A 32 year-old man has been beaten to death by an angry mob after he was caught stealing sugarcane in Machinjiri Township in Blantyre.
Deputy Public Relations Officer for Limbe Police Pedzesai Zembeneko has confirmed the incident and he identified the deceased as Lameck Chibwana of Machinjiri. According to Zembeneko, on Tuesday.
Chibwana went to steal sugarcane at one of the gardens within Khukuteni village in Machinjiri.
However he was spotted by the garden owner who was also in the garden at the time.
“Upon seeing the garden owner, Chibwana started to run away but the gardener shouted for help. The villagers flocked in and arrested the suspected thief,” he said.
The community members agreed to take the thief to Mzedi Police Unit but on the way they began beating him until he died.
Meanwhile the dead body is at Queen Elizabeth Central Hospital for post-mortem.
Lameck Chibwana hailed from Khukuteni village, Traditional Authority Machinjiri in Blantyre.
chonde chonde tisanapange chiganizo chathu tiziyamba tadzifunsa tokha mmene ife tilili.tisamadzitenge ngati ndife olungama .kuti tizingoweruziratu tokha choncho sibwino ai.oweruza momveka bwino ndi mulungu yekha.anthu ena atabwera naye mkazi wogwidwa ndi chigololo kwa yesu,chpncho yesu adalamulira anthuwo kuti amene akudziwa kuti sadachimwepo ayambe kumponya miyala mkaziyo.palibe angakhale mmodzi amene adachita izi.kusonyeza kuti panalibe olungama.chimodzi modzi ifenso sindife olungama.
Oh no… That’s so bad ..muthu akafere sugarcane …
RlP
mwa chita bwi chifuwa mani kulima zimapweteka iye wakhala ndiakazi ake ine kudimba ayi kumwamba waziyankha kale sharp ine sadam from mzimba mtelemuka
thats too much, kumupha mzako mkumuweruza, no one has that right its only God who knows how to judge, enanu mumapanga machimo onyasa okuti simumatenela kukhala moyo, but God never take your life away, He gives you a room for repentance.
Zoti Malawi is A God fearing country sizoona ayi.zambiri zikuchitika zikuonetsa kuti satana akulamulira anthu ochuluka Mdziko la Malawi,eg kupha albono, uhule wa amuna ndi azimai omwe. Katangale ,ziphuphu, kuphunzitsa ana ufiti. Kupha nkhalamba.kuononga zachilengedwe. Kukodza ndi kupanga chimbuzi paliponse. Kuzunza nkhalamba, kugwilila wana.kusalemekeza akulu komanso makolo.ndidziko lamalawi lokha lomwe ndatchulazi zikuchitika in 100%
Brilliat idea Mr president
Stupid pipo ndinkhani yophera munthu iyi how much is the sugarcane? Ngakhale sim’bale wanga koma i feel pain, so what is the benefit anthu opanda nzeru inu
kunena moopa Allah apa sizinsye
Nzimbe abale mmmm Malawi
Not good at all, atengera lamulo in their hands
Aliense wachita nawo izi sazaupezanso mtendere. Waba chakudya munthuyu mkutheka anali ndi njala. Bola mukanangomugwira ndikumupatsa chilango china kaya chosesa pamalo panu pa mizimbepo, koma mpaka kumupha? Mbava zenizeni ndinunomwenso mwamuphanu, tsoka lanu muzimve mumtimamo
Thanks Dr. sule for your kindness, everybody know HIV is a deadly disease I was once a HIV positive and Cancer, am from south africa am 32 years I contacted this disease when I was 27 I was using drug over since, just last week here I see this mary benjami testimony that her HIV was cured by dr sule so surprised when I read the testimony and I dont believe there is cure to HIV and I see another testimony about the same man, then I have to try I get the real true of this testimony and I whasaap the number below it and the man answer me he ask to t sent money to buy the necessary iterms that he wiil use in prepareing the cure so we can start immediately i send the money well I dont know how he did it but god know. I promise you,you we rejoice like me pls dont ignor this message is real god dont come to heal by him self he sent his servant and this man is used by god believe me dont believe that evil tout that hiv dose not have cure becouse there is nothing my god can not do just have fiath and try him this is his whatsaap no +2348162447651
Thats out of line really. Ma savage
Taking something priceless for just sugar cane…….i don’t understand what is happening warm heart of Africa……
Machinjiri walelo akundipasa mantha…….
Anthu amene akubweretsa mavuto mdziko muno akungoziyendera okha pazimagalimoto. Anthu amene akuba ndalama zankhaninkhani pano ndi afulu..koma inu mukukapha munthu oti waba mzimbe..shame..osangatenga nsonga ndikukadzala bwanji? mupite mukagende anthu amene akuba ndalama zaboma, akuba mankhwala mzipatala..Do better Malawi.
Zoba zina guys mwawonjeza
Tikhara tikupemphera kuti inuso murakwile azanu koma azanuwo akukhululukirani apampamene mungatengele umuthu afiti inu
that’s not asolution to solving the problem, R.I.P
Because of ordinary sugarcane? Opha ndi lupanga naye azaphedwa ndi lupanga.
mmmm ayi apa nde mmm sizoona chifukwa cha mijuwa. police must do smethin zinthu zoti utha kubzala kuseli kwabafazi nkumera
This is not the right way to treat thieves.Very bad .What is sugarcane after all ,pliz aMalawi tisinthe.
This is not the right way to treat thieves.Very bad .What is sugarcane after all ,pli aMalawi tisinthe.
koma anthu kuchotsa moyo chifukwa cha nzimbe?????
Killing someone coz of sugarcane,mchiyani kodi a Malawi
opha nzake aphedwe.
kunphela chifikwa waba mzimbe?
#Isaac lungu see they hav killed someone again.
mmmmmmm GOD, was he wanted to sell? or he was hungry ?
Too bad
😮 only that
Am in machinjiri but didn’t knw this…be specific machnjri z big
Kuba Kumabwela Chifukwa Chanjala Learn To 4giv Osamaphana Ngati Nkhuku.
Koma Gyz zinaz kungozipalamulira machimo kwa Mulungu nzimbe omwewu mpaka kupa zoona ayi zonse azaweluza eka mulengi mwini zonse tsiku lachiweluzo.
Its too much. Bt i cud be happy if he ws suspected of killing albinos not stealing sugarcane. Anyway no reverse here. Bt lets learn to prosecute da suspects b4 we punish them.
kulanga ndikwamwini wake yehova amene azapeleke chiweluzo mogwilizana ndintchito imene iwe umagwila amalawi tatani kodi ndinkhanza zotero chepesani mbiteee
Mawa ndinu akanakhala kut mwapeza akubanyumba koma zimbe inalinjala imeneyo a police apangepokathu kumwambaso muli pamavuto opasa zanu chilango chifukwa chazimbe,
HMMM MALAWIANS TIKUPITA KUTI NDINKHALINDWE LOTERE ABALE KUPANDA PAKA DEATH OF THAT POOR FELLOW MALAWIAN PIPO KUNJA UKU UR DOING ZINTHU ZOOPSYA KWAMBILI KOMA SAKUPHENDWA.KUTI MUONESESE MUONA KUTI ANALINDINJALA MUNTHUYO KUMENEKO KUNALI KUSOWA KUTI ADYE B4 U ACT SUCH CRUELITY MFUSANI MUNTHU KAYE DAT WHY IS HE/SHE DOING THAT AKUUZANI MAY B FROM THERE U CAN ACT HOSPITALITLY.NOW POTI POLOBULEMU HAS COME ON US B CONCERN CITIZEN 4 DIS POOR SOUL4 HIS BURIAL CEREMONY.MHSRIP.
I FEELSORRY FOR THE LOSS. ONLY GOD KNOWS. ANTHUFE TIMAKANIKA KUPANGA MOYO KOMA TIMATHA KUUCHOTSA MWAKATHAWI KOCHEPA .ESH!!!!!! WHERE IS LOVE CHISONI CHIDZIKHALAPO POPEREKA CHILANGO GUYZ. WHERE IS THE LOVE MALAWI???
I think amalawi wachuluka ndi umbuli ndi kuvutika, chomuphela munthu chifukwa cha mizimbe ndichani no no no no thats bullshit, osasiyila apolosi ndi a court ntchito yawo mxiiii. Bad.
That u have done killers its too bad.
Vry Sad en get redy God wll burn yo guyz.
anthu akupha ma alubino mukungowaona,kuwapasa nyama kundende!! kumakapha munthu chfukwa cha nzimbe? mulungu akuonen
killing a person bcoz of “Panda”.. thus kwathu language..shame on us Malawians..!
U r fakin all of u mitimayanuiyo mkaonaporekera
Kufa chifukwa cha nzimbe weniweni ? Brainless fool
wakuba nzimbe waphedwa koma wakashgate zake zinayera wat iz it my malawi. where to iwe malawi. Kodi mizimu ya John Chilembwe & other friends koma ikugona. pepa malawi. I crying 4 my country malawi.
They have done well to kill him the man had done a lot before stealing sugarcanes.The 40th day had come to be killed as wages of sin.
Wake up u barbarians, imbeciles, Moran’s. That’s wat Malawians are capable of. They take actions before thinking, koma never forget kuti the country is on crisis. Sugarcane that’s why tizafa ndikumavutika chifukwa chopondelezana Malawi is a pathetic country. Kupondeleza that’s why pa nation anthem pali njala, nthenda , nsanje. Wake up!” Kupondeleza that’s even koyenda kunja upeza chigulu cha amalawi chikuwopsyezedwa ndi munthu modzi, kunyenga, ufiti, nkhanza, kupha, kuba, nsanje ndiye kumalawi. Sleepy foools. Corrupted fools, agalu achidima m’maso.
Sorry for dat nzimu wake usemutendere zimachitika
Koma mayetsa njala nthawi dzina tidziwakululukira anthuwa.mavuto ndi amene achuluka
Mwalak guys mwin nd njala mukanangomulipirisa mpaka kumupha muziganizira muli inu tizikondana ngat ndife mtundu umodzi
So sad
Love one another as you love yourself this is not right
street justice……LMFAO
Bolani otchola nyumba osati nzimbe
wht kinda ov ths booshit luk @ yhu streets kidz you are fake memberz…f**k
WORLD PLEASE GIVE THESE PEOPLE SOME FOOD!!!!!!! this just too much!!!
Where is your respect Malawi, beat someone to death because of stealing sugarcane? What is sugarcane compaired to humanlife? Police do something on this case.
Sure Munthu Kuba Zmbe ndkumupha? Ah Amalawi Mwatan it iz not good, azathu nawoso al nd ufulu kukhala nd moyo. May hiz sol rest in internl peac
Malawi were is umunthu shame
wachita bwino kuphedwa ameneyo
Tell us their names so tht we cn sell them to the south african pple cz to kill someone cz of stealing is a bad habit,, thts yy we hve got police ndamene amathana ndi nkhani yakubayi
No good guys!
Ayi panali chifukwa china osati mzimbe.
WAKUBA MZIMBE KUPHEDWA POMWE WAKUPHA ALUBINO KUMASAVAIVA MMMH SHAME MALAWI!!!
hauza pa funso la MISALA. Inuyo muunikilapo pa mafunso onse okumayambiliro. Ndi amene akuwongeleleni kuti wolakwa ndani pakati pa wophedwa mmodzi ndi mob justice. I dont encourage Mob Justice to done un justifiably. But I strongly support mob justice bcoz it has helped in reduction of criminal behaviour hence easing police work.
Kodi amene waba Mbuzi ndi amene waba Ng’ombe wakuba ndi uti? Kodi mwini dimbalo aberedwa mizimbe yochuluka bwanji? Kodi Blantyre yonseyo wanjala anali yekhayo? Kodi kumukhululukila sikukanakopa ena kukakafanizapo mizimbe yonseyo? Kodi iyeyo ndiwachibale wa mwini dimba? Chinamupangisa nchiyani kusakapempha kwa mwini dimba angakhale mnjila yaganyu? Funso lomaliza nali, kodi iyeyo anali wamisala?? Ngati yankho ndi INDE onse ayimbidwe mlandu wakupha koma ngati ndi AYI onse asayimbidwe mlandu. Ndikutan
Hey Mr idiot.!!..dont take laws in ur hand….,,Nawe tikufunse..kodi wakuba amti akapezeka aphedwe?…kodi ,chinabvuta ndi chan..kupita naye kupolice?….Kuba sikwabwino..ngakhale ataba kochepa timadziwa…koma musaganize kut kuba kuzatha pomaphana.ok?,,,.ndi anthu angat aphedwa chifukwa chakuba?…ndiye ndibwino..kut anthu otere apolice azigwira vep yawo..chifukwa taona anthu atasinthika chifukwa cha ndende……anywae mwachotsa moyo….mukut uduli…tsopamo moto upita komwe kwatsala tchire..uyo kwake kwantha…Tione mwini Dimbayo ngat Sakalimira zimbe zakezo ku prison..(life in prison)…..chifukwa thawi zina mumaona ngat mukukoza koma mukuononga……khan yoti oberedwa inakamukomera tsopano itembenuka chifukwa wagwira ntchito..ya enuwake….# ma proffesional apolice ndi ma judge……Chonsecho kusukulu sanapiteko..chomww akudziwandinzimbezo..ndiwe yemwe
Uli ndi nzeru, koma zauchitsilu!. Mwakholo lako linagwirilidwa kapena kugwilira, ndiye kubala sanakudziwe. Iwenso ngati uli ndi ana ndiye kuti amabadwira ngozi yosowa condom kapena umakagwilira. Usandilankhulise pambali. Wangoziwonesa kuti olo mwana wako nsungampange guide. Achitsilu.
mwaitha guys big up
GUY’S ZIMBE??
Aaaaaaa!very sad guys.ineso sizinakhale bwino
Nzimbe????????
Apangabwino chifukwa kupezachithu kopwetekat
Zowoonadi ngati mene unapezela suit yako yangati wapachika pantengo chimutu ngati bus.
Only sugarcane? People lyf is precious we must not do that plz
Mmmmh that’s so sad killing someone just for a sugar cane… what’s happening to Malawi I grew up knowing Malawi is a peace country but now um scared….
My Malawi where we are going to? To kill who steal Sugarcane but while all those who commited for killing Albino’s they are just arrested. Malawi wakukulira ndi umphawi
ULOVO UMAPANGISA ZONSEZI ANTHU AKUMANGOKHALA MMA LOCATION UMU NDYE AKAPEZA WAKUBA AMAKHLA NGATI APEZA CHOCHITA MUNTHU WA PA TCHTO WOPHUNZIRA SUNGALIMBANE NDIKUMENYA MZAKO CHIFUKWA CHA MZIMBE KOMA MA VENDA NDI MA SIKINI AMANGOPAMGIRA MOLARO MPAKA APHA MUNTHU CHIFUKWA CHA ZIIII NGATI CHIMENECHO.INE SINDINAWONEPO MUNTHU WOTCHENA BWINO ALI MU SUIT WA DOLA AKUMENYA MZAKE CHIFUKWA CHOBEKANA KANTHU KAKANGONO…….Anyway RIP but don’t forget #feesmust fall.
Mwalakwa kupha munthu chifukwa chamzimbe,njala yake imeneyi nanga atani?
Dziko lathu,,,,,, opha abale athu ma Albono kudende koma oba nzimbe aphedwe basiiii ,,,,, A MALAWI
koma guyz ndi mzimbe yomwe kumuphera munthu hmm, mwina mzanu anali ndi njala, kulakwa.
Aaaa, zausilu. Bola akanati agwira aziwalo.
MALAWIANS HMMMMMMM SO BAD. ….Mzimbe? ???
aaa mzimbe kkk ndiye bwezi khotakota athu atathatu a
Thiefs must learn a lesson keep it up !!!
Thief’s!?. Nawenso chinkhope chako ngati wakuba. Koma iwe waziwalo.
Mmmmmm, bola akanangopempha kuti amugayire. Wafera mzimbe?
sugercane in chichewa mzimbe mpaka kumupha shame u devil kod anaba ma truck angat amene zandinyasa bwanji
Mmmmmm mwalakwa kupha munthu osalakwa.I hope inali njala
Amalawi uwu siumbuli koma nkhanza kukula kwa amphawi okhaokha anthu olemela kale anaba ndalama bwanji sanawaphe. Akanakhala kuti Mulunga amalanga Nthawi yomweyo olo munthu akapempha amachita Nthawi yomweyo bwenzi tapempha kuti aliyense amene watenga nawo gawo pakupha naye afe. Musandide ayi pepani kkkkk.
Why Malawi jst becoz of sungarcane
Aliyense wakuba adzafa imfa yowawa ndithu. Judge no one. it is written “… udzadya thukuta lako” so??
Ambuye bwerani nthawi yanu yakwana anthu angopanga zomwe afuna osati mwa malamulo anu
inu munati usaphe anthu angopha anzawo ngati nyama ife latikanika
Death penalty because of nzimbe? No ways. I think he was one of the targeted person or criminal.
foolish Galatians!!!..the so called peaceful nation(warmheart of Africa..is it true?)…..why malawians?..mmmmmh so bad…started well & now bad ending….nthawi nde yatha tikukhala masiku otsiliza,,mukapanda kusintha,moto ukubwera munyeka ambiri…
Ndi mzimbe yomwe? Chilango chimenechi chakula. Mukanampatsa phunziro la saizi yabwino
This is bad
Kufera nzimbe?too bad,,,mwina inali njala mukanangompatsa chilango chotipula kudimba lanzimbe lo.
Mob justice yopusatu imeneyo. Kujaila basi! Mukaphe munthu chifukwa cha nzimbe? Kulibe police kumeneko? Za usilu eet? Those idiots killers should face the law.
Onse amend apha munthuyu akuyenela kumangidwa ndikuphedwa
amen
Noooooooo!!! This is not fair at all, nzimbe weniweni osathira fataleza angakhale manyowayi???
ichi ndiye chamba malo moleka kupha anthu a cash gate aja mukumupha munthu kamba ka nzimbe zopusa basi
N’chani A malawi?………Amalawi alero..popanga zinthu..mukumazitenga ngat Madolo,,,,think twice before acting…Simungatchuke popha munthu ndi khani zozira…,,Amalawi..no one z above de law….hope police will do something better for de killers
Poyamba timatchuka kuti we are a people of ‘Warm heart’ and beautiful smiles. Koma pano tikutchuka ndikupha abale athu akhungu lachinapweri, komaso pfuko la ‘mob justice’. What kind of mob justice yokachitira mphawi wanzimbe? Shame!
Very bad Bro..Thats y..uzaone olo..kumalawi..tizipani…mbwee,,Reason..aliyense amaziona kut ndi wanzeru atha kulamurira…komanso kupanga chilichonse,,which z bad mind…,,,,,,,Dziko langa…ufulu pano ana patsa Galu #Satana..
Uchitsiru basi, kusazindikira, sugarcane=life, impossible life is precious, kupha m’bale wathu coz of Mzimbe, shame!!! Vuto la umphawi wa mdi choncho, kusowa zochita mapeto nkumapha munthu coz amaba mzimbe
Uchitsirutu weni-eni…koma..ndikudziwa kut apolice apanga zonthekera kut,,mwini Dimbayo..Akapitilizire ulimi wazimbewo ku Prison….(life in prison)..nde tione amene anve kuwawa…akakhala..m’bake wanthuyo kwake kwantha ..moto upita komwe kwatsala ntchire Now
A Malawi ambiri sanazindikire Zachepa, vuto nkutsalira kwa dziko lathu lino, ndipo tiri kutali tu ndi chitukuko ukuziwa, nkpsauka kuno Zachepa nchifukwa chake akuphana kamba ka mzimbe, zomvetsa chisoni
Kkkkkk,,,ndaseka..mozinvera chisoni…..Sukunama…,,sure tilikutali..et Bro nzimbe?…..mwinanso Chimbowa cha nzimbe
Hahahahahaha! Komanso atsogoleri anthu amaba kwambiri tu koma samaphedwa, mphamvu zawo zimawateteza. Billy Kaunda sananame kuti osauka alibe mawu. Musadzabwereso kuno pokhapokha ine ndizayambe kulamulira dziko limeneli hahahahahaha! Our nation is a century behind bro. Bagwirani kaye magobooo kumeneko hahahahahaha! Mu rize hahahahahaha
sad news we really nid God’s intervation
Ha ha ha ha.Zachepa.Sured….Sindizabweranso…….pokhapokha upange zothekela….mwina iwe..utha kuzayendetsadi bwino….
Ukundiziwa kale, nkhanza, chinyengo etc ndizachepetsa kufika pa very low percentage sinanga sizingatheretu ukuziwa iweyo…Ndizakhla mtsogoleri wa chikondi ndi wachilungamo kwa anthu ake hahahahahaha! Campaign ndiye ndi imeneyi ndayambayi
Kkkk..usamaletu zachepa
koma zoona mpaka kuchotsa MOYO wamunthu chifukwa #Nzimbe?
koma amene apha munthuyi chonde akuyenela kulangidwa sichifukwa chokwanila chimenechi
nzimbe yeni yeni, mukulephela kupha anthu anakubelani ma billion a makwacha but Malawians aaa
Yes we all know that stealing should not be condoned BUT killing somebody for sugacane??? NO! Hopefully the police wil work to bring those involved into book. We are losing Umunthu at a very fast pace Malawi!
Kamphera misale waaa pywanyanya mukanangomulipirisa,Nazinjalazi zakaka makaunozi ndiye kamuphera nsale nepidakomebi ndithu
Mmmm killing some bcoz of sugercan , really? police must rock those mobs in jail including the owner of the garden its so sad
Kupha munthu chifukwa cha Nzimbe, mmmmmmmmh amalawi.
ZIMBE YOMWEYI BWANJI OSAPHA ANTHU ACARSHGATE
Shame sugar cane
Why malawi mizimbe ndichani mpaka kupha munthu, shame on you .
mmmm ayi apa nde mwalakwitsa mzimbe??? mmmmm..bola akanakhala walowa mnyumbatu …Mulungu akulangani nonse amene wachita izi….inu mmene mmapanga zimenezo munayamba mwazilingalira nokha kuti simunachimwepo??
Kulima nkopweteka khasu sidzibwana ndiye iwe udzivutika ndi kulima bambo wina ndevu pepeya kungobwera kukubera? Shatapu! Ukanakhala kuti mzimbe sikanthu kofunikira bwanji anapita kukaba? Munthu walima munda ndiyenso udzikhalanso pantchito yolondera kwa anthu a ulesi?
True Bro . . But the punishment its above de crime……sikut kuba ndikwabho…..koma pliz Apolice anakapeleka chilango choyera kotero..nkulu anakatenga phunziro..we learn through mistakes..
True Bro…But the punish its above de crime…..sikut kuba ndikwabwino,,olo katachepa nkako..koma pliz Apolice ndiomwe anakapeleka chilango choyenera,,kotero wakubayo anakatenga phunziro…ndaona antthu atasitha chifukwa cha ndende…DONT FOR GET WE LEARN FROM MISTAKES…..nde pot mwapanga zinthu mwakufuna kwanu..ndikhulupirira kut..Nzimbe zimenezo..mukapitiliza kutilimira ku prison..,,Chifukwa apolice sakusiyani…Thawi zina anthu amaona ngat akukhoza akuononga…….iyo wapita ,,kwake kwantha..tsopano kwakhala kwa Mwini Dimba…nde tione kut anve kuwawa ndan?…..he he he..kaya sikhala life in prison kaya…
Zinazi zimangokhala nkhaza munthu ukachotse moyo wa zako chifukwa cha nzimbe zoona….kuba sikwabwino nakoso kupha sikwabwino ….pamaso pa chauta ophedwayo akayakha mulandu oba nzimbe enanu mukayakha mulandu opha munthu ..tiyeni tizikhala anthu achisoni ndi owopa chauta..mitima yathu izakhala yofewa ..yochitilana chifundo wina ndi zake
I wish that was fit for the cashgaters.
Kodi bwanji mumaleka kupita naye Ku police mukudelera ntchito yawo …komanso u don’t know Mwina munthuyu unali ndi Njala tiye tiphunzile kukhala anthu achifundo ndikuonetsetsa kuti tikusatira malamulo adzikoli moyenera tisatenge malamulo adziko kuyika manja mwanthu sindikunenena kuti kuba ndi Kwabwino ayi koma umoyo wamunthu ndi ofunika
U knw Malawians..nowdays. akumazitenga ngat Madolo…chomwe akudziwa ndi Ma violence bas…which z not Gud….
Not a bonafide reason for an extermination! sad! sad! sad!
Malawi is being stained with human blood. ..no wonder we are facing many problems as a nation
Koma anaonjeza mpaka kumupha iwowo mulungu anakakhala amalangila2 zomwe amalakwa bwizi ali moyo osamatelo okuba kupolisi basi
aaaaaaa thus very unfortunate bcz u cnt take somebodys life bcz of a Sugarcane thus inhuman
Mmmmmmmmm Malawi walero mpaka kupha munthu kamba ka mzimbe
this z inhumane,osamapha amene akupha ma albino olo zigawenga zoopsa bwanji ?
mmmm. chofela sowe.zimbe chikhale chinthu chophela munthu?
Kodi akadakhala mwana wanu wakaba zimbeyo kwa wina ndikumupha mukanava bwanji that’s not fair please think be for you kill the person rest in peace brother
Koma abale ! Mizimbenso ndikanthu ? Samangomulipilitsa bwanji ? Okuphayo 4 life in Jail please !
Eishhhhh,Mzimbe basi?
Kodi ndi chifukwa chani aliese amene ali ndi dimba aka gwila munthu kuti amaba nzimbe zotsatila zake ndiziwili kumudula dzanja wa ntcholela nzimbelo kapena kupha kumene kumakhala ku nkhwima chani
Are you interested in Joining the Illuminati in any part of the world, Whatsapp the agent for more information +2347010357750..do you desire to be rich and famous in life? what do you need? are you a banker,lawyer,engineer,harbali st,pastor,lecturer,professor,business man or women,actors and actress,musicians,politician do you seek wealth,fame,powers or any thing you desire in life here is the opportunity to change your life for the better ,would you want to join the brotherhood? for more information kindly Whatsapp the agent for more information +2347010357750? ..or add him on viber or imo your destiny is in your hand
Malawian Pipo Hw Can U Slaughter Ur Felow Man Jst Coz Ov Sugarcane?Mukulekeranji Kumpha Zimphona Zomwe Zili Ku Jail Zomwe zakhala Kupha Ma Albino Athu.Its Ashame Guyz
Kiling aperon because he was caught stealing sugarcane is very unfortunate
Chikondi tilibe anthufe, kuchotsa moyo wamunthu cifukwa cha nzimbe? Komatu zikuwoneka zophweka pansi pano kumwamba zikavuta.
Zoonad big
Anthu amenewowo ndiomweaja akumaphanso powabisalira,ndie asowano……….
Eee koma a Malawi mwatani? Mzimbe mpaka munthu kuphedwa nawo! Koma okupha alubino mukukamusiya ku police wamzimbe kutaya moyo. R IP
No mercy for criminol Police,catch the suspected killers,and kill em too
yaap!its better to kill dem once found kwaomwe sanabeledwe sizabwino but 4me killin dem iz good
Aaaaaah koma akuluakulu nzimbe mpaka kuchotsera moyo wanzanu? Mmmmmmh ndafooka kwambiri
Sinkhani yomuphela munthu iyi,zinazi zimangofunika kumvana basi,sizinayendepo apa,sindikulimbikisa mchitidweyu ayi koma aliyense amalakwa in one way or the other…
Yes bro agree. No one prefect
Give this guy a botle. Of bells
zoona!!!! nanga zimbe? koma anthu akuba zikuluzikulu akuyenda free
zoona!!!! nanga zimbe? koma anthu akuba zikuluzikulu akuyenda free
Thats the agrey side of mob justice
Ufulu omwe anthu amawufuna ukuwonongesa znthu n azawufulu aja alikuti popeza a police akati agwile ntchito amati akupha ufulu wa anthu
Pepani apapa osanama zaonjeza #zimbe???????? Mpaka kuchotsa moyo. Anthu opha anzawo akuenda mumtendere kukafika kupoli station osapandidwako
Welcome To Malawi
Kupha munthu chifukwa cha nzimbe ?
Mulibe Mzimu Waumunthu !
Kulakwa Kumeneko !
Mmmmmm koma guys lets think about our responsibility to the community
Mwalakwa guys nzimbe weni weni mpaka mwapha munthu mwatenga sambi pa chabe bola anakakhala kuti anaba nyumba kapena kupha munthu …. munthu pofika kuba nzimbe ndiye kuti anali ndi njala zinthu zavuta ku Mw kuno kumaganiza nthawi zina musanapange zinthu guys
Exactly not good at all
so sad just for a mere mzimbe
amaba mizimbe kumakagulitsa ndalama kumamwera mowa
Too bad…killing coz of nzimbe…
Very bad……
Very bad……
mmm guys we must learn to respect life remember yu can tek someone’s life but can’t giv it back
Shaaaaa sugarcane has made him lose life. Very bad. A lesson to others.
Not fair
This is so messed up. Killing someone over sugarcane? And we claim to be peace loving people?
No!
Naye Nde Kufela Zaxiiiii
Oooh only sugarcane and it has costs someone’s life? #mothermalawiyousellyoursoultothedevil
Old news
ok…?zosakhala bwino I think he’s just a hungry man
Msambi abalee, simungamuphe mzanu chifukwa chamapesi. MHSRIP