30 August 2016 Last updated at: 1:46 PM

Malawi police arrest 13 over charcoal

Police in Machinga district have arrested 13 people for being found with 145 bags of charcoal.

Machinga police public relations officer Dave Sulumba has confirmed the arrest and identified some of the suspects as 42 year-old Fedson Masale and 26 year-old Alex Maulidi.

Sulumba said on 26 and 27th of August police in the district had a joint operation with the department of forest and game reserve officers in the protected areas surrounding the district with an aim of apprehending charcoal burners.

Charcoal- Malawi“On 26 and 27 August we had a joint operation with the department of forest and game reserve officers in Machinga so as to apprehend charcoal burners in the district and we had a successful operation,” said Sulumba.

Sulumba added that during the operation 13 people were arrested for being found in possession of 145 bags of charcoal worth K147,000. The police seized the charcoal and the bicycles the charcoal burners were using.

“During the operation we arrested 13 suspects, seized 145 bags of charcoal valued at K147,000 and 23 bicycles for the suspects were seized during the operation,” he said.

Meanwhile all the 13 suspects are expected to appear in court soon to answer charges of being found in possession of forest produce which is contrary to section 38 of the Forest Act.

Maulidi hails from Nyamuka village, Traditional Authority Malemia in Zomba whereas Masale hails from Mjale village in the area of Traditional Authority Chamba in the same district of Machinga.179 Comments On "Malawi police arrest 13 over charcoal"

 • ndiwerenga katatu ngati simuwamsula ndikuchotsani ntchito. mwanvaaa

 • Bravo policemen. Any criminology with charcoal?This shows u dont have what to do.Whoever taught u that protection of trees is at charcoal level is as empty as u are.Sorry maningi.U have arrested them fine,how many trees have u protected?Wake up n find something to do with ur uniforms.

 • Apolice akumalawi kuba akamulande munthu makala cholinga chao ndi chan akudiwa kut boma la malawi ndilosauka lilibe presedent kut azithandiza anthu ovutika

 • Dave Tembo says:

  By the law. Not above the laws

 • Tisinthe maganizo chilengedwe nchofunikira.

 • Amalawi ku4ila,mulimbana ndi wamakala mukumusiya opha alubino ndi wa cashgate zopusa bx

 • Bola akawabvale akhale mitengonso

 • kugulitsa makala kugula sopo msonkho wadula nanga vuto ndichani? school ndipa five azanuinalifizi yaana mupeleka? mbuzi za anthu.

 • Ine ndimakhala kundilande ndipo sindingakwanitse kugula magetsi ndipo sindidzasiya kugwiritsa mtchito makala. Nanunso apulezident mukutikhaulitsa ife ogwiritsa ntchito makala chifukwa inuyo chilichonse ndi chaulele, nanunso muzikhoma msokho tione ngati simugula makalao mmene adulira magetsimo wakumudzi angakwanitse?

 • Ndiye azidya chan?

 • tikakudyelani kuti a Mozambique mukulandaso ngati anuu

 • Zachamba basi akakwachani makala omwewo inumukuphikilanso makalaomwwewo mwatengakuti wakumangani ndani

 • Maiko anzathu sagwiritsa ntchito makala akafuna kuphika kapena kuwotha. Izi zili choncho chifukwa adagawa magesi paliponse kuti munthu agwiritse ntchito. Malawi government, yambani mwathetsa umphawi kwa anthu ngati amene akuwotcha makala komanso magesi apezeke m’dziko muno paliponse pamtengo woti mtundu wa a Mw uthe kulipira.
  Taonani vuto la magesi limene lilipo kale,timaunikira nthawi yochepa mwamwayi akayaka pa tsikulo, koma bill ikati ibwere , ndiye ngati unakakwera ndege pangogole # zimandiwawa

 • Chifukwa mitingo ndi ya mulungu koma inu mmazitenga long

 • Mapolice Pena mmalakwa chifukwa munthu sakugwila ntchito ndalama ayipeza bwanji?

 • Koma yaaaaaaaaaa tikadya kuchipatala. Nanga tipange business yanji pa Malawi pano??? Tima freezes ( no electricity) tikapikule mafuta ophikira ku Mozambique ( ndizosaloledwa) tigulitse makala ( kumangidwa) I really feel sorry for common people, kodi akanakhala anduna ajawa Mukanawamanganso???

 • Kuwapezelera amakalawo eti tamachitani manyazi zinazi

 • Mukulephela kumanga mbava zazaza ma taunimu.mukulimbana ndi amphawi zoona???

 • Iya bodza limenelo, munthu sangamangidwe chifukwa chopedzeka ndi makala. Ku Mulanje kuno a MDF akumangowalanda makalawo basi anthuwo osati zowamangazo ayi.

 • Iya bodza limenelo, munthu sangamangidwe chifukwa chopedzeka ndi makala. Ku Mulanje kuno a MDF akumangowalanda makalawo basi anthuwo osati zowamangazo ayi.

 • Madolo alero ndi makape amawa ndawonera Kasambara

 • Madolo alero ndi makape amawa ndawonera Kasambara

 • Eishhhhhhh magetsi mmene akuvutila ku Malawi paliso zomagwilana chifukwa cha makala. Who ever anapanga malamulo amenewo nde bola apeze alternative yoti tiziphikila. Eishhh unbelievable.

 • Eishhhhhhh magetsi mmene akuvutila ku Malawi paliso zomagwilana chifukwa cha makala. Who ever anapanga malamulo amenewo nde bola apeze alternative yoti tiziphikila. Eishhh unbelievable.

 • A police nonse mundimvetsere kodi mukudziwa kuti mutha kufa infa yowawa mukudziwa? Apolice nonse ndinu zitsilu mukundimva koma pachakuti panu pamamu agalu opanda mnzeru inu . tsono makalawo mukulandawo mukupita nawo kuti? Tandiyankhani inu ndiye akapolo adzikolino bwanji mumakana chilingamo ngatitu uliunphawi ukuphani tidzitsilu tawanthu . muwamasule anthuwo nsanga fack you a police nonse inu zoona mokuti muzigwila zigawenga zokuba ndalama m’boma koma kulimbana ndiyamakala pathako panu a police kkkk ngati zakuwawani ndipezeni ndikutibuleni nonse agalu. Guys musawanyengerere mbuzi zawanthuzi .

 • Dats y i hate to be a police man…..em a stabon…aaaaaah nanga ndili ndi thumba lamakaka mnyumba nkamangenso munthu ali ndimakala thumba limodzi…..apolice olo chowona Akuchiziwa amachitabe zofoira…..f**k….

 • Kulimbana ndi kumanga ndi anthu owotcha makala mudzango peza thembelelo chabe. mukusiya zigawenga zikuba ndalama m’bomamo zachamba basi. muwamasule amenewo alibe mulandu

 • Bob Maseko says:

  alot has been said that arresting these is not a solution…just do the necessary thing and the problem will arrest itself

 • mmmmm police kuba basi…mungakwanise cooker or even hotplat inu….mumadalila makala nanuso iya…..

 • Akuyesela kupanga ma bizness kuti ana apite ku xul mukaponya mundende pofuna kusamala banja lao osawathandiza bwanji anthu achuma kupondeleza aphawi

 • Are you looking for a sugarmum whatsApp an Agent on +265996912464

 • Stupid amhawi akakudyereni kuti?.

 • Hello my name is john I want to give a testimony about my HIV virus that was cured by a great spell caster. Since last 4years I have being a HIV AID patient. I never think I will live long again and am so grateful to Dr sule who help me cured my HIV AIDS last 3 weeks. I was in a great pain so I told one of my best friends; he told me that there is a great spell caster that can cure my VIRUS. I asked him if he had his contact, he gave me his contactl, I contacted him he talked to me and he perform the necessary things and sent it to me through corrier delivery company and deliverd to me at my place and he told me that after two weeks I should go for a test. Which I did, when the doctor told me that am now a HIV negative I couldn’t believe myself I went to see another doctor the result was still the same, I was human on planet earth, so I emailed him and thanked him. Please if you are having a similar problem please visit him/contact him via whatsapp +2348162447651

 • Tisu Stima says:

  My question goes like this ndie makalawo apita kut r u going to change it back to be trees again.. this is nonsense… magesi ake awa ozimazimawa komaxo kuba kwachuluka zedi apa

 • Nanga a policewo amaphikila magetsi kapena? Awa amangotsogolera owotchawo koma tonse amene timaphikila pa mbaula yamakala, including awa a police tikuwotcha nawo makalawa! What other options do we have?Malawi sazatheka!

 • Aaaah you police be honest sometimes. Do you mean that police never use charcoal in your houses? Are you telling us that your job never uses charcoal? Police be serious sometimes, do you people work with enthusiasm? Why don’t you enforce your laws to those displaying thousands of bags of charcoal along Zalewa road and other charcoalized districts in malawi? Aaaaaah police be serious sometimes. Nde makala mwagwirawo mutani nawo? Muotchanso monga muchitira fodya wa Chamba?

 • Restrictions without alternatives will achieve nothing,make electricity affordable please

 • Apolice ndinu agalu a anthu bwanji osamagwila anthu amene akuba ndarama zaboma mukulimbana ndi anthu akuti nawoso akufuna kuthandiza mabanja awo,ukachokaso kumene uliko ukapeza hule lako lija lakuphikila pamakala mbolo za manu nose apolice

 • Apolice masukwano mukumasowa zomanga ait????

 • Ndiye Tikakudyeran Kutiko??

 • Kare mudayamba kulanda makara koma kotaya sikuwoneka , anthuwo ali ndi ana ,komanso mabanja zowona avutike chifukwa chainuyo mitengoyo adambzara ndagogo anu

 • afunileni ntchito anthuo kuti aleke kuotcha makala zapamtumbo basi komaso mukachoka apo mukupita makwanu mukuotha mbaula zamakala

 • Apolis Nonse Ndinu Mbuzi Ngat Simukumvetsetsa Link Me Thru This amonsilu55.gmail.com

 • Kumalawi hehehehe kungoyesa kugulisa chamba mmmmm akukumanga Nde makala zinthu zosadibwa ngati izo komanso zopserera why don’t you give them back heeee!?

 • Chimanga ndi 15000 mukufuna anthu azibaa

 • I have seen truck loads of charcoal being shipped to Malawi from Mozambique daily. I do not see any problem of troubling your people there

 • Mthwalo ndi deal

 • Inde apolice mwagwila tchito yanu,,, fuso ndilot ndemukuganiza kut athuwo angasiye ku wotcha makalawo???chabwino mukalanda makalawo mumapitanawo kut???

 • Release them,,, what else do u want pipo to do with these black outs?

 • Mumati anthu akabe. ?????? Asiyeni.

 • bomboclat police zakumalawi otimuzikagwila mbala zopha alubino mulimbana ndimumthu ozigwilila ntchito apa

 • Nice work however we are waiting to hear that ur have destroyed them as you did with the ivory.Osalanda ndicholinga choti muzikaphikira.

 • Nde mukupindulapo chani mukamatero?za ziiiiii agalu okha okha osowa zochita

 • pali chowamangira pamenepo?Inc mumaphikira chani?n mukawalanda mumapita nawo kuti?muwamasule ak agulitse okha

 • Charcoal burners share a 50-50 blame with Timber on deforestation but very unfortunate for the charcoal burners that they don’t contribute to the Forestry Officers personal shortfalls & that’s why they fall prey. Legal or illegal cutting down of trees have the same effect on the climate cos seedlings can not replace fully grown trees. It’s time Malawi started importing wood products & that’s if the ministry responsible & ourselves are really serious on adressing the devastating effects of climate change.

 • Zitsilu inu mwasowa chochita eeti?

 • Apolice nd a Army amaphikra makala asamanameze anthu

 • Kkkkk akuti pamenepo ndiye ntchito yagwiridwa koma odula ziwalo za wanthu aja awadusa pomwepo.zizeee zili chaka chino nza tonse

 • Apolice muziona zomanga zake, nanga makala ndizithu zot muthu akagone ku ndende ? Simumava chisoni? Muthu akhale pabwino angamaonche makala mkumagulitsa? Mutavala zigoba ngati athu ovina ben choncho

 • Awotche makala walakwa atsekure Store mukamuberxo kumuwombera ndfuti zanuzo munthu akat akat akabe walakwaxo nde chomwe mukufuna ndchan ndipo tzikhala motani???

 • Galu wanena kuti amangidwe

 • Musatichimwitse agalu inu

 • Osauka, asaukiletu bas

 • Arest them because there nt hlping the counrty

 • Eeee makalaso ndi mulandu kodi? Is malawi a country or a village? Kadziko kotembelelleka aka

 • NONSE A POLICE MITU YANU AGALU OVALA ZOLANDILA INU CHOMWE TICHITE WA POLICE AKAPEZEKA MALO ALIWONSE ALI YEKHA KAPENA AWIRI APHEDWE KAYA KUCHIPATALA KUMOWA KUMALIRO PAUKWATI PENA PALI PONSE.BWANJI NGAT ASOWA NTCHITO AKAIPUTEJ #JANJAWID KU DAFU KAPENA #BOKOHARAMU KU NIGERIA

 • Apolice mukugwira anthuwo inu muli ndi ma hotplate?koma pamalawi,anthuwo ndi osauka,mukuti aziba?ndakwiya nanu apolice,

 • people in Malawi are selling charcoal due to poverty , hanger and no job creation .If you don’t have brother in police, army,heathy, education and other posts, have no opportunity.Infact : oppression, corruption is in climax in Malawi. Everyday , the policemen are standing on the road robbing the people. Who arrest them? Watch out ! The gangsters are coming soon to kill the mocking birds.Ameen

 • kumanga owotcha makala kusiya adaba 577 billion kwacha aja? komatu MULUNGU akuona zosezi

 • Komaso even a police omwewo zitsilu bcz even ma nyumba mwawo ukugwilitsa nchito makala omwewo mkumati makala akupezeka ku shoprite chani ….zachamba umpawi ulili ku Malawi athu azitani to survive. ..

 • Kumaloko kulinjala koma police yakumpanje imakonda kupanga attack osauka akuba mbuzi nkhuku owotcha makala obamagalimoto ndiye abwezi awo koma mpwanga tikaonana

 • My name is Samuel Tapologo and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i never thought i will be totally cured from HIV/AIDS, i have been suffering from HIV for some years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness most especially HIV/AIDS with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { doctorolumo@gmail.com} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) Dr Olumo can also cure, HERPES, CANCER, HEPATITIS.

 • Zokondera basi, there is no alternative source of fuel

 • Just release them.Stupid police why don’t you arrest the buglers

 • Too late,where were you in the early 80s,90s,70s???? #The sign of failure.

 • Atayeni akakudyelani kuti

 • Makara mwalanda , Magetsi kulibe ndiye tidya abàle?

 • Apa timati umbuli waanthu ophunzira kulimbana ndi anthu osauka. Mpake malipiro akuchedwa. Lamulo lanu limakhala lamphamvu kwa amphawi.

 • Za zii basi!! Pitala achoke bas!!

 • TIPATSE MPATA KUT TIKAONA TRUCK YA MAKALA TIZIKANENAKO KOMA OSATI KU POLICE KAPENA KU FOREST CHIFUKWA ANTHU AMENEWA AMACHITA KUPELEKEZEDWA NDI A POLICE AMENE AMAKHALA NDI MA LINE AMPHAMVU KUKAKHALA EMERGENCY ROADBLOCK AMAUZANA MA TRUCK AJA AMAKAWABISA KUT ROADBLOCK IJA ITHE KAYE AKACHOKAPO AMABWELERANSO PA MSEU WE KNOW THIS SHIT MUSATIPISITSE

 • Or apolisioso amaphikilaso makala or pitalaso amaphikilaso makala inu ndinu agalu kobasi Poland’s makalao

 • John K. Banda says:

  Well done. It is a worrysome the way the forestry resources are being depleted in Liwonde & Zomba Malosa forest reserves. The beauty scenery of the reserve along Liwonde – Zomba road is vanishing. I hope such forest joint patrols will continue for benefit of the country. But the section quoted is wrong possibly section 68(1) a,b of forestry Act of 1997

 • Amangidwa Chifukwa Analibe Ndalama Zohongera Mu Ma Roadblock Mukumadutsa Truck More 5 At A Time Odzadza Ndi Makala In The Presence Of Police Awa Ndie Mwawamangiranji? CORRUPTION AT ITS BEST

 • Njalazi anthu adya kuti abaleeee…..ndetiziphikira chan

 • give us an alternative ya nkhuni ndimakala.magetsi amangozima,mukufuna anthu atani apumbwa inu

 • Inu mukunena matumba 145 ndichaniso ameneo kakhaleni pa zalewa mukaone matumba omwe akudusa usiku 2 am apolisi ali pompo

 • Kodi agalu inu anthuwa akulakwa chani asiyeni akasamale banja lawo inu apolice nyooo

 • Atigulitseko matumba awiri nkhuni zavuta kuno

 • Instead of arresting akuba mukulimbana ndi anthu oti akuthandiza mawanja awo koma zikakhala zigawenga ndiye kuzisiya mwinanso kuwabweleka mifuti kuti azitibela kapena kutipha kumene,padziko la pansi ngati ulibe ndalama chabwino palibe!!

 • Apolice pena muziganiza pochita zinthu, mukagwira ntchito yabwino timayamika ndipo mukalakwitsaso ndizidzudzula.Dziwani ichi mmwamba muli Mulungu yemwe alalenga chili chonse.Anadalitsa anamwino posamvera mfumu Falawo kuti aphe ana a muna a Israeli.Khalani ndi umunthu.Kodi amai anu, apongozi anu nadi achi bale anu onse akuphikira magetsi kapena chiyani?Ganinizani bwino moto usanakunyeketsaeni.

 • #magetsi mmene akuvutiramu ndiye muzikalanda makala?… Anzanu salary yawo nkuotchya makalawo basi whether you like it or not!…osamagwira ma 2finger ali balalabalala mtownwa bwaaaaaaaaaa? Mukawalanda makalawo ndiyo mumakawabzala kuti azimera mitengo? Nanga amzanuwa omwe amapeza mchere kudzera mmakalawo..mukawalanda mukufuna aziyamba kuba?.. Nanga akayamba kuba ..muwakwanitsa kuwagwira?…..

 • Kodi inu Apolisi mulimbe mbaula m’gowero mwanumo, nanga mbaula zimenezo zikugwira ntchito yanji?

 • Akakudyereni kuti abale mulibe chisoni

 • Zitsilu za police makala ayamba ndamenewa okha pa nkholo panu mumadana ndi chilungamo bwanji mumapanga zinthu ngati kuti simugwilitsa ntchito makala bwanji abwezeleni anthu makala awo muwatayeso osati zogwilana zo tapitani mukagwile anthu ku boma ko osati awa siolakwa makala imeneyo nkhani tikudziwa inde ndimaluzi amene akupangitsani inde malipilo sakuenda bwino malasha nde geni yanthu osaukafe inu malo anu ali ku boma tamaka bani kumeneko

 • Boyd Lifa says:

  Sadawanyemere asakuziwa ndani kuti Blantyre yonse anthu a magwitsa ntchito makala ndani? Magetsi anu ndi odula komanso osadalilika
  Kupusa tawatuluseni anthuwo please

 • Mukulephela kugwira mbava.kukalimbana ndi owotcha makala.

 • Ha!ha.!ha! Ali mu mseuwa?kkkkkkk koma abale,osauka alibedi mau.

 • Agalu amenewa akuwononga chilengedwe phiri lanthu la zomba anayeresa pano

 • Makala mukalanda,inunso mukumagulitsana k1000 ndalama zimapita kuti?

 • Kodi p
  amenepa a mangidwa ndi apolice kapena Amakala?

 • How about criminals?

 • Anthu anaba ndalama za boma, mpaka pano palibe akugwidwa, asiyeni anthuwo akasamale banja awo, nayenso wapolice mutapita kunyumba kwake mukapeza mkazi wake akugwiritsa ntchito makala.

 • Peter John says:

  asa asowa zochita amenewo tangodutsani zalewa road amene aja simakala amayika mu msewu aja?komaso iwo akuphikira chani kunyumba kwawoko u wii never reward 4 this

 • Chinachitika ndichiyani kuti Amangidwe? Aaaaaa kalipo kalipo

 • Amasuleni apolice nu ndiamene muli pa 4 front kupikulitsa makala umboni ndirnawo kupolice college ku zomba mmamawa wina uliwonse ndikalawirira kuntchito ndimapeza ka lory kia 2 tone kakutsitsa makala atachita kuika lona daily ndiye mukuti chiyani apa amasuleni anthu oxungulira police collegeyo monga chikanda,mpondabwino amadzapikula kumeneko

 • Kodi Magetsi akudula komaso angothimathima ndiye mukuona ngati anthu aziphikila chani?kodi mukalanda makala mumapita nawo kuti?kapena mumakadzalaso.stupid government since nthawi ya kamuzu.mkuona ndimakhala Ku south Africa.Malawi dziko lomvetsa.

 • Hie my fellow Malawian am here south Africa but if you want destroy to feeling trees, give them the one use paraffin to cook or supplying electricity in the village like kankhande up to go pumulan lodge down to kasanķha

 • Mukulimbana ndi wamakala kuputsa komatu muzalozedwa mufunse apolice apachikunda analanda makala kwa #Gogo ina mkuwapakira mu van koma galimoto inakanika kuyenda mudzafa imfa yowawa apolisi 4cek

 • Zitsiru za anthu,ntchito ikhale imeneyo koma ya anthu apha ma albino palibe ndi modzi yemwe amangidwapo.Agalu awathu enieni kusowa chonchita kumanga anthu owotcha makala.

 • Mukalanda mupita nao kut ?? Mesa muzikaphikiranso!!! SO WHAT?? Apolice ndi akapolo,ndimavuto amenewo just release them please!!

 • koma zovesa chisoni kuti dzikoli limavulaza anthu aumphawi komaso awusiwa…ine ndinafufuza kulibe kuti owotcha makala amaononga mitengo poti iwo amawotcha mitengo yodulidwa kale nde y not osakalimbana kaye komwe kumachokela vuto logwesa mitengo?anthu olemela amadula tengo for matabwa ndizina..nde chikauma wamakala kupezako mwayi kumamugwila kupita naye kupolice while olemela ali muzinyumba omwe anadulisa tengowo?shame on yoooooooooo anthu ozuza aumphawi asaaa.

 • Fuck Dem ass broke damn police /// Moti mukagwire anthu akuba dollar za boma

 • The problem shall never end. We do not have alternative ways . Even kunyumba kwa District Forest Officer mukapeza madam akuphikira makala

 • Nanunso apolisi mwayamba kuba mobisalira muzigwidwa mmodzi2 ndiye sitikusiyani chonncho tithanananu basi .

 • Guys popcorn amaphika bwanji kuti afike pophulika chonchija? Ndathira madzi katatu koma sanayambebe kuphulika! tandiuzeni ko ine ndufuna kumwela tea

 • Nanga akalanda iwowo apita nawo kuti?iwowo titati tapita mmakomo mwawo sitikapezamo matumba amakala?bwanji osapita kugwila amene amene akuwotcha akudula mitengo nkumaotcha makalawao munthu yemwe akulandidwa makala ndiogula o order

 • Kusiya mbava aaaa zitsilu za anthu inu…

 • Ahmad John says:

  Tizabwela kumalawi ndalama,mtendele,chikondi,chikayamba kupezekako ndikuchepa kwa asogoleli oziva kukoma

 • Mukumanga anthu olimbikira ntchito mukusiya otchola mabank,Bastad!!Team#Dmc

 • Mmalo mogwira ma cashgate suspects dey hapy 2 catch charcol pple loolz

 • Love Yalu says:

  Apolice aku #malawi ndi #agalu kwabasi,kodi agwape inu makomo mwanu mumaphikila chani?mmalo molimbana ndi amzake a #PETER_MUTHARIKA amene akukhudzidwa ndi ndalama za #CASHGATE,mchifukwa chani mukulimbana ndi anthu osauka?ndiye chifukwa chake mukumapeza nazo matembelero agalu inu malipilo osakwezeledwa ndi boma mapeto ake #AZIKAZI Anu akumanyengana ndi anthu ogulisa #MATEMBA.Muli nditsoka kwambiri nkhumba zawanthu,akapolo adziko.mwezi ukamatha salary kumalandila K28,000.Mulungu akukuwonani ndipo muzikhalabe osauka choncho.mukakumana ndi wapolisi aliyense muziyang’ana jombo yake.Shoe maker achita kutopa nayo kuisoka.mbalame zawanthu,kufuna kubela anthu osauka.

 • Aaa nde uchitsiru umenewo

 • Apolice ntchito yanuyooo izakupitisan kumoto osalekeza koz u pretend tu 4 laws kma u knw the truth abt wat ua going tu du wth the charcoal

 • nziko losauka zoona inu apolisi munzikalimbana ndi makala akuthandizani chAni popanga zimmenezo ndie kuti okagulitsao zawavuta

 • munzikalimbana ndi makala osalimbana ndi ndi okuba bwanji kusowa zochita etii donolo osangoewasiya bwanji akagulitse apenze chokudya

 • Magetsi akudula,sopano inu apolisi olo kusowa ntchitoko ndiye muxigwila anthu ooootcha makala??? that is nonses

 • BASI MAKALA MAGETSI MWATSITSA.GWIRANI AKUBA OSAKHALA KUGWIRA MAKALA .MTENGO USANADULIDWE NDIYE NTHAWI YABWINO CHIFUKWA MWATETEZA KOMAYAPA PALIBE CHABWINO

 • Ndipo if u want kuthetsa makalawa muwonetsetse kuti magetsi sakuzimazima even a second

 • Ngati muli ndi nyanga ingowalodzani amenewa. Isaaaa. Magesi munakaawapasa anthu akumudziwo? Mumati azidya zosaphika. Magesi kudula kaya ngati chani? Ngati mukufuna zimenezo, magesi akhale paliponse and aulere. Apo biiii mitengo idulidwa. Vuto ndinu.

 • Are u deleting coments admin. Why?

 • kenako mazulo azimutuma mwananxo umva iwe Mary, tapita ukagule makala uko , u think amachokera kumwamba? nonsense

 • Amenewo NDE àkuderani mmaso, makala onsewa mu msewu wa zalewa a few metres from the road block. Chilungamo choona nkhope!

 • Makala awonjezadi pamalawi, mitengo ithelatu, koma mvula idzabweraso? Koma nanga tidziphikila chani?

 • Ndemakalawa mwapita nawo kuti i hp simunapite nawo kumanyumba kwanu inu apolice. Kmanso ineyo i was cming 4m Machinga ndinawona galimoto la boma litanyamula makala and it means linadutsa ma road block angapo ndimakala amenewo kodi zizikomera anthu wogwira ntchito m’boma wokha eti and panali pa lizulu pomwe ndinawona galimotoyi itaima that was on a sunday

 • Omar Nason says:

  Koma uwapeza a police omwewo akuphikila makalawo, zitsilu zopanda mzelu

 • Penapake-abomanu-muziganiza-anthu-khobidi-logula-sopo-alipeza-kuti-poti-dziko-lathuri-ukapeza-ntchito-ndiyaulonda–Eishiiiiiiiiii

 • akakudyeleni kutiko anthuwo

 • Umenewo ndiye timautcha ufiti,moti munthu wakumudzi atani kuti apeze ndalama,inu mumalandira salary koma munthu wakumudzi alibe njira ndi imodzi yomwe.

 • Zachamba Basi. Akungofuna pobera makalawo. Akamange anthu chosecho nawo akuuphikira makala omwewo

 • xopusa alakwa chani anthu xilibe mwinitu kodi ndiwapolice uti anaxalako mtengo kumeneko,mmalo mogwila oba njovu kumapitanaxo joz mukuona mulimbana ndiwamakala hahahah kuwaonerera eti

 • Apolisi Akumalawi Mukachita Bwino Timayamika Kma Mukaononga Ndiye Mumawaputa Amalawi Umfit Mwachita Apo Muvulala Nao Kdi Mukufuna Anthu Azitani?Mitengo Ndi Ya Kwanu?Muonaso Ngat Anthuo Samasulidwa

 • Nawoso a Apolice akwathu amakhala busy ndizithu zopusa kobasi and busy kulengeza pamaso pa anthu,kusiya mbanda za m’bomazi mxm

 • Sam Aphoto says:

  Muwapatsetu chilango chokhwimatu anthu amenewa,akuwononga kwambiri chilengedwe.

 • Kusiya Kugwira Mbava Koma Kugwira Amalawi Osalakwa

 • Apolice akumalawi phuma pochita zinthu.apolice momwe zavutira mbava pamalawi pano inu zoona kumalimbana ndimunthu ofuna kudzithandiza?koma polic yakumalawi?

 • Magesi ndamene mukumathimisawo nde mukuti tiziphikira chani??? Nkhuni kulesa, magesi kuthimisa, makala kulesa mmmmm tilimba???

 • Amasuleni anthuwo!!! Ndimavuto amene akuwapangitsa ku wootcha makala.Kodi chakudya,chisamaliro komanso fees, azitenga kuti?

 • Uwu Ndetimati Uchindele, Mphawi Akawadyele Ku Chichiri Prison

 • Owotcha makala musamawagwile pliz pliz amathandiza anthu ochuluka

 • Zachamba2 zimenezo, Mesa anthuo akuotcha makala kuti azipeza chithandizo

 • apolisiwo akumaphikira chani ndi mmene magesi akuvutiramu?

 • eishhh,tilithawa dzikoli.kumulanje nde zafka penapake,kukukhala kumenyedwa,kupakidwa matope,kutengedwa mchilory kukatayidwa patrading uli mbuuu.

 • zopusa mukulephela kudyetsa dziko lanu ndi bwana wanuyo ndie anthuwo mumati apange bwanji? ndani asamale mabanja awo? zaziiiiiii

 • Makalawo atatenge ndi ndani?

 • Osauka atani kodi??,, mitengo analenga Ndi mulungu

 • why arrest???.who is going 2 feed their families

 • Makono-Kaya says:

  magesi akudula..

 • steve says:

  mmalo momakagwira a cashgate mukulimbana ndi anthu ovutikawa… mukuti akapeza kuti ntchito??? mbava zazikulunso ndi inu nomwe a polisi iya!!!