Salanje condemns APM’s speech on TB Joshua


Pastor Hasting Salanje

The flamboyant Malawian man of God Hastings Salanje has faulted the President Peter Mutharika’s outburst against the Nigerian prophet TB Joshua.

Salanje, who is the founder and pastor of God’s Chapel International, said Mutharika’s insults aimed at TB Joshua were the work of the devil to attack Malawi.

Pastor Hasting Salanje
Sides with TB Joshua.

He praised Joshua as the only favoured man of God worldwide and says he does not know another prophet from God who is greater and straight like him. Salanje added that it is worrisome to insult Joshua. “I want to believe that the president spoke that at his capacity and not as a person and not as a president of Malawi. But him being a leader of a country I want to believe that whatever he says covers a country.

“Therefore I choose to take this stand and disassociate myself, my family, my church and my country that we are not part of the speech which he made on the prophet,” said Salanje.

The pastor asked God to bless Malawi and TB Joshua, saying he has disconnected himself from the curse that can come after insulting a man of God like Joshua.

Mutharika attacked the prophet for a prophecy he made that one of the presidents in Africa will die even though the Nigerian did not mention the name of the president.

This did not go well with the president who said Joshua did the same to his brother Bingu wa Mutharika.

296 thoughts on “Salanje condemns APM’s speech on TB Joshua

 1. Zikuonesa kuti athu ena simunasukusulebe zonse zikuchitikazi nzoti zinalembedwa kale mufuna zizindikilo zotani ena akuyemda mmalele zikuphelezela chisilizilo athu kukonda ndalama zikuchitika kuphana asanduka masewela pano

 2. what kind of prophetic that prophesier the Bad things only. we are not dead pipo, God has created human with purples, stop interfere. Peter is right, we also read the Bible and understand the prophetic worlds, kunali Elijah who was a prophet he never did such, when he prophesy about some one he used to send his follower to go direct to a particular person to tell her/him, then choice was within a person to accept the truth or not. what kind of prophet,, ukufuna ndalama kuti azibwela nadzo mokupembeza kuti adziwe ngati ndiwowo… peter ndiochenjera ngati. iwe okhulupira ngati wadziwa bwamji osaitana ma presidents onse kuti uwapepherere pamodzi kuti izi zisachitike… lies stop lies!!!

 3. what kind of prophetic that prophesier the Bad things only. we are not dead pipo, God has created human with purples, stop interfere. Peter is right, we also read the Bible and understand the prophetic worlds, kunali Elijah who was a prophet he never did such, when he prophesy about some one he used to send his follower to go direct to a particular person to tell her/him, then choice was within a person to accept the truth or not. what kind of prophet,, ukufuna ndalama kuti azibwela nadzo mokupembeza kuti adziwe ngati ndiwowo… peter ndiochenjera ngati. iwe okhulupira ngati wadziwa bwamji osaitana ma presidents onse kuti uwapepherere pamodzi kuti izi zisachitike… lies stop lies!!!

 4. Mtumiki wamtundu wanji ongokamba za ndrama osamakambako za moyo wa uzimu mmmmmmm akungofuna ndalama basi poti sionse omwe amati amen amen akalowe mu ufumu wa mulungu nafe tidikire lathu tsiku

 5. Mtumiki wamtundu wanji ongokamba za ndrama osamakambako za moyo wa uzimu mmmmmmm akungofuna ndalama basi poti sionse omwe amati amen amen akalowe mu ufumu wa mulungu nafe tidikire lathu tsiku

 6. Ngati kutumikila YEHOVA kukuipilani muzisankhile lelo yemwe muzamtumikila kaya ndi milungu yomwe anaitumikila makolo anu nsidya lija,koma ine ndi a nyumba yanga ndizamtumikila YEHOVA.YOSWA 24:15.Ndiye ngati kuti inuyo mumatumikila milungu ya pa dziko lino lapansi monga ma prothet pitilizani kuitumikila chifukwa ndi komwe mumapeza thandizo,koma ine ndi a nyumba yanga ndizamtumikila yehova.

 7. Ngati kutumikila YEHOVA kukuipilani muzisankhile lelo yemwe muzamtumikila kaya ndi milungu yomwe anaitumikila makolo anu nsidya lija,koma ine ndi a nyumba yanga ndizamtumikila YEHOVA.YOSWA 24:15.Ndiye ngati kuti inuyo mumatumikila milungu ya pa dziko lino lapansi monga ma prothet pitilizani kuitumikila chifukwa ndi komwe mumapeza thandizo,koma ine ndi a nyumba yanga ndizamtumikila yehova.

  1. Mfundo Yako Yandigwira Mtima Kwambiri.Mtima Wanga Umandipweteka Pomvera Chisoni Anthu Ambiri.Anthuwa Akanakhala Kut Amamudziwa Mulungu Oona,makhalidwe Ake Abwino,zomwe Amafuna Kut Tidzichita Komaso Tisamachite Bwezi Satanayu Titamugonjetsadi.Vuto Ndilot Anthu Samamudziwa Yehova.Mmalo Mwake Ayamba Kukhulupilira Anthu Omwe Amachita Zozizwitsa Koma Mulungu Wawo Sakumudziwa.Sindinamvepo Atumiki Alerowa Atatchulako Dzina La Yehova Mmapemphero Awo Mmaro Mwake Amangoti Lord Jesus Lomwe Liri Bodza Lenileni Chifukwa Yesu Anawatchula Kale Kut Adzachita Zodabwitsa Kudzera Mzina Lake Koma Anatichenjeza Kut Iwowo Ndi Aneneri Onyenga Choncho Mpofunika Kusamala Nawo Kuopela Kut Angatisocheletse.

 8. #thocco ,ndiziwanda zikukupangitsa kuyankhula mopanda nzelu,i no it’s not you, wekaso utha kudabwa atakuchosa ziwandazo so i don’t blame you, couz wanomor sangabwebwetuke zimenezo,may god forgive you,,

  1. Stuıpit..prophet..wanzeru..azıkhala,akungokamba,,zot wına akufa.?..umuze azıtchura ma date ake..omwe munthu adzıfera..osamangoganiza..tonsetu..tızafa,,mde osat mukakhala..ndı Joshua yooo..muzılotezera zopusa ok?…umuwuze lyeyo atıuze tsıku lomwe azafe

 9. plz #wisdom nyasulu,, watch your mouth,, don’t speak against men of God plz uzatembeleledwa anthu onse amene amapita kwa prophet tb Joshua sikuti ndiopanda nzelu inu kukhala anzelu,, uzifufuze wekha who are you in god’s presence? pezani zina zochula mwachibwanana,not this pipo, of god, mulungu anakana kale don’t torch my anointed one, tb Joshua z not your mate, have fear

 10. Mr Isaac chigalu bible ndimalidziwa from geneses to chivumbulutso and ngati inu mumaligwila bible popita Ku church musayelekeze ndi ineyo.ma prothet omwe mukuti ndi milungu yanu ziyipembezani koma ine ndi anyumba yanga ndizamtumikila yehova mulungu wa ku mwamba.yoswa 24:15.

 11. just show me one true man of God. it looks like aliyese ndi wasatanic. Ndiwuzeniko modzi yemwe inuyo mukuti Tb joshua ngwasatanicnu. kuti uyu nde true man of God…. timusatile….eshi

  1. am not trying to follow munthu i follow christ my saviour but every believer has a spititual father who guides him or her thats what am asking here.

 12. In your life believe no man, but God. then you will always stand, man is their to dissapoint while God is their to rescure you and give you better life that you want.,,,,,,,

 13. Osaiwala mau a bukhu loyera, za matsiku otsiriza. Kuzabwera aneneli azachita zodabwitsa, koma sindiye kuti ndi mphavu ya mulungu, ayi koma ya nyerekezi.

 14. Apm Sanalakwa Coz Za Ifa Zowawa Ndindani Safuna Kunjoa Aa?

 15. TB Joshua is such an idiot n that simply shows that the president will be from Malawi. Just 2days ago we’ve lost our songbird Chinga n APM will be the next. The bible says “Never trust anyone on Earth” so TB Joshua must piss off from our long live president. Joshua shame yourself

 16. guys musamvutike kumat tb joshua is a real prophet….just go and search on google……”list of nigerian illumnate members…..”then mubwere ndi ma coment anu..

 17. Kunyoza anthu a mulungu sikunayambe lero kunayamba nthawi ya kale Koma zomwe zimachitika kwa onyozayo guys simudzakhulupirira. In the bible muli mau ana amanyoza Elisa amati wadazi wadazi, adangopemphera kuti ambuye ana awa muchite nawo, kunatuluka mikango 40 kuwagwira ana onse aja so tinene kuti umeneo ndi satanic? something is coming very bad to those harassing men of God mwina bible simaimvetsetsa bwino kwanu ndi kupanga comment zinthu zomwe simukuzidziwa God bless you

 18. Kunyoza anthu a mulungu sikunayambe lero kunayamba nthawi ya kale Koma zomwe zimachitika kwa onyozayo guys simudzakhulupirira. In the bible muli mau ana amanyoza Elisa amati wadazi wadazi, adangopemphera kuti ambuye ana awa muchite nawo, kunatuluka mikango 40 kuwagwira ana onse aja so tinene kuti umeneo ndi satanic? something is coming very bad to those harassing men of God mwina bible simaimvetsetsa bwino kwanu ndi kupanga comment zinthu zomwe simukuzidziwa God bless you

 19. To you who follow Tb and other prophecies mungandiuzeko tsiku lomwe ananepo za salvation like telling one kuti lets repent God is coming soon let’s prepare our hearts? 2. Can you tell me when he once said certain country will be blessed this year I the other year? Isn’t it always about money? Prosperity? Wealthy? Families? DEATHS? but the way we are living these days is it meaningful to be talking about zolemera, n nor salvation? Mind you chuma ndi zina zonse sizikalowa kumwamba only US so don’t you think it’s good for us to prepare our hearts for His second coming? Lemme tell you this *these people you call prophecies just want to blind fod u so that o yo minds shud dwell in chuma, and other worldly things mutaye Mulungu wanu but musalole kutaya Mulungu wanu kaamba kazonena zaanthu claiming to be men of *God* Mind you the Bible clearly said matsiku otsiliza azabwera aneneni ambiri onyenga. Are we not in the last days? Are these not the people that God once warn us before ascending to Heaven??????

 20. To you who follow Tb and other prophecies mungandiuzeko tsiku lomwe ananepo za salvation like telling one kuti lets repent God is coming soon let’s prepare our hearts? 2. Can you tell me when he once said certain country will be blessed this year I the other year? Isn’t it always about money? Prosperity? Wealthy? Families? DEATHS? but the way we are living these days is it meaningful to be talking about zolemera, n nor salvation? Mind you chuma ndi zina zonse sizikalowa kumwamba only US so don’t you think it’s good for us to prepare our hearts for His second coming? Lemme tell you this *these people you call prophecies just want to blind fod u so that o yo minds shud dwell in chuma, and other worldly things mutaye Mulungu wanu but musalole kutaya Mulungu wanu kaamba kazonena zaanthu claiming to be men of *God* Mind you the Bible clearly said matsiku otsiliza azabwera aneneni ambiri onyenga. Are we not in the last days? Are these not the people that God once warn us before ascending to Heaven??????

  1. ukanaziwa bwenzi sukukamba zomwe ukunenazo.tek tym out of your busy schedule nd listen 2 tb joshua’s sermon nd see if u wil hear anytng abwt miracle money or wateva,his sermons r totally dferent frm diz other prophets,his sermons every sunday r based on salvation as t z mekng Gods words de standard of our lives.as 4 peter he z jst afraid of death coz tb joshua sed we shd pray 4 our leaders in southern africa coz samtng wil hapen 2 aperculiar leader bwtn feb nd april end,sanatchule zina la munthu or ziko.

  2. Joshua preaches salvation n,love,,there is nothing like yuo wu b rich,or u wu b famous in scoan my brother,,,joshua is nt centred on worldly thing,,,watch de way u acuse men ov God

  3. Joshua preaches salvation n,love,,there is nothing like yuo wu b rich,or u wu b famous in scoan my brother,,,joshua is nt centred on worldly thing,,,watch de way u acuse men ov God

  4. I love yo speech starting at ‘but the way we are living is it meaningful…. going down, u cannot know hw much it has inspired my soul…I say God bless

  5. I love yo speech starting at ‘but the way we are living is it meaningful…. going down, u cannot know hw much it has inspired my soul…I say God bless

  6. Etina Mwams I know wat am tokng n u cnt muv me abt those guys I swear by my living God… am not saying u shudnt lik him like him it’s your choice

  7. @Thocco Jean Malefula am nt telling u 2 like him bt mind de way u talk abwt de man of God.let God alone prevail coz God z de only judge.

  8. @Thocco Jean Malefula am nt telling u 2 like him bt mind de way u talk abwt de man of God.let God alone prevail coz God z de only judge.

 21. Mateyu 24 v 11. Mutu wankhani YESU ANENELATU ZA MTSOGOLO CIYAMBI CA MASAUTSO. aneneri Onama ambiri azauka, nazasocheresa ambiri. Pa M 24 pomwepa v24 mutu wankhani CISAUTSO CACIKURU. Chifukwa Akristu onama adzauka, ndi aneneri Onama nazazaonesa zizindikiro zazikuru ndi zozizwa kotero akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe.

 22. Salanje aint a man ov God hz a man ov riches en fame… Nkhan ya APM en TB Joshua inasasa iyi panop we shud b lookin’ forward kt kod mma minda mu tikolora matumba angat nanga maungu tikavutura ochuluka buaj

 23. Bloody Fuck! U so called prophets,go and take a dump if u ain got non 2 do,have u eva been on a mountain 4 40days? Wen was da last tym u fasted,ur not worth 2 b calld prophets,u bring so much shame,ur a disgrace,abormination and i declare ur end z coming and if u dnt repent u will dance in the lake of fire with the snake which is manipulating u now…VILLAINS! Pinheads!

 24. at my age sindinganyoze mtumiki aliyense wa Mulungu amene anavomereza kuti Yesu ndi Ambuye chifukwa komwe ankazozedwa ndi Mulungu ine kunalubeko

 25. let me tell them, ” you people so called prophets, firstly let me tell U that U r idiots, why always your sermons R a bout money, I even get wondered because most of your tym what U lyk to preach is that” every one who want car should type amen,” for what do U think we do not wan’t to see heaven? this the only fact I know that U R force prophets , now, U stupid motherfuckin prophets risen and resen good, U people U r stupid and your ways R fuckin shit, TB,salanje,ETC, U R not men of God, but U R the sons of fuckin demon, I do not trusting U, please my people get out from them let them alone perish, leave them, I know some one will talk rubbish against me from this fucking shit prophets Am out

 26. Kikikikikikikikiki paja amalawi amankhulupilila chili chose ineso mzandi nkhulupilila ndikazalowa #llluminati satanic mkuwona ngati ndi anthu a God ameneo eti awo ndi anthu a satanic llluminati ??????

 27. masku otsiliza kudzadza anener onyenga, azapanga zozizwa mu dzina langa……….chaxalaxo nd chaaaaa ??? osakhulupira munthu dzako obadwa mwa mkaz, khulupiran mmodz ekhayoo emwe anagonjrxa imfa pamtanda paja. #Amen

 28. No !!!!no !!!!!! Nothing is gonna happen to peter mutharika nop bcoz jb Joshua is not man of god !!!!! Why he is bussy against mutharika’s family why ??? I know in he’s power nothing can happen ppl thy are jersus wth mutharika’s family kodi athu anafa ku church kwa Joshua anja bwanji iye monga prophet kuwapulumusa ndiye asalanjewa ndiopega end onsewa akuti ine ine prophet ndi masatana shit !!!!!

 29. No !!!!no !!!!!! Nothing is gonna happen to peter mutharika nop bcoz jb Joshua is not man of god !!!!! Why he is bussy against mutharika’s family why ??? I know in he’s power nothing can happen ppl thy are jersus wth mutharika’s family kodi athu anafa ku church kwa Joshua anja bwanji iye monga prophet kuwapulumusa ndiye asalanjewa ndiopega end onsewa akuti ine ine prophet ndi masatana shit !!!!!

  1. Noo bro I dnt care abt man of god bro bcoz is nothing end sindimaopa athu asatana bro true I dnt mind evil people bcoz thy can destroy our country I believe in god not in devils people s bro

 30. Anthu tonse tilape ufumu wakumwamba siwa ma prophet okha ai kuteku kuweluza kuli kwa Iye mwini
  Ndikuona ngati mmalo mosiya nyasi zathu tikuchedwa ndi kulankhula zosaenela
  Marko 16v16 kwalembedwa kut kwa okhulupirila….. zizindikilo izi zidzawatsata komanso ku Mateyu 24v24 kutsimikiza kuti alikonso oona ndi onyenga aneneri ndipo tizaadziwa ndi tchito zao
  Simungamuziwe kuti uyu ndioona uyu ndiwabodza muli olankhula mosefukila ndipokhapo mutayamba mwathanga ufumu wake
  Tizingonyoza popanda chotolapo chifukwa maso athu ngotseka kupatulapo aneneri onyengao ubale wanu ndi Mulungu Wamoyo ndiotani? Nanga ine?

 31. Anthu tonse tilape ufumu wakumwamba siwa ma prophet okha ai kuteku kuweluza kuli kwa Iye mwini
  Ndikuona ngati mmalo mosiya nyasi zathu tikuchedwa ndi kulankhula zosaenela
  Marko 16v16 kwalembedwa kut kwa okhulupirila….. zizindikilo izi zidzawatsata komanso ku Mateyu 24v24 kutsimikiza kuti alikonso oona ndi onyenga aneneri ndipo tizaadziwa ndi tchito zao
  Simungamuziwe kuti uyu ndioona uyu ndiwabodza muli olankhula mosefukila ndipokhapo mutayamba mwathanga ufumu wake
  Tizingonyoza popanda chotolapo chifukwa maso athu ngotseka kupatulapo aneneri onyengao ubale wanu ndi Mulungu Wamoyo ndiotani? Nanga ine?

 32. Bola mukamanyoza ma prophet anuwo inuyo onyozanu mukhalenso opanda banga pamanso mulungu..In short are you born again john3;3,,,,if not not NDE u don’t have the right to discredit men of God no matter how good the reason may be…

 33. Salanje nd Ambuyake Tb Joshia Tsopano.kkkkk i dont Blive In U2,ma Prophert Abodza Ongofuna Kudyela anthu Ndikutchuka.,.!Ine ndina Typa Amen,kma Or Yokankha Galimoto ndlibe.#zabodzabasi….

 34. Asalanje mwalephela kuukisa munthu wathu nde inu musatinyase kajosua kakoko ukauze kakuchotsa ziwanda muchala chazelezebuli

 35. Ku Nigeria anthu aphana ngat animal ,Boko halam yawavuta bwanji osaletsa Kaye mavuto akwao Mr Tb Joshua go to hell Mr

 36. Za ziiiiiiiii zopanda ntchito!!!!!!!…….za ziwanda basi,,,,,,,osamayenda nzipatala kumakathandiza anthu bwanji koma nku mambo zina miss kuti mmalosera zansogolo……….ZAKUMIDIMATU IZIIIIIIII

 37. U GUYS ZIWANI MULUNGU ALIBE MZAKE AND MEANING OF DEATH SPIRIT SIMUKUIZIWA.AKUTATHAUZA KUTI MUNTHARIKA ATASIYA CHINTHU CHINA CHOMWE AKUCHITA CHIFUKWA CHIKHOZA KUMUBWERETSERA NGATI SANGASIYE CHINTHUCHO AVAYA BASI CHIFUKWA CHAKUSAMVA KWAKE & PROFESE IMAFOTOKOZA ZTSOGOLO LAMUNTHU, KUMASULIDWA AND NGATI SIMUONA MUUZIMU NDIBWINO KUKHALA CHETEA

 38. Inuyo mukumaikira umboni T B Joshua mayayembe lero kupemphera komanso muziwelenga baibulo lanu . zikuoneka kut simukuziwa kut Baibulo likut chani. Kungoyambila Bushiri ,Iweyo ukuti ndiwe Salaje TB Joshua nonse zotengela zasatana.ine mmene ndikuziwila pano sitikudikila kukhala ndi prophet mwazitenga kut zimenezi. Sindingalore kuti azingopanga attack ziko lanthu lamalawi .I be ndikuti go to hell with your TB Joshua.

 39. Pentecostal churches are full of sheet they always prophecy long thing’s only let’s say Grace chinga your R.I.P we loved you but God has love you most.It’s about time tomorrow it’s me then you.only God knows everything

  1. Careful,Pentecost involves the Holy Spirit,cause the Holy Spirit filled the disciples on the day of pentecost,so u dnt want to anger the Holy Spirit,boy! Ur gonna be sorry coz the Spirit never forgives,piece of advice!

 40. TB Joshua ndiwasataniki ngati inu anakuthandizani ndiye kuti nonse ndi a satanic.prothet wanji wolosela imfa ya munthu?chifukwa chani amakonda kulosela imfa ya ma president okha okha?tandiyankheni anthu ozindikilanu.

  1. And tamufunse kuti awerenge ma prophet in the bible who came with a very good message ndi amene amabweretsa bad message akuchuluka ndi ati. Why are u busy questioning God? How did u knw that he is not a prophet of God? Anati muyeze mizimu muwone ngati uli ochokera kumwamba, mwauyeza? Bwinotu a Henry John. How often do u read the bible and understand it? Tipeza kuti umangoligwira ukamapita kumpingo. Kumasanthula mau bwana. Am not saying he is man of God or not but am just saying samalani mau anati do not touch my annointed and do my prophet no harm. Kumbukirani za ana omwe amamunena mtumiki wa Mulungu Eliya

 41. More Fire T B Joshua Kp On Prophesyng Asakufuna Azisiye Ngati Ali Wa Satanic Satanic Yake Nde Yamphindu Chifukwa Amathandiza Nayo Anthu Osati Zinazi Zili Mmalawi Mommuno Koma Ana Ena Kummasowa Xool Fees Ntchito Kudzikundikira Nokha Basi Nde Bolanso Asatanic Akuthandiza Ine Ndi Nkatoliki Koma Joshua Ndimatsata Hevy Man Chikwangwani Olo Chitanyasa Chimalozabe Njira Apange Prophsy Zabwino Kuti Chani Mmesa Zimakhala Zabwino Kale Anthu Osabala Amabala Aja Zimenezo Nzoipa Za Ziiiii Basi Vuto Lowonera Ma Screen Pawindow La Kwa Neibour Ndilimenero Zikusokonekerani

  1. You R More Than A Fool Urself Which School Did U Go To Look At Ur Poor Grammar Ur So Stupid If U Hate T B Joshua Then Keep Quiet And Dont Ans Me Again Ur A Stiff Naked Fool TB JOSHUA SHALL REMAIN MY MENTOR NO MATER WHAT ukhale munthu olongosoka usayika dzina lako lenileni bwa chineke ndekuti chaaa

 42. NDIPONSO NGATI MUKUKUMBUKILA MUNTCHALICHI CHAKE MUNAFELA ANTHU MUJA BWANJI OSALOSELA KODI FUNSO NDILAKUTI BANJI OSALOSELA BWAAAA

  1. Koma Scoan Mumaitsata Kapena Munangomva Kwa Aneba Anu Ngati Vuto Linali Iyeyo Bwanji Pano Athu Amadzadzabe Muchurch Mwake Iye Kodi Anthuwo Amachita Kukatenga Mmesa Amabwera Okha Nde Inu Mukuti Chaaa

 43. Salanje I read your speech on Malawi 24 about the death of Grace Chinga, it cleary shows that you are not fit for your position as a Man of God. and I don’t know if you are spirituary motivated

 44. A Malawi njira yina yakuti Dziko lathu lilemere ndiye kumvera Atumiki a Yehova.. osati kulemekeza Mpingo mulibe mu Bible, koma Atumiki a Yehova.. Ambiri anatenga tsoka ponyoza

 45. he just pretend to be…man of GOD…but he is not…he is aman of satan…..osayiwala masiku otsiliza…kuzakhala…alosi ambirimbiri…opanganso zozizwitsa..in the name of GOD…but in power of satan…ine sindimakhulupilira…alosi otchuka…apasi panyanjawa…bora kumangogwada ndikupemphera wekha…..

 46. Somebody is saying why prophesing death, kodi anthunu makamaka vuto lanu nchani? Anenere za prosperity mukuti ayi. Imeneyi ndimphavu yokana kulapa for sure. MULUNGU AKUTHANDIZENI

  1. Akuthandize Iweyo Chifukwa Ndiwe Wa Blind Koma Mwauzimu.Nthawi Ino Siyolosera Zamtsogolo Ayi Koma Ndiyokwanilitsidwa Maulosi Choncho Ngat Wina Akukuuza Kut Ulape Ndipo Ulandile Yesu Ncholinga Chot Upeze Chuma Kapena Banja Dziwa Kut Nde Onyengawo Amenewo.Koma Wina Akabwera Kwa Iwe Ndikuuza Zot Umudziwe Yehova Mulungu Komaso Yesu Kenako Ulape Ndi Kubatizidwa Pambuyo Poti Wadziwa Choonadi Chakumasula,wadziwa Za Ufumu Wa Mulunguyo Ndipo Akukuuza Zimene Ungachite Kut Udzalandile Moyo Osatha.Yamika Mulungu Chifukwa Udzapeza Nzeru Komaso Chuma Chambiri Kwamuyaya Osat Izi Zakanthawi Kochepa Kulemera Kenako Nkumwalira,kupeza Banja Kenako Kufa Nkulisiya.B Wise M’bale Ufumu Wa Mulungu Uli Watiana Kusonyeza Anthu Amene Amaoneka Ngat Otsalira Kudzikori,ooneka Opusa,osakonda Chuma,onyozedwa Koma Osapsya Mtima,kulira Pompo Kuseka,achikondi,opanda Tsankho,okhala Ndi Chidaliro Cholimba Kwa Atate Awo.Chachikulu Khulupilirani Yehova Komaso Kumvera Yesu Mwana Wake.

 47. Kkkk, dont push me to suggest that the presidential advisor on religious affairs is not doing our president good. Well prophesies come from God & prophets are just vessels but the fact is TBJ did not mention anyone but the prophesy will come to pass, what is needed is to repent thats all

  1. Inunso nanu musamayankhule ngat anzelu apa,ur nat makn sense u gotchaself twisted lady/sir,not mentioning names doesnt justify ur TB,i dnt blame u tho,ur brainwashed

 48. A Bullets munya muona season ino tizngokukwapulani, team ya mbala mavenda matelala, koma chimodz pa game yanu nd noma kulibe kugulitsa fodya chifukwa ndkoletsedwa kusuta pagulu

 49. Idnt believe in all this alluminate prophets, Peter was right,where were all this prophets when Mandela,Doctor Banda,kabila and other presidents died?why did he fail to prophesis the collaps of his church that claimed the lives of 90 people?Does his power only arise to Mutharikas family?or you use them as your recrifies

 50. Peter mutharika is true,why u always prophecy abt the death of the president? muziwapemphelera kuti akhale ndi moyo not kuti amwalire ndiye inu muzisangalala poti mwalosera,its not gud please salanje and Tb stop doing that,be like my prophet Bushiri

  1. Asaa #Bushiri nde ndan?. Kachiwanda kasatanako?. Tamutenge #Bushiri upite naye ku mangochi akayende pamwamba pa nyanja tikaone ngat alidi mwana wa mulungu

 51. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS

 52. Salanje amangofuna potchukira,everyday kumangoyika magalimoto basi amvekere,”hee nanunso mukhala nawo magalimoto mudzina la ambuye,Amen”,attention seeker.Nayenso Joshua daily prophesising about death death death,bwanji sumaloserako za mvula kaya njala olo tchalitchi chake chenicheni!Kaya.

  1. kkkkkk wandikumbutsa analonjeza de last December kuti amene a Type amen before April apeza chozidziswa cha Galimoto…..ndindani achipeza atidziwitse ka kuti ndixoona

  2. all this prophets R idiots silly people, stupid they think we R blind that we do not see their fucking dem ways, shit go to hell you cocksuckers, am out,

 53. Why he always prophecies about death?why he didn’t prophesied about the fall if his church that killed alot of people,and he cant even prophecies something good.and if God told him that he must said why that person will die and what can he or she do to escape that punishment of death.that’s how it was before with all that God prophets.

 54. Why he always prophecies about death?why he didn’t prophesied about the fall if his church that killed alot of people,and he cant even prophecies something good.and if God told him that he must said why that person will die and what can he or she do to escape that punishment of death.that’s how it was before with all that God prophets.

 55. Why he always prophecies about death?why he didn’t prophesied about the fall if his church that killed alot of people,and he cant even prophecies something good.and if God told him that he must said why that person will die and what can he or she do to escape that punishment of death.that’s how it was before with all that God prophets.

  1. peter akuwopa infa tb joshua sanatchule zina lake anat btwn feb nd april end we shd pray 4 our leaders in southern africa coz aleader wil die dats all he sed.abwt za building yomwe inagwa he prophesied abwt dat buildng 2months b4 de incident hapend,he sed there z notng he can do dat t was Gods will.so hu can question God??

  2. If he prophesied abt dat building why he let those people still using it instead of abandoned it for he knew that anytime it wanna fell,do u want to tell me dat it was God’s plan to kill those people who died there?

  3. #Etina Mwans am not surprised you’re speaking like that because “he_did_not_mention_any_names” is just a slogan used by blind followers of fake prophets trying to justify their prophet’s fuzzy ‘prophecies’. News flash, Joshua doesn’t mention names. He plays his games just like that. In 2012, he didn’t mention a name yet he was on his tv bragging about it saying Bingu himself knew the prophecy was about him. What a joke!

  4. What about Jesus, didn’t he prophesised about his own death,? And why is it that he could not run away from the deith he surely know was comming through his own deciple? Guys there are other things which happens which we will never anderstand until Gods time comez for us to anderstand. So dont speak about some of these things which you dont understand, you might be cought in your blindness by Gods rough.

  5. Giliad,u cant compare Jesus to TB,Jesus is Lord,He wasnt suppose to escape death that wasnt the plan,He gave Himself as a sacrifice,being the firstborn He had what it takes 2 escape death but He died 2 fulfill His purpose…so i dnt knw where ur gettn all that,dnt get the scriptures twisted,read the bible daily and carefully with understanding and grow in knowledge

  6. If Jesus could have escaped that death then God could have failed his already made plans and those scriptures in old testament bible zidakakhala ndizabodza,there was no way jesus could have escaped the death bt about that building the chances were there to be avoided,simply it was his plans to kill those people

 56. Awa angofuna potchukira amadikira kae kut chinthu chichitike then azibwera nkumasokosera aaaaaaah ndakwiy,,,,,,,,, nawe wamva!!!!!

 57. Awa angofuna potchukira amadikira kae kut chinthu chichitike then azibwera nkumasokosera aaaaaaah ndakwiy,,,,,,,,, nawe wamva!!!!!

 58. Peter is crazy..Is a dead man walking..is He only a president in Africa?amamutchula dzina?Ine mutembelero waliputalo Mulibe.ndi lake ndi Mkazi wake komanso ndi Ana ake.Am out of curse.

 59. Peter is crazy..Is a dead man walking..is He only a president in Africa?amamutchula dzina?Ine mutembelero waliputalo Mulibe.ndi lake ndi Mkazi wake komanso ndi Ana ake.Am out of curse.

 60. Peter is crazy..Is a dead man walking..is He only a president in Africa?amamutchula dzina?Ine mutembelero waliputalo Mulibe.ndi lake ndi Mkazi wake komanso ndi Ana ake.Am out of curse.

  1. Àaah aise sukuziwa kti munthu ukatukwana munthu wa Mulungu umaputapo temberero?Peteryo ndi president wa Malawi.Ndie ngati watukwana TB Joshua prophet.dziko lonse can be affected ndi temberero.it’s what am tryn to emphasise my bro.

  2. Salanje wachan?.tiziwanda tama satana timeneti ma prophet?. Satanism ili tho!!!! Tamutengen #salanje ndi #Bushiri ngat alidi ana amulungu apite kumangochi akayende pamwamba pa madzi ngat sakamira!

  3. So who is a false Christ and who is a false prophet?Is TB Joshua a false Prophet?am not agree wth you bro.Joshua is a Man of God.You have to honor him.If you indeed fear God what does your spirit tells you who Joshua Is?musamangoti poti wina wakunamizani kti wakutiwakti ndi false prophet inunso nkumasatira zomwezo muzalakwa nazo.sometyms you mst try pray or fast own ur own to ask God abt this Prophet kt kodi ambuye Aneneli enawadi ndi osankhidwa anu?God hear Us bro whn we pray to him,and He is ready to answer answer Us.osamangowaweruza molakwika azineneri enawa.mukamangoti mneneli uyu ndi onyenga,uyu onyenga ndie oonayo azabwera litilo poti we ar in last days..Aneneli ndi omwewa bro..onyengaonso aliko the thing is kungowqfunsa Ambuye kti ati segule Maso poti we are indeed in the last days. .@Peter

  4. Only work to b done by true worshipers of GOD b4 END OF WORLD as did JESUS SON OF GOD is to……..Matthew 24:14 read yourself PILLAY

  5. Got the bible wth Me nw bro..let me read..and this Gospel of the Kingdom wll be preached in the whole world as a testimony to all nations,and then the end wll come.(Good news bible).

  6. mathew 24 vs 24,akristu onama adzauka,ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindkiro zazikulu ndizozizwa kotero kut akanyenge,ngat nkotheka nd osankhidwa omwe.onani ndakuuziranitu pasadafike

  7. mathew 24 vs 24,akristu onama adzauka,ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindkiro zazikulu ndizozizwa kotero kut akanyenge,ngat nkotheka nd osankhidwa omwe.onani ndakuuziranitu pasadafike

  8. Mtima wanu usavutike khulupilirani ine khulupilirani Mulungu… Vuto ndilokuti ambiri mwaife we r gud @ comentng things moweluza komatu kuweluza nkwake kwa Mulungu..ndiangati mwaife amene tikamva nkhani zotelezi timapinda mawondo athu nkupemphera? Tiziwe kuti tilinako kuthekera kokaniza satana mdyelekezi kukwanilisa zokhumba zake kuzela mukukhala muuzimu ndi muchoonadi

  9. Mtima wanu usavutike khulupilirani ine khulupilirani Mulungu… Vuto ndilokuti ambiri mwaife we r gud @ comentng things moweluza komatu kuweluza nkwake kwa Mulungu..ndiangati mwaife amene tikamva nkhani zotelezi timapinda mawondo athu nkupemphera? Tiziwe kuti tilinako kuthekera kokaniza satana mdyelekezi kukwanilisa zokhumba zake kuzela mukukhala muuzimu ndi muchoonadi

  10. A Beatrice..Inuyo ndie Aneneli onyengao [email protected] is to pray in truth and in spirit?osamangoyankhulatu kkk.@George ndizoonadi mukulankhulankhulazo..komanso ngati munanvapo nkhani ina yake inu ndikupinda bondo ndikupemphera ai Mulungu alemekezeke choonadi amachiziwa ndi Mulungu.ambiri amangoziwa kulankhula koma osamachita zinthuzo.Afalisi ndi Saduki a lero.

  11. A Beatrice..Inuyo ndie Aneneli onyengao [email protected] is to pray in truth and in spirit?osamangoyankhulatu kkk.@George ndizoonadi mukulankhulankhulazo..komanso ngati munanvapo nkhani ina yake inu ndikupinda bondo ndikupemphera ai Mulungu alemekezeke choonadi amachiziwa ndi Mulungu.ambiri amangoziwa kulankhula koma osamachita zinthuzo.Afalisi ndi Saduki a lero.

  12. ngati simuli sure if the person is realy a man of God or not. Trust and read the bible and pray for the pouring of the holy spirit for the holy spirit shall lead u into all truth

 61. aaah Salanje n tb Joshua popezera mchere mpamodzi kaya! wat do u xpect? they know how to conive pplez minds! induction by hipnotics!

 62. aaah Salanje n tb Joshua popezera mchere mpamodzi kaya! wat do u xpect? they know how to conive pplez minds! induction by hipnotics!

 63. aaah Salanje n tb Joshua popezera mchere mpamodzi kaya! wat do u xpect? they know how to conive pplez minds! induction by hipnotics!

Comments are closed.