Bushiri angers government

767
Bushiri

Bushiri angers government

Government has blasted Prophet Sheperd Bushiri for donating K44 million to the Malawi national football team instead of government Account Number One.

Minister of sports Grace Chiumia, according to a report by one of the local radio stations, said government is not pleased that Bushiri donated the money directly to Football Association of Malawi (FAM) rather than through the Ministry of Finance.

But Bushiri said he made the donation as a soccer loving Malawian and added that he had to do it quickly so the Flames could travel travel to Guinea.

Share.

767 Comments

 1. Thanks Bushiri Malawian goverment is full of sheet,they want to still ur donations that’s y ,they a against u. Keep on doing the good Job and leave that so called government

 2. koma amalawi ndife oseketsa kwabasi are we trying to put blame on bushiri why? walakwitsa chani that’s what his heart is telling him to reach out and touch. anakakhala mzungu munakayankhula. its high time for malawi to change because we a fond of receiving not knowing the actual sources of funds. good example is that some projects here are being funded by gay communities that’s why we are having many controversies on homosexuality. other things are happening for us to learn lessons we need to reform our system. if we always say we are God fearing country join hands and pray that God’s will shud be prevailed. Kwacha amalawi tiyeni tidzuke.

 3. can c kut the page iyi z for thoz against the rulling party sorry am neutral i talk where it has gone wrong not every tym critising xopanda mphindu mkomwe pliz stop n shutup if got nothing to say ma admin mukuononga gulu u cant y cant u regulate the posts we r serious pple

 4. can c kut the page iyi z for thoz against the rulling party sorry am neutral i talk where it has gone wrong not every tym critising xopanda mphindu mkomwe pliz stop n shutup if got nothing to say ma admin mukuononga gulu u cant y cant u regulate the posts we r serious pple

 5. Eheeee……….. Komandiye mwalebwa m,madzi munanena nokha kuti sitikufuna chithandidzo chochokela kuma iko akunja sono bwanji mukukakamila ndalama wapeleka bushili ku frames mpangedzanu mukulempela kuthandidza athu akufa ndinjala mwanya kkkkkkkkkk

 6. Eheeee……….. Komandiye mwalebwa m,madzi munanena nokha kuti sitikufuna chithandidzo chochokela kuma iko akunja sono bwanji mukukakamila ndalama wapeleka bushili ku frames mpangedzanu mukulempela kuthandidza athu akufa ndinjala mwanya kkkkkkkkkk

 7. Mukwiya Ndi Chyn Kod Zimakusangalasan Tikamadya Matuvi Anuwa Et? Mudzivele Chson Ndipo Ndikamba Pano Kwathu Kuno Anthu Akufuna Mtsogoleri Wachnyamata Magogonu Nose Tingopha Mwatikwana.Ogalu Muuzane Nose Kumene Muliko.

 8. Mukwiya Ndi Chyn Kod Zimakusangalasan Tikamadya Matuvi Anuwa Et? Mudzivele Chson Ndipo Ndikamba Pano Kwathu Kuno Anthu Akufuna Mtsogoleri Wachnyamata Magogonu Nose Tingopha Mwatikwana.Ogalu Muuzane Nose Kumene Muliko.

 9. Mboma la afiti okudya matewera a manyi ovunda, agalu achabe chabe. Bushiri-yo akudziwa sangaelekeze kupanga umbana otereo, ndalama imeneo ndiiithu anaigawana anyapala ameneo. Ku Malawi kuno boma kulibe izi ndi ziwanda za satana, si anthu awa ai, ndi mzukwa izi.

 10. Mboma la afiti okudya matewera a manyi ovunda, agalu achabe chabe. Bushiri-yo akudziwa sangaelekeze kupanga umbana otereo, ndalama imeneo ndiiithu anaigawana anyapala ameneo. Ku Malawi kuno boma kulibe izi ndi ziwanda za satana, si anthu awa ai, ndi mzukwa izi.

 11. Mboma la afiti okudya matewera a manyi ovunda, agalu achabe chabe. Bushiri-yo akudziwa sangaelekeze kupanga umbana otereo, ndalama imeneo ndiiithu anaigawana anyapala ameneo. Ku Malawi kuno boma kulibe izi ndi ziwanda za satana, si anthu awa ai, ndi mzukwa izi.

 12. You must learn to say thank you. This man he’s been donating lot of things at Malawi, left right and centre. And he’s been led by the spirit of God, don’t blame him

 13. You must learn to say thank you. This man he’s been donating lot of things at Malawi, left right and centre. And he’s been led by the spirit of God, don’t blame him

 14. You must learn to say thank you. This man he’s been donating lot of things at Malawi, left right and centre. And he’s been led by the spirit of God, don’t blame him

 15. Sorry DPP government send me your account number I want to send you some thing I think 75Milion will be fine. Forget about Bushire s donation mmmmm! Bwanji?

 16. Sorry DPP government send me your account number I want to send you some thing I think 75Milion will be fine. Forget about Bushire s donation mmmmm! Bwanji?

 17. Sorry DPP government send me your account number I want to send you some thing I think 75Milion will be fine. Forget about Bushire s donation mmmmm! Bwanji?

 18. matafale,anaimba kale ingoti peee tione,nsogoleli sikuti azikupasani zakudya think kuti kuli athu angati amuzungulira iyeyo,amalawi monangobadwa monyoza basi shaaaaaaaa koma lamulirani inuyo muziwapasa athu ndalama ndi zakudya,come and see RSA zim ndi maiko ena,aaaaaaaah mukusalila ndi kuloza zala osogolela m’malo molimbikira

 19. Kkkkkk hahhahahaha ds my government z sick physically for sure kkkkk Iwowo akulephera kuipatsa ndalama flames wina wathandiza walakwitsanso,,,,,koma agalu amenewa……..Bravo Bushiri nyc work en thanx for da miracle money en i hop its gona b a miracle win for da flames

 20. Kkkkkk hahhahahaha ds my government z sick physically for sure kkkkk Iwowo akulephera kuipatsa ndalama flames wina wathandiza walakwitsanso,,,,,koma agalu amenewa……..Bravo Bushiri nyc work en thanx for da miracle money en i hop its gona b a miracle win for da flames

 21. When Bushiri was distributing maize to the hungry malawians, the govt did not thank him for doing so and even he still continues to be a good citizen in his charitable acts, still the govt blames him….the govt becons me to a question, is donating an illegal act in malawi? And at some point I come to agree with the govt but they are misplacing their anger; instead of putting it on the challenges facing the dying nation they put on such people of good will. Yes the govt knows the areas which are in great need of funding coz it runs the govt but Bushiri don’t and in addition he does not stay in Malawi… so it sounds unfair to blame him. I think the best the govt could hv done and can still do is to ask for a help from such willing to help individuals so as to deal wit critical issues at hand. Otherwise I would like to sincere thank Bushiri and all those of good will for what they are doing to my people and my nation…God bless Malawi-Amen…

 22. When Bushiri was distributing maize to the hungry malawians, the govt did not thank him for doing so and even he still continues to be a good citizen in his charitable acts, still the govt blames him….the govt becons me to a question, is donating an illegal act in malawi? And at some point I come to agree with the govt but they are misplacing their anger; instead of putting it on the challenges facing the dying nation they put on such people of good will. Yes the govt knows the areas which are in great need of funding coz it runs the govt but Bushiri don’t and in addition he does not stay in Malawi… so it sounds unfair to blame him. I think the best the govt could hv done and can still do is to ask for a help from such willing to help individuals so as to deal wit critical issues at hand. Otherwise I would like to sincere thank Bushiri and all those of good will for what they are doing to my people and my nation…God bless Malawi-Amen…

 23. Naneso ndimafuna ndithandize netball national team ndi 36 million kwacha direct ku timuyi… Koma basi ndikuopa government indipanga criticize kkkkk!

 24. Boma lanji la nsanje ndi nzika zake? Pa donation pokhapo musiyen munthu apereke kumene akufuna. Akanafuna akanakupatsani inu pamodzi ndi prezdent wanuyo. Ngati zakunyasan pitani kumental mukachire misalayo.

 25. Boma lanji la nsanje ndi nzika zake? Pa donation pokhapo musiyen munthu apereke kumene akufuna. Akanafuna akanakupatsani inu pamodzi ndi prezdent wanuyo. Ngati zakunyasan pitani kumental mukachire misalayo.

 26. Mumafuna akaike kwa acount # 1 ndicholinga choti mukaphatikize ndi za MAGAY zija.Izi ndi za ma FLAMES zisiyeni zipite kwa ma FLAMES.

 27. ndiye amene mwalandila ndalamaku sizoti muyambeso kulodzana cholinga mudye nokha kapena anyhu adziti ndindalama za blood ngati m’mene zikuyamkhulila zitsiru zina zopana mzeru zimafuna tizivutikabe kt team yathu ngati iwowo angapeleke kanthu

 28. kkkkk apagwila pafinda paboya ena adatsegulilatu ti ma account toti aponyemo ng’oooo! mukhaula mwadya zomwezo izi zokha mwabibila pambali mwa biba dyela ndi ndalama zamwini kuboma kuboma kwa chani kuli tchito yanji yazeru

 29. Kodi abale 44million yo church chake cha ku mzuzu sichikanakhala chitatha ndipo ndi zomvesa chisoni chifukwa azitumiki omwe anawasiya ku mzuzu akuvutika molapisa. Analakwa chani anthu wa chonde bushiri athandize

 30. kuthandiza kwazifukwa sikwabwino pamaso pa mulungu chuma chidzabedwa koma mawu adzasungidwa chikhalile do if u

 31. Direct donations are more appropriate than the unsusual stages of account number one. We are all aware of the urgency with which our team needed the money. May be the government should involve this Bushiri next time if ever there is need for money, food, prayer , fertilizers, decision making etc.

 32. Bright tiye nawo amalawi ngatulo akufuna azizatitopesaso ndikulira kutsogoloku ndi blood money magazine akuyenda m’misewumu,muthu umalowa nyumba mwayini ake opanda odi ngakhale muli mwa m’bale wako?ndi mwano,ndakuvesani amalawi tikusukusula kumene sitikuziwa malamulo m’mene amayendela ,ndinalotapo za blood money amalawi be careful!!!!! Dziko latha ili tiyeni nazo zolandila landila,mundikhululukile ndine mwana wang’ono ndangodusamo m’mundanu sindinatchole khwani ,NDIZAULULA

 33. Hahaha MALAWI mwagwa nayo mumafuna muthyolele muthumba
  Wakuchenjelerani kkkkk amakudziwani khalidwe lanu ndipo palibe amalikhulupilira boma la malawi.

  Bwanji simunakwiye kuti chimanga wagawa kwa anthu sanatumize mu nkhokwe za malawi?? Poti ndi ndalama mwakwiya nayo kkkkkk

 34. This man Bushiri wants the leadership by coming 2019, munthu wa Mulungu sangathandize Mpira kusiya anthu opemphera akupemphelera kunsi kwa mtengo palibe chamzeru apa, keep my words, munthu uyu imeneyi ndi underground campaign akufuna utsogoleri ndithu uyu ali ndi chidwi pa utsogoleri mkulu ameneyi mumuone bwino

  • 4 him 2 become a president its dimotion anayakhanso kale live a pa times tv akuchedza ndi brian banda man!! ndipo atafuna kuyimira u president ndi vuto kodi??? is he not a dzika of dis county kodi???

  • 4 him 2 become a president its dimotion anayakhanso kale live a pa times tv akuchedza ndi brian banda man!! ndipo atafuna kuyimira u president ndi vuto kodi??? is he not a dzika of dis county kodi???

  • kodi anthu okalamba akuwamangila nyumbawa sikuthandiza??? nanga chimanga chambiri wagawa dziko munochi sikuthandiza hmmm unalinso mpira kodi??? let him help were ever he feels dat he can help man osamakhara anthu okonda kuyakhura ndikunyoza popanda chifukwa bro!!!

  • kodi anthu okalamba akuwamangila nyumbawa sikuthandiza??? nanga chimanga chambiri wagawa dziko munochi sikuthandiza hmmm unalinso mpira kodi??? let him help were ever he feels dat he can help man osamakhara anthu okonda kuyakhura ndikunyoza popanda chifukwa bro!!!

 35. Well done men its for malawi national team sizaboma ayi kodi ati national team of malawi alibe yawo account aaaaaa

 36. isa viwanthu vopanda nzeru ivi vimangofuna vtadya ndalama tsapano….Mwagwa nayo Bushiri go on dnt even drop a single note into de gvt account…Luk at dem wth dere Money Desire Boils(MDB)…Osatinyasa ife ngati mwakwiya kakolopen Indian Ocean

 37. Koma dpp guyz zoona bushiri sakukugonetsani tulo? Kkkkk, koditu iyeyi akuthandzani kuendetsa dziko cz zukuvutan heavy nde mukulilira 44m wapereka kumpirayi? Kkkk inutu musekedwa koopsa tangoisiyani nkhaniyi

 38. Agalu Inu Akuchitan Bwino! Aike Acount N#1 Mubeko Mwakhaula & Ndi Ndalama Zake Osat Zaboma Kaziban Ndi Mr Ibu Wanuyo Kumeneko Mpaka Muzilamulila Zochita Ndi Ndalama Zamthumba Mwanu ? Muyaluka

 39. Abushiri kumeneko kuphiphirisa kutiseka maso cholinga tisawone zomwe mwachita?takutulukilanibe there is no secret ander de earth,NDIDZAULULA by GRECE CHINGA

 40. This government is dull and baseless Bushiri was donating maize to starving Malawians the government critised, He stoped this time He has donated k44 million it is also babbling. should we say Bushiri amangolakwitsa anything? amafuna abenso that money! Bravo Big man,moreover whenever our nation team is going abroad complains about less funds yet Government and account number one is there.foolish!!

 41. Yes we know that most of goernment officials are thieves but the little could reach the poor if that amount of money was shared and put into all district to buy grain.

 42. My psychic readings focus on positive thinking & positive change. It may assist in bringing clarity to a confusing situation, help you prepare for the future in a more focused way and may empower you with positive potential. If you are seeking spiritual guidance with your relationship, marriage, love, family, career, money, health matters, or life’s daily issues, my insightful accurate psychic reading will help you answer the questions that weigh heavily on your mind. I would love to assist you with making the best decisions for your Future. No matter where you live I can help you.Call +27738951830 MUNIL SALEH, I do Whats-App, Face book/munilsaleh, Phone and personal readings.

 43. Jealousy from Govt…….there is no need for him to deposit the money into Govt account 1…this is myopic thinking from the minister of sports

 44. Kubomako olo nzeru mulibe kut muunikilaneko, chosangalatsa mchani ma player anu azikhalira kulandira ka k10000 pa mwezi,ndemkumakhaliranxo kunyoza ma player adziko lanu kut mbatata chonxencho munthu akulandira kandalama ka lunch yanu yatxiku limodzi, muzikhutitsidwa ndizomwe matikolora kale amphawife mudzina lamsonkhozo ok!….bushiri kip it up posatengelaso kut ndalama zanu mazipeza munjira yanji!

 45. Bushiri did nothing wrong to donate that money directly and i appreciate him,because the government already allocated money for sports so the Gvt officials just want to pull the money in their pockets

 46. To me, a donation is a donation though it comes in either through the window or the door. What matters here is that this one is a direct donation. Wina sanayione. Palibepo kususa apa. Big up Bushiri.

 47. hahaha abraz whats wrong with Bush kkkkk mesa mukanika kuithandiza teamuyi kkkkk inu ndalama mulinazo koma kakaka muonangati mukafa muzanka nazo hehehe shame my gvnment

 48. Fearing of the unknown why Govt spending sleepless nights and having diarrhea with Bushiri is it because he is closer to JB? Take it easy you are in control let Bushiri help where he can he has financial muscle simutha kuletsa he is a Malawian and he has big surport world over ! Just receive and say thank you Bushiri the son of Malawi!

 49. If i was me i would share that money equally to all the distrct of Malawi to buy grain. It could be K44 milion divide by districts.

 50. Let the richer help the poor,. It gives a sense than what gvnt is doing by kukwezga katundu with the aim kuti atolele ndalama from poor people, some millionaire you can help bushiri kuti amphawife tisafe ndinjala through this regime

 51. Inuyo a minister tengani ndalama zanu mukaike ku account number 1. Bushiri ali ndi ufulu kupereka direct kwa amene akusowa thandizo. Morever inu aboma mwathandizako ndi ndalama zingati? Ntchito kumangokokera anzanu pansi amene akupanga zabwino.inu mwaoneka tsopano kuti muli ndi zima problem

 52. idont know what the hell this stupid government of ours thinks about what kind of procedures do they need big up ma prophet sherpherd bushiri malawi loves you government doesnt

 53. gavernment or no government.major 1 has done what every malawian cld have done.he loves sports and thats what exactly has happened.no one is to be trusted in government.

 54. Thanks Major one,do not listen to these thieves call themselves government asowa chakuba amenewa.They can even steal condolence money,

 55. Grace who doesn’t know that ukudwala. Why don’t you just go to Prophet and ask for prayers.
  Mwamuna wako anafa ndichiyani. Just ask a total healing.Don’t be jealousy just appreciate that you are a minister. You know forsure that what you are doing is wrong but you want to kiss Muthalika’s ass

 56. Brainwashed Malawians, Where Did Govt. Blusted Bushiri? Bushiri Is Malawian Based In S. Africa. Let Us Put This Dark Gospel To Rest Once And For All. For Those Who Are Blessed To View Where Eyes Cannot Not See Use The Gifts To Enlighten Others…….. Judge Not!!!

 57. Inu ndinu zisilu kwambili kodi bushiliyo kumalawiko anathawa chani mesa anathawa mavuto akumalawio kumazaanamiza anthu pretoria westmu ndalama zimenezo ngati tumiki osafikila nazo anthu okalamba kapena osaona ndi ena akupasa anthu olemela kale zopusa amalawi maganiza zopusa

 58. 1,Malawian Donert K44 million What about 44,malawian=MORE, NDIYE MUZINDIPEMPHA MUKANDIONA NDI K100 Yanga Nkumati Ndiinu Osauka, Kkkk Wina Ayerekeze Ndimuluma Ndimupasire Edzi.

 59. helping the national team is just the same as helping the gvt.kodi si inu munamuletsa kugawa chimanga kwa amalawi ovutika?lero mukuti he could have come straight to the ministry of finance… you must appreciate you pipo.kuthandizidwa ndi munthuyu mukukufuna koma simukufuna kuonetsera .anthu opanda pake inu…

 60. Bushiri has donated that money on good will because he has seen a need to do so.Therefore,government should not blast anyhow without examining the intensity of the assistance.As Malawians lets work together.Don’t disappoint people of good will.

 61. Bushiri has donated that money on good will because he has seen a need to do so.Therefore,government should not blast anyhow without examining the intensity of the assistance.As Malawians lets work together.Don’t disappoint people of good will.

 62. koma mw gvt mukasowa zchta ngat uli ukalamba bola kungoutaliktsa Major prpht sanalakwitse kutero mot inu cmukudziwa kut iyeyo wadziwa kale kut zthera Mmatumba mwanu as a prpht asiyen anyamata nayeso Gaba akamange yake cashgate style kumnda mukumakamanga kuja

 63. koma mw gvt mukasowa zchta ngat uli ukalamba bola kungoutaliktsa Major prpht sanalakwitse kutero mot inu cmukudziwa kut iyeyo wadziwa kale kut zthera Mmatumba mwanu as a prpht asiyen anyamata nayeso Gaba akamange yake cashgate style kumnda mukumakamanga kuja

 64. Anthu oipa inu muli ndi sanje mumafuma kuba ndalama za mtumiki ndiye mwalemba mmadzi somba zawerenga,thanks Bushiri pliz dont do any business with the government,they are full of shit

 65. Anthu oipa inu muli ndi sanje mumafuma kuba ndalama za mtumiki ndiye mwalemba mmadzi somba zawerenga,thanks Bushiri pliz dont do any business with the government,they are full of shit

 66. There is something fishy somewhere, Bushiri just want to make headlines, imagine here in Mzuzu his church is in a dilapidated condition, why can’t he use that money to construct his church in Mzuzu and many parts of this country. Why can’t he construct a magnificent church in blantyre and Lilongwe then after doing that he may start throwing money like the way he is doing, why can’t he priotise things of god?

 67. There is something fishy somewhere, Bushiri just want to make headlines, imagine here in Mzuzu his church is in a dilapidated condition, why can’t he use that money to construct his church in Mzuzu and many parts of this country. Why can’t he construct a magnificent church in blantyre and Lilongwe then after doing that he may start throwing money like the way he is doing, why can’t he priotise things of god?

 68. Koma munthu sazayamika BushirI chimanga anapereka, kwa nathu ovutika, pano wathandizako mbali ina basi akanaguliora chimanga! ummm mwaziwa ma plans ake? thi z Man f God wil do other mirracles to other departments one day jst wait. #NO_Blames

 69. Koma munthu sazayamika BushirI chimanga anapereka, kwa nathu ovutika, pano wathandizako mbali ina basi akanaguliora chimanga! ummm mwaziwa ma plans ake? thi z Man f God wil do other mirracles to other departments one day jst wait. #NO_Blames

 70. koma bomaso nalo kodi ndalamazo akufuna a BEAM azidye monga momwe ana dyera za NAC zija? nde mwina boma likufuna kuti azathu akunjawa asatithandize? eeeee koma mlungu tichoseleni athuwa akuvuta

 71. koma bomaso nalo kodi ndalamazo akufuna a BEAM azidye monga momwe ana dyera za NAC zija? nde mwina boma likufuna kuti azathu akunjawa asatithandize? eeeee koma mlungu tichoseleni athuwa akuvuta

 72. Kuzolowera kuti muyambe mwazisungunura zikafike zoche kofunikira. I wish other well wishers(countries) could learn spirit of Bushiri. Giving direct to ther suffes. They do steal so much. Mwagwa nayo

 73. Zachamba_Mesa_Poyamba_Mmene_Ankafuna_Kuthandiza_MwGovt_Ndchmanga_The_Same_Govt__Inkang’ung’udza.Com Pano_Pot_Wathandiza_Fam_Direct_Mukumpanganso_Blame_Eee_Kma_Malawi_Kuvetsa_Chson_Anthu_Kuganiza_Ngat_Sadaloweka_Mkalas_Muisovenge.Com

 74. Zachamba_Mesa_Poyamba_Mmene_Ankafuna_Kuthandiza_MwGovt_Ndchmanga_The_Same_Govt__Inkang’ung’udza.Com Pano_Pot_Wathandiza_Fam_Direct_Mukumpanganso_Blame_Eee_Kma_Malawi_Kuvetsa_Chson_Anthu_Kuganiza_Ngat_Sadaloweka_Mkalas_Muisovenge.Com

 75. Wow! keep it man of God osawapatsa ndalama anyani amenewa amaona ngati zifikira kwa iwo cholinga abe iiii Koma mbava zili ku Malawi eee donate direct paja chimanga adakuletsani ati kulibe yet pple are dying ati mupanga campaign kuti muzakhale president.Ee ife tikhoza kuzavota nyasi zilipozi

 76. Wow! keep it man of God osawapatsa ndalama anyani amenewa amaona ngati zifikira kwa iwo cholinga abe iiii Koma mbava zili ku Malawi eee donate direct paja chimanga adakuletsani ati kulibe yet pple are dying ati mupanga campaign kuti muzakhale president.Ee ife tikhoza kuzavota nyasi zilipozi

 77. Aunikira mbali yomwe kumapezeka magazi ambiri mosavuta. Masapota akakagendana nkutulusana mwazi, mpingonso ukukula. Zonsezi kufuna kulowetserapo za ulosi wanu okupha uja.

 78. Aunikira mbali yomwe kumapezeka magazi ambiri mosavuta. Masapota akakagendana nkutulusana mwazi, mpingonso ukukula. Zonsezi kufuna kulowetserapo za ulosi wanu okupha uja.

 79. A prophet bushiri chithandizo chanu muzitapasa nokha mukampansira munthu samatipasa chonse china amabako.Kumufunsa atha kutimanga chifukwa ndife osauka tiribe lawyer akatiponya ku maula munthu ameneyo.Kutsogoloko akuti azitimanga tikamakuwuzani zamavuto athu pa facebook.

 80. A prophet bushiri chithandizo chanu muzitapasa nokha mukampansira munthu samatipasa chonse china amabako.Kumufunsa atha kutimanga chifukwa ndife osauka tiribe lawyer akatiponya ku maula munthu ameneyo.Kutsogoloko akuti azitimanga tikamakuwuzani zamavuto athu pa facebook.

 81. Kodi amene mukuti Bushiriyu ntchito yeniyeni imene amagwira ndikumapeza ma million onsewa ndiiti? Yomweyi yotumikira nkhosa za Mulungu pozidyetsa mau akeyi kapena ali ndi ntchito zina? Mmmhu Mulungu wanga ndipemphero langa masiku otsiriza muonetseni mMalawi mtumiki amene azamutumikire za ufumu wanu osati wapansi pa…….#Amen#

 82. Kodi amene mukuti Bushiriyu ntchito yeniyeni imene amagwira ndikumapeza ma million onsewa ndiiti? Yomweyi yotumikira nkhosa za Mulungu pozidyetsa mau akeyi kapena ali ndi ntchito zina? Mmmhu Mulungu wanga ndipemphero langa masiku otsiriza muonetseni mMalawi mtumiki amene azamutumikire za ufumu wanu osati wapansi pa…….#Amen#

 83. komadi pena kumali ganizila boma, 44 million is too much, anthu akuvutikatu , pena kumali vetsesa boma mavuto awo osawona zoyipa zokhazokha.

 84. Protocal must always be followed, sakulakwa kuthandiza, koma a Bushiri monga munthu ozindikila akuenela kupanga zinthu mosatila malamulo a boma.

 85. Masa iweo uti ulibe problem nde ndalamazo nzachani kuti akupatse……??? Big Up Bushiri….ndipo akulira aBoma salnati…….

 86. anthu ofunika u president ndi achina Bushiri mwina zosololazi iwo sangazikwanitse akhoza kutukula malawi wathu wavundayi(wanunkha ngati galu wowola).

 87. anthu ofunika u president ndi achina Bushiri mwina zosololazi iwo sangazikwanitse akhoza kutukula malawi wathu wavundayi(wanunkha ngati galu wowola)

 88. Bushiri wachita bwino chifukwa pafupifupi wina aliyense ndi wakatangale ndipo katangale wavutadi paziko pano. Pano okawa pandalamayi ndi oona za masewela a mpila basi pamene zinakazera ku Boma okawa anakachuluka. Ndalama zikanafika masiliva ku Fam.

 89. But government why do you really HATE Bushiri?He gives food to the needy you hate him.He donates money for Flames trip you get angry.Kwenikweni ndi chiyani??

 90. does the Govt have to rely on donors? I knw its not bad but do we need emotions to be part of this? And I guess independent of who the money has been given to human beings are entitled to criticism

 91. She wanted the money badly ku account no 1; with an aim kuti akasololepo kaye zisanayambe kugwira ntchito imene zaperekedwera. Because of this mindset Malawi sadzatukuka.

 92. She wanted the money badly ku account no 1; with an aim kuti akasololepo kaye zisanayambe kugwira ntchito imene zaperekedwera. Because of this mindset Malawi sadzatukuka.

 93. koma mw gvt????They only onted to mis-use the money..kkkkkkk timati ‘kugenda katauluka’ koma nsaname am tired eish…Bushili this, Bushiri th@.Tamsiyani ameneyu hiiii.

 94. Don’t you know that Bushiri is a form 4 drop out? His actions always tell a story. He hails from Gongolo village in Ntcheu but his parents are settled in Salima. He mostly grew up with his brother in Mzuzu. I learnt this from the interviews he had with TVM the other day, years ago. You can’t trust him. He is dangerous indeed. Ask his his family relatives and you will be shocked

 95. Major 1, hope these miracles money will turn things around for flames to win.and it is good that you give directly to the team not to the government otherwise these could go into their pocket instead of supporting the team.well done pastor keep supporting our national never stop no matter their talk bad about you. GOD BLESS YOU

 96. ma guy … Osapanga act ngati ndalama ikuchoka m’thumba mwanu __ if that K44 mill was coming from my pocket, mmh you couldn’t tell me nothing. Nothing like Who I should give or how I should spend it!! Cut the drama and let Bushiri do his thing! Broke *ss

 97. Sopano inu a boma zakuwawani pat?kod smuzwa kut flames nthandawuzo kake nd MALAWI?Nanga ndalamazo zaptakut?mesa zapta ku bomako?mnangozolowela zodalira….inu mkanakwanisa kuwapasa ndalamazosezo….kupusa

 98. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: dr.collinsherbalhome@gmail.com or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: dr.collinsherbalhome@gmail.com AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS…

 99. Oh!! Poor Malawian, We Alwayz Feel Comfortable When W’re Recieving Something From Well Wishers. Let Us Change That Software And Blame Bushiri 4 Suppor Football Team Keep It Up Mr Only God Will Replace Where You Have Removed.d

 100. Oh!! Poor Malawian, We Alwayz Feel Comfortable When W’re Recieving Something From Well Wishers. Let Us Change That Software And Not Blame Bushiri 4 Suppor Football Team Keep It Up Mr Only God Will Replace Where You Have Removed.

 101. anthu kumangokomenta koma simukuyamba mwaganiza ndikuzifunsa mafunso awiri kapena atatu kuti ntolankhani walembayu amalifunira dziko lamalawi zinthu zabwino kapena wangomukulira ndi umbuli pomapeka nkhani zake zabodza kuti amve maganizo a anthu,please please osamatengeka ndinkhani zabodza mukangoona ka page kalembedwa kuti Malawi mumaganiza kuti alembawo ndianzeru koma kuti muwaone anthu akewo yamayunitsi amachitanso kupemphetsa cholinga agure ma mb opangira post zinthu zabodza shame on u and ur page I’m disliking it ndakwiya nanu

 102. There is no way to tell him where to donati the money its for him he have the lite to shose were to donati and hom to give mwarembam’madzi

 103. Kikikikikikikikiki wa #llluminati uyo azimayi akufuna ndalama zawo kuno ku south Africa 4ways unawanamiza akufuna ndalama zawo #R150000 video yako ndili nayo and xool unali kuphuzila pa moyale barracks ku mzuzu wa satanic??????

 104. Malawi24/7 please tiuzeni ndani wadandaulayo? Bcoz if fan ask for donation, no one pay that donation to government account. Bcoz government account its for them not Fam…

 105. Major One,am impressed wth your donation,from tody onwards,mek direct donations,this is ur country and that shows patriotism.what wud pipo say if u donated to another contry?Kip it Major One but Fam shud give details of expenditures,more faya !!

 106. Hehehehehehe…aMalawi amenewo! Shaaaaaa…inde tivomereze kuti ka Nyamilandu nditanzake tina taku FAM n’timbava. Koma amangwetu nanga kuba azingoba aku Capital Hill basi? Enafe kubako sitikukufuna, muyesa njalayi yatolepa munthu? And, by the way, when did FAM stop having an account?

 107. who gives a fuck about that fuck the government fuck malawi 24 fuck flames fuck whatever you feel,fuck that money & fuck u all who are supporting this fuck u

 108. I dont see anything good Malawi National team they hav money… Reach out and touch to those who doesent hav shelter food and clothes…. shame…. but please let us think about the needs

  • you are very right even my self , l don’t agree with the donor 44 million is too much for football only at this current situatian here in malawi.

  • you are very right even my self , l don’t agree with the donor 44 million is too much for football only at this current situatian here in malawi.

  • Its his money, he can donate to whoever he wants. Its not bushiri’s fault that some people don’t have shelter, food or clothes and its not even his duty to take care of them.

  • Its his money, he can donate to whoever he wants. Its not bushiri’s fault that some people don’t have shelter, food or clothes and its not even his duty to take care of them.

  • Even when Jesus christ was here same ppl wea there lame , cripped poor etc but he neva touched them all instead he went to chill wt Zacheaus the rich man .. Its nobody faults

  • Even when Jesus christ was here same ppl wea there lame , cripped poor etc but he neva touched them all instead he went to chill wt Zacheaus the rich man .. Its nobody faults

  • Tracy Jackson I think you’re one of them,anthu opanda chikondi ndi dziko lanu.take a good look to our national team how poor it is?our players then I can’t say it,they are poor more than any player around the world.ndiye munthu wina wa kufuna kwabwino waithandiza team yathuyi,now you start complaining mumafuna wa bwino azipanga bwanji? can’t you feel shameful to what you are complaining?look at to the one you call your President what he done to the team?and even to the people of Malawi?absolutely nothing but punishing people with hunger.tandiuze ndi dziko liti lomwe zipatala za boma zimakhala zolipitsa?

  • Kod Kukhala Chilala Ndie Alephele Kuthandiza Ena Omwe Akusowanso Ndalama? Mukuona Ngat Malaw Team Ili Mu Gud Condition? Zimenezo Auzen A Boma Athane Nazo Icho Ndi Chikozelo Cha Bushiri Coz Iyeyo Atakhala Anaona Kut Pakusowekela Kuthandizapo, Ndie Nanunso Ngat Mwaona Kut Nyala Ya Vuta Pangan Donation Yanu Osat Kutsusa Budget Ya Nzanu Umbuli Umeneo Ngakhale Mukudziona Ngat Ndinu Ophunzila, Kwanu Nku TSusa Bas Inu Tidakudziwan Thandizan Anjalawotu?

  • kkkkkk iweso nde mutu wako sumagwiratu,,waiwala kuti bushiri ankagawa chimanga koma its da sem ur govt whch stopd him,,,,,,,u cnt hlp anyone in ur country or villagr my friend…tiyeni timuyamike Bushiri for what he hs done

  • kkkkkk iweso nde mutu wako sumagwiratu,,waiwala kuti bushiri ankagawa chimanga koma its da sem ur govt whch stopd him,,,,,,,u cnt hlp anyone in ur country or villagr my friend…tiyeni timuyamike Bushiri for what he hs done

  • Amenewo ndi maganizo anu chemwali.Inuyo mutenge ndalama zanu muthandizire anthu amene akuvutika.Izo zina ndalama zake.aliyense amakhala ndi ufulu pa chinthu chake.

  • Amenewo ndi maganizo anu chemwali.Inuyo mutenge ndalama zanu muthandizire anthu amene akuvutika.Izo zina ndalama zake.aliyense amakhala ndi ufulu pa chinthu chake.

 109. You cash gaters, stop blaming welwishers. Bushiri as well as anybody has right to donate their money to whichever govt sector or anything without to blame. It’s high time that all donors too should send their funds literally direct to where the projects are being implemented and not through central office ~feudalism

 110. I think m’Malwi muno tikanaganizabe mopotoka,ndaonanso wina akut dzina lake ndi bright waitha,nayenso ndi nyapapi cos malo mot angoyamika akungokamba zopanda nzeru….iwe ukuona chalakwika ndichan munthu kuthandiza ngat ali ndikuthekera kupanga zimenezo….shupit zako wava…munthu opanda nzeru iwe….bright waitha…big up MAJOR 1….UR BLESSED TO B A BLESSING TO THE LESS PREVILAGE

 111. M’mafuna almost 12million itsale konko ya MSONKHO? KKk iwe Gilley ukatofuna allowance kokalandira cheke eish mbuyanga mwagwanayo. Don’t hate Earnest 4 approaching the Major paja mmayamba kulowetsa ndale. Best wishez my FLAMES God bless.

 112. boma loola ngati iri sindidalionepo! poyamba ati ndilibe probrem uchoka apo akuti sindifa kkkkkk opanda problem amatero? inu mr mulinayo problem!!!!

 113. boma loola ngati iri sindidalionepo! poyamba ati ndilibe probrem uchoka apo akuti sindifa kkkkkk opanda problem amatero? inu mr mulinayo problem!!!!

 114. boma loola ngati iri sindidalionepo! poyamba ati ndilibe probrem uchoka apo akuti sindifa kkkkkk opanda problem amatero? inu mr mulinayo problem!!!!

  • Akanathandiza ma Condom 51.million directly kwa MAHULE onse a mMalawi, Boma likanati zi.i.i.i.i:-| -koma poti ndi Nalamaaaa,,;-(

 115. Chomwe muziwe amalawi azanga tingotayapo time kumuda bushiri kodi inuo mavuto adzikowa anjala simukuwaona ?? Mukuchitapo chani inu aboma tsopano man of God by God wisdom wathandiza Lero mukumuda kumunamizira kut akufuna kulanda boma or president ganizani bwino apo n bible limati musamatoza azitumiki a Mulungu tiyeni timuyamike pa zonwe wakuchita osati kumukumba ziwani kut judgement is for God himself not us esh sitizatukuka chifukwa cha sanje ,, kaduka , kupondelezana mmalawi muno tizivele ntolo yakobo 2 vs 14 goin down

 116. Chomwe muziwe amalawi azanga tingotayapo time kumuda bushiri kodi inuo mavuto adzikowa anjala simukuwaona ?? Mukuchitapo chani inu aboma tsopano man of God by God wisdom wathandiza Lero mukumuda kumunamizira kut akufuna kulanda boma or president ganizani bwino apo n bible limati musamatoza azitumiki a Mulungu tiyeni timuyamike pa zonwe wakuchita osati kumukumba ziwani kut judgement is for God himself not us esh sitizatukuka chifukwa cha sanje ,, kaduka , kupondelezana mmalawi muno tizivele ntolo yakobo 2 vs 14 goin down

 117. Chomwe muziwe amalawi azanga tingotayapo time kumuda bushiri kodi inuo mavuto adzikowa anjala simukuwaona ?? Mukuchitapo chani inu aboma tsopano man of God by God wisdom wathandiza Lero mukumuda kumunamizira kut akufuna kulanda boma or president ganizani bwino apo n bible limati musamatoza azitumiki a Mulungu tiyeni timuyamike pa zonwe wakuchita osati kumukumba ziwani kut judgement is for God himself not us esh sitizatukuka chifukwa cha sanje ,, kaduka , kupondelezana mmalawi muno tizivele ntolo yakobo 2 vs 14 goin down

 118. A bright waitha mmm!! tiyeni tiziyamika abwino akatithandiza pamene tapeleweledwa. kapena zakunyasani kuti………….. ndangodusa ine but shame on you because of your comment

 119. A bright waitha mmm!! tiyeni tiziyamika abwino akatithandiza pamene tapeleweledwa. kapena zakunyasani kuti………….. ndangodusa ine but shame on you because of your comment

 120. A bright waitha mmm!! tiyeni tiziyamika abwino akatithandiza pamene tapeleweledwa. kapena zakunyasani kuti………….. ndangodusa ine but shame on you because of your comment

 121. Our Ethics, Values, Culture as Malawians. Timathokoza ngati Ku Mpoto, “Timati Bayethye, Zaliro, OBanda”.
  Contrary someone is Blasted .
  Kkkk. Napansi Dweku!!

 122. Our Ethics, Values, Culture as Malawians. Timathokoza ngati Ku Mpoto, “Timati Bayethye, Zaliro, OBanda”.
  Contrary someone is Blasted .
  Kkkk. Napansi Dweku!!

 123. Our Ethics, Values, Culture as Malawians. Timathokoza ngati Ku Mpoto, “Timati Bayethye, Zaliro, OBanda”.
  Contrary someone is Blasted .
  Kkkk. Napansi Dweku!!

 124. ndalama sizimachuluka ukasololo lero m’mawa umafuna. They know Malawian are good in speaking not actions even if they can see some one stilling we cant act.

 125. BUSHILI ndikuyamike pa chinto yomwe ukupanga onena zinenani oweluza weluzani thanx bushiri ples kofunikaso timuyi kuyipephelela ziwanda zoluzaluza

 126. BUSHILI ndikuyamike pa chinto yomwe ukupanga onena zinenani oweluza weluzani thanx bushiri ples kofunikaso timuyi kuyipephelela ziwanda zoluzaluza

 127. BUSHILI ndikuyamike pa chinto yomwe ukupanga onena zinenani oweluza weluzani thanx bushiri ples kofunikaso timuyi kuyipephelela ziwanda zoluzaluza

 128. Hehehehe kaya wina akwiye kaya asakwiye koma ndalama zapita m’manja mwaathu oyenela,,mumafuna akupaseni muzizisakazanso kkkkkk mwalemba m’madzi achule awelenga,,,, #major_1 do it iyeeeeeeeee

 129. Hehehehe kaya wina akwiye kaya asakwiye koma ndalama zapita m’manja mwaathu oyenela,,mumafuna akupaseni muzizisakazanso kkkkkk mwalemba m’madzi achule awelenga,,,, #major_1 do it iyeeeeeeeee

 130. Hehehehe kaya wina akwiye kaya asakwiye koma ndalama zapita m’manja mwaathu oyenela,,mumafuna akupaseni muzizisakazanso kkkkkk mwalemba m’madzi achule awelenga,,,, #major_1 do it iyeeeeeeeee

 131. Iwe bushili machende ako galu mfiti muthu wasataniki iwe, wokumwa magazi anthu mchifukwa chani ukupusisa khosa zamulungu ndi chuma cha mwazi wa athu ndigulu lako, mulungu sekulani maso akhosa zanu kuwala kwanu kuwalise maso awo, tinabadwa opanda kathu tikupita opanda kanthu limbisani njila zaolungama jah rastafarai jah rastafarai sela.

 132. Iwe bushili machende ako galu mfiti muthu wasataniki iwe, wokumwa magazi anthu mchifukwa chani ukupusisa khosa zamulungu ndi chuma cha mwazi wa athu ndigulu lako, mulungu sekulani maso akhosa zanu kuwala kwanu kuwalise maso awo, tinabadwa opanda kathu tikupita opanda kanthu limbisani njila zaolungama jah rastafarai jah rastafarai sela.

 133. Iwe bushili machende ako galu mfiti muthu wasataniki iwe, wokumwa magazi anthu mchifukwa chani ukupusisa khosa zamulungu ndi chuma cha mwazi wa athu ndigulu lako, mulungu sekulani maso akhosa zanu kuwala kwanu kuwalise maso awo, tinabadwa opanda kathu tikupita opanda kanthu limbisani njila zaolungama jah rastafarai jah rastafarai sela.

 134. Or zitakhala zoona kaya zonama donation yopita ku zigawo ngati zimenezi za mbali ya boma even kuchipatala donation ikakula imayenda mudongosolo nkati chete aaa ndayamba kudabwa nawo a prophetwa iwowa ali ndi cholinga.

 135. Or zitakhala zoona kaya zonama donation yopita ku zigawo ngati zimenezi za mbali ya boma even kuchipatala donation ikakula imayenda mudongosolo nkati chete aaa ndayamba kudabwa nawo a prophetwa iwowa ali ndi cholinga.

 136. Or zitakhala zoona kaya zonama donation yopita ku zigawo ngati zimenezi za mbali ya boma even kuchipatala donation ikakula imayenda mudongosolo nkati chete aaa ndayamba kudabwa nawo a prophetwa iwowa ali ndi cholinga.