…No erection allowed
…Gazing at others’ private parts not allowed during naked protest
The drama that has ensued after member of Parliament for Mulanje South Bon Winiko Kalindo dared that he will walk naked if there is no enforcement of a death penalty for those convicted of killing people with albinism refuses to die.
A statement that has gone viral which is purported to have been authored by the organising Committee of the naked parade has set out a few rules for the parade which are nothing but satirical.
Malawi24 has a copy of the satirical rules from the Press Statement and hereinafter it will be published unabridged:
PRESS RELEASE
NAKED PARADE IN PROTEST OF THE KILLINGS OF PEOPLE WITH ALBINISM
Hon. Bon Kalindo, MP would like to express his gratitude for the overwhelming support he has received from the general public for his proposed naked parade in protest of the ritual killings of people with albinism and their perpetrators. A good number of people have expressed their interest to participate in this parade.
However, Hon. Kalindo would like the general public as well as those who have expressed interest to take note of the following rules which shall apply during the parade:
1. Cameras shall not be allowed within a radius of 100m
2. Staring or gazing at others’ private parts shall not be allowed both among the participants themselves and the general public (onlookers).
3. Erections during the parade shall not be entertained. If you know you cant hold it up, dont come.
4. Commenting on others’ private parts shall be prohibited.
5. Any kind of touching shall be prohibited
6. While swaying of hips shall be allowed, pole dancing shall not be allowed.
Any person found breaking the above rules shall be deemed as one of the perpetrators of the killings of people with albinism hence shall be stoned to death.
ndili pambuyo pa winiko tizakhala limodzi
E MAYE NERA INE LOYID SHUGAR
kkkk no erection eti
Going with your mother’s in law sound suicidal to me. I will definitely go alone.
Ati osayelekeza Ku……… Kutani. Kkkkkkkk reflex response sapanga control. Tikaphela konko wins ndiiiithu Honourable Madalitso Nthenda kkkkk
Hahahaha! Aise imeneyi fans isazadye cassavatu
Hahahaha! Izi zokha za ma rules izi ayayayaya.. Amy Banda
nde mwati bwanji???? kkkkk idzakhale usiku basi
I join u winiko!!!
Cikho icichi chindi pitilile place
so bad, we understand that Mr Winiko is concerned, but he don’t have to reach this extent, no other ways to show the public
Inenso ndikunyamuka kuno ndikubwera
Ndilikonkooo!
Kkkkk…koma winiko akazi akenso akayenda nawo ali mbwamuswe???bolani asakhale akupanga comedy olemekezekawa
Kkkkk…koma winiko akazi akenso akayenda nawo ali mbwamuswe???bolani asakhale akupanga comedy olemekezekawa
kkkkk
kkkkk
That Will Totally Show How Sympathetic And Corncerned Malawian Citizens Are About The Bluto Kings Of Pple With Albinism. Thats What The Concerned Patriotic Citizen Has To Do! But Mmmmmmm Malawians Why Cant We Uz Another Way Of Showing Our Angerness Not This One. You Knw This Is A Very Repectiful Nation With Good History. Let’s Nt Copy From What The Other Countries Do. Lets Nt Spoil The Good And Respectiful History Of Malawi. We Are Complaining About The Rape Cases Here In Malawi, What Do You Thnk Gonna Happen After This Shameful Way Of Protesting?
You Will Have Your Innocent Grand Ma Raped That Means You Are Creating Another Vast Problem To End Another….
kkkkkkk long live malawi osa onana punana eti
Tilikumbuyo kwanu bwana winiko ndipo ziko limve ndithu.
it true
Abale ndani amene safuna moyo
Tose zikutiwawa winiko naye zapweteka kodi amalawi bwanji timadana ndichilungamo kutsata choipa winiko more fire
Winiko umandiseweretsa kkkk
Koma zoopsya kwabasi,
Koma zoopsya kwabasi,
munthu kupanga petition ku boma lomwe likulamulidwa ndi chipani chake chomwe si kuwukira chipani chake kumeneko. uku ndikutionetsera kuti boma la chipani cha DPP lalephera kuteteza anthu ake.
munthu kupanga petition ku boma lomwe likulamulidwa ndi chipani chake chomwe si kuwukira chipani chake kumeneko. uku ndikutionetsera kuti boma la chipani cha DPP lalephera kuteteza anthu ake.
Others sat by the grounds outside their work places yet nobody stopped gazing and admiring each other but ofcourse ladies were at a distant. Erection will be the order of the day asa.
Others sat by the grounds outside their work places yet nobody stopped gazing and admiring each other but ofcourse ladies were at a distant. Erection will be the order of the day asa.
APM can you hear this
APM can you hear this
am not amased we r talking drama instead of tangible solutions…this is ”Winiko tikuferanji episode 16”.. just fast forward it and talk sense..
am not amased we r talking drama instead of tangible solutions…this is ”Winiko tikuferanji episode 16”.. just fast forward it and talk sense..
his number pliz …nanga tizayambira pati..am a concerned citizen ithink this will help ….mahope anganso nde anaphedwa kale nde chondiletsa kumatcher sindikuchiona….
Koma ndiye zikuchitika kunyasalandiko .
Nanga mwangoz wina atatota anthu ali nkat moyend sindiye kut azangodula nkuponye galu.kkkkkkki koma nyasalandee
Bwelani nonse amuna azitho mulandu ogwilila kulibe patsikuli sakha wekha
zokomela ma hule izi. he could think of another best way than this . its abomination son to see his mother privacy. why my Malawi
Winiko asiye kubanda…. Apenga… Hahaahahaha
dahm I cant wait to see this happenin
kkkkkkkkk, stupid
Kkkk Winiko sazatheka ma jokes ndi parliament momwe tiona ngati zomwe akunenazo angazichite
tingophemba kuti mulungu zikoli awontche moto tachuluka machimo anthu anuwa ambuye muliwontche moto basi
Kkkkk all the best Mr Bon Kalindo
hiya ambwiye hosatheka iyayi apunana ngati amavuta iwo zalewa alimudelesi hi kamuone patetete zavuta basi tikokelana kupandatu basi hi nanga nitani handionjezatu,hasakuwapanga mbuzi mbuzi hanthuwo bwanji?tikamudye uwende hachitira kaza zakewo?nakwiya nazo ambwidye.
Tikavulira komko?????
Che winiko muwayendese anthu maliseche kkkkkkk ndiwe wamadramadi hahahahaha***
He make history
Za mkutu nde zikugwirixana bwanji Zophana ndikuvula?.
am ready for that match Viva Winiko
this is what happens to disillusioned individuals i understand his state of mind and naked parade
Ndiye mwati mukavulira kuti?lizakhale tsiku loweruka kuti ana nawo azaonelereko zabwinozi
This is not spiritual according to the bible. Koditu MULUNGU siwopusa, find another way of protesting. Mukufuna dziko lichuke ndizimenezi? Munthu sangavule pamaso paapongzi,anaake, neba, bambo ndi mai ake, achimwene or sister wake. Think as a MP not as a comedian
Just visualise a naked Winiko marching on the street! kkkkkkk
Just visualise a naked Winiko marching on the street! kkkkkkk
Bziko la malawi limadziwika kalero chifukwa chowopa #Yehova.koma lero ili pa number 1 kuchitata mchitidwe odana ndi #Mulungu.zoti anthu azayenda maliseche tazimva.koma funso ndiloti.KODI ZIMENEZI MUKUZIWA ZITHA KUPANGISA KUT MATENDA A EDZI AFALIKILE?AFALIKILA BWANJI?.Kumeneku kukakhala azibambo ndi azimayi.ndiye avule onse.pali azimayi ena oti chiyambileni akudziwa maliseche amunawo basi.ndiye akawone mamuna wina ali ndi zinthu zochuluka,(maliseche akulu)pamene mamuna wake ali ndi kakang’ono.kodi mzimayi ameneyu samva njala kufuna chachikulucho.pls maliseche tiyeni tiwalemekeze.Winiko ndi wasewelo akufuna poti atchukilepo.asiyeni avule.muzawone azibambo adela la chigwa cha Shire.Chimwawa ndi Nsanje.muzabisa ndudu zanu zafodyazo
Bziko la malawi limadziwika kalero chifukwa chowopa #Yehova.koma lero ili pa number 1 kuchitata mchitidwe odana ndi #Mulungu.zoti anthu azayenda maliseche tazimva.koma funso ndiloti.KODI ZIMENEZI MUKUZIWA ZITHA KUPANGISA KUT MATENDA A EDZI AFALIKILE?AFALIKILA BWANJI?.Kumeneku kukakhala azibambo ndi azimayi.ndiye avule onse.pali azimayi ena oti chiyambileni akudziwa maliseche amunawo basi.ndiye akawone mamuna wina ali ndi zinthu zochuluka,(maliseche akulu)pamene mamuna wake ali ndi kakang’ono.kodi mzimayi ameneyu samva njala kufuna chachikulucho.pls maliseche tiyeni tiwalemekeze.Winiko ndi wasewelo akufuna poti atchukilepo.asiyeni avule.muzawone azibambo adela la chigwa cha Shire.Chimwawa ndi Nsanje.muzabisa ndudu zanu zafodyazo
Kkkkkkkkkkkk koma kumeneko more fire Mr mp winiko
Kkkkkkkkkkkk koma kumeneko more fire Mr mp winiko
He is insane
ine nizavulils kunyumba kumayenda koma nizakhala ndi girl friend wanga
Ife ku nyanja kuno tazolowera kusamba maliseche ndiye tiri wokonzekanso iaaaaa,kkkkkkk
nde mwati no erection and gazing??.. enawa zawo ngati analumalazo shaaaaa kukavuta…. ine ndikayenda ndi mkazi wanga.
get agrip n’ grow up both admin n’ winiko plz
Ulendo umenewu tili limodzi aise Winiko
eeee koma yaaah
Ine l wil join mr Winiko
anthuwo akavula ndekuti anthu okupha ma albino aja asiya?pamenepo sindikunvesa
Let’s just find ways of dealing with these barbaric acts than exposing our privacy. Mufuna a chazukulu anu alaulidwepo kkkkk
These killings and abductions r barbaric, devilish, evil and unhuman. But i dnt understand hw the display of our private parts fits into this. Otherwise evryone is entintled to the right of life regardless of our genetic differences.
Musiyeni munthu ayende bamuswe zamukhuza
Kodi amalawi ndi chaninso abaleanga nthunduwanga bwanjinso aazaaaaaaaaaaaaa joooo mpaka apa
ine ndadula kale ticket mawa ndikwera bus ya Zambia-malawi nawe nduzaguba nawo basi
ine ndadula kale ticket mawa ndikwera bus ya Zambia-malawi nawe nduzaguba nawo basi
Am very concerned with the issue of killing albinos,,,,however lets pray hard that this man should not go mad
Ana achibwana .awaaa za manyi nkhosi basi
aaa malawi wanga akupita kuti? kkkkkkkkkk!!!!!!!
kkkkkk Tamusiyeni ndiwama comedy uyu angofufuna kutisekesapo apa
awiniko ndigwape yamuthu adzavule mesa ndichipani achakwawo bola mudzangonditumizila ine ndizaziwone kuno
tiyeni nazoni awiniko anthu awone mphiri,ndi ti a salulu ! apanda ku vomeleza next guess will be Sex in public. since kupha munthu 4 body parts ndizoopya komanso ndi malawulo.
but i think such protest arent good! akangopanga vigil kaya ku high court, parliament or state house… why walking whle naked?
We vote 4 Democracy bt in Democracy ai ndithu zoona munthu kupha mnzake mosinga ndi mpeni nkumakhalanso ndi ufulu omangodya mgaiwa ku prison moyo wake onse.Ngati maphunziro ophera munthu adatha ku prison ko tazingowathililani temic enafe ndi a mdulidwe pamalisecheponso eee mapeto ake ndipatapo mlandu ogwilila kotelo ndizavula koma ndizangokhala mnyumba.
ife takonzeka!!!!!!!!!
Mwangofuna kuonesa malisechewoo ,mwina ndi a chisena
Akufuna atchukile2 sinanga akuziwa 2019 akupakila,,,,,ana ndakazi ake akuwaganizila bwanji?u call that a leader too?kkkkkkkkk
The police must release all suspect found with human bones to the community
Kkkkkk nde mwati azakhale amuna okhaokha? Kapena aliyese
Kkk Ngwazi Amuna Gremie
Akudwala uyu iiiiiyaaaa
kkkkk kkk no comment
koma after ma demo kudzakhala kulasana hvy
Uncle kalindo i will join you
Kupha munthu ndi tchimo osatero ndichifukwa chakupsya mtima ena akuti ayende maliseche. Zosathandiza.Zokoperazi mudzalakwitsa. Akamati zionetsero kumatcha,pachionetsero pazifanana ndi zomwe inuyo anthu mukufuna monga kaya ndale,mumayenda mmiseu ndi ma flag anthu amadziwa mukuyenda za chipani olo za kugwiririra ‘rape’mmaonetsa maliseche komabe zamkati mutavala. Koma izi nde ai kuonetsa maliseche chifukwa cha kuphana?’Be civilised’inu nomwe mukuti anthu avule,asaonane maliseche. Missing the target
NO WONDER.. ndnamuona pa tv ya m.b.c ali nd nyamilandu akuyitanira anthu kwa prophet wna wake..ithk amutuma…uko.
Maganizo a honourable amenewo kikikikikiki iiih zinditalikile mmmh,Malawi eeeeh
Kkkkk, Zoopsa Ambuye Bwelani Nsanga,
hahahahahah mpanje adaa yafikapo
kkkkk ķodi ndiliti abale mwina mkuzakoñzekà kumwera tu mowa mwina mkudzapha mañyadzi
Amene mukudana ndi maganizo a Winiko Mulungu akukhululukileni.
kkkkk ķodi ndiliti abale mwina mkuzakoñzekà kumwera tu mowa mwina mkudzapha mañyadzi
Kkkkkkkk Koma winiko
akazi akeso adzaende maliseche,kupanda apo banja lidzakhalaposo?
Kkkkk tikubwera kokho
Kkkk kkkk kkkkk!! Koma Guyz!!
Have they given their CHILDREN the rules. Remember that you are husbands/fathers of which such irresponsible actions will have life long effects on your families.
Zooonadi Mr MP
Mweziwu sichina ayi
Kodi pali azimayinso?zilemekezeni abale…musalore munthu wadzitsuzo akupeperetseni….kuyenda maliseche will not solve the problem we have mow.mutangozionongera mbili anthu ana anu aone malisache anu.pali makameratu amajambula or 10000km…stop the killing of people wit albinism. .they never chose to be one
Zokomera anthu otamba zoyenda buno bwa muswe.
We are ready .
Aaaasa koma ndiye kuzakhala nchito! Mabatchala ndi ambeta basi akavula. Ndani angaloleze mkadzi wake akaonese New York?
NAKO KU MULANJE KULI ZINTHU, ENA MALISECHE ENA A KWINAKU AKUKHAZIKITSA DZIKO LAWO. ANTHU WOPENGA MWAPANGA BWANJI?
Don’t n worry guys, l will distribute dick lockers free of charge.
Humour, kkkk Nazoni
Kaya tiziona
Kkkkkk vuto lovotela azisuzo angoikako thabwala bac
Mutiuzetu tsikulo ife takonzeka.
Enjoy the meat forget the animal kkkkkkkk Malawi sidzathekadi
Press TV once beamed a group of naked men in a certain country protesting in such a fashion. they were ridding bicycles in that state. no erection rule was also used in that protest. one guy complained that he was suspended from taking part for breaking this rule, however, he denied having broken any rule. my only question has sth to do with the issue of PUBLIC DECENCY; wont this kind of protest offend the public decency norm? have the police been informed? to whom shall the petition be presented?
Offend who? That the whole point, it’s to get enough attention
Kuletsa makamera its okay
…koma kutota sumachita kufuna munthu..koma sibho abale…vomelezani kuti okupha aziphedwa osadikira mpaka olemekezeka ationetse michira
That’s fake as fuck
this is not drama abale ndikuwawidwa ntima si wamisala Winniko koma palibe chikuchitika mutakhala inu yo muku phedwa ngati buzi kapena nkhuku abale wa ku ntcheu unja bwanji zimawawa munthu kuphedwa ndi galimoto nde munene chikwanje amalawi zoona? ambilinu mukudziwapo kathu zoona munthu ndithu kupha ngati monga aphela nkhumba mailko ena amaponga zionestelo ali maliseche amayakhula zopelala ena mukamba apizi? nonse musutsana ndi Winniko God bless u.
Be serious, there is more that can be done rather than this drama. Infact this issue needs to be addressed with sober mind
Dzatioloseni mbuye wanga…
Kodi wapenga? kapena kukalamba paja nzeru zimabwerera ku umwana.
Koma chonde muzamete patsikulo kkkkk kuti ndizaonesese ine zomwe zingayenere kuthesa mabanja kkkk
Kodi zoyenda malisechezi tinganene kut ndi mulankho wa dziko lonse poyimirila azanthu a ch albino??
Akati ndiyenda maliseche doesn’t mean uvule ndekuti ndi panti ekha osati kuonetsa ziwalo zobisikazi please respect private parts
kkkkk will be best match
Winiko apa ndiye wapenga misala kkkk
Ithink dis guy so called Winiko something is wrong in his brain,in addition he,s not matured enough 2b a member of parliment
He is fit to be a member of parliament. Are u happy to hear or see people with albinism been brutally murdered like this? Im behind him.
tell him and he is lucky that he was born not albinism
i totaly agree with Bon Winiko a true malawian.mukanakhala inuyo wachialubino you could have seen how painful it is to live with fears of being killed.u see death at your doorstep.
Ndi zopweteka izi
Ndi anthu ngati ife tomwe. Tangoganizani muli inuyo kapena mwana wanu, mudakazinva bwanji? Winiko is a patriotic malawi. We need mps of such cariber
Mwina akukhuzidwa ameneyu.. Kulankhula kopanda nzeruku bwanji. Zikuphweka coz sizili kwa inu.
Zanu zikubwera. Tidzakuonani…..
Im 100% agree with Winnico he knows hw painful is by living in fears in ur own home like malawi lets not tolerate such nonsese.
ndiwa misala winiko
Dziko muno mukufunika anthu ngati winiko, he is not fool he knows what he is doing bro
his number Pliz nanga tizayambira pati…concerned citizen …
He is the only powerful real parliamenatarian.
am also ready to join Kalindo am going there
Kkkkkkkkkkk
Why we malawians to come at this extend. This is total unfair for the nation. How embarrased you want tobe at world level. If we are poor lets admit our porvety and leave albinos
PRESS RELEASE
NAKED PARADE IN PROTEST OF THE KILLINGS OF PEOPLE WITH ALBINISM
Hon. Bon Kalindo, MP would like to express his gratitude for the overwhelming support he has received from the general public for his proposed naked parade in protest of the ritual killings of people with albinism and their perpetrators. A good number of people have expressed their interest to participate in this parade.
However, Hon. Kalindo would like the general public as well as those who have expressed interest to take note of the following rules which shall apply during the parade:
1. Cameras shall not be allowed within a radius of 100m
2. Staring or gazing at others’ private parts shall not be allowed both among the participants themselves and the general public (onlookers).
3. Erections during the parade shall not be entertained. If you know you cant hold it up, dont come.
4. Commenting on others’ private parts shall be prohibited.
5. Any kind of touching shall be prohibited
6. While swaying of hips shall be allowed, pole dancing shall not be allowed.
Any person found breaking the above rules shall be deemed as one of the perpetrators of the killings of people with albinism hence shall be stoned to death.
Kkkkkkkkk
Koma mwafasako anthu kumudziko ndithu
Koma mwafasako anthu kumudziko ndithu
Kkkkk awin
Hahahahhahahaha tienazoni tikazione zimenezo……. Koma ndye ma bhongedwe akakhala high2,, ndye muzitsukiletu-tu……..
Ndiye ndi mithubulo mumamwa daily mudzalimba a Winiko ?
kwa ine erection yo eeeee
kkkkkkkk koma zinazi kambanga mwala ndithu
ndye ku Malawi kumeneko kkkkk
Kkkkkkkkk koma yaaaa mwafasako ku Nyasalande
Kkkkklkkkkkk koma tizaona zinthu ndithu nde mwati ndiliti ndikonzekere
Mudzatiuzako tsiku ndi nthawi Awiniko tidzaone nawo
It shows that winko is stupid killing albino is not good .walking can’t stop the killing find another way
Mai kalindo akakhala konko….lol
Walking naked is not a solution mr MP muzakula liti?
ma shadada awoneke basi.
Govtmt z de founder of dez babar actv why they’re jst stay calm wtht taking finalstep;(
Nde mwati chilombochi chidusa liti kkkkkkkk.
ngati udzayenda nawo …………………………………… nawo . mwati no zisankho pa tsikuli ?
kkkk zavuta
Komatu ngati mukumasuta chamba pa tea break ku parliament ko ndiye mwayamba udyo
Are ladies welcome to march?
apapa ndiye kuti parade siitheka basi chifukwa erec mukulesayu ndi ovuta kumupanga control especially maso akaona, kkk
koma anaiwala rule imodzi kuti osameta mabwizi/mavuzi sali ololedwa kuzapanga nawo
Zikawoneka komweko
Mwina Winiko ndibatchalatu komaso mutu wake suyenda bwino. Munthu wanzeru wamzimu komaso okwatira sangavule nkumayenda mumsewu
Well, its unfortunate that drama is taking centre stage than serious business to do away with the vice of albino killings and abductions.
Ok? Azizayenda to coz commotion cholinga those with albinism azasowe on that day? Hes trying to cover up something am telling you… He knows this will get more attention just wait n see.
Mulowelerepo Ambuye!
Stop dramatising serious issues.its getting boring.
kkkk koma guys ndaimika manja asaa mwati no erec what? mmmh Malawi wanga ine
jane bwa?
kkkk chonena chagwera mkati
Kakakakaka koma yaaaaaa kuli Zithu
ndie mukavula koma zinthuzo kumangopitilirabe simuzaoneka uchitsiru
Koma ziriko inendimaona ngati bodza avuladi zatsimikizika apa chenjezo kwaomwe malota satana chilombo choopsya tangopitani patsikuri turo simudzationa sure
Foolishness at its best
complete foolishness
I think kuti tizapewe ma erection pazafunika kuti tipeze malo oti anthu tikabozane kaye b4 we start marching
kkkkkkkkkkkkkkkk iwe ndiwamisala straight kkkkkkkkkkkkk
Chonchi kumati pali Olemekezeka apa? Kuphwekesa u mp
kind of like this Winiko mp. how about him being a president ?
hehehe Koma kuzavuta ndithu mitondo mmanja kkkkk
Are there ladies allowed
thats ironic
zioneke pamalawi ndizanyowani winiko tiyenazo anthuwa akuphwekesa Malawi wanthu kukhala Malawi woipa
koma abale
Kkkkkkk kkkk koma a winiko wokha
Mukukana chani musiyeni ayende
Koma dziko la malawi laling’ono koma zochitika zazikulu zikulu…nthawi ya Mcp anthu amkakaponyedwa mu nyanja,nthawi ya UDF azimai amkadulidwa mabele,nthawi ya PP cashgate,nthawi ya DPP anzathu albino kuphedwa,yatsala nthawi ya Aford…kuti kudzachitika chani….
Aford ndi anthu odzindikira,adzangomubwezera ku mangalande matchonayo coz ndi amene abweresa malonda opha ma albino.
Kkkkkkk ukuwaikila kumbuyo a Aford…
Kkkkkk, eeee please guys nonse a kwa Ziyenda mmanja ku Ntcheu, don’t participate…. You will be stoned to death…
Why???
Gyz Chilombo Chikulila Kom Chadzuval K.k.k.K
Ndikale ndidakhumba nditaona katundu wanu bwana ambiri amanama kuti ndinu wakuda koma katundu wanu ndiwachizungu mukazavula ine ndizavotaso turn inayo chikhala chitukuko chanu bwana
kkkkkkk i cant stop laughing
Ccta apa zavutatu basi
ndaona zavuta apa
Madness at ts bst
Sindinawerenge, ndiwerengabe nthawi ina.
Nde mphepo yake imeneyi, mabatire amakhala ali nguuu, ziwindi-ziwindi kkkkkkk tiye nazon
ONLY MEN OR BOTH ? KKKKK
Mbolo yake iti ingayende pamtunda osadzukayo bodza bas
ok tamva nde mai kalindo tikakhala. nawo limodzi?
mbwana mp mukakhuta ma drick muziyakhula zabwino osati zonyasa mongainu mungabvule ndikumayenda musewu niye ife tikumfuna inumukhale oyamba kubvula kenako imfeso tibvula zopunsa ife ayi
Are you crazy????
Koma zilipo ine ndidzangikhara penapake ukumagona katundu wa athu akumvina
kkkkkkkk koma ziliko chaka chake m’chino
kd mukayenda naked ndiye chithandize ndi chani kt khalidwe lokupha ma aibino lithe? uchisilu at it’s lowest point
Ayayayayayay!!
Lol no erections allowed
kkkk
Ofcoz ma killings a ma albino akupweteketsa moyo komano kuvulako nde eeeee zingoonjezera zochita moti anthu akhare busy kumakambirana za momwe tingathetsere mchitidwe okupha ma albinowu azizakhara busy kumakamba za ma size azida zanuzo ? Kuzangokhara chipwilikiti chabe poti mmmmm ganizani bwino man
hahaahhaahaaahaaaaahaaa
zafika povuta iwe tangoganiza anthuwa akuphedwa mwankhaza ngati nkhuku oti ine ndili mgulu lokachita nawo ndithu
No punani admiring be redy for highest number of rapecases
it will no longer be raping but as dogs, goats, cattle en other animals but in time of Adam and Eve.
Winiko umandisewesa……..kikikikkk
Azayambe kuvula ku state house ndi aphungu onse
kodi nd amuna okha okha ali so concerned
Bt there z no need to walk naked mr mp we don’t want 2 see hw big u are #mkabudula
As far as im concerned am at Winikos side. Killing people with albinism is evil. More evil. Mutation is not something that should divide us people hence matching naked is a must
Something very pathetic indeed how could somebody who is normal slaughter his fellow human being as if its a lamb?I also support Winiko’s cause and i will also be part of the whole procession.
They are just like us. We just differ the genetic make up!
I am bringing my dick too
uchi wako wan’dulidwe paja..kkkkk
Hahaha tiyeni tipitise ma weapon athuwo basi. @ Zita,it doesnt matter lol
kkkkkkk mwana ndi no gazing and erection..kkkkk akatchera mifuti
Ha! Abambo maso nde oyang’anawotu. Tikaika tintedi kapena?
kkkkkk tintedi wachepa nsaru kumanga kunkhope + akatimanga machain ngati maslaves kkkkkk
Hahaha ndinziwira john muja. Akadula ma chain mbamba. Kufuna kupenya gama
kkkkkk kodi ndi liti timwe madzi okwanira ikakhale long standing tikagwetse mwambo.
Cry My Beloved Country…..
Nanga nsapato?
Maliseche eti? Kkkkkk
vuto lake yanga ndiyamanyazi sifuna kuonekela imakana kuitola usilu
Kkk Zachilomwe ase, Zamakutu namudya namukoka tikazione, nazo zachitonga zili phwii ngat panyera ng’ombe, naye nsena yake ija mchila ngat Bulu zili kumeneko go konkoooo
kma nde walakatulatu….
Kkkkk musadzasale ambwiye mukazionere nokha
koma iwe galu zedi.ndiwe mtundu wanji wamunthu?
Ya Ntongayo nde ya ndi wanza
kkkkkkk kkkkkk mbuyache umatha kkkkkk ya mdyomba yopanda chipewa? kkkkkkkkk
kkkkk pepani makosana ngat simukaugwira zanu izo
kkkkkkk…eeee koma mwayankhula man
jkkk mwatero?
Kkkkkk midyomba yabeya kkkkk tikaionedi kkkkkk
za drama izi kkkkkk
is serious bro
Msata wa mbwiyaku, uwakambiyi wo akutuma kuti pamataku pawu
Uku ndiku kukamba kwa uyu. Ausu ndi a nyoku wakukupeleweza ndipu mitu yau njakupele.
Mwana wakukuliya mthangala iwi
Ahaha njakupele? Ukukamba vichi? Jemanja mkuwecheta yamanyi pelepa ife sitimanva zmenezo manje ungakhulume masimba walongosi futseck!!!
kkkkk masimba amakhuru nyani
kasi nananga vichi imwe mwa wanthu. kkkk
kkkkkklkkest eee koma yea ee
koma
Sizikugwirizana olo mpang’ono.
Leopard apa mukavilila nkonko ndithu kkkkkk
angopitiriiza anaziyamba kale
Angie Helen Botha
Ahahahaha#nafwa#if you can’t hold it don’t come oh!!!hahaha
Koma mkazi ndi mwamuna angagundane mu chigulu without erection? Zizakomera akazi izi…..mutiuze tsiku ma 4n azakhale ozaza….plus new memorycard for 4tos
kkkkkk iiii!!! Amwene zizakhalatu zoopsa kwabaasii!!kkkkk Bola Asazagwililaneko.
Ine Ndendidzavala Pamti Mmutu
I Will put my underwear on my head lets join him
kkkkkkk ndiye mwati palibe kusuzumila punana wanzako heitiiii?
Kungosuzumila ndimwayi
kkkkkkkkkkkkkk u r not serious
Hahaha
mhkkkkk koma mun’de?wandiwaza ndi coment yakoyi bmanji!kkkk
mhkkkkk koma mun’de?wandiwaza ndi coment yakoyi bmanji!kkkk
hahahahahhaha kkkkkkkkkkkk lmao!!! no erection ndi deal yabho!! kma zingatheke kuyenda ndimabebi nonse mutavula without kubonga? no way!!
Hahahaha mpikisano woonetsa Anamlondola kkk Anamgogoda kk
maso alibe mpanda dolo.anthu akasuzumula zida
Kkkkkkkkkkkkkkkk!zoonadi man
kod akaloraxo kuteNga Ma selfie????????
kkkkkkk Malawi @51
What about ma journalists and passersby,also not allowed to look?
They Say No Cameras
Its not only Winiko, we are many. Some of us have been rehersing since Winiko made this proposal. Dont take it as a joke! Enough is enough!
kkkkkkkkkkkk usandwaze
Rehersing, where exactly?
Bonifaci, rehersing mu tima street ta kwathu
Bonifaci, rehersing mu tima street ta kwathu
Kkkkkkkkkk ukooooo
hahahaha rule #1 and #2 kkkkk
Koma chambachi
ndiye pamenepo awiniko akuti tizavuliretu kunyumba kapena tikavulira komko ku msewu ? pamenepo sindikuvexa….
Tikabvulira Ku Parliament
Koma abaleee! Kkk
ok zovala akatisungila tikavala tikazamaliza etiii nkhani yabwino
Koma A Bale Zinazi Ayi Ndinthu. K K K K K
Ineyo mza matcha ndi iweo Linda Nyasulu, tikaone zachitumbukazo kkk
Kkkk
kkkkkk hahahaha Tizavulira kunyumba nkumapita kuzavaliranso kunyumba kkkk mwikhoooo
Kkkkkk Koma
nonse mukakavula mufunsidwa mukaike mafoni anu mmatumba kkkkkkk
Afuna Kuzavula Ndine Ndani?
ndakomoka nkuseka…bwa bwa bwa… njamadoda okhaokha akazi aye chifukwa lamulo la no ere***n sizagwira. koma killing of these innocent ppo, is not fair.
Kkkk funso loseketsa kwabasi,kkkkk
go konkooooo basi iyaaaaa
Aah mzamasewero izi ndawona
kkkkkkkk
hahahaha
Kkkkkk koma zinazi, koma zizathekadi? Bola osamazasowa awiri awiri kkk
Kkkkkkkkkkkkkkk koma adhaa aaasssa,,ndakomoka
no wemen allowed
cant wait #ONfollow venue and date pliz notify me
tikavulira poyambira ndipo tikavalira pothera. pafunika kuyenda ndizikwama. Apolice nao tikayenda nao atavula
Shaaaaaaaa tikavulira komko
kkkkkkk ziliko!!!
kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk winiko the grt
kkkkkkkkk komatu patsikulo ntchito ikakhalapo shuwaaaaaaa
koma za date Mwamvaa etiii …
bambo inu misala imeneyi pangani at your own risk
Wamisala adawina nkhondo kkkkk nthyolo mulanje = Mulli kkkk Bwapini paying loan kkkkk bwana you are murderer
We are still waiting to see how stupid you are!
Malawi!
Big up # winiko
Yanga ndizaveka jumbo!
kkkkkkk
kkkk,let him go nd walk naked,pple will see nd forget
Kuyenda maliseche ndimlandu kumalawiko. Mumuuze ameneyo