EAM condemns APM’s speech on TB Joshua

Advertisement
Peter Mutharika

The Evangelical Association of Malawi (EAM) has condemned President Peter Mutharika for hitting out at Nigerian Prophet TB Joshua.

Peter Mutharika
Mutharika: has been condemned after his outbursts

Speaking as he was presiding over the ground breaking ceremony for Daeyang Luke University Teaching Hospital in Lilongwe, Mutharika said Joshua makes false prophecies.

However, the general secretary for EAM, Pastor Francis Mkandawire says the president has behaved inappropriately.

“I think the president was not supposed to comment on that issue. As the father of this nation he was supposed to unite us. For me I can conclude that the speech was not good,” said Mkandawire.

The EAM general secretary has since called on politicians to stop commenting on religious issues since they are sensitive.

Mutharika’s outbursts came after a prophecy by Joshua who said an African leader would die though the prophet did not mention the name of any president.

Yesterday, Malawian prophet Austine Liabunya reacted by saying that God is angry with the Malawi leader and He will take away the president’s life.

Advertisement

336 Comments

 1. Zoonadi zake nzakuti aneneri a Mulungu Alipodi ( Eph 4:11) Komanso aneneri onyenga aliponso ( Math 24:11). Ndi udindo wa aliyense kuonetsetsa kuti akulandira zinthu zoyenera kuchokera kwa anthunso oyenera. Ngati Munthu Akuona kuti zomwe akuudzidwa nzosoyenera malinga ndi chikhulupiliro chake, ali nako kuthekera kozikana, sakakamizana, chifukwanso Mulungu Sakakamiza Munthu Kuchita Kapena Kusachita. Tingathe kudzindikira aneneri kapena uneneri/ulosi oona kapena wabodza poona zinthu izi: 1. nchito zao : Yesu ananena kuti mudzawadziwa ndi ntchito zao. 2. mau omwe akulankhulawo ngati akufunana ndi mau a Mulungu. 3. Ngati Zomwe Akulankhulazo/zingachitikedi. Zikangophonya Ndiye Kuti Ulosiwo Ndi Wabodza, Ambuye Sanamtuma Iye. Tiyeni Tiyembekedze Ndi Mapemphero, Zikachitika Tinene Amen, Zikaphonya Tinenanso Kuti Ndi Bodza. Lets Wait & See The Outcome Of The Prophecy

 2. I love Sr. Prophet TB Joshua. Just repent your sins. Even Jesus one good day had to pose a bit and ask who do people say I am. Several answers were given to him. You too ask Malawi to talk freely on who you are and even your ministers. Then repent and reconcile quickly. There’s no much time.

  To all Malawian let’s go to church and not pubs where you don’t get any wisdom at all. Let promote Malawi in prayers. I would advise that you read the Bible and by free banquet to watch Emmanuel TV. You will stop talking this madness when you for yourself the man you are arguing against.

 3. Ndiponso EAM iyiyi ndi yopusanso ikuchita bwanji comment nkhani yosawakhudza. Who are you to dictate to the President not to respond. Inenso ndikukudzudzulani kuti bwanji mukuyankha zoti inu simunatchulodwepo? A gwenyenthe inu ana anjoka inu. Infact ngati mulidi akhristu mukuyenera mudzudzula Joshua wanuyo. Otherwise you may as well go to hell.

 4. Anthuni, sindikumvetsani kuti pamene mukanika kumvetsa ndipati. TB J. He did not mentioned the country or a name of some body please!!!! paja mudaxolowera kumva nkhwangwa ili mmutu.

 5. The Bible says,touch not my annointed one and do no harm to my prophet.I think its special grace to be told dat u r going to die coz it helps to create gud relationship with God.

 6. Iwe prophet asamangolosera zaimfa zokhazokha amalekeranji kulosela zabwino zikamafuna kuchtika mudakali mtulo akulu omapembedza mafano! Haaa! Kkk! Munthu wakumalawi,matsiku omalidza satana adzavala mkanjo oyera nazanyenga ochuluka ndi opusa akuziyesa achrist km asanafike, tidzapulumuka mwachisomo lekani kugwadila mafano TB josual? MULUNGU akuyendereni

 7. Let understand one thing God is love… When the prophecy come is to the prophet to pray and intercede upon the prophecy to have the fullness of the prophecy….. But the Bible we have authority to refuse bad message from almighty book of isaiah 38; king hezekiah refused….the problem is we are worship man of god more than jehovah …….president is also a leader chosen by god . so he can stand against prophesy ….to be president is to be anoint also by god … To be prophete is to be anointed by god ….now let us thing one together …… God is love …does not take pleasure in death ….he gave us long life …..so people let us go and hear and obey god . we will discerned some message and how to react upon it . all is well to our love president and to the prophet too.

 8. TB Joshua, wayankhula monga munthu ndipo President Munthalika wayankhaso monga munthu, palibe choletsa ndiso cholakwika Kuti president wayankhapo. Musiyeni Mulungu akhale Mulungu, kunalembedwa Kuti tidzafa, nayeso Joshua tsiku la imfa yake ikubwera ndipo amene akudziwa nthawi ya imfa ya munthu ndi Mulungu Yekha

 9. he has right to react on behalf of his fell leaders,mukanasangalala akanayankha win a papa zalakwika, is he not one of african presidents? kķkkkķkkkk yes sanatchule dzina koma wayankha as president wa mu Africa hahahaha EAM mukumudzudzula as if inuyo nd i ma saint, fit I zokhakha, dyela, corruption, nkhaza zilo thooò then muli fwifwifwifwi a papa, rubbish

 10. Opani mulungo osat tb joshua ndindani ndikape ameneyo. Chifukwa chake a naphesa wantho mazana mazana awantho nanga bwanje sanalosele zangozi yanyumba yake lnagwa ndifit ameneyo

 11. He needs prayers.pple nid food,proper education,proper healthy facilities,saraly increament,graduates nid jobs,country nid to be developed,mr pres!u cant c these things?ask the spirit of ur brother,u want to follow ur brother?DONT SPEAK AGAINST THE PROPHETS!AM warning u my pres.u hv failed to run the government like ur Dead brother.if things r tough just give up!ur education is just bringing poverty in my mother land,NYASALAND,THE LATE Dr H K BANDA was the best.we went to school,we had food,he taught us to lv each other.u r a failer.

 12. ZACHAMBA PETER YOMWEYO ALI BHO OSATI INU KUNGOBISARIRA ZINA LA MULUNGU BASI OLO MUTAKHALA INU SIMUNGATHE KUTHESA MAVUTO AMALAWI

 13. yesu sanaloselopo za kufa kwamunthu olo sananene dziko kapena munthu , pa uzimu wamulungu wamoyo sungalole kulosela ifa ya munthu koma zikuphatikizidwa ndi mdima wamaso awona utumika kwa cholowa kuma wumitsa mtima mulungu amalekelela kuti achite natchuka koma tsiku lakuwatsitsi iwo sadzadziwa moyo sudzatha uli pamodzi ndimau ine ndikutiso munthu mndani avutika osapuma ifa idzatipumitsa tonse tingowopa tchito za moyo wathu kawa ipelekedwe kwa mulungu ,yehova osati milungu yo wukila nidzutsa aneneli adziko la ifa

  1. Khala chete sudziwa Bible iwe, Yesu analosera za imfa ya Simon Petulo pa Yohane 21 – 18-19

   Mbuli muuzimu iwe, mwana wa njoka

  1. Tazingomwani ma ARV anuwo musalimbane ndi munthu wamulungu, munakatenga nokha kachilombo iye kunalibeko

  2. Tazingomwani ma ARV anuwo musalimbane ndi munthu wamulungu, munakatenga nokha kachilombo iye kunalibeko.

 14. Guys tiyeni tiyeni tiwapephelele a President athu posayanganila kuluphela kwawo,timugonjese satana ndi ziwanda zake achina TB joswa ,Bushiri ndi ziwanda zina zambali,tikate muwona chozizwitsa chikuchitika phathupi pawo ,atha kusanduka chinjoka chifukwa maloto awo aku satanic sanagwile tchito,iwe zanga okonda ma profet usamale ma profet anali akale dziko lisanachimwisise palibe pano angayakhule ndimulungu pano awa ndianeneli onyenga amend analoseledwa zaka zambuyomu azitchula dzina la ambuye cholinga akupusiseni samalani

 15. President wanthu wawonetsa kupusa kwake konse, chifukwa TB Joshua sanatchure Malawi, anati maiko aku Southern Africa komwe kuli ma Presdent opitilira 10 iyeyo chomwe akubalarika mpaka kumawona ngati akunena iye ndi chani?

 16. TB Joshua iz Afool akumutuma amayi Jb ameneyo Ma prophet onyenga awa kumangolosela zoipa zokha zokha bwanj samalosela za Mvula inapha anthu ambilimbili ku Malawi kuno Chaka chatha? anaphesa anthu ambilimbili kwawo samalosela bwanj kuti anthu apulumuke?? Zopusa basi

 17. Malawi and Malewians,I greet you all in the name of God almighty, Please be courteous when you handle and comment on things of God, He the mighty God is highly incomprehensible to man and I believe you will all agree with me that he is more than any man or anything living or non living. God is so complex such that it is not easy to fight for him at times if you do you may be commended and at times you may be doomed. It is even more dangerous to touch an object of God, remember the ark and Uzar and remember Moses and Kora,Abram and Datam Remember Elisha and the 42 Children. God himself said, through one of his prophets that touch not my anointed and do my prophet no harm. I pray for Malawi, Nigeria my country and Africa in General to receive God’s Mercy and Favour with his mercy we will be the greatest in the world. God bless Malawi, God bless Nigeria and Africa in General. We should all remember that no one is bigger than God, No individual is Bigger than Malawi No individual is bigger than Nigeria or Africa no matter his position. Thank you all.

 18. Vuto ndiloti mayiko a m’dera la kumwera kuno kwa africa ndiwosauka kwambiri. Anthu ake ambiri ndia khristu okonda kupemphera . Ndiye masiku ano style ndiwekha, aneneriwa akupezerapo mwayi wakusawuka kwathu kumatiyenda business pomalosera za imfa, kumatipusitsa kuti tilemera . Anthu ambiri masiku ano akukonda chuma that’s why prophet yemwe angakambe zandalama anthu alikomweko. Osalosela ku middle East bwanji kuti wina afa kumeneko??? Mulungu amangokuwonetsera kuno basi??????

 19. Vuto ndiloti mayiko a m’dera la kumwera kuno kwa africa ndiwosauka kwambiri. Anthu ake ambiri ndia khristu okonda kupemphera . Ndiye masiku ano style ndiwekha, aneneriwa akupezerapo mwayi wakusawuka kwathu kumatiyenda business pomalosera za imfa, kumatipusitsa kuti tilemera . Anthu ambiri masiku ano akukonda chuma that’s why prophet yemwe angakambe zandalama anthu alikomweko. Osalosela ku middle East bwanji kuti wina afa kumeneko??? Mulungu amangokuwonetsera kuno basi??????

 20. Aneneri omangolosera za imfa basi……………sangalosereko za mtendere tsiku lina?……..komanso anakanika kulosera za tchalicthi chake chomwe chinapha anthu ambirimbiri chija….pls leave the president alone.

 21. Kodi ndi munthu wantundu wanji osalosera za chilala, koma zomwalira anthu. komanso ndimadabwa amangolosera za president zokha kodi ma minister samwalilra, iwe TB Joshua si iwe prophet ozozodwa ndi mulungu

 22. YOU ARE IDIOTS DONT PUT THE MAN OF GOD IN YOUR USELESS CHEAP POLITICS THAT IS WHY BUSHIRI LEFT YOU TO GO WHERE HE IS BEING APPRECIATED

 23. YOU ARE IDIOTS DONT PUT THE MAN OF GOD IN YOUR USELESS CHEAP POLITICS THAT IS WHY BUSHIRI LEFT YOU TO GO WHERE HE IS BEING APPRECIATED

 24. Uleme Upite Kwa ATATE, MWANA NDI MZIMU OYELA….Osati TB Joshwa ayi!!!. Chipulumutso mulinacho mnyumba mwanu momwemo…Ndilo Buku Lopatulika (Bible) stop praising TB Joshwa anthu inu…..GOD basi.

  1. We are in the same boat .brother currently prophets are those announced in the bible they are bayesu.

 25. Uleme Upite Kwa ATATE, MWANA NDI MZIMU OYELA….Osati TB Joshwa ayi!!!. Chipulumutso mulinacho mnyumba mwanu momwemo…Ndilo Buku Lopatulika (Bible) stop praising TB Joshwa anthu inu…..GOD basi.

 26. What do you know? What sort afterall a prophet is TB Joshua? Are you sure he not satanic and that he worked hand in hand with Joice Banda to kill Bingu? Nigeria is facing alot of problems from Boko haram. Why does not talk to God to intervain?

 27. What do you know? What sort afterall a prophet is TB Joshua? Are you sure he not satanic and that he worked hand in hand with Joice Banda to kill Bingu? Nigeria is facing alot of problems from Boko haram. Why does not talk to God to intervain?

 28. yobu 14 v 5 Popeza masiku ace alembedwa ciwerengero ca miyezi yace chikhala ndinu ndipo mwamulembera malire ake kuti asapitilirepo. palibe amene amadziwa za imfa ya munthu ndi Mulungu ekha basi osamamvera za munthu ayi naye masiku ake amawadziwa ndi Mulungu stop this

 29. yobu 14 v 5 Popeza masiku ace alembedwa ciwerengero ca miyezi yace chikhala ndinu ndipo mwamulembera malire ake kuti asapitilirepo. palibe amene amadziwa za imfa ya munthu ndi Mulungu ekha basi osamamvera za munthu ayi naye masiku ake amawadziwa ndi Mulungu stop this

  1. M’mozi wa aneneri onyenga ndiye TB Joswa amalosera za imfa ya munthu ngati Iye sazafa ngakhale Yesu sanaloselepo za imfa ya munthu, iyeyo kutani

 30. guyz wat I don’t understand is that.. when predicting Bingus death he mentioned the name….. y sanatchule dzna dis tym around….?? amazwa kut fanz imunena

 31. Vuto Amalawi Simukhulupirila Anthu A Mulungu Koma Asing’anga Enanu Ufiti Uli Thooo Zithumwa Mkati Apa Mukuyakhula Ngati Opemphela Koma Mchunomo Muli Zithumwa Mbweee!! Mbweee!! Satanic ili Thoooo! Simukhulupirila Mulungu Koma Asing’anga Tsiku Lanu Likubwela Nonse Muzakayakha

 32. Vuto Amalawi Simukhulupirila Anthu A Mulungu Koma Asing’anga Enanu Ufiti Uli Thooo Zithumwa Mkati Apa Mukuyakhula Ngati Opemphela Koma Mchunomo Muli Zithumwa Mbweee!! Mbweee!! Satanic ili Thoooo! Simukhulupirila Mulungu Koma Asing’anga Tsiku Lanu Likubwela Nonse Muzakayakha

 33. Peter should be concerned about the country s economy and how to save the pipo from this draught. busy busy throwing stones to every dog that backs.

 34. Peter should be concerned about the country s economy and how to save the pipo from this draught. busy busy throwing stones to every dog that backs.

 35. Inu Tb Joshua Sadatchule Munthu Hahahahaha Kaninso Pitala Munthalika Umaoneola Emanuel Tv Eti??? Kkkkkk Usazaonelenso Uzafa Ndi Mtima Amene Uja Ndi Munthu Wa Mulungu Sungafanane Naye Amene Uja Ufumu Wake Siwapansi Pano Ziwanso Ufa Ndinthu Kodi Ukuopa Imfa??? Nde Ngati Ukuopa Kufa Ingolapani Palibe Wamuyaya

 36. Siatumiki oonse ali ocokera kwa mulungu, mu njira ina ngakhale satana amazionesa ngati mngelo wakuunika.upulofeti wanji olosera maliro?

 37. how can you feel to be a Malawian and a DPP follower while your leader is calling your spiritual father a fake?? religous advisor walemphera ntchito

 38. Big mistake your doing to oppose the mans of God sir..First was prophet Bushiri now is TB Joshua..careful cos consenques may follow you

 39. Ine olo nditanyoza Josua Mulungu sangandilange chifukwa iye sinneneli chomwendimadziwaine, n’neneli amapanga dzizondikilo zimene anthu amupempha 1 komanso, n’neneli samapemphela mudzina lan’neneli nzake, nde chamba chimenecho Jesu, muzawona munthawiyo azachuluka aneneli onyenga ndipo azanenela mudzinalanga ndidzinalanga azakhala akuchosa ziwanda

 40. 2, kings 20 when king Hezekiah received a prophecy from Isaiah that ur dying that says God… He never argued with the prophet he simply prayed to God to forgive him and consider his good works. God heard Hezekiah prayer and he was given 15years more..Akunjenjemela sanakonzeke hahahaahahahha ife timaziwa zamulungu zinthuzi

 41. Florence, nawenso sumazitsata Joshua sanatchule dzina la munthu kapena dziko anthuni bwanji simkufuna kunena chilungamo mukuopa kufa bwanji!!!! Mmora nawenso ungokhala ngati sunapite ku school pali anything to blame apa you people are very funny shamefull

 42. Ukagenda mwala pagulu la agalu wina akati keeee ndiye kuti mwala walasa iyeyo. Joshua angoti one of southern Africa now wina wamveka mau kuti keeee otchedwa MUNTHA

 43. I wonder why people are blaming the actions of the President.do u forget that this is the same Joshua who prophecise the death of bing? And by then even bingu knew that Joshua is targeting him and now this… So we r blaming Peter like really? These Presidents in southern Africa they have a right to take him to court and explain to them but our presidents r even better than man of God

 44. sibwino kumutenga ngati TB joshua ndiwolungana musawuze ena inu simuzaweluzidwa.wolungama azadziwika mwini wake mulungu akazaweluza.mulungu sanapeleke mphavu kwa munthu kuti aziseweletsa miyoyo ya anthu ngati zingelengele kuti awa afa mawa.

 45. what you people don’t know is that Bingu was killed by satanic for not joining them and hé didn’t want any shit from them ,TB knew it because hé is illuminat ……..Now they want APM to join satanic if not hé will be killed too ……thats it believe me …….This is one of the reason why this country is on Economic crisis……..If hé would have joined,,you would have seen this country having its economic on track again……….infact hé did well …….TB is not à man of God but à SATANIC…..Yes you heard me right……à SATANIC

 46. Matthew 24:24
  For false christs and false prophets will
  arise and perform great signs and
  wonders, so as to lead astray, if possible,
  even the elect. Ma profeti akuba awa. Amafuna akalosela za imfa choncho munthu athamange ndichithumba cha ndalama . Peter wachita bwino kumuthira mphepo ameneyo. Likakhala boma la Cameron linasamba kale m’manja kwa yense amapita kwa TB kuti zawo zimenezo chifukwa zimachitika kumeneko siza chi god ayi. Kwa amene mumamutsatila pitilizani poti ulendowo ndi each each bfore God.

 47. Be aware with de false prophets coz we r living in de last dayz n dnt respect hm prophet wanj wolosela za imfa zama president ? Nanga bwanj osamupempherera kt asamwalire ? Nanga bwanj osalosera za infa za anthu 93 anafa pofuna machiritso ake ? Bas kudziwa kulosera za chisankho ? Nanga zimakhala ndi impact yanj kwa ife Akalosera zopanda chipulumutsozo TB J Z A FALSE PROPHET DONT RESPECT HIM

 48. To what i hv read i can say mr president has ovariacted bcz it says one of african president will die nt malawian president unless u r telling me dat its only malawi called africa then i can understand ur frustrations!

 49. Inu Tazikhulupirirani Zolembedwa M’Baibulo: Poyamba Mulungu Analankhula Kuzera Mwa Aneneri, Koma Tsopano Akulankhula Mwa Mwana Wake Yesu Khristu ( Ahebri1:1-4).

 50. this man is nonsense TB Joushua sanatchule muntu wina aliyese koma anati southern africa president yimodzi aduwa kapena gogoyuu wasandika president wa southern africa yonse akuwopa kumwalira bwapini koma ngati JB Joshua wanena zimakwanilisidwa wait peter dont be harry tikukwira watiwonongera dziko .

 51. I hope many Malawians went to school.Firstly,A PROPHET is a person called or appointed by GOD to speak on his behalf.PROPHECY,or ORACLE are GOD’S words spoken through a prophetic. at work any employee does his work in order to please his master(boss) just applies to the prophet,he does things to please God not mankind that is to say, he obeys what God has commanded him to do regardless of whether man will throw stones at him or take the message as a warning.Remember this, always an oracle always comes when God is not happy with how things are being conducted by his creatures(mankind).IF you want God to please you please him first and u will see wht follows(joy) .MAY THE BIBLE BE YOUR EVERY DAY BREAD IN JESUS NAME Bettie Nyirongo Khwima Jughashvilli Mafeni Soko Temwanani Alaba Msowoya Paul Chizanda Stephano Chobwe Kanyinji Chrispin Petani Chancy Nyirenda Kaunga Jdams Msutu Kampango Eliud Ndhlovu Phallyce Kamwendo Happy L. Qoto Noxy Nyika Kapatamoyo Emmanuel Thnd Manzy Brian AB Kar Hia

 52. Ntengo ukamauma amayamba ndi masamba kuwuma#Tb Josh sanatchule munthu or dziko noo if you go pa net mumva zomwe analosela ena amati mwina ndi mugabe poti wakula. But why our APM. Kufulumila ku yankha ngati big nan samayenela kuyankha coz TB Josh anati one of president not Malawi president No…… But wayankha mwina akuzikai kila komaso sii boo kunyoza atumiki a mulungu ndi tsoka lalikulu ngati ali onyenga zawo but we need to respect them or kukhala chete ngati simuku wa khulupilila…… Koma my president wayambila pa bushili ayi aku gawa chakudya ngati. Ndani amutuma mai JB hahaha lelo ali pa TB Josh??? Something is long for sure

  1. Zoonadi #Martin TB Joshua sadatchule munthu kapena dziko. Komanso sadapange prophecie imfa iliyonse. Vuto liri ndi ma advaiser apresident, amamunamiza mmalo monena choonadi. Ambuye atithandize ndithu.

  2. zovuta kwambiri sanaone source yakhani internet imasokoneza ukukakhala leader umangova zinazilose wina anangopeka basi iye walakhura molakwika

  3. sibwino kumutenga ngati TB joshua ndiwolungana musawuze ena inu simuzaweluzidwa.wolungama azadziwika mwini wake mulungu akazaweluza.mulungu sanapeleke mphavu kwa munthu kuti aziseweletsa miyoyo ya anthu ngati zingelengele kuti awa afa mawa.

  4. Mr Peter P thanks…. Pena timalemba mofulumila coz of kukhumudwa ku why nkhani za zii big man mpaka kumatulusa mkwiyo…. But. Thanks…… God bless Malawi and for giving us.

  5. sanalosere coz mulungu sanamuuze… much as he says he’s God’s prophet, it means wat he prophecy comes frm his God.

  6. Ine ndilibe chilichonse cho tsutsa kaya kuvomeleza Kut TB JOSH ndindani no koma ndingoti mulungu ndamene a ku ziwa kuti TB Josh ndindani…… Ngati mukumuweluza mukulakwa kuweluza mkwa mwini mulungu. Ndichifukwa chake or. Thawi yamose Lazalo anali okhulupilila mulungu koma anthu akamu wuzakuti atukwanr mulungu coz akuvutika but. Azalo anakana. So inu ndi ine tisachedwe ndi kuweluza atumiki amulungu no. Kaya ndiowona kaya ayi mwai or tsoka lawo have good day

  7. Brother. Inu kukhala nsilikali sikuti akuba sanga kubeleni no or inu kukhala dokotala sikuti anthu samadwala ku family kwanu no mulungu ama lola zina kut zichitike mwa kufuna kwake

  8. Koma mau a mulungu akuti mulungu salanga munthu asana mu dzudzule ku losela za imfa ndimulungu ameneyo ku chenjeza kuti be 4tsiku la imfalo alapekaye koma sanati Malawi. President no one of African president. Anatelo

  9. a Saukila if u check mbaibulo aneneli ambiri mwinanso onse adafa infa zozunza my question to you is,,,this..ngat iwo adali aneneli bwanji sadanenere za infa zawozo nkuzipewa?!being mneneri sikut chilichonse chokhudza moyo wako ungadziwe no!! i consider John the baptist as one of the great prophets ever leaved he made the most powerful thing pozindkira kut uyu akubwera apayu ndi mwana wamulungu olonjezedwa uja,,,bt check how he died bwanji sadanenere kut aphedwa mmene adaphedwera muja?! being a doctor doesnt mean sungadwale and sungafe

  10. Big up thengolose sikuti to be a man of God ndekuti akuziwazonse ngati iwo ndi mulungu no but pazochepa zomwe mulungu wa awonesela akuyenela kunena kut ochenjela alape

  11. Big up thengolose sikuti to be a man of God ndekuti akuziwazonse ngati iwo ndi mulungu no but pazochepa zomwe mulungu wa awonesela akuyenela kunena kut ochenjela alape

  12. zoonadi he is human being like us its only by grace of god he was chosen as vessel to preach the word of god ndiye sizidakatheka kuti anene kwa anthu athawe komaso sitifano anaphedwaso imfa yovuta ndiye the will of god was done kuti nyumba yake igwe!!

  13. zoonadi he is human being like us its only by grace of god he was chosen as vessel to preach the word of god ndiye sizidakatheka kuti anene kwa anthu athawe komaso sitifano anaphedwaso imfa yovuta ndiye the will of god was done kuti nyumba yake igwe!!

  14. Yaa or nthawi yanowa aneneli analipo ambili but mulungu ana uza nowa aseme chombo aneneli ena sana uzidwe palibe anga mupangule mulungu zo chita but mulungu amatipangila ife but. Tsoka kwa amene aumitsa khosi lake atadzudzulidwa mau akutelo

  15. Yaa or nthawi yanowa aneneli analipo ambili but mulungu ana uza nowa aseme chombo aneneli ena sana uzidwe palibe anga mupangule mulungu zo chita but mulungu amatipangila ife but. Tsoka kwa amene aumitsa khosi lake atadzudzulidwa mau akutelo

  16. Kodi muprophet ameneyu amangolandira ulosi waimfa yokha? Ngati ali muprophet weni weni bwanji asaloseka chaka chomwe mankhwala a Edzi adzapezeke?

 53. Vuto la anthufe timakhala ngat tili ndi maso koma sitimaona………ndipo timaoneka ngati tili ndi makutu onvera koma sitimanva coz nkhaniyi yafotokozedwa monveka apa akuti………..president wa mu sourthen africa amwalira …..ndiye takhalani mwa kamphindi ndikuganizira kuti kodi mu sourthen africa muli ma president angat???….kapena ndiye yekha peter???……..please dn’t rush to comment b4 u understand………..u shud learn hw to understand…..

 54. koma anthuenainu mumandi dabwisakobasi kodi zimakhala ziwandaa chani mmakhulupilira t b joshowa zimene amalankhula simungamazifuse nokha penapake kuti ndichifukwachake ndichian sana loseleku charch changachi chizagwa sikulirilonse tikhale miyezi ingapo tisanape phere komabe inu kakaka kumukhulupira ngatitu simukuziwa munthuyi ndiwa satanic ngati mukufuna zammbili ndipezeni ku wats app ma vidios ake ndilinawo mwana muzasiya kakakayo

  1. Mbuzi iwe Tb Joshua sanatinyozere president wanthu wamva, anati mmodzi mwa ma president aku Southern Africa komwe kuli mayiko opitilira 10 iye chomwe akuyakhira ndi chani ngati anamutchura kuti amfa?

 55. TB Joshua is stupid, fond of prophecizing bad things. Why he failed to forsee the fate of his house wich killed people. Shame on u EAM for supporting TB to make his false prophecies up to date. No matter he didnt metion anyone but its bad to forsee the death of someone and publicise it. U EAM KNOW GOD DOENT TAKE AWAY ASOUL( 2sam 14:14) the power to 4 c the death and to take away a soul is from a certain bad source DEVIL where is he getting the power to prophecize bad things 4 africa

 56. koma anthuenainu mumandi dabwisakobasi kodi zimakhala ziwandaa chani mmakhulupilira t b joshowa zimene amalankhula simungamazifuse nokha penapake kuti ndichifukwachake ndichian sana loseleku charch changachi chizagwa sikulirilonse tikhale miyezi ingapo tisanape phere komabe inu kakaka kumukhulupira ngatitu simukuziwa munthuyi ndiwa satanic ngati mukufuna zammbili ndipezeni ku wats app ma vidios ake ndilinawo mwana muzasiya kakakayo

 57. Kodi maprofetiwa amangolosela za anthu a ndale (maPresident) basi? Masoka okhawokha? Nthawi yakampeni ija Presidential candidate anali ndi a Profeti ake ake pano ali kuti? Ndi maprofeti afegi a Peter sakunama

 58. Fuseck you EAM,so you also behind TB? Why you didnt condemn when he always talks shit abt our president? What evidence do you want to see kuti TB is an Illuminati member? This man is a devil himself he must stop talking shit about Malawi,leave Mutharika’s family alone!!

 59. How was his burst divisive to us Malawians? I guess these religious leaders are not ok in their minds. He is saying political leaders should not comment on religious issues coz they are sensitive. How dare they comment on political issues. Are they biblically allowed to do that?

 60. Amene akuti prophet tb joshua ali nonsense renew ur mind osayitana matembelero pa nthupi lako bcz tb joshua sanathule munthu so why ur tolking to much..ask forgiveness ngati uli mugulu lo nyodza tb joshua and adzitumiki ena muno mu dziko ndi madziko ena

  1. man can u tel me if tb profecy good tins to malawi canu tel wat profet owez profecy only death only bad luck to pipo was profet eriya profecy jst lyk our profets doing nowadays or mayb their prophecie is part of gettin money from pido so am nat gud for english but i hope u go get me wat am i trying to say

  2. Iwe jus repent……bible sayz dnt tach my anointed ones…..palibeso discusionz……jus repent……again repent….en b a born again……u nid God’s mercy…..

  3. sibwino kumutenga ngati TB joshua ndiwolungana musawuze ena inu simuzaweluzidwa.wolungama azadziwika mwini wake mulungu akazaweluza.mulungu sanapeleke mphavu kwa munthu kuti aziseweletsa miyoyo ya anthu ngati zingelengele kuti awa afa mawa.

  4. Kodi amuna abwino bwino ngati inu , okhala ndi three common sense musokonekela naye TB akamapanga tima miracle take tachinyengo tija??? Ine ndimakhulupira Mulungu mu dzina La Yesu osati prophet. Paja anati kudzabwera aneneri ochita zozwizwitsa mpaka kuwukitsa anthu kwa akufa, koma anati tisadzatengeke ayi .

 61. EAM are condeming Mutharika for what?that is nosense you have no right to condenm him yours is just abody of your church and he, he stand for what he believe in,Big up Mutharika stand up for what you believe in like Daniel, Misheck,Shadreck and Abdinegor jahova will be on your side dont fear the said prophet he is athief abastard,he thought you are going to be afraid of him never and never reversa your words in our time we have no prophets but thieves who are getting rich in the name of God

 62. Inunso a Evangeri kodi peter alibe ufulu woyankha ngati wina akumunenera zoyipa? Bwinotu musakhale inu okwaniritsa malemba. Ndinu asaduki ndi afalisi eti.

 63. I think people need more education on their understanding.A person is born and he awaits to die.This is a fact but it becomes so anoying to be told kuti ufa munthu.Achimwene anafera ku state hse shoul be your good teacher Peter, life is temporaly on us and we can not resist to keep it when God says yes am takin it. kufa ndi nkhani? ndinabadwa ndakhala mdziko ndanjoya and I expect death.President wadziko ukaope kufa hahaha.Izitu ndizimene munabadwa APM muzafa muli Bizwik Phiri.u dont want to accept reality.

 64. Is your marriage on the verge of breaking did u loose a loved one and you want them back.this is ur chance to get Wat you’ve been praying for.contact Maama Shaiza the best female spiritualist from Tanzania.CALL:+27745041566

 65. Is your marriage on the verge of breaking did u loose a loved one and you want them back.this is ur chance to get Wat you’ve been praying for.contact Maama Shaiza the best female spiritualist from Tanzania.CALL:+27745041566

 66. Is your marriage on the verge of breaking did u loose a loved one and you want them back.this is ur chance to get Wat you’ve been praying for.contact Maama Shaiza the best female spiritualist from Tanzania.CALL:+27745041566

 67. God speaks thru prophets. God himself has power to give or to take life. Word of God will be fulfilled upon one. Whether we like it or not

  1. Kunena Kuti Sizichitika Sikutumbwa Inu Mwamva? Mmafuna Azilira? Inenso Ndikugwirizana Naye Kuti Palibe Chitachitike Mdzina La Ambuye Wathu Yesu Khristu!

 68. Why can’t the so called prophet prophesise about Boko Halaam which is killing his cousins ,sisters,brothers,friends, inlaws and followers at his home. Leave us alone . The so called prophet is not a Malawian. I support Mr President he has also freedom to about his life.

 69. No one would be happy with any prophecy about one’s death be it clergy or otherwise.Issues of ethics as a moral imperative comes to mind now.

 70. Anthu awa ndi amodzi akudziwana zawo ndi zimodzi awa, you can say that tb Joshua is a prophet of God but the truth is u know nothing about his private life!

  1. Philip akukamba zoona. Mukanakhala ndi nthawi yomawonera TV bwenzi mukumva zomwe akulu akulu aboma akukambirana zama prophet a business wa. akufuna ayambe kuwalipitsi chi nsonkho chokwera kwambiri chifukwa zomwe amachita ndikuba.

  2. Masiku ano kulibe prophet woona ayi! onse from west east south and North, okuba okha okha. Mawukaliki anu amangokaba zandalama m’malo mowawuza anthu kuti akomze mitima kuti akalowe mu ufumu wa Mulungu.

  3. Man musaone ngati ifeso ku SA sitinakhareko ife tabadwira koko kukurilaso koko, ngati umazisata Tb Joshua adamchura zina ndani? osati kuwalemekeza peter ndindani joshua ndindani bushiri ndindani all ndi human bng iweso ndindani ineso ndindani? ndife akaporo chabe pazikorino man usamanyoze amalawi mayi ako alikuno bambo ako aliso kuno stupid ur self and ur family nyani wachabechabe mbolo yako garu opanda machende kape iwe unachita kuthawa kuno lero uziti nyokonyoko apa mbuzi.

 71. Bwanji samalosera nyumba yake inapha athu 90,kulosera imfa sinavepo,azaukasom mr ayi,ndasiya kukhulupilira athu opephera,amati oyimba amapasa amwalira,amakamuuza kuti ufe ndiwe kuli chete sakufa joshua alumuziwa ndi mulungu zitchito zake,koma waleke zopha athu ndimau ake kuzera mzina lamulungu

 72. fighting men and women of God is like fighting God him self , people must think before we speak or comment anything against them .it is not wise for a leader who represent Malawi as a nation to speak in that manner

 73. No body wants to die, if it was yu ( EAM), munakamva bwanji? Or if this prophessy inali pa ma families anu, inu mumvekere chimwemwe m’saya. Peter is like any of us the same as TB Joshua. We are all human beings not happy when one dies. THINK B4 critising someone. Why not blame TB Joshua. Only God takes someones life. Am not a fun of Muntharika but it is wrong .

 74. Iye TB Joshua’yo bwanji sakumalosera anthu a kwao akamapangidwa kidnap ndi Boko Haram? I see nothing wrong on what our President said…Inu mmati azisekerera nkhani ngati zimenezo? Infact akanakhala wina akanalalata kuposa pamene paja…Kodi TB Joshua’yu, ndi prophet of doom iyeyo? Atiuza liti za kubweranso kwa Yesu? Mxm…

 75. pipo live on facts instead of blindly following someone else’s facts, matter how angry pipo get it won’t change his mind

 76. Ngati sumapephela zoona ngati sumawelenga Bible nde uvomele zomwe wanena TB josou why akumalimbana ndi ma President amalawi okha anthu onse samachimwa. TB josou stay away from Malawi ulimbane ndi mavuto amene Ali ku Nigeria .

 77. kodi bwanj #TBJOSUA amangolosera zoyipa zokhazokha?,thats why my self i dont bliv in this man.osaloselako kut 2020 malawi idzatukuka ngat john?,izi zikusonyezelatu kut josua amapanga zinthu zaufiti ndimuneneli wapasi panyanja ameneyu.

 78. May the Almighty rescue us soon. This evil man is causing lots of problems among us

 79. Has the right to speak wrong or good inuyo muli 100% right before God. Muli mgulu limodzi lofuna kupha president. Mp wamwalira uja musakapanga prophesize bwanji?

 80. Mmmmmm guyz zina kambu zina leku kodi joshua uneneli wake ndi waku africa konkhakuno ndizophweteka dont blame peter even anakapanga prophecise kuti inuyo mumwalira bwezi mukuyakhula

 81. Mmmmmm guyz zina kambu zina leku kodi joshua uneneli wake ndi waku africa konkhakuno ndizophweteka dont blame peter even anakapanga prophecise kuti inuyo mumwalira bwezi mukuyakhula

 82. Has the right to speak wrong or good inuyo muli 100% right before God. Muli mgulu limodzi lofuna kupha president. Mp wamwalira uja musakapanga prophesize bwanji?

 83. I Choose To Disagree With EAM’ Pastor Mkandawire: Following The Bible Prophecy, God Sent Prophets To The Concerned Person Directly To Deliver His Message eg. Isaiah To King Hezekiah. Isaiah Did Not Stand On The Pulpit And Deliver The Message But Went To The King. Why Did He Do That? These Prophets Must Follow The Same Method. By The Way, How Can The President’s Response Divide Malawians? Tell Us. Mind You! This Concerns The Life Of A Human Being. Between Joshua And President Mutharika, On Your Opinion, Who Is Bringing In Division? Can’t You See That This Unprophetic Approtch Has Confused Alot Of Malawians?

 84. Ma prezident aku africa aphweka. Talosera ifa ya Obama tione. Mwina enanu simukuziwa. Samalosera ifa koma amapha mumasenga inu muziti zakwanilisidwa. Ndli ndi ma umboni okwanila. Hit ma inbox

  1. Be serious chaniso???? Ndkunena chomwe ndkuziwa. Amapha mumasenga. Kodi ngati ndizowona unavapo akulosera ifa maiko otukuka ngati south africa or even maiko a ku europe? Amaona ophweka…easy to kill

  2. Haha ndie ukuzitsutsa2 cz ts easy to kil a European in matsenga than an African.. Cz ku africa ndi komwe kuli matsengawo, African leader cn b well protected than Europe leaders cz ey dnt kno anything abt matsenga

 85. A EAM osavutka ndianthu opanda uzimuwa mapeto ake akugwesan mu uchimo,anthu akumidima amaziwika ndi ntchito zawo.anthu akufa ndinjala apresident ali problem

 86. Our Malawian leader has run out of senses, he now bucks on everything whether for his concern or not. Let’s just hold hands as bonafide citizens of this land and ask for God’s guidance

  1. @vitan chirwa which sense are u talking about?As long as he z a humanbeing nothing z wrong.as for me i dont praise fake prophets!only jesus is king

 87. MR PRESIDENT please humble yourself and apologize the worst is to befall upon yo itsa mistake to attack men of GOD most of us have respect for TB JOSHUA stop that adamance if I was you it would have been better to repent before death rather than die an idiot or a fool!

 88. Sometimes it’s good indeed not to overeact on religious issues. Lets keep on praying for our political leaders. Ine zikungondikhuza kuti our leader is just reacting to any issue. As a leader must portray leadership skills.

 89. munthu akakhala pafupi kufa amagontha mkhutu, amabwebweta, amatukwana, amalalata. oooohh! very sorry RIP

Comments are closed.