Skeffa responds to stroke reports

Advertisement
Skeffa Chimoto

Musician Skeffa Chimoto has responded to social media reports that he has been attacked by stroke.

Reports have been awash on social media that Skeffa Chimoto has been struck by a stroke that has caused weakness in his legs such that he cannot wake up from his bed.

Skeffa Chimoto
Chimoto: Goes angry on ill health rumors.

According to the social media reports, Skeffa was introduced to a satanic church through his friend in Zambia.

But when he was asked to sacrifice his daughter and wife the musician refused.

The refusal led to a leg stroke for Skeffa. However, the Chinamuluma Chakuda star has denied the reports labelling social media as a platform for stupid people.

“Social media is for stupid people and they tell stupid people because a wise person cannot believe social media. What I can advise people is to use their God given heads to find the truth but as of now am very fine walking from the market to home,” Skeffa told a local radio.

Since entering the music industry, Chimoto has made hit after hit with famous songs like Chikondi Chabodza and Chinamuluma Chakuda.

Advertisement

386 Comments

 1. When a person gets a higher position or prosper in life, you have to admire his position not the way he have used to get to that position coz pamakhala njira zambiri zofikira pamenepo, zina zabwino zina zoipa, choose which is better for you. These are tough issues coz anthufe sitingadziwe zoona zake chifukwa ndizachisinsi but God knows.

 2. Only God knows dont worry about some pple ur the best of the best in malawi always i love ur songs and am ur fan.

 3. Kd amene akuba Ndalama zabomawa or kupha azawo kapenaso anyanga si asatanic? Pakut zones zolakwila mulungu ndiye piano mukuweluza skeffa

 4. Kd amene akuba Ndalama zabomawa or kupha azawo kapenaso anyanga si asatanic? Pakut zones zolakwila mulungu ndiye piano mukuweluza skeffa

 5. So what????? Am minding my own business,and busy with God,I don’t care if you are a Satanism or not your heart knows the truth and that truth it can not be hidden in presence of God!!!! What I can tell you is only born again Christian,who obey the word of God and only those who do the will of God shall see God,and be with Him in heaven for internal life and for those people whom I do not mention them kugahena chilango ndi kulira kosatha……..finishhh

 6. So what????? Am minding my own business,and busy with God,I don’t care if you are a Satanism or not your heart knows the truth and that truth it can not be hidden in presence of God!!!! What I can tell you is only born again Christian,who obey the word of God and only those who do the will of God shall see God,and be with Him in heaven for internal life and for those people whom I do not mention them kugahena chilango ndi kulira kosatha……..finishhh

 7. ZAMABODZA NENELENI INE,MBIRI YANGA IPITSANi INE ,ONYOGODOLA NDI NYOGODOLENI INE KOMA MUDZALEKA,MUDZALEKA @INE KHONDO SINDIMENYA NDEKHA ANDIMENYERA KHONDO NDI AMBUYE INE MWINI WAKE NDILICHETE NDATI@MUDZATOPA. Nsanje simanga mudzi

 8. This is not about being rich, it’s about reality of what is happening now, you can deny it but it’s real. Satanic now is own a centre stage, last days, son of God is at the Zion gate, ready to fulfil his promise,anati “mukazawona izi zikuchitika ziwati kuti mwana wa Mulungu wayandikira”. So don’t worry about skefa, worry about yourself.

 9. Why people hate the truth?soon or later the truth will come out, know that there’s no smoke without fire. How many rich people do we have in Malawi?, many,why do people not talk them, because there’s nothing to talk about them for now,just accept it brother that it’s time to reap what you sowed. There’s nothing hidden under the sun,that’s the book of revelations.

 10. Akachuluka anjiru uziyamika chauta, poti kaduka sikangadze popanda chipambano, chauta wanga wabwino sindingaiwale komwe mudandichotsa, tsogoleranibe moyo wanga mwandekha ndilephera!!!! ngat mwayi uchoka kwa mlengi azaulandaso ndani!!!! #singing …… Koma a malawi sazathekaso eish!! instead kut azipanga .ind ma biznesses awo ali bizy ndikupanga za anzawo, kungotayapo nthawi basi,,, #umphawisuzatha

 11. Tisatenge tchito zawozo koma uthenga munyimbozo poti uthenga wakewo ndie upangingitsa moyo wanga kukoma komaso kunditsogorera kuzoona zabwino m’moyo uno. Keep praying for you am still your fun.

 12. zovuta kwambri..GOD knws the truth & himself skefa knws the truth bt accordng to human understandng & hw illuminat work its hard for pple to admt f the story is tru…bt my question is why him?? what abaut black missionaries r they nt famous?? our father n heven knws the truf & he promisd HE wl never lv us blndfoded for us truth z camn lets hod our hands together n pray!!

 13. Aliyense ndi ochimwa amangosiyana ndi matchimo kma the goodness z dat kwa mulungu we are all siners.mwaona bwanj stroke ya mzanu kusuya cancer ya azibale anu yomwe sinaziwike.matenda sapita pa media kma kuchipatala kkkkkkkkk weee malaw where are u going?

 14. Aliyense ndi ochimwa amangosiyana ndi matchimo kma the goodness z dat kwa mulungu we are all siners.mwaona bwanj stroke ya mzanu kusuya cancer ya azibale anu yomwe sinaziwike.matenda sapita pa media kma kuchipatala kkkkkkkkk weee malaw where are u going?

 15. kOdi Mukanganilananji ndiliti idayamba mbiri yake kuti ndi wasatanic kapena mwanva pompano ? aaaa kwamene mukakamila kuti ndi munthu Wa mulungu pa zocita zake ndiye kuti inuso ndikuti unuyoso mukudziwapo kanthu tieni tikhale Maso zidzatsimikizika patsolo wina adzacita manyazi ndi makani opanda pake

 16. Dont call every media user stupid.So if everyone is stupid,then who is good?? Kapena iwo amene. But mukuwona kwanga ,You,yourself you are stupid2 for you have posted on the same media that you have hate .

 17. Ku malawi kuno kuli nsanje heve ndipo sitizatukuka,,maboza ndi mijedo sizitithandiza,,Sitifunira aluso athu zabwino,,Bingu,Grace.Izeki munkawatchukisa kuti amwalira koma asanamwalire muli ndi mtima oipa anzanga,,,ngati iwo ali ochimwa inu simukudziwa kuti kuweluza ndi kwa yehova? Inunso ndinu ochimwa popeza simufunira anzanu zabwino,,

 18. or mukambe kut this media its so stupd z 1 of my FAVOURYT PAGES even if i hv created almost 1,000,000 somethng accounts i wil be de positivly liker in each ‘n’ every account i create ®.Takumvan!!!!ma followers onse a page yathuyi makape pamoz nd admi.nde popeza inuyo ndnu dolo cnu kape takmvesesan nde commentor pa page ya makape

  wha>u>hv>done=0/10′

 19. Jealousy was created from Malawi and spread all over the Earth.

 20. Asatanic ose ochita uchimo .osatembenuka mutima ndikulapa .satanic ndi ufumu wasatana njito zake ndi kuba ,kupa,ndi kuwononga ,opembeza mafano ,acigololo,anyanga , akungonda kulicita boza ndizonyatsa zambili ochita zimenezi ndi asatenic . sazaona ufumu wamulungu .ambuye mulungu wambavuzose amucilise mr k chimoto muzina layesu

 21. Chisisi chamunthu aliyese ndichayekha or utakhala khazeni or mchimwene or ccta sangakuuze zomwe amapanga so its hard to defend the secret of someone, so the bottom line is only God knows about skeffa’s secret so give him a break

 22. Chisisi chamunthu aliyese ndichayekha or utakhala khazeni or mchimwene or ccta sangakuuze zomwe amapanga so its hard to defend the secret of someone, so the bottom line is only God knows about skeffa’s secret so give him a break

 23. Since this media is for stupid people, how can we believe your reaction through this stupid social media? Answer me Skeffa pliz. it appears that you are also stupid for commenting on stupid issues.

 24. Since this media is for stupid people, how can we believe your reaction through this stupid social media? Answer me Skeffa pliz. it appears that you are also stupid for commenting on stupid issues.

 25. Wea z de truth nw?bt for show usi sumafuka popanda moto.dats wt we believe.dnt blame social media.

 26. Bible limayankhula momveka bwino kuti zitsiru zimati kulibe Mulungu nidzichita zotsutsana ndi Mulungu

 27. Amalawi sitidzachitapo bwino.ukufalitsawe panga zoti zikuthandize pamoyo wako.nthawi imene wataya pa skefa ukanapanga chinthu cha phindu pamoyo wako.munthu oyipa iwe.chibadwileni chako ndikoyamba kumva kuti munthu wadwala?ndiye kudwala kwa skefa kwakudzidzimusa?skefa ima njiii pa yesu usagwedezeke.only God will judge.zabwino zonse skefa

 28. Amalawi sitidzachitapo bwino.ukufalitsawe panga zoti zikuthandize pamoyo wako.nthawi imene wataya pa skefa ukanapanga chinthu cha phindu pamoyo wako.munthu oyipa iwe.chibadwileni chako ndikoyamba kumva kuti munthu wadwala?ndiye kudwala kwa skefa kwakudzidzimusa?skefa ima njiii pa yesu usagwedezeke.only God will judge.zabwino zonse skefa

 29. Amalawi sitidzachitapo bwino.ukufalitsawe panga zoti zikuthandize pamoyo wako.nthawi imene wataya pa skefa ukanapanga chinthu cha phindu pamoyo wako.munthu oyipa iwe.chibadwileni chako ndikoyamba kumva kuti munthu wadwala?ndiye kudwala kwa skefa kwakudzidzimusa?skefa ima njiii pa yesu usagwedezeke.only God will judge.zabwino zonse skefa

 30. Vuto ndiloti amalawi samukhulupilira kuti munthu umatha kulemela popanda kukhwima. Akanakhala Alicko Dangote ndiwakumalawi bwezi mukutiso ndiwa satanic, hahaha amalawi safuna kukhala olemera.

 31. Vuto ndiloti amalawi samukhulupilira kuti munthu umatha kulemela popanda kukhwima. Akanakhala Alicko Dangote ndiwakumalawi bwezi mukutiso ndiwa satanic, hahaha amalawi safuna kukhala olemera.

 32. Vuto ndiloti amalawi samukhulupilira kuti munthu umatha kulemela popanda kukhwima. Akanakhala Alicko Dangote ndiwakumalawi bwezi mukutiso ndiwa satanic, hahaha amalawi safuna kukhala olemera.

 33. Anthu oipa inu,,,skeffa anakulakwilan chan kut muzingomupekela nkhan za uchitsilu, munthu asatchukitse dziko lake, basss ndi wa stanic shame on u!!!!! ng’ooooooo!!!!!

 34. Anthu oipa inu,,,skeffa anakulakwilan chan kut muzingomupekela nkhan za uchitsilu, munthu asatchukitse dziko lake, basss ndi wa stanic shame on u!!!!! ng’ooooooo!!!!!

 35. Anthu oipa inu,,,skeffa anakulakwilan chan kut muzingomupekela nkhan za uchitsilu, munthu asatchukitse dziko lake, basss ndi wa stanic shame on u!!!!! ng’ooooooo!!!!!

 36. limenelo ndiye nziko lanthu samafuna Wina achite bwino,,akachitabwino amakhala Wa satanic ndimomwe anawauzila agogo awo kut ziko lapansi sikuzakhala olemera zomvuta. Kwabas

 37. we must go to his page so that he can answr bcz ndamva kuti amauzidwa kuti aphe mawana wake kapena nkazi wake. Iye adaka na. Ndiye ati amulumalisa sakutha kuenda

 38. Munthu alive pabwino. Kuimba nyimbo zosakukomelani. MUKURU oyimba ndimbora. Zikakhala zabwino akapata ndalama Mukiti ndiwa satanic.amalawi kodi aliyense zamuyendera bwinoyo

 39. Kolingana ndimawu chowonadi amaziwa ndi mulungu ineyo ndizakonda mpaka kale uli ndi mphaso yabwino yoyimba uthenga umene umapereka kuzera munyimbo ndimapindura nawo ngakhare ndili kunja koma ndimadalisika Maka Maka munyimbo yako yomwe wunati ndili ndi manyazi Ku bwera pamaso panu mbuye GOD be with you Sikefa

 40. mmmm am i stupid for reading this skefa? say what is wrong rather than using wrong words. should i say the truth hates? why are you angry.

 41. SORRY MR S.CHIMOTO WE ARE NOT STUPID BUT REMEMBER THAT WE BELIVE IN SOCIAL MEDIA

 42. Inu nonse satanic dziwani mwatsala ndi kathawi kochepa chifukwa yesu alipafupi. Ktunali bwino mukanalapa . Musakomedwe ndi kutchuka? Kapena ndrama, baiblo likuti ikudza nthawi yowawitsa.

 43. Inu nonse satanic dziwani mwatsala ndi kathawi kochepa chifukwa yesu alipafupi. Ktunali bwino mukanalapa . Musakomedwe ndi kutchuka? Kapena ndrama, baiblo likuti ikudza nthawi yowawitsa.

 44. Inu nonse satanic dziwani mwatsala ndi kathawi kochepa chifukwa yesu alipafupi. Ktunali bwino mukanalapa . Musakomedwe ndi kutchuka? Kapena ndrama, baiblo likuti ikudza nthawi yowawitsa.

 45. Umakwana skeffa tangozisiya zitsiru zimenezo lwe pheee Bola zako zikuyenda

 46. We on social media, we like it but we are not stupid. Stupid are those who interfere in your corcens…
  Thank you.

 47. Kwanthu ku Malawi munthu akakhala ali ndi ndrama timakonda kunena zambiri zonyasisa mbiri yache.Malawi malawi dziko lamaboza la umphawi lonyoza anthu onse opeza bwino.
  Pano mumalo muzilemba nkhani zoti musamamphe ma Albino pano nazo za skeffa kuti ndi wa satanic.Kodi Church chamasatanic chimenecho bwanji inu simumalowa nanga bwanji anthu samachiona nanga satanic imeneyo imalowedwa ndi anthu amene ali ndi ma business awo.Ambiri mwaife timakonda kunena ndi kumati uja ndi wa satanic timasoweka ndi sopo wanima anthu omwe akatigulira timakhalaso pa tsogoloro kumalandira.Kaya zanu izo mawa ndinu mukazadwala stroke nafe tizizati mumampha ma albino ndinu

 48. Kwanthu ku Malawi munthu akakhala ali ndi ndrama timakonda kunena zambiri zonyasisa mbiri yache.Malawi malawi dziko lamaboza la umphawi lonyoza anthu onse opeza bwino.
  Pano mumalo muzilemba nkhani zoti musamamphe ma Albino pano nazo za skeffa kuti ndi wa satanic.Kodi Church chamasatanic chimenecho bwanji inu simumalowa nanga bwanji anthu samachiona nanga satanic imeneyo imalowedwa ndi anthu amene ali ndi ma business awo.Ambiri mwaife timakonda kunena ndi kumati uja ndi wa satanic timasoweka ndi sopo wanima anthu omwe akatigulira timakhalaso pa tsogoloro kumalandira.Kaya zanu izo mawa ndinu mukazadwala stroke nafe tizizati mumampha ma albino ndinu

 49. Kwanthu ku Malawi munthu akakhala ali ndi ndrama timakonda kunena zambiri zonyasisa mbiri yache.Malawi malawi dziko lamaboza la umphawi lonyoza anthu onse opeza bwino.
  Pano mumalo muzilemba nkhani zoti musamamphe ma Albino pano nazo za skeffa kuti ndi wa satanic.Kodi Church chamasatanic chimenecho bwanji inu simumalowa nanga bwanji anthu samachiona nanga satanic imeneyo imalowedwa ndi anthu amene ali ndi ma business awo.Ambiri mwaife timakonda kunena ndi kumati uja ndi wa satanic timasoweka ndi sopo wanima anthu omwe akatigulira timakhalaso pa tsogoloro kumalandira.Kaya zanu izo mawa ndinu mukazadwala stroke nafe tizizati mumampha ma albino ndinu

  1. Sikuti ku Malawi kokha komwe anthu amayakhula kwambiri za anthu wochita bwino ayi kma ndipena palipose dzikoli ngati pamalopo pali munthu,ngkhale ku europe, asia,america zimachtika anda uone..

 50. On a serious note though, Malawian celebrities need to learn to keep a healthy lifestyle: I know money comes too quick for them so they just get fat. Look at Sikefa now and the Sikefa we saw in his first videos: Talk of Piksy: Katerere, they are all too fat you can’t even recognize them if you knew them from their old music videos: Come on folks, there are gyms: get to know them and use them: Fat is no longer fashion or a sign of success; fat is unhealthy, fat leads to stroke, heart dieseses and BP. Someone please show those brothers doors to some nearest gyms:

 51. On a serious note though, Malawian celebrities need to learn to keep a healthy lifestyle: I know money comes too quick for them so they just get fat. Look at Sikefa now and the Sikefa we saw in his first videos: Talk of Piksy: Katerere, they are all too fat you can’t even recognize them if you knew them from their old music videos: Come on folks, there are gyms: get to know them and use them: Fat is no longer fashion or a sign of success; fat is unhealthy, fat leads to stroke, heart dieseses and BP. Someone please show those brothers doors to some nearest gyms:

 52. On a serious note though, Malawian celebrities need to learn to keep a healthy lifestyle: I know money comes too quick for them so they just get fat. Look at Sikefa now and the Sikefa we saw in his first videos: Talk of Piksy: Katerere, they are all too fat you can’t even recognize them if you knew them from their old music videos: Come on folks, there are gyms: get to know them and use them: Fat is no longer fashion or a sign of success; fat is unhealthy, fat leads to stroke, heart dieseses and BP. Someone please show those brothers doors to some nearest gyms:

  1. “Fat is no longer a fashion” wow i like that!! Most of our musicians are still living in past! look at most musicians from Nigeria,their body structures say it all, that gym is part of their lives! wake up Malawi.

  2. “Fat is no longer a fashion” wow i like that!! Most of our musicians are still living in past! look at most musicians from Nigeria,their body structures say it all, that gym is part of their lives! wake up Malawi.

 53. Ine oyimba onse akwathu Ku Malawi makamaka amene amatchuka ndi mbiri zoyipa, nyimbo zawo sindimagulanso, pazimene ndidali nazo kale muma music system anga ndinaphwanya ma disc ake komanso kudilita momwe ndimazitsunga , akumatchula zina la Mulungu munyimbo zawo pomwe akumakhudzidwanso ndi za satanic, pajatu usi siufuka popanda moto.

  1. Muziyamba mwafufuza bwinobwino. DNT just believe anything u hear. Mudzaluza zokoma zambiri moyo mwanu chifukwa chokhulupilira ma rumours. DZANA MDAKWATA MKWAZI WAKO INEYO. Ndiye umupilikitse lero. Sinanga u believe anything u hear. Pafuka utsi pali moto. CHASE HER AWAY THEN!

  2. Zina timachita kuziona ndimaso athu zina timamva choncho zomafufuza nzosafunikila, zikuchita kusonyeza zokha ,na matsiku ano technology ili advanced kwambiri nkosavuta kuupeza umboni.

  3. Zina timachita kuziona ndimaso athu zina timamva choncho zomafufuza nzosafunikila, zikuchita kusonyeza zokha ,na matsiku ano technology ili advanced kwambiri nkosavuta kuupeza umboni.

  4. Zina timachita kuziona ndimaso athu zina timamva choncho zomafufuza nzosafunikila, zikuchita kusonyeza zokha ,na matsiku ano technology ili advanced kwambiri nkosavuta kuupeza umboni.

  5. Jelson ndiinu achitsiru nzeru mulibe simungalembe ngati simukuona ndithu…. Dziko mumalidziwa koma??? Malamulo mumawadziwa??? Kunena kapena kuikila umboni pa chinthu chonama mumadziwa kuti ndi tchimo?? Palibe cha nzeru chimene mwakamba apa kodi mukati munasiya kuvela nyimbo zaku Malawi nanga bwanji mwa comenta chifukwa nkhaniyi ndi ya oyimba waku Malawi??? Malete awena…….. Mosono wa ntate wako….wa utwa??

  6. Jelson ndiinu achitsiru nzeru mulibe simungalembe ngati simukuona ndithu…. Dziko mumalidziwa koma??? Malamulo mumawadziwa??? Kunena kapena kuikila umboni pa chinthu chonama mumadziwa kuti ndi tchimo?? Palibe cha nzeru chimene mwakamba apa kodi mukati munasiya kuvela nyimbo zaku Malawi nanga bwanji mwa comenta chifukwa nkhaniyi ndi ya oyimba waku Malawi??? Malete awena…….. Mosono wa ntate wako….wa utwa??

  7. Oweluza ndi Mulungu, Aliyense cheteeeeeee osalimbana ndi ntchito yamwini YEHOVA kuti ikhale yanu. Potchula mbiri yanzanu kuti akhale oyipa number one nanga kumbali yanu osatchulako choyipa chimodzi bwanji kuti gulu la anthu limve zoti ndinu otere. Oyipa ku moto basi. Tsiku ndi ora zili nkudza.

  8. Yammie: muwuze Jelesoniyu kuti amasende akhe! Kkkkkkkkkkkk! Mpaka malete ake? Akukamba Zopusa munthuyu. Tiye timutukwane in afrikaans: SE MA ‘S PUSS! SE PA’S PIL!

 54. Paliutsi pali moto,lets wait n cee,bingu,izeki woxewa adatsutsaxo momwe achitira madalawa…koma alikut lero..azindukire kut kukhala cerebrity sizophweka.

 55. skeffa your are correct , these sons and daughter of rats are evil, samakufuniza zabwino, unayiwala kuwauza azafa wosauka

 56. Keep cool man,zopoilazo zitayeni inu ndi Mulungu wanu mukuziwana. Ifeso full time pa social media koma timapanga select zinazo timazitaila uko zikangwere

 57. Skeffa is just ok he was on galaxy yesterday pa sports …they called him ….komano I think tikasowa zokamba just off data your phone than kumalemba zopusa I’ve started hating this life……plz tiyen tilikonde dziko tifunilane zabwino kuti tipite chitsogolo……..skeffa is ok

  1. Don’t call people who are on social media stupid, because you are also a member of the social media.

 58. ngat ukutelo bwanjiiweyo wapeleka uthenkhawakou pa social media pomwepa bwanji umaleka kupele unthengawakou kuzelammawailes mommo???ndekusonyezakut chabwinocho ndchit?kkkkkkkkk ifetu timakukondan aneba

 59. ngat ukutelo bwanjiiweyo wapeleka uthenkhawakou pa social media pomwepa bwanji umaleka kupele unthengawakou kuzelammawailes mommo???ndekusonyezakut chabwinocho ndchit?kkkkkkkkk ifetu timakukondan aneba

 60. ngat ukutelo bwanjiiweyo wapeleka uthenkhawakou pa social media pomwepa bwanji umaleka kupele unthengawakou kuzelammawailes mommo???ndekusonyezakut chabwinocho ndchit?kkkkkkkkk ifetu timakukondan aneba

  1. Man post iyi apanga ndi a Malawi news 24 komabe Skefa walakwitsa kuti media its for fools akanangoti rumours spread by haters n carried by fools

  2. yaaaaa ndzoona zalakwika komabe ngakhale akutiika otinyoza mmagul azimenetili komaife timamfunila zabwino palusolake ife sitinamnyozeko palusolake komakwathu mkumuyamikila zake..ndewationjeza apapa

  3. yaaaaa ndzoona zalakwika komabe ngakhale akutiika otinyoza mmagul azimenetili komaife timamfunila zabwino palusolake ife sitinamnyozeko palusolake komakwathu mkumuyamikila zake..ndewationjeza apapa

  4. yaaaaa ndzoona zalakwika komabe ngakhale akutiika otinyoza mmagul azimenetili komaife timamfunila zabwino palusolake ife sitinamnyozeko palusolake komakwathu mkumuyamikila zake..ndewationjeza apapa

 61. The fate of social media in Malawi.Zokamba thooo!!!si uyu Skeffa wasutsa.

 62. Sibwino nzanu kumulengezetsa kuti wa mwalira muli inu mungamve bwanji?zimenezo ndiye zompusa,simumakondwera ndi anthu aluso adziko lanu bwanji koma kusapota za maiko ena

 63. Sibwino nzanu kumulengezetsa kuti wa mwalira muli inu mungamve bwanji?zimenezo ndiye zompusa,simumakondwera ndi anthu aluso adziko lanu bwanji koma kusapota za maiko ena

 64. Sibwino nzanu kumulengezetsa kuti wa mwalira muli inu mungamve bwanji?zimenezo ndiye zompusa,simumakondwera ndi anthu aluso adziko lanu bwanji koma kusapota za maiko ena

 65. Social media is like the rain it falls anywhere and good or bad things grow, koma kunena chabe yomwe ya kuluma One can use it to their advantage if it was meant to hurt them, now we all know that our beloved Chimoto is well and sound. Continue in God’s ways .

 66. Social media is like the rain it falls anywhere and good or bad things grow, koma kunena chabe yomwe ya kuluma One can use it to their advantage if it was meant to hurt them, now we all know that our beloved Chimoto is well and sound. Continue in God’s ways .

 67. Social media is like the rain it falls anywhere and good or bad things grow, koma kunena chabe yomwe ya kuluma One can use it to their advantage if it was meant to hurt them, now we all know that our beloved Chimoto is well and sound. Continue in God’s ways .

 68. chisilu ndiyeyo nditchito zakudimazo mesa akumuulula ndachizake, asova ndiusatanic wakeyo ife zisatikhuze timazuka kukaseza cement kuti tipeze chakundya podikila sikulo kuti tikamulandilee

 69. chisilu ndiyeyo nditchito zakudimazo mesa akumuulula ndachizake, asova ndiusatanic wakeyo ife zisatikhuze timazuka kukaseza cement kuti tipeze chakundya podikila sikulo kuti tikamulandilee

 70. chisilu ndiyeyo nditchito zakudimazo mesa akumuulula ndachizake, asova ndiusatanic wakeyo ife zisatikhuze timazuka kukaseza cement kuti tipeze chakundya podikila sikulo kuti tikamulandilee

 71. chisilu ndiyeyo nditchito zakudimazo mesa akumuulula ndachizake, asova ndiusatanic wakeyo ife zisatikhuze timazuka kukaseza cement kuti tipeze chakundya podikila sikulo kuti tikamulandilee

 72. ok if social media is for stupid people then ur also stupid because ur also on social media we are reading from there

  1. Yes chitsiru choyamba ndiyeyo kape wachabechabe sakuziwa zomwe akulankhu,pogulisa nyimbo zake amadusira kuti simeadia yomweyoooooo chamuluma chakuda wagwa nayo

 73. But facebook is also a social media and you have contributed, are you stupid too?? coz mwambi wina umati kumenyana ndi wamisala anthu owonera amati nonse ndi amisala

 74. Malawians u knw wat? what u r sayn about this guy u r wrong…this is stupidity and u will not penetrate to the highest level neva bcoz of ur stinking habbit skeffa is cul screwed u all bitches

 75. Malawians u knw wat? what u r sayn about this guy u r wrong…this is stupidity and u will not penetrate to the highest level neva bcoz of ur stinking habbit skeffa is cul screwed u all bitches

 76. Malawians u knw wat? what u r sayn about this guy u r wrong…this is stupidity and u will not penetrate to the highest level neva bcoz of ur stinking habbit skeffa is cul screwed u all bitches

 77. I beg to differ with Bro. Skeffa that social network is not for stupid people but fools abuse it. He is one of the beneficiaries of the same social media through sales on line, adverts e.t.c.

 78. Pamenepa ndiye wayankha chamba bwanji! Social media ndi ya anthu opusa? ndiye anthu onse aliku fb, and many more ndife opusa? Chamba eti

 79. wayankhula mau opusawo ndi Skeffa?.sakumunamizira et………. ndakhulupira ali mgulu lomwelo.sanganyoze a Malawi ogwirixa ntchto social media motero

  1. Page ya Social Media paja ndi iti pumbwa iwe? kkkkkkkkkkk koma aMalawi simuzathekanso. Kodi zinatipeza titagona izi eti?

  2. Page ya Social Media paja ndi iti pumbwa iwe? kkkkkkkkkkk koma aMalawi simuzathekanso. Kodi zinatipeza titagona izi eti?

  3. Page ya Social Media paja ndi iti pumbwa iwe? kkkkkkkkkkk koma aMalawi simuzathekanso. Kodi zinatipeza titagona izi eti?

 80. Now I’m so happy for hear that after nditamva zoti skeffa wafa ziwalo bt y people we are busy kupanga post zinthu zamaboza ngati zimenezi osamufunila mzanu zabwino koma zoipa zokhazokha ndathokoza kwambiri skeffa popanga respond khani imeneyi ndaziwa momwe uli l love your songs

  1. Ine pic yake ndiyaipeza pagoogle pamamembers asatanic kumalawi nde funso langa limakhala loti nanga achina ujeni awa mukuwaziwawa bwanji sakutchuka nawo?

 81. ok we are shupid pple we believe soc media? but shupid are those they post nosens

Comments are closed.