiye Mphoto Yake Ya Uchimo Pakut Mphoto Ya Uchimo Ndiyo Imfa. Kwake Kwatha Kwasala Kwa Ife Tisinthe.
musaipise mbiri yabwino ya mowa,,munthuyo wafa ndi njala
Congratulations!
wachita bwino
Wautsi timadyera makosana pliz…
olembanununso tamalemban zomveka musatiyipitsile chakumwa chathu kachaso siipha munthu ine ndimamwa tsiku lililonse bwanji asakundipha mfufuzen ameney mwina njala ndiyomwe yamudabula osat kachaso dele mulekeletu osadzalembans zimenez mukapitiliza ndikausumilan kukhoti
nde kut kachasu ndiwabwinotu? nanga munthu kumalira nd 57yrs that’s mean akhala akumwa mowa 4 long tym pamene timasprit ta ma factory munthu umafa short tym
Timadyela kaye wapakhuniwo kkkkk sorry
So sad.
Kkkkkkk mwambo wa kachasu ndiwomwewo ukamwa osadya ndi yimfa bax. Ukadya b4 no die asaaaaa RIP man kachasu wapulumka kumwedwa
Vuto razachuma limenero mowa wa k100 ungaphe munthu fufuzani bwino.
Its called Ombike here in Namibia. A kind of local, home- distilled Grappa. Most of the time the alcohol content I.e. percentage is not known and it can be deadly!!
Njira zofera nzambiri thawi inangomukwanira mpadepot tangosiyana manyamukidwe RIP
Wafa ndi dilu yabwino bwanji.
Musamuipitsire mbili aaaaaaaaaha
walozedwa ameneyo ife solid-solid pano-mowa supha munthu
Malamulo pa kachasu anaperekedwa kale
ine kachasu ndimamwa daily am strong, ameneyo wafa ndi vuto lake not kachasu, kachasu sapha mufufuze there is no poison in that beer
Kachasu mmene Akomelamu Ndemukuti Wapita Nditchaso Ndakayika Ndithu, Chilipo Chomwe Chinamuchitikila Osatikachaso
Munthu wafa chifukwa sanadye nsima , eee zowipsya man
Government please anthu akutha bwanji kungoletsa kufuula mowa umenewo
wafa ndi njala amaneyo….
Mowa siwoutumbwila bolani ife sitimwafe tilibe pulobulem. Kaya kazimwani muzifa nawo. Mapeto akeso wakumoto
Moti Amene Amwalira Lero Kumudzi Kwanu Amwalira Ndi kachaso?Ok Ukapulumuke Iweo Opanda Tchimowe
Uzaziona. Wakula watha Sukudziwa kt mowa. Ndiwamachimo Zako izo uziona
Abinto koma mahule et?
Ha Ha Ha Ha Ha Ha. Ife koma kuswali madala zapadziko lapasi sitimadzitsata Zazinjoy ife. Njeeeee. Madala #Chisomo. Matsiku otsiliza ano
mmm ine ndye ndasiya mowatu
Mmmmmmmmmh anali atadyerela kale uyo….
kuputsa zinazi si ngozi koma kupepera.Ieo samaziwa kuti kumwa kachaso osadyera koopsa
yakwana yakwana palije kuthawa
Asaipitse mbili ya kachasu ameneu wafa ndi njala.
Asaipitse mbili ya kachasu ameneu wafa ndi njala.
kujoga kulima uyu!
Think twice b4 before you drink too much
Kkkkkkkkkk koma Malawi akanapezeka munthu akanaligula pangongole dzikoli basi mpaka pamenepo hhhhhhhhhhhhkkkkkkkkkkwwwwwwwwwwmmmmmmmmmmlllllllllllll
Wazipanga embalm ,RIP
Kachasu ndi mo
Anamwa mutu uyu!! RIP!!
kachasu mmm?Good beer not blam£ %
Wafa Nd Njala uyo zoona iye adzkamwa pelese,zuzen zup wth no food axow asanyazse our locally beer
Bad
Chslu!
Kafike….
Rip monga mwachkhalidwe koma mmmm
57 years is evin better.my parents died before that age.dont worry so much.
(Y)
Kachasu is not a beer. Its a spirit.
Sanadye poyamba kumwa.
wakumoto
Wapita atakhutha
Ok he must rest in peaces
Probably the best beer in malawi
In water there z bacteria, in kachasu there z wisdom,….anthu akafa ndi njala osamanamizila the swt drink #kachasu de legendary drink
The beer of the year (2017)
Nthawi yake inakwana ameneyo musanamizire kachaso
hey!! dont blame my cultural beer(kachasu), time for this old man to come out of the world came when he was at drinking joint,NOTE:kachasu doesnt kill
Kkkkkkkkk kuwuteteza tsopano big
Kkkkkkkkkk koma big man waitha
Anzanga acha kumwa tiyeni tiziyesetsa kudya kenakake tisanayambe kumwa.
he dies of hunger not kachasu
Probably the best beer in the world
only the fittest survives
Kkkkkk kuukondesesa mowa mpaka kusowa time yakudya shame kachaso brewers kumaphikila nsima ma customer look now you have loose good customer not good
Vuto la magetsi kuzimazima sanaphike magatsi anathima.
Kachasu is not brewed but distilled and as such is a very strong spirit to drink if unsaturated and on an empty stomach.in most of the times,cheap things are not very pleasant things in life,as we grief the death of our friend,let it be a learning point.RIP.
kachasuyotu osamangomunamizira adzakukanirani
This guy died of hunger
thats the fact,kachasu doesnt kill
Eee.because win and midoli they banned them
Nthawi yakwana not kachasu
Eti kumanamizira kachasu
koma anthu ena anangobadwa mofooka zoona mpaka thiii ndi mowa kapena munaikidwa poison?
Kkkkkkk mowa sumapha munthu osamaipitsa zinthu zabwino mowawo ndiomwe unamusingila moyo kanthawi komwe amamwako
…so even in Malawi it’s Kachasu,Zambia too!
kodi anthu mumalimbana ndi zinthu zopanda ma vitamin bwanji?
Kkk wafa ndi njala osat kachasu . . kufuna kuyipisa Mowa uku
kuma ka mpalamula dzupe usanadye result yake ndimeneo butR.I.P tikusowa padziko pano
Mmm ndisaname kuno kwathu Ku Malawi, anthu achikulire taluza nawo mmmm…whats wrong with old people in this country? I never got it.
zoziyamba dala
Thats part of ignorance, pita ndi mtendele wako m’bale! RIP
wafa ndi njala ameneyu mbuzi inu!!!!!