One of Malawi’s renowned herbalists fondly known as Dr. Nyanga Zidana has died, Malawi24 can report.
According to reports that Malawi24 has been following today, Nyanga Zidana died in the morning hours of Tuesday.
He died at his residence in Blantyre.
The herbalist who was based in Mbayani Township, died after a ‘strange illness’, reports indicate.
Details about his death have remained sketchy thus far, with sources indicating the family members intend to make a statement on the fallen traditional healer’s death.
He hit the limelight having flown several media adverts on local radios.
Nyanga Zidana was from Kawiliza Village in Thambani, Mwanza district.
when oz the burial
Nyanga zachita bwino
Imfa imaoneka yopusa ili nyumba ina,But
Wanyanga amafa kodi? Analephera kuzipulumutsa? We have the DOCTOR of Doctors….HIS name is JESUS CHRIST!
Kumanda kulibe njomba
RIP ny`anga zidana ±
Apa Ndipamene Mungadziwire Kut Bible Ndi Mau Amulungu Ndipo Ndilamphavu Kuposa Msupa
Ufulu Fm yatha basi.
Mmawa zili kwa ife.
Mulungu atikhululukire , chifukwa tikungobwaza ngati achule madzi.
In that day shall he swear,saying,iwill not be ahealer,for in my house is neither bread nor clothing : make me not aruler of the people
Msing’anga wamkulu ndi yesu
Jesus never existed!Problem of following foreign religions!
Ndie kuphaziko kuli chani?
Waiona mosshko. Kukhwima kose zzzz. Gwiran bango omwe munakakhwima kwa iye. Muli next
Kunonso a herbalist Dr Ng’anga idzafanso amwalira, so sad
Kunonso a herbalist Dr Ng’anga idzafanso amwalira, so sad
Kunonso a herbalist Dr Ng’anga idzafanso amwalira, so sad
Anthu timangoiwala kut tidzafa ndithu ndpo ndfe dzivundi maka tikakhuta,tkatchena ,zinthu zikamatiendera.
Kungomuontcha mbasi
kodi anthu oterewa amafa? so y do we believe them and put God aside who endures forever? God is the only source of life
kodi anthu oterewa amafa? so y do we believe them and put God aside who endures forever? God is the only source of life
Kd amakhwalaso amafa? Ndimaonangati amadzitsirikatu kut asazafe RIP
ati anadwala chan kod…??
Ndiye mukufusa ndani pamenepo
Yesu ndiye sin’ganga, mbuzi ndi zomwe zili ndi nyanga, anthu onse amankhwala go to Hell.
Napepe mbambadi wawa kwanonse inu your were believe in him not the living God am serving nde shauli yanu wawa poti mulungu wanu mgwakufa ntheradi wawa …wanga He is Still alive today and forever more
I think Africans we need to know the difference between herbal, artifical and witchdoctor. I have been reading comments. Panado,asprin etc are medicine which came from western culture. Herbal is a natural mixture to cure diseases. So if he was a herbalist why are we so judging that it is against God while panado u are using. Becoz it is 4rm fellow African then it is against God command. Maula and herbal are two different things. Google hermopathetist. This is a natural medicine without any chemical. So born again church must stop taking western medicines becoz its a mixture of herbal and drugs that cure then it is also against God command.
Enanu simukuziwa! Munthuyu anali olungama.
ufulu fm business basi yalowa pansi coz uyu anali customer wankulu
Ngati muli baibulo pafupi tawelengani pa yesaya 3v7 chipangano chakale
In that day shall he swear,saying,iwill not be ahealer,for in my house is neither bread nor clothing : make me not aruler of the people
Ameneyu ofunika kumuzondosela pansi mu coffin yake, kuti akasanduka chinthu ndikuyamba kukumba kuona ngati akupita mwamba azingopita pansi. Akasambile mu water table.
Rest in pc
rip doctor
sing’anga wankulu ndi mulungu bax
kkkkkk No comment let God judge it
Eeeee koma atangoti aliyense emene wanyoza APA afe nayenso….eeeh!! Hehehe
Zamdziko zotsala, tinazipeza ndipo tizazisiyanso, amen.
Anthu munali chete! Malemuyu Ali moyo, wamwalira ndiye mukutha zakukhosi. Analidikatakwe eti?
Kulibe wa muyaya
shame! but his slogan claimed timachiza matenda ali onse, (meaning, was able to heal any illness) so he forgot to heal himself huh?
Hahaha anali ndi mankhwala awa khuzumule,mankhwala oletsa mowa ndi fodya komanso chitaka ndipo mukapeza pafupi ndi Chifira cool club mphepete mwa nseu ku Mbayani
amupha ndi A DPP?
Ameneyu ndie musamunamizere kut wafa ndi cardiac arrest. ameneyu wafa ndi nyanga arrest klkkkkkk
Chepesa mwano
Apa nde nyanga zadana basi
Sing’anga wa mkulu mkulu. Ndi yehova
MUSAMUTELO MZANU! BWANJI MUKUBWEBWETA CHONCHI NGATI INUYO NDI CHTSULO ENANU MWATSALA NDI UZINGO /MTSEMPHA UMODZI MSIYENI MZIMU WAKE UKAUSE MUNTENDELE.NDIEN
anapezako chithandizo ndani pano???
ndiye zimatero winawe utakatengako mvunguti.nde anakuuza zoti upitenso after 2wks. kut akakupanse komalizano.lero ndikumamvano izi eeeeh
Sing’anga wamkulu ndiye yesu.awa mmmmh!zamdima akapumule
WANYANGA NDILEKE. NDILEKE MKAIMBILE YAWE.YAWE MWAMBA!
abale anga mukafuna kusewela kasewelen zina. koma imfa musasewele nayo palibe amene azamwalire osava ululu wa imfa popeza mawa nd ineyo kapena inu amene tikupumafe samalan. moyowu suzachoka ngat mmene timazimisila nyali
abale anga mukafuna kusewela kasewelen zina. koma imfa musasewele nayo palibe amene azamwalire osava ululu wa imfa popeza mawa nd ineyo kapena inu amene tikupumafe samalan. moyowu suzachoka ngat mmene timazimisila nyali
Yah zoona bale auze ifa siyosewera nayo aliyese azafa bx
AMBUYE YEKHA NDIYE MWINI MOYO. AMEN
Hahhahahahahhahahahahahaahahah
This is why bible remains the strongest book on earth. God said you shall die. It is happening. Don’t waste time with the person who shall also die.
amen powerful iyeeeee
Amen!
AUSE MU NTENDERE
I am samuel.I don`t no how to tell the world the greatest thing that happen in my life.I was so sick that i loose all the money I have in so many hospital still yet there was no solutions on till I go for blood test for different hospital almost five doctor told me I am H.I.V positive . & after then all hope I have was lost I was waiting for the lord will called me. One nite I woke up in mindnite start crying so my mind told me to check in google so I see many testimony so i found dr sule I was daubting if the man is real a great man but just because of the testimony of his good news.I said let me try & I email him he reply me back I told him my problems he said that he will help me but i will also help my self by sendi;g him money in posting the cure to me wich i did after recieving the cure he told me the precuation on how to take the cure for 14days after that i should go for test then i will be free forever wich i did i was so suprise when the doctor told me am negative i did not believe so i go to another hospital it was still negative pls if you no your case is positive contact him via whatsapp no +2348162447651 dont believe hiv has no cure becouse your case is defferent belive there is nothing that is imposible in the sight of God
Chiv 13vs 14 pepani
Anapita ndi nyanga zomwe kumanda……. Tsoka liyenda
if it is true go in #piece nt in #pieces
Onse amadalila man wa ngati mulungu wao mwina apano mwazindikila kuti mwaiwowa samapasa moyo koma MULUNGU yekha basi
Aliyense adzalawa imfa nyozani lankhulani nenani bwebwetani ngakhale nthawi imeneyo anzanu analankhul choncho, koma tsiku lina inunso muzakhala kwala ngati mmene wachitra nkuluyi anzanunso nkumalankhula momwe mukulankhuliramo eeeeee wadunga eeee wavaya eeee s a n a l a p e Tsono iwe ukunyoza mtembowe walapa? Don’t be happy with the death of ur fellow human being coz we shall all die. Tizimvere tokha chisoni imfa ndi power siona mphamvu za munthu.
Wanyanga aferanji?
Achibale ake apiteso kwa sing’anga wina kwachisapo dzinalake Dr Akufa Adzauka akathandizidwe.
Chinsapo chambuzi moyang’anizana ndi Chinsapo Secondary school,,,Mwawapeza….Eish…Akufa adzawuka….
KKKKKK
Wachita bwino munthu woyipa uja,, adatha nyamata ndikuvulaza m’bale wake waopedwa ku mbayani adali nyanga zidananu, amafuna azisewela ndi anthu agule wakumana nazo amupininga anzake, amati atani wakupha aphedweso naye, go to hell nyanga zidana
kodi zowonadi kut he was de one responsible for dat incident??
Eyaka anakazipeleka yekha kupolice ataona kut watupa mimba ndi anzake ena 4, zamusata
samakapepensa bwanj kwa awo anapanga chopongwewo??
Anamukanila atapepesa amati as long as m’bale wawo wafa, that means wokuphayo afenso
man ndiye mukumufotokoza bwinotu
Zosakhala bwino
Neba zamuvutanso apa nkuona chauka wamapenalty waguga et?
Musatelo man,infa njowawa.
Ndikuziwa story yonse thats why ndikufotokoza
a maluwa musanamizepo anthu panoo,,,ifa ndiyowawa inuso atakhala makolo anu ife ndikumalemba nyas mwalembaz mungave bwanjiii osamangolankhula ngat mwakhalira mutu ayiiii….
new asalongosore coz was? amalawi kukonda kulemekeza wokufa
Kkkkkk,, wakufa sabwelela, iwe sunamvepo kut chisoni kumatenda kumalilo kumakhala nkhani,, zamunyasa akakolope nyanja
Kodi mukupti zidatani? Tidziweko
eish ku malawi kulibe fiti
Kkkk anakuuza ndani?,, ukadzakumana nazo udzasiya chibwana chakocho
Bodza
Wamwaliradi man musasuse
Akasanduka mundipeze
Aliyense adzalawa imfa nyozani lankhulani nenani bwebwetani ngakhale nthawi imeneyo anzanu analankhul choncho, koma tsiku lina inunso muzakhala kwala ngati mmene wachitra nkuluyi anzanunso nkumalankhula momwe mukulankhuliramo eeeeee wadunga eeee wavaya eeee s a n a l a p e Tsono iwe ukunyoza mtembowe walapa? Don’t be happy with the death of ur fellow human being coz we shall all die. Tizimvere tokha chisoni imfa ndi power siona mphamvu za munthu.
MHSRIP
Shaaa kaya Gondolosi ndi nchape komaso tseketseke ndizimupeza bwaj kaya?
Tsano oja omanama kuti iwo nio Nyangazidana ozinama kuti nioya?
Komanso, nifunseko, kodi ong’angawo dzina lawo loyamba la mchedzera linali Nyanga, lotate wao nalikhala Zidana?
Pita ukafuse komweko. Coz no 1 knws here
Kuputa ndewo n’kuyimilira, muluchita apawu dala, niupandu.
Ali koyankha mafunso kwa sing’a wankulu yesu
Moto umapita kwasala tchire awa apita tasala ndi inu ndi ine RIP
big sorry rip
RIP DR NYANGA ZIDANA!
So sad news omwewa apambayaniwa haaah his soul rest in peace
Aliyense adzafa palibe chachilendo apa
WANYANGA AFELANJI?
Ufulu radio
Uthenga udali wake
Basis kaya azilengeza
Chan kaya great lose
Kkkkkkkk koma iweeeee
Yea this is very true koma akuti amene uja ndi JR koma kuzipopa kokhako eysh nawoso a presenter ake kumachemelera nawo kaya amanyemera kaya mmmmmn koma talks too much mpakana made me to hate the station
Typing,,,,,,,,,,,,,,,,
R.I.P
Chauluka chidzatela its time for Dr nyanga zidana RIP kauseni muntendele kumene mukumkako
Analibe ufiti?
Mwati chani?
Bwanj mwazuzumuka ngat simunawerengetu?
Mudapatukilako kapena?
Mfiti idzafanso
Shaaa .Zodabwitsa !!! Kumwalila mankhwala ali myumba ? R .I .P. DR.
maliro amenewa akhala ovuta ndithu nsinjo (musi) uzanyamulidwa ndi mwana osavinidwa atatsogola. kuyamba kunyamula wautali
iwo sachita maula koma amakhulipira malemba a bible the advert imatero yodzichemelera
Kupezetsa ntchito pasanathe sabata limodzi lol
RIP
Wapha anthu uyu m’masenga akuti kunamiza anthu kuti alemele wanya lelo wakhaula wafa naye
Kkkk!
Mwatero big?!
Wafa moputsa kwambiri
Kkkkkk Sing’anga iyeyo ng’anga ndi yesu christ
after atawabela anthu mmatsenga pano wakakomana ndi msing’anga wamkulu yesu.
R IP
INFA IKUTENGA OTETEZA INFA OMWEWO YOO
Inna lillah wainah illaih lajoonah
Hmmmmmm!!!!!!!!! Komatu inu,Mkamphindi akufa,ngakhale pakati pa usiku,Anthu agwedezeka napita.Amphamvu acotsedwa opanda dzanja lowalanditsa.Pakuti palibe m’nthunzi wa imfa kuti munthu angabisaleko.Pakuti maso a Yehova ali panjira ya munthu aliyense napenya mopondamo mwace..(YOBU 34 V 20 – 23) Mantain your ways Now!!!!!!
Amen munthu wa mulungu.
dont judge abook by its cover…..U nver knw kut mnene amamwlira …Kut ananena wat …..Az his last words
Wanyanga azafanso!
Wabodza ameneyo ine lero ndinalikoko panopasindinafike kunyumba
Sati zuza awa mukuti sauka zosa uka awa mwati zisa chitike ngati zija zina chitika ku………….zouka chinguluwe zija sizokha zokhazi nde mbola kopita ndizi ntchito zachabe kulibe ntendele mmmm ifa ilibe ulemu ndinthu opita usana lape shaa basi ngati ndimu ntendele apite koma ndaka ika #nyanga_zidana R I P
Sati zuza awa mukuti sauka zosa uka awa mwati zisa chitike ngati zija zina chitika ku………….zouka chinguluwe zija sizokha zokhazi nde mbola kopita ndizi ntchito zachabe kulibe ntendele mmmm ifa ilibe ulemu ndinthu opita usana lape shaa basi ngati ndimu ntendele apite koma ndaka ika #nyanga_zidana R I P
Auka ng’anga singamwalire mopusa chonchi,komaxo osaziteteza bwanji? koma kunamiza anzake we hve to learn
Langokwana tsikuli anali atafa kale
Mfiti izafanso
Auka ng’anga singamwalire mopusa chonchi
Sha!! Maliro atulusira pa window amenewo, or else azazuka chinyama kuzuza mmudzi mose
kkkkkkkkk koma ndipo….i think pamaliropo ake pasapepeke olira…
kikikikikikiki and polowa mmanda azikalowa cham’buyo
Ayi Azikakwilira Ali Chafufumimba
kikikikikikiki kungolakwisa zizimba zimenezo, eeeshiii anthu sazangonera that time!
Get yo facts straight. Witchdoctor and herbalist are two different things. If u take panado do u know that it is drug?
anyway, may his soul rest in peace if possible
Ufulu radio has lost a big client.
Thats very true…
Sukunama Braz.
Okay
Zoona zake yooooo
Kodi ndi ambiri mumanva ayt ? Komatu kuzipopa kumene kuja ine ndimadabwa nako honestly ng’oma yolilitsadi koma iyayi taphunzilapo China chake
Tachokani Uko, Iyaaa, Mwasowa Chokamba Eti?
Eh….
shaaa koma chaka chino mchawanthu ochuka eti
bola akhale atalapa mulungu awalandile…..r .i. p
Maliro otulutsira padenga tsopano
Khani lelo zidasowa eti mpaka ndi awa omwe #LOL
wanyanga afelanji? kkkkkk!
kkk tafuxan bro amatan kuzionjera moyo wna
kkkkkk! komabe RIP
ok rip
nde ife titani?
tipite ku maliro
Kkkkk
Kukatani?
eti man? oyamba ndi iyeyo kumwalirako?? enafe makolo athuso anatisiya nde tizikati RIP ngat tinapangapo deal ndi iyeyo!! ukukhala iwe Leonard utha kupita is anakukhwimisa? kkkkkkkkkkkkkkkk! joking @ #Leonard
Pali zoseketsa apa,? imfa siiona nkhope idzakupezani
so sad indeed,he was agreat man in terms of herbals.May his soul RIP
Apita ndi nyanga zawo.
Next is Mugabe
aaaaa ya zilizonse kuposita, ma herbalist?
Iiiiii rip.
kkkk zakhala bwanjiñso mankhwala anamuthera?
so wat?
Machende ako wava ? ? ? osangokhla buaj ngat Ulibe zolakhula
Shaaaa! tisowa kopita.RIP
ma pillow a akulu angotisiya kumene aja
Ki!ki!ki! Mwatero eti,