Three bodies of people that were found in Bunda forest last month have been identified, Malawi24 can report.
The bodies are said to have been of headmaster from Monga Primary School in Rumphi district Dalious Chawinga aged 42, his wife Queen Zgambo and a 5 year-old daughter Olipa Chawinga.
According to Lilongwe Police Spokesperson Kingsley Dandaula, the family left Rumphi for Lilongwe where they had planned to buy a family car on 9th April.
A relation to the family Mabvuto Chilembo said the family told their relatives that they had succeeded in buying the car and they were registering it at Road Traffic.
Reports suggests that car sellers might have had a hand in the brutal murder of the three.
The three are to be buried at Chilundika village, Traditional Authority (TA) Chikulamayembe in Rumphi.
R I P once again, eish.
very bad,mizimu yawo iunse my mtendere anafa imfa yowawa anthu awa kufa family yonse? kumfa ngati ziweto? Mulungu odziwa kutothonza mwini zifundo Tonthozani banja lotsalali In the name of Jesus Ame.
Kulengesyana uli sono
yapezeka kuti ,inali ndi ndani?
Buying vehicle in Malawi is it something major in life or what l wonder why u killing each other coz somebody buy himself or herself vehicle…Shame poor Malawi..and its people.
Pepani Malawi .mwinatu ndi chimanga chomwe tikudyachi chimene akugawa kuchokela kwa Bushilichi ndiye akufuna abwezelese pomwe akuchosa.Eashiiiii.
but what can someone do such things to murder the entire family please God
so sad.mtsriep
RIP
Wow!!
Ndinu nomwe anthu akumalawi omwe mumati osamapha mbava.koma taonani kodi zidachitika apa ndi umunthu? zovetsa chisoni.anthu kuwadula makosi ngati nkhuku.adalakwa chani?NDE MUTAMABAKILA MBAVA. KODI UBWINO WAMBAVA NDI UT?
Apolice akumalawi saziwa ntchito yawo, koma kumwa midoli ndichomwe iwo amaziwa osati kufufuza nkhani ngati izi• wash out malawian police!!
Since the bodies have been identified now the remaining task is with the police to catch the culprits. And i am sure that our police is very competent that it will not take long to bring the culprits to book .Things like analysing the call log of the deceased may give the clue to apprehend the culprits.
If there is justice in Malawi thi case its easy to solve and i pray justice to previal: The culpuit is the vehicle seller cn be traced in seconds!! REST IN PEACE THE Zgambo’s
Ndiye mkumati kumalawi kuli chitetezo ??
Me no comments
Very bad kweni RIP
Anthu okhakhala mtima
These evil, satanic murderers will be caught, mwazi wa munthu supita pachabe!
Mmmmmmm koma Malawian why zithu ngati zimenezi xikupitilirabe
Malawi is becoming a dangerous country. This is Satanism and witchcraft. God forbid. Evil people God will punish you.
ndi chifukwa chale ife a mob justince of malawi (mojuoma) timalimbikitsa kut anthu otelewa akagwidwa nawoso aphedwe.
Mitu ya,anthu amenewa akuti yapezeka lero ku ntchisi! Malawi Wanga..ukupita kuti??
So the bodies were taken all the way from Rumphi and dumped in Bunda or they met the fate there?
Killing the whole family just bcoz ov cash, mmmmm Lord hav mercy. Let the robbers b punished by God while alive aumve moyo kuwawa
Ma let’s do business amenewa munthu kukugulisa chinthu kukufwambaso
Muzitambasura nkhani kti aliyense aztha kumvesa
Very sad May Their Souls Rest In Peace
Komano a #Malawi24_Za _Link_Zanuzi_ayi_zikution ongera_nthawi
Makobili Akuvuta.
Malawi Wanunkha Mpaka Banja Lonse Sad News Koma A Componyo Mmmmmm :> ?
But why a Malawi???
R i p
There’s evil amoung us,May good Lord strength Chawinga’s familly to bear the great pain..
Ine palibe chomwe ndanva ndingoti Rip poti ndaona magaziwo
Hmhmhmhmmm
Sad Malawi ukupita kuti iwe
My Primary Teacher and friend of my family, Why all this to you. And the problem is a Buying a Car? why Malawians? LORD HAVE MERCY ON US
My Primary Teacher and friend of my family, Why all this to you. And the problem is a Buying a Car? why Malawians? LORD HAVE MERCY ON US
Very bad
So sad
Why all this to my primary teacher#DaliousChawinga tell me what exactly hapened to them?
Shame my Malawi
VERY DISTURBING…HAPPY FAMILY TRAVELLING TO FULFILL THEIR DREAM,AND NOW THIS??
when someone standup and say plizz improve security in malawi some will say ndiwa opposition. shame on malawi
BUT WHY
Koma Malawi waopsa,rip
Malawi where are we heading to? Progressing or retrogressing?
Azilangidwa within villages
May God…hv mercy hmmmm
Malawi24 plz write grametical english bodies are said?what kind of this english is?
NDICHANI AMALAWI? Mtunduwathu wukupitakuti? Mizimuyawo yiwuse mumutendela
In a Land where Faith Leaders nolonger exist & the entire environment becomes all of wild Beasts who prey on each other. A once very PEACEFUL Nation is now the Devil’s stronghold all in the name of Democracy & Human Rights. (making evil look & sound pleasant).
Ambuye yehova amaona zonse bwino lomwe ndiye sikuchenjera kumaononga miyoyo ya anthu motere mkwiyo wa yehova uwalange mwapaderadera ochita nkhaza onse amen
Its very unfortunate and sad hearing about this news , The government of Malawi should look into this so that justice must prevail, Make sure these satans,monsters/beasts are brought to book
R I P,
kwa omwe sakumvetsa,,,
nkhaniyi inalembedwapo masiku apitawo,,apa ikungopitilizidwa,,
apolisi adapeza mitembo itatu mu nkhalango ya Bunda ku Lilongwe, koma samadziwika kuti ndi matupi andani,,,,,,
ndiye apa zadziwika kuti anthuwo ndi aku Rumpi,,,,,,
anaphedwa ku Lilongwe komwe amakagula galimoto,,,
,,,,,,,,,,,,,,,zikomo,,,,,,,
TOO Bad.
Where did you do your journalism studies you Malawi 24 journalists? just close this page if u think you are not ready to write well cooked stories! Ndakwiya
Follow the link
Please try to arrest those mother fuckers
Very Sad,,,read this Augustine Kakowa
Zomvetsa chisoni
Malawi 24 be serious in ya writing!! The whole country is reading this!!!
Muphuzire kuremba zoti anthu aziva kapena mumarota kuzorowera kurenba zandare mkhani simukuyidziwa mwaremba kale kupusa eti
Tiuzeni tiziwe
NENAN BWANA TIMVE NAWO
Anthuo anaphedwa mu mkharanga ya bunda koma mitu anaribe nde panopa adziwika kuti ndi a hedi akumpoto ndi akazao komaso mwana nde awawa anaremba ngati zachitika dzuro
Vry bad! Rest in peace Mr Dalious & ur familly
Vry bad! Rest in peace Mr Dalious & ur familly
My brother my brother
Why,may my living GOD have a part on this…..RIP
very sad..amfa imfa yowawa mpaka kuzinga ngati nkhuku?eshii bola akanangolanda ndalamazo kuwasiyira moyo..moyo ndi waulele kwa wina aliyense
The pple who did this act will heavily be punished by God.
Very disturbing news!!!!
The three beheaded bodies who were found in Bunda forest have finally been identified as a 43 year old Mr. Chawinga of chiundika village in Rumphi, a headmaster of a school, his wife and their 5 year old daughter.
The three left Rumphi for Lilongwe to purchase a family car on 9th April. After successfully purchasing the vehicle, they informed their relations that they are processing registration at road traffic directorate. Little did they know that, that was the last communication. The bodies have been identified at Kamuzu central mogue yesterday.
The vehicle in question is still not yet known. It seems the vehicle sellers have a hand in the ordeal.
Anthu ena amarimbikira kuremba zinthu kuti anthu ave koma kukanika kufotokoza moveka bwino big inuo nde mwafotokoza moveka bwino enawa afotokoza ngati zachitika dzuro akujambura mnyumba koma zinachitikira kumkharango
good narration
i would love George to work with my Radio;DVC RADIO!! kkkk !!!malawi 24 eiiish!!so far very sad
Thanks for your collection. Keep it up.
Now I get the point
Thanks bro,ife za ma link sitimazitha.
Nkhani ndi link apa ambiri simukuitsegula George wangotenga zomwe Malawi 24 yalemba sanasithepo kathu then your thanking him for narration ???? instead thanking him for sharing you what is in the link.
Komaso Times Tv Ananenadi Zimezi! U Ar Right! Rest In Peace!
Follow the link the story yalembedwa ku website not face book
Adziwapo kanthu ogulisayo I think
Komad athuwa zikükhala ngat ãmakagula galimoto koma anapangidwa chipongwe kmabé mulungu walowéreLa kale pa nkhaniyi achitapö ka2
Matter Of Fact Dont Even Give Us These News At All Unless U Gv ABrief Story And Not Summary
Be active man, i can’t blame u bcz u like kumvera mbc radio. Tamaveraniko ma radio enawa simuoneka opusa ai mdzamva zambiri za dziko lanu big man.
Ait Ok
Here in Malawi usually we r killing each other for success ,pempho ndiloti wakupha nzake aziphedwa kuti mwina mchitidwe onunkhawu utheletu,munthu sungagwile ntchito molimbika kuti ulandile mphoto ya imfa,kumpha banja lonse?alandile mphoto ya uchimo awo akumphawo komanso ngati anali ogulitsa galimotoyo nde kuti sanali yenkha (just thought ) mwana waphedwayo sitikuziwa kuti mawa lake lidali lotani komanso makolo akewo amathandiza achibale powalipilira school fees ndizina zotero mmene zatelomo zasokoneza tsogolo la anthu ambiri chifukwa nawonso amene amathandizidwa ndi banjali pa mawa adamathandizanso anthu ena,ndi chain chothandizana nde mkuwapha? Pemphero ambuye Mulungu wathu wamoyo mukathe kutionetsela anthu amtunduwu poti alipo ambiri koma patokha sitingathe, kalandileni mizimu ya abale athuwa ndikwakhululukila pa zomwe adalakwa ndi kwapasa moyo osatha chifukwa mwainu muli chilichonse khalani ndikuthekela kowatonthoza anamfedwa chifukwa samayembekela kuti zitha kutelo (AMEN)
Amen!!
Amen
Amen amen
Amen bra
Dziko lapansi liri manja mwa oipayo
Ameen
Fact
Agree
Shame
eee RIP
No Where To Run,may The Good Lord Who Cursed Cain Lead In The Capturing Of These Barbarians. Lord Hear Us!
Perpetrators must be dealt with communities not police.lmean burn them alive.we dont want to stay with animals in our peaceful country.
Camera yakumwamba yaunika zonsezi palibeamene izamuphonye imfa
What’s happening ?coz idont get any areal infomation about the story.
Hw many fake information hv u got?
It’s many of them my bro.
Mufuna kunena kuti chani zimene mwalembazo tanenani mu chinyakhuro chathu timve bwino bwino
Kwa mbiri olemba khaniyi sakutiwuza momwe zakhalira momveka bwino.
Kodi chachitika ndi chiyani kwenikweni kuti Banja lonse lichitidwe chipongwe momvetsa chisoni chonchi?
Vuto la free data ndilimenelo there is link when you open it all information is right there.Mmalo mongopepha kuti ena awelengako akuuzeni mukuyakhula mukula mtimanso kuti sizikumveka anga mwawelenga nkhani yonse.?????
Eeee!zoona zimachitika! Thanks.
Ndiye yake man ??? zamacheza izi
Good night and be blessed.
This family went to Lilongwe to buy their car it’s were they meet robbers cut off their heads in Lilongwe it’s not means these things happen in rumphi no it happen in Lilongwe Rip my former primary school headmaster and ur family we will miss u
Malawi kumvetsa chisoni
pakati pake pati mmesa apeleka link kodi? simukuona kapena?
Sitikuona tilongosoleni
Too bad,killing the whole family,can’t enjoy bloodmoney.
Never. They will suffer like he’ll.
Hell
Last days ppo will kill their fell without mercy,may their souls rest eternal peace.
Which bodies you inexperience writers
2 bad
shaaaa
What wrong did a 5yr-old-daugher commit?What about de mum & dad of de family?Deeply saddened!!!
nkhani kumalemba zoti timve.Kutisiya ndi mafunso mbweeee
Kkkk kkkk!
shaaaaaa
Koma amalawi….
I do not undestand explain plz journos your work is incomplite
Sunamve pati tikuuze??
Nena timve bwino
From Rumphi to Lilongwe? Koma abale….. Sad
Amakagulatu Galimoto ku LL-ko
Kuteroko eti??? Ok
Go well cousin Dalius though in a cruel manner I will always miss your advise
plz malango, may u furnish us with details of wat happened to our dear colleagues. we are also mourning with u. may their souls rest in peace.
Don’t give us bits and pieces of the story. Full story please.
That’s why they provide a link
Open the link and read it
Why people do this to innocent people .?? Only God knows
Malawi why ar u fond of summarizing story?we ar left behind we dont know wat hapned.u say 3 bodies identified.from where?pliz try to giv details
Yap Its A New Story 2u Bt Ths Hapened Last Month Whr By Father,mother & Child Killed By Unknown Pipo,& Bodies Found Wizaut Heads.
Open the link baba that’s prblm of free data.
These ppo went to LL to buy a car and they attacked there chopped their heads off and dump their bodies in Bunda forest.Eiiiiiish so sad!!! May their souls rest eternal peace
Kkkkkkk Alick Kazembe
ok bro.understood.too bad,may their souls rest in peace
Open the link man
I like where the link is already opened, koma data yambiri ndithu.anyway thanks tamva nao
So bad
Kumazisata as concerned citizen anyway añaphedwa anapezéka alibe mitu
Yah sure guyz oti remains bodies anyamulidwa dzulo kupita kumudzi kwao from central i was there, RIP.
l cant say anything bt there is no scret under the sun.. GOD IS WATCHING.. .LAST WORD I JUST SAY……R,I,P
Mmmmmm from Rumphi kuzaponyedwa ku lilongwe Nanga ma roadblock onsewa osagwidwa.
Akuti Anali Ku Lilongwe Amagula Galimoto Afterkugula Anauza Abale Kuti Ali Kolembetsa Zimakalata ,but Mmmmm Malawi Waopsa Pano RIP
What is the bold line of the story
Abaleanga mizimuyanu yiwuse mumutendere tilibe chonena
osamayambila nkhani pakati ngati kuti aliyense akuiziwa kale ayi, kapena tiziti ndi za ku bunda forest?
Tingopitiliza pomwe tidalekeza last month coz zinaimila poti a Police akufufuza ma identification a wanthu omwalilawa.Komabe ndimmene wafotokozela admin munthu omvetsetsa wamva angakhale kuti waiona koyamba nkhaniyi.
Nkhani zanu zidzikhala mwa ukatswiri ndimayesa kuti mumakhala mutamaliza maphunziro? Ikondeni ntchito yanu.
Mmmmmmmm very sad
this is evil
eish!! koma zilombo tikukhala nazo pamozi masiku ano. adalakwa chani anthuwa? zomvesa chisoni ndithu
Kodi nanga okuphawo agwidwa? Ndipo ndibwino kut anthu opangawo, police isiye mmanja mwa community achite nawo
Zoopsa Izi,a Malawi tikungophana ngat nkhuku!!
Nsambi,mizimu yawo iutse mu mtendere
i you mean no more
Eeeeeeeee ndiye Akuganisa chani
So Bad Departure Of The Family,
sorry site ,MSRP
Malawi,,,,,,,,,,,ukupita kuti malawi?. Zoona Mpakana kupha banja lonse!!!!!! Chonena ndilibe mizimu yao iuse muntendere.
mmmmhu zoopsaa
Oooooooh God help!
Sad news
zakhala bwa
Mizimu yawo yiuse mumutendere
mmm
Sad
from neno accident or what
The ones whose bodies were found in bunda forest with no heads.
Ooooo my God
Anavaya Elazi kukagula galimoto ndiye aphedwela kumeneko very sad
eish amayenda ndicash.
Nde frm rumphi kukapezeka ku bunda?