Malawi mob justice continues : Machinjiri residents kill sugarcane thief 

Malawi Mob Justice

A 32 year-old man has been beaten to death by an angry mob after he was caught stealing sugarcane in Machinjiri Township in Blantyre.

Deputy Public Relations Officer for Limbe Police Pedzesai Zembeneko has confirmed the incident and he identified the deceased as Lameck Chibwana of Machinjiri. According to Zembeneko, on Tuesday.

Chibwana went to steal sugarcane at one of the gardens within Khukuteni village in Machinjiri.

Malawi Mob Justice
Mob justice on the rise: (Library)

However he was spotted by the garden owner who was also in the garden at the time.

“Upon seeing the garden owner, Chibwana started to run away but the gardener shouted for help. The villagers flocked in and arrested the suspected thief,” he said.

The community members agreed to take the thief to Mzedi Police Unit but on the way they began beating him until he died.

Meanwhile the dead body is at Queen Elizabeth Central Hospital for post-mortem.

Lameck Chibwana hailed from Khukuteni village, Traditional Authority Machinjiri in Blantyre.

Advertisement

184 Comments

 1. chonde chonde tisanapange chiganizo chathu tiziyamba tadzifunsa tokha mmene ife tilili.tisamadzitenge ngati ndife olungama .kuti tizingoweruziratu tokha choncho sibwino ai.oweruza momveka bwino ndi mulungu yekha.anthu ena atabwera naye mkazi wogwidwa ndi chigololo kwa yesu,chpncho yesu adalamulira anthuwo kuti amene akudziwa kuti sadachimwepo ayambe kumponya miyala mkaziyo.palibe angakhale mmodzi amene adachita izi.kusonyeza kuti panalibe olungama.chimodzi modzi ifenso sindife olungama.

 2. thats too much, kumupha mzako mkumuweruza, no one has that right its only God who knows how to judge, enanu mumapanga machimo onyasa okuti simumatenela kukhala moyo, but God never take your life away, He gives you a room for repentance.

 3. Zoti Malawi is A God fearing country sizoona ayi.zambiri zikuchitika zikuonetsa kuti satana akulamulira anthu ochuluka Mdziko la Malawi,eg kupha albono, uhule wa amuna ndi azimai omwe. Katangale ,ziphuphu, kuphunzitsa ana ufiti. Kupha nkhalamba.kuononga zachilengedwe. Kukodza ndi kupanga chimbuzi paliponse. Kuzunza nkhalamba, kugwilila wana.kusalemekeza akulu komanso makolo.ndidziko lamalawi lokha lomwe ndatchulazi zikuchitika in 100%

 4. Stupid pipo ndinkhani yophera munthu iyi how much is the sugarcane? Ngakhale sim’bale wanga koma i feel pain, so what is the benefit anthu opanda nzeru inu

 5. Aliense wachita nawo izi sazaupezanso mtendere. Waba chakudya munthuyu mkutheka anali ndi njala. Bola mukanangomugwira ndikumupatsa chilango china kaya chosesa pamalo panu pa mizimbepo, koma mpaka kumupha? Mbava zenizeni ndinunomwenso mwamuphanu, tsoka lanu muzimve mumtimamo

 6. Thanks Dr. sule for your kindness, everybody know HIV is a deadly disease I was once a HIV positive and Cancer, am from south africa am 32 years I contacted this disease when I was 27 I was using drug over since, just last week here I see this mary benjami testimony that her HIV was cured by dr sule so surprised when I read the testimony and I dont believe there is cure to HIV and I see another testimony about the same man, then I have to try I get the real true of this testimony and I whasaap the number below it and the man answer me he ask to t sent money to buy the necessary iterms that he wiil use in prepareing the cure so we can start immediately i send the money well I dont know how he did it but god know. I promise you,you we rejoice like me pls dont ignor this message is real god dont come to heal by him self he sent his servant and this man is used by god believe me dont believe that evil tout that hiv dose not have cure becouse there is nothing my god can not do just have fiath and try him this is his whatsaap no +2348162447651

 7. Anthu amene akubweretsa mavuto mdziko muno akungoziyendera okha pazimagalimoto. Anthu amene akuba ndalama zankhaninkhani pano ndi afulu..koma inu mukukapha munthu oti waba mzimbe..shame..osangatenga nsonga ndikukadzala bwanji? mupite mukagende anthu amene akuba ndalama zaboma, akuba mankhwala mzipatala..Do better Malawi.

 8. Tikhara tikupemphera kuti inuso murakwile azanu koma azanuwo akukhululukirani apampamene mungatengele umuthu afiti inu

 9. This is not the right way to treat thieves.Very bad .What is sugarcane after all ,pliz aMalawi tisinthe.

 10. This is not the right way to treat thieves.Very bad .What is sugarcane after all ,pli aMalawi tisinthe.

 11. Koma Gyz zinaz kungozipalamulira machimo kwa Mulungu nzimbe omwewu mpaka kupa zoona ayi zonse azaweluza eka mulengi mwini zonse tsiku lachiweluzo.

 12. Its too much. Bt i cud be happy if he ws suspected of killing albinos not stealing sugarcane. Anyway no reverse here. Bt lets learn to prosecute da suspects b4 we punish them.

 13. Mawa ndinu akanakhala kut mwapeza akubanyumba koma zimbe inalinjala imeneyo a police apangepokathu kumwambaso muli pamavuto opasa zanu chilango chifukwa chazimbe,

 14. HMMM MALAWIANS TIKUPITA KUTI NDINKHALINDWE LOTERE ABALE KUPANDA PAKA DEATH OF THAT POOR FELLOW MALAWIAN PIPO KUNJA UKU UR DOING ZINTHU ZOOPSYA KWAMBILI KOMA SAKUPHENDWA.KUTI MUONESESE MUONA KUTI ANALINDINJALA MUNTHUYO KUMENEKO KUNALI KUSOWA KUTI ADYE B4 U ACT SUCH CRUELITY MFUSANI MUNTHU KAYE DAT WHY IS HE/SHE DOING THAT AKUUZANI MAY B FROM THERE U CAN ACT HOSPITALITLY.NOW POTI POLOBULEMU HAS COME ON US B CONCERN CITIZEN 4 DIS POOR SOUL4 HIS BURIAL CEREMONY.MHSRIP.

 15. I FEELSORRY FOR THE LOSS. ONLY GOD KNOWS. ANTHUFE TIMAKANIKA KUPANGA MOYO KOMA TIMATHA KUUCHOTSA MWAKATHAWI KOCHEPA .ESH!!!!!! WHERE IS LOVE CHISONI CHIDZIKHALAPO POPEREKA CHILANGO GUYZ. WHERE IS THE LOVE MALAWI???

 16. I think amalawi wachuluka ndi umbuli ndi kuvutika, chomuphela munthu chifukwa cha mizimbe ndichani no no no no thats bullshit, osasiyila apolosi ndi a court ntchito yawo mxiiii. Bad.

 17. anthu akupha ma alubino mukungowaona,kuwapasa nyama kundende!! kumakapha munthu chfukwa cha nzimbe? mulungu akuonen

 18. wakuba nzimbe waphedwa koma wakashgate zake zinayera wat iz it my malawi. where to iwe malawi. Kodi mizimu ya John Chilembwe & other friends koma ikugona. pepa malawi. I crying 4 my country malawi.

 19. They have done well to kill him the man had done a lot before stealing sugarcanes.The 40th day had come to be killed as wages of sin.

  1. Wake up u barbarians, imbeciles, Moran’s. That’s wat Malawians are capable of. They take actions before thinking, koma never forget kuti the country is on crisis. Sugarcane that’s why tizafa ndikumavutika chifukwa chopondelezana Malawi is a pathetic country. Kupondeleza that’s why pa nation anthem pali njala, nthenda , nsanje. Wake up!” Kupondeleza that’s even koyenda kunja upeza chigulu cha amalawi chikuwopsyezedwa ndi munthu modzi, kunyenga, ufiti, nkhanza, kupha, kuba, nsanje ndiye kumalawi. Sleepy foools. Corrupted fools, agalu achidima m’maso.

 20. Where is your respect Malawi, beat someone to death because of stealing sugarcane? What is sugarcane compaired to humanlife? Police do something on this case.

 21. Sure Munthu Kuba Zmbe ndkumupha? Ah Amalawi Mwatan it iz not good, azathu nawoso al nd ufulu kukhala nd moyo. May hiz sol rest in internl peac

 22. Tell us their names so tht we cn sell them to the south african pple cz to kill someone cz of stealing is a bad habit,, thts yy we hve got police ndamene amathana ndi nkhani yakubayi

 23. hauza pa funso la MISALA. Inuyo muunikilapo pa mafunso onse okumayambiliro. Ndi amene akuwongeleleni kuti wolakwa ndani pakati pa wophedwa mmodzi ndi mob justice. I dont encourage Mob Justice to done un justifiably. But I strongly support mob justice bcoz it has helped in reduction of criminal behaviour hence easing police work.

 24. Kodi amene waba Mbuzi ndi amene waba Ng’ombe wakuba ndi uti? Kodi mwini dimbalo aberedwa mizimbe yochuluka bwanji? Kodi Blantyre yonseyo wanjala anali yekhayo? Kodi kumukhululukila sikukanakopa ena kukakafanizapo mizimbe yonseyo? Kodi iyeyo ndiwachibale wa mwini dimba? Chinamupangisa nchiyani kusakapempha kwa mwini dimba angakhale mnjila yaganyu? Funso lomaliza nali, kodi iyeyo anali wamisala?? Ngati yankho ndi INDE onse ayimbidwe mlandu wakupha koma ngati ndi AYI onse asayimbidwe mlandu. Ndikutan

  1. Hey Mr idiot.!!..dont take laws in ur hand….,,Nawe tikufunse..kodi wakuba amti akapezeka aphedwe?…kodi ,chinabvuta ndi chan..kupita naye kupolice?….Kuba sikwabwino..ngakhale ataba kochepa timadziwa…koma musaganize kut kuba kuzatha pomaphana.ok?,,,.ndi anthu angat aphedwa chifukwa chakuba?…ndiye ndibwino..kut anthu otere apolice azigwira vep yawo..chifukwa taona anthu atasinthika chifukwa cha ndende……anywae mwachotsa moyo….mukut uduli…tsopamo moto upita komwe kwatsala tchire..uyo kwake kwantha…Tione mwini Dimbayo ngat Sakalimira zimbe zakezo ku prison..(life in prison)…..chifukwa thawi zina mumaona ngat mukukoza koma mukuononga……khan yoti oberedwa inakamukomera tsopano itembenuka chifukwa wagwira ntchito..ya enuwake….# ma proffesional apolice ndi ma judge……Chonsecho kusukulu sanapiteko..chomww akudziwandinzimbezo..ndiwe yemwe

  2. Uli ndi nzeru, koma zauchitsilu!. Mwakholo lako linagwirilidwa kapena kugwilira, ndiye kubala sanakudziwe. Iwenso ngati uli ndi ana ndiye kuti amabadwira ngozi yosowa condom kapena umakagwilira. Usandilankhulise pambali. Wangoziwonesa kuti olo mwana wako nsungampange guide. Achitsilu.

  1. Zowoonadi ngati mene unapezela suit yako yangati wapachika pantengo chimutu ngati bus.

 25. Mmmmh that’s so sad killing someone just for a sugar cane… what’s happening to Malawi I grew up knowing Malawi is a peace country but now um scared….

 26. ULOVO UMAPANGISA ZONSEZI ANTHU AKUMANGOKHALA MMA LOCATION UMU NDYE AKAPEZA WAKUBA AMAKHLA NGATI APEZA CHOCHITA MUNTHU WA PA TCHTO WOPHUNZIRA SUNGALIMBANE NDIKUMENYA MZAKO CHIFUKWA CHA MZIMBE KOMA MA VENDA NDI MA SIKINI AMANGOPAMGIRA MOLARO MPAKA APHA MUNTHU CHIFUKWA CHA ZIIII NGATI CHIMENECHO.INE SINDINAWONEPO MUNTHU WOTCHENA BWINO ALI MU SUIT WA DOLA AKUMENYA MZAKE CHIFUKWA CHOBEKANA KANTHU KAKANGONO…….Anyway RIP but don’t forget #feesmust fall.

  1. Thief’s!?. Nawenso chinkhope chako ngati wakuba. Koma iwe waziwalo.

 27. Amalawi uwu siumbuli koma nkhanza kukula kwa amphawi okhaokha anthu olemela kale anaba ndalama bwanji sanawaphe. Akanakhala kuti Mulunga amalanga Nthawi yomweyo olo munthu akapempha amachita Nthawi yomweyo bwenzi tapempha kuti aliyense amene watenga nawo gawo pakupha naye afe. Musandide ayi pepani kkkkk.

 28. Aliyense wakuba adzafa imfa yowawa ndithu. Judge no one. it is written “… udzadya thukuta lako” so??

 29. foolish Galatians!!!..the so called peaceful nation(warmheart of Africa..is it true?)…..why malawians?..mmmmmh so bad…started well & now bad ending….nthawi nde yatha tikukhala masiku otsiliza,,mukapanda kusintha,moto ukubwera munyeka ambiri…

 30. N’chani A malawi?………Amalawi alero..popanga zinthu..mukumazitenga ngat Madolo,,,,think twice before acting…Simungatchuke popha munthu ndi khani zozira…,,Amalawi..no one z above de law….hope police will do something better for de killers

  1. Poyamba timatchuka kuti we are a people of ‘Warm heart’ and beautiful smiles. Koma pano tikutchuka ndikupha abale athu akhungu lachinapweri, komaso pfuko la ‘mob justice’. What kind of mob justice yokachitira mphawi wanzimbe? Shame!

  2. Very bad Bro..Thats y..uzaone olo..kumalawi..tizipani…mbwee,,Reason..aliyense amaziona kut ndi wanzeru atha kulamurira…komanso kupanga chilichonse,,which z bad mind…,,,,,,,Dziko langa…ufulu pano ana patsa Galu #Satana..

  3. Uchitsiru basi, kusazindikira, sugarcane=life, impossible life is precious, kupha m’bale wathu coz of Mzimbe, shame!!! Vuto la umphawi wa mdi choncho, kusowa zochita mapeto nkumapha munthu coz amaba mzimbe

  4. Uchitsirutu weni-eni…koma..ndikudziwa kut apolice apanga zonthekera kut,,mwini Dimbayo..Akapitilizire ulimi wazimbewo ku Prison….(life in prison)..nde tione amene anve kuwawa…akakhala..m’bake wanthuyo kwake kwantha ..moto upita komwe kwatsala ntchire Now

  5. A Malawi ambiri sanazindikire Zachepa, vuto nkutsalira kwa dziko lathu lino, ndipo tiri kutali tu ndi chitukuko ukuziwa, nkpsauka kuno Zachepa nchifukwa chake akuphana kamba ka mzimbe, zomvetsa chisoni

  6. Kkkkkk,,,ndaseka..mozinvera chisoni…..Sukunama…,,sure tilikutali..et Bro nzimbe?…..mwinanso Chimbowa cha nzimbe

  7. Hahahahahaha! Komanso atsogoleri anthu amaba kwambiri tu koma samaphedwa, mphamvu zawo zimawateteza. Billy Kaunda sananame kuti osauka alibe mawu. Musadzabwereso kuno pokhapokha ine ndizayambe kulamulira dziko limeneli hahahahahaha! Our nation is a century behind bro. Bagwirani kaye magobooo kumeneko hahahahahaha! Mu rize hahahahahaha

  8. Ha ha ha ha.Zachepa.Sured….Sindizabweranso…….pokhapokha upange zothekela….mwina iwe..utha kuzayendetsadi bwino….

  9. Ukundiziwa kale, nkhanza, chinyengo etc ndizachepetsa kufika pa very low percentage sinanga sizingatheretu ukuziwa iweyo…Ndizakhla mtsogoleri wa chikondi ndi wachilungamo kwa anthu ake hahahahahaha! Campaign ndiye ndi imeneyi ndayambayi

 31. Yes we all know that stealing should not be condoned BUT killing somebody for sugacane??? NO! Hopefully the police wil work to bring those involved into book. We are losing Umunthu at a very fast pace Malawi!

 32. Mmmm killing some bcoz of sugercan , really? police must rock those mobs in jail including the owner of the garden its so sad

 33. mmmm ayi apa nde mwalakwitsa mzimbe??? mmmmm..bola akanakhala walowa mnyumbatu …Mulungu akulangani nonse amene wachita izi….inu mmene mmapanga zimenezo munayamba mwazilingalira nokha kuti simunachimwepo??

 34. Kulima nkopweteka khasu sidzibwana ndiye iwe udzivutika ndi kulima bambo wina ndevu pepeya kungobwera kukubera? Shatapu! Ukanakhala kuti mzimbe sikanthu kofunikira bwanji anapita kukaba? Munthu walima munda ndiyenso udzikhalanso pantchito yolondera kwa anthu a ulesi?

  1. True Bro . . But the punishment its above de crime……sikut kuba ndikwabho…..koma pliz Apolice anakapeleka chilango choyera kotero..nkulu anakatenga phunziro..we learn through mistakes..

  2. True Bro…But the punish its above de crime…..sikut kuba ndikwabwino,,olo katachepa nkako..koma pliz Apolice ndiomwe anakapeleka chilango choyenera,,kotero wakubayo anakatenga phunziro…ndaona antthu atasitha chifukwa cha ndende…DONT FOR GET WE LEARN FROM MISTAKES…..nde pot mwapanga zinthu mwakufuna kwanu..ndikhulupirira kut..Nzimbe zimenezo..mukapitiliza kutilimira ku prison..,,Chifukwa apolice sakusiyani…Thawi zina anthu amaona ngat akukhoza akuononga…….iyo wapita ,,kwake kwantha..tsopano kwakhala kwa Mwini Dimba…nde tione kut anve kuwawa ndan?…..he he he..kaya sikhala life in prison kaya…

 35. Zinazi zimangokhala nkhaza munthu ukachotse moyo wa zako chifukwa cha nzimbe zoona….kuba sikwabwino nakoso kupha sikwabwino ….pamaso pa chauta ophedwayo akayakha mulandu oba nzimbe enanu mukayakha mulandu opha munthu ..tiyeni tizikhala anthu achisoni ndi owopa chauta..mitima yathu izakhala yofewa ..yochitilana chifundo wina ndi zake

 36. Kodi bwanji mumaleka kupita naye Ku police mukudelera ntchito yawo …komanso u don’t know Mwina munthuyu unali ndi Njala tiye tiphunzile kukhala anthu achifundo ndikuonetsetsa kuti tikusatira malamulo adzikoli moyenera tisatenge malamulo adziko kuyika manja mwanthu sindikunenena kuti kuba ndi Kwabwino ayi koma umoyo wamunthu ndi ofunika

  1. U knw Malawians..nowdays. akumazitenga ngat Madolo…chomwe akudziwa ndi Ma violence bas…which z not Gud….

 37. Kodi akadakhala mwana wanu wakaba zimbeyo kwa wina ndikumupha mukanava bwanji that’s not fair please think be for you kill the person rest in peace brother

 38. Kodi ndi chifukwa chani aliese amene ali ndi dimba aka gwila munthu kuti amaba nzimbe zotsatila zake ndiziwili kumudula dzanja wa ntcholela nzimbelo kapena kupha kumene kumakhala ku nkhwima chani

 39. Are you interested in Joining the Illuminati in any part of the world, Whatsapp the agent for more information +2347010357750..do you desire to be rich and famous in life? what do you need? are you a banker,lawyer,engineer,harbali st,pastor,lecturer,professor,business man or women,actors and actress,musicians,politician do you seek wealth,fame,powers or any thing you desire in life here is the opportunity to change your life for the better ,would you want to join the brotherhood? for more information kindly Whatsapp the agent for more information +2347010357750? ..or add him on viber or imo your destiny is in your hand

 40. Malawian Pipo Hw Can U Slaughter Ur Felow Man Jst Coz Ov Sugarcane?Mukulekeranji Kumpha Zimphona Zomwe Zili Ku Jail Zomwe zakhala Kupha Ma Albino Athu.Its Ashame Guyz

 41. Eee koma a Malawi mwatani? Mzimbe mpaka munthu kuphedwa nawo! Koma okupha alubino mukukamusiya ku police wamzimbe kutaya moyo. R IP

 42. Sinkhani yomuphela munthu iyi,zinazi zimangofunika kumvana basi,sizinayendepo apa,sindikulimbikisa mchitidweyu ayi koma aliyense amalakwa in one way or the other…

  1. Pepani apapa osanama zaonjeza #zimbe???????? Mpaka kuchotsa moyo. Anthu opha anzawo akuenda mumtendere kukafika kupoli station osapandidwako

 43. Mwalakwa guys nzimbe weni weni mpaka mwapha munthu mwatenga sambi pa chabe bola anakakhala kuti anaba nyumba kapena kupha munthu …. munthu pofika kuba nzimbe ndiye kuti anali ndi njala zinthu zavuta ku Mw kuno kumaganiza nthawi zina musanapange zinthu guys

 44. Msambi abalee, simungamuphe mzanu chifukwa chamapesi. MHSRIP

Comments are closed.