A 30 year-old farmer in Dowa district on Saturday committed suicide after failing to recoup the money he spent when growing his tobacco.
Dowa Police Public Relations Officer Richard Kaponda has identified the man as Mandaachepa Kandikana Kachipere.
Kaponda said Kachipere went to Kasungu in 2015 Kasungu where he was cultivating tobacco.
“When he took his bales of Tobacco to the auction for sales he did not come out with profits due to low prices,” Kaponda said.
The deceased later thought of returning home in Dowa at Kauma village.
When he arrived home, he told his relatives about the losses and his elder brother told him to sleep in his house.
“The following morning in the wee hours of Sunday 24th July, 2016 he was found dangling from the roof of his brother’s house after he hanged himself by using a rope.” Kaponda said.
Postmortem conducted revealed that death was due to suffocation and medical workers did not suspect any foul play.
Kachipere came from Kauma Village, Traditional Authority Msakambewa in Dowa District.
Very bad
Mmmmm
olima wina olemela ndi wina eish #kulima_fodya_nkulimba_ntima_paMalawi#
Inde braz…. Ndi mbavadi ngati alibe ndarama zogulira fodya, anene kwa alimi kuti , atsiya kugula fodya.
Kambanga mwara zinaukaona,koma mukudziwa kuti uphawi ndikhondo kupasa yamifuti?Nchikumbe uuse muntendere.
Anali ndi gogole uyu wagona kut sakwanisa kubweza ndi loss wapezayo
Chonde Imvanikoni Chisoni Moyo Wamunthu Wapita Banja Lake Pano Lili Pamavuto Fodyayo Amalimila Inuyo Kuti Muziyendela Magalimoto Opuma Koma Iye Angakhale Njinga Analibe Man R I P Koma Man Mwalakwa Heavy Simunaganize Za Ana Anu Kuti Mwawasiya Pa Dzuwa Ndawamvela Ana Abale Ndi Mkazi Wanu Chisoni
Eeeeh! Koma zafikapo,yambani kulimano mtedza ndi soya kumango kakamila kulima zosadyedwa ndizimenezo.R .I. P. MAN???
Feeling sad for this. RIP
Eish kma guys
kkkk
Rip!, a loss is part of the game in tobacco farming
Yes he made a wrong decision koma ntchio IJA ndiyopweteka kwambiri.kulima chaka chonse osapindula.pamenepo amafuna alipile ma tenants ,ndi ngongole zona but he end up getting nothing.mmmmm its painful
Aleke bwanji munthu kudzipha fodya umu avutila mkumakamubelaso kunsika
Lughano Mwalwanda
What kind of business where u does everything on ur own then someone from abroad comes n give u a price.
Zomwe Boma Lakoza Kut Alimi tisapindule Chaka Chino
Ndiye Demo wapangayo akhaulitsa nayo ana ndi mkazi waketu.
Komano kwa ine sichinakwane chifukwa chodziphera.
TAMA & TCC should change their names.
alimi naonso saamva…osangosiya bwanji ndikulima mbeu ina. & see if those stupid buyers will not suffer it.
Tobbaco farmers should protest by not growing this crop….
Ma company ogula fodya amayiwara kuti kupanda mulimbi nawoso business yawo palibe…
Zimenezi ndi zomwe a zodiak ndi a mec amafuna kut anthu adzathe ndikudzipha, koma ene ndimaona kut vuto ili adatibwelesela ndi chair.
ZIMACHITIKA MOYO UNO,BASS ANGOMULANDILA AMBUYE EMEN.
Ulimi wa fodya sizinthu…
basi dilu ndiyomweyo tikakumana heven lol RIP
ok
ok
malonda a fodya abvutadi mpaka munthu kuzimangilira?
malonda a fodya abvutadi mpaka munthu kuzimangilira?
#Gracious check yur spellings not MSB is MBS
#Gracious check yur spellings not MSB is MBS
1.Kulima Ndikopweteka
2. Zipangizo Zogwilitsira Ntchipo Polima Ndi Zongongola.
Mumugulenso Mulimi Momubera Mukuganiza Chani?
1.Kulima Ndikopweteka
2. Zipangizo Zogwilitsira Ntchipo Polima Ndi Zongongola.
Mumugulenso Mulimi Momubera Mukuganiza Chani?
mayyyyiiii iiiineeee iioooimayoooo
mayyyyiiii iiiineeee iioooimayoooo
Ooo! no good at all.we all know that,the problems are there!But with permaculture there many solutions than this.venture into permaculture my fellow Malawians
Ooo! no good at all.we all know that,the problems are there!But with permaculture there many solutions than this.venture into permaculture my fellow Malawians
Mpaka pamenepo?
Mpaka pamenepo?
Mwati, mandaachepa kandikana kachipere ndamene watisiya? Rip
Mwati, mandaachepa kandikana kachipere ndamene watisiya? Rip
Inde Man!!! Ogula fodya ndinu mbava zotheratu!! MSB…bwanji mkaoneso ma scale awo…..anthu amenewa kaya ndinyanga….sitikuziwa! Zoona fodya mpaka pano simunatigule, alangizi nawo akufuna tiwapaseso ndalama……nanga tithawira kut ife!!!!
Inde Man!!! Ogula fodya ndinu mbava zotheratu!! MSB…bwanji mkaoneso ma scale awo…..anthu amenewa kaya ndinyanga….sitikuziwa! Zoona fodya mpaka pano simunatigule, alangizi nawo akufuna tiwapaseso ndalama……nanga tithawira kut ife!!!!
Nkhaniyi ndiyowona kapena yongopeka? Zinthu za 2015 munthu akadzimangilire july 2016? Lol lol
Not gud to hear
Not gud to hear
Zavuta
Zavuta
Vuto ndipitalayu basi
Muzilima zodyedwa nanunso
mbuzi ya munthu
To commit suicide was not a solution to his problem but now he has added the family’s problems instead of reducing
Pali mau oti usaphe iye ndiye wazipha eeeeee panopatu ayamba kale kumukuntha komanso moto pambalipa
Usilu basi imeneyo nkhani yozikhwezera mbuyao
Wafela mavuto ake
Rip
Akulumwe waaaa koma pinangopi ungapiva kuphesa nsolo.Kuzipheranji thangwi yakuti pidakufambire tayu.adachite pywadidibi asiya mkazi na ana panyatwa.Ngamala pikhaziphepyo adakuva kupha tayu?Mzimu wache usause mumtenderebi
Shem
fodya sichithu chabwino komwe wapitako ndiye iii akaziona koposera apo chifukwa akakumana ndi chilango
ndizowawa chifukwa antchito,angongole zakatapira komaso za limbe leaf komaso zosatha komano thats a wrong decision
nthawi,,,,,rip
Very Bad…,but Government must do something for Famers..
Yah neh its sad
nthawi,,,,,rip
Iiii akadangosintha chaka chino ulimiwo sizozikwizingazo ayi sidilu imeneyo
RIP
Kuzipha si kuthetsa mavuto ai
RIP
Ok.
Wrong decision.Ofcourse nzopweteka he was expecting much.
Dats Gud Solution!!Hell Will Welcome Him!!
Shaaaaah
chonchobe ngakhale azipha MHSRIP.
Chonchi ndiye muziti mufuna mupite kumudzi mukalime… Nanunso mukamusatila mzanuyu Amili Saidi Manzy Phiri Allie Daya Trabo Phiri Rashird Robert M
hahahaha. tipitabe
hahahaha. tipitabe
Ife tinalima kale
Tapitani nanu mukazimangilire.. Ulimi wa chamba si zithu ankolo
Tapitani nanu mukazimangilire.. Ulimi wa chamba si zithu ankolo
Thats not government’s fault R.I.P
the simplest way to calculate profit is to set off cost with proceeds.if cost is higher than proceeds then,u’ve made a loss.this government is making the cost of producing increase with its useless policies.so its ridiculous to say what u’ve jxt said
Mmmmm i doubt coz there is alot happening in a country, the person could hv devised abetter way to solve it than that,e.g find another crop to grow the next season remember the govnt was tellin farmers not to rely on tobbacco only, as for me no pity for the man #nu_me
Life is hard now on earth, what we can do is to understand it
A mw 24 nkhani tizikhalira.ma sulcide kodi?
Mufuna azikamba zazibwezi?
Hahaha tamufunseni ndinu ameneyu #Dolo
Aaa ayiso koma zanyanya
Aaaaa athu timava zithu kupexa phuzilo
Kkk ok
Its really sad.ulimi ndiwooooovuta!
kkkkk, ndemunthu uziphe chifukwa sizinayende kumsika wafodya,, mmm.chamba sizinthu abale plz
Ndizopwetekadi ntchito yonse ija
No comment.
Malemuwa apta nd ndalama zanga
Get life bru. Of course he commited sucide, but that does not mean u must mock with death. It seems he was stressing a lot. So is it painful if u just keep quiet
Kkkkkkk!Ndalama Zngati?Kk!
Kkkkkkk!Ndalama Zngati?Kk!
Mayina a Kaliati ndi a Madness ,unalimapo fodya iwe kuti umve momwe ulumi umapwetekera Shupt
Mayina a Kaliati ndi a Madness ,unalimapo fodya iwe kuti umve momwe ulumi umapwetekera Shupt
Ulumi or ulimi shupt 2?
Vuto ndilakuti chilichonse chomwe amagwiritsa ntchito anthu amenewa polima chimakhala cha ngongole. Ndiye kumawagulaso mowabera aaaaaaa!!
shaaaaa koma ! its so sad’ Tama, Aret, TCC are not helping these farmers
RIP BRO,
Waziwa kuti sakwanitsa kupereka feez ya mwana wake ku University
madness thats madness how can you take your life over useless materialy things were as you can find them in future mhsrip
Simukuwaziwa mavuto madusa mwa while
mwakulira pa chinyezi inu mavuto simuwadziwa
mwakulira pa chinyezi inu mavuto simuwadziwa
Muuzeni ameneyuuu munthu kulowesa ndalama zambiri mbiri or ndi yako yomwe osatuluka mmmmm very bad ationjeza ogula fodya
Muuzeni ameneyuuu munthu kulowesa ndalama zambiri mbiri or ndi yako yomwe osatuluka mmmmm very bad ationjeza ogula fodya
Nde mpaka kuzipha. Ngakhale mulungu wakwiya naye ameneyu
pepani abale mavuto ndiyamene koma mayo ndi wamtengo wapatali umoyo watu ndiozala na mavuto even i myself have got a lot of catastrophy
APM shld ans tht,,,,, vry xry RIP.
so sad…God knws
MAYBE SOMETHING ELSE WASN’T RIGHT IN HIS BRAIN. . PEOPLE WE MUST LEARN TO CONTROL OUR MINDS
kkkk kkkk fodya si dhilu