Two women have been arrested after they were caught stealing beer from a Chipiku shop in Lilongwe.
According to a source, the women have been stealing items from the shop on several occasions but they have been getting away with it.
However, when the two entered the retail shop on Monday, workers recognised them and used the facility’s CCTV to monitor their movements.
The women packed some beers and wine in their handbags and at the till they only paid for some small items. After they had paid, they confidently stepped out of the shop and started walking towards their car but a security officer for the shop pounced on them.
Chipiku workers then recovered the stolen items and the women were detained at the shop where management ordered them to pay K700,000.
kodi Leman Nthala panopa ali kt
in malawi why people are stealing
inenso ndimaba mowa koma kawalala ndi amene wagwidwa
inenso ndimaba mowa koma kawalala ndi amene wagwidwa
Models in two finger business tumbiyang’ambe utu
Models in two finger business tumbiyang’ambe utu
Mukudandaura zowawazo imeneyo sinkhani,,ema akubachuma chadzikolathu komankhani mukungokhalira why this one..zankutu zikaphweka zibedwe basi..
Mukudandaura zowawazo imeneyo sinkhani,,ema akubachuma chadzikolathu komankhani mukungokhalira why this one..zankutu zikaphweka zibedwe basi..
shame on you
shame on you
akadyesele amuna awo ku nyumba njala pa malawi
akadyesele amuna awo ku nyumba njala pa malawi
it happens gals next time be careful chilembwe wavuta heavy
it happens gals next time be careful chilembwe wavuta heavy
it happens gals next time be careful chilembwe wavuta heavy
http://YouthToEarn.com/?ref=223152
http://YouthToEarn.com/?ref=223152
http://YouthToEarn.com/?ref=223152
Following with interest
Following with interest
Following with interest
Wakuba ndi wakuba zimai zibambo ngokuba bas fullstop
Wakuba ndi wakuba zimai zibambo ngokuba bas fullstop
Wakuba ndi wakuba zimai zibambo ngokuba bas fullstop
AMalawife kodi tinakhala bwanji? Kukokomeza nkhani ing’onong’oyi chonse okuba ma mk577bn ndi enao tangoti nao ziii. Paja m’mafuna ma donor communities ndiwo aziti sokolera nkhani eti!

Its not them but the devil @ work.
Its not them but the devil @ work.
Today one cought led at same chipiku for failed att empt of stealing a vehicle
Today one cought led at same chipiku for failed att empt of stealing a vehicle
give those ladies a bells
give those ladies a bells
SHAME!!!
SHAME!!!
Nde mwati winayo ndi wamu ghetto mwathu oh anthu asafanane povala magalasi kikkkkkkk ife timaba bwanji simutigwira?

Anayamba kale LA 40 langokwana kkkkkkkkkkk ma model opusa
Anayamba kale LA 40 langokwana kkkkkkkkkkk ma model opusa
Anayamba kale LA 40 langokwana kkkkkkkkkkk ma model opusa
kkkkkk akongolerenji azimayi… shame.
kkkkkk akongolerenji azimayi… shame.
kkkkkk akongolerenji azimayi… shame.
Shame on them
chati mbeee hachinaphye! mukungoona magalasi mwati mamodels!akang`wing`wi okuba atavula awa!amagulisa nyini ndiye pano amuna sakugulanso akumagura ufa osati matako
Nima shop lifters ameneo
Angofuna kupanga mbiri
mmmh… zamanyazi
hahaha dzimahule dzimenedzo atopa ndikuwabela amuna mabala ayamba kuma kuchipiku mbuzi zazimayi
Nanuso azimai mulemekeze osaba ufua mukadye ndi ana mukuba mowa Malawi ikupita kuti chocho mungasogolele ziko ngati mukuba mowa ndalama mungaisiye inu
Not serious
mmalo moba thamba la ufa….mowa wachan. ..mahule
Muli bhoo
Muli bhoo
What type of journalism is this? I thought people are supposed to know who these people are, where do they come from and by the the guy what do they do for a living? People want to read stories which are well investigated. Ok
Mukuwalipira?
zogumuka izi
ma model ake nde panjanso bwanji…shit!
no comment
Pano ndinafatsa ndikanalalata ok ndimalize kaye izi!
That’s totally ridiculous gorgeous ladies like u why u despise yourself? Selfishness?ignorant?sham on u.
Timadziwa awa ndi mahule a mu area 49, kunamizila banja mukumaba mmashop manyazi bwanji a bethi mwachititsa manyazi mwamuna wanu……
Chikomekome cha Mkuyu mukati muli nyerere. Ine sindikumvesa kuti azimayi achsonzera kokongola chonch kuba mabotolo amowa. Very shame and frustrating. Chondidabwitsa kwambiri nchakuti kuba mowa kaya tima litres tingati, chonsecho anabwera a njale. Mafunso kuchokela kwa Lawyer wamkulu:- Kodi mafuta agalimoto anagula kapena anabanso? Galimoto limene linali lawo kapena anabanso? Lomaliza, kodi mtengo wamowa anabawo umaposa mtengo wamafuta agalimoto lawo?? Iiiii! takazipenyeni kundende zima BAD MODELS
Hahahaha eh
Hiiiii
kkkk beargate acity nao bas
Pa Malawi di mbava zavuta ,malo moti mube ndalama muba mowa. Musanditseketse kkkkkkk yrrrrrree!
Idiots
So you say the management ordered them to pay K700 000? For alcohol packed in the hand bag or maybe its human body parts??
These are models?…. Koma ku malawinso guys….
Sizachilendo,kunonso ku salima zinachitikapo mkazi wabwana kuba colgate,koma 50 ooo ili nthumba.
Ndiye mwati waba mowa mpaka kuchitolokosi shame malawi….oba ma bilion ndi ma free
mmmh no comment kikikiki mudziona atsikana
Kkkkk zanzi.
Kkkkkkkk akaznso kuba
Ndi deal
Aba mowa wandalama zingati? ndiwa lipilile
ziphadzuwa
kupepela.
Mahule awo 12 yrs
Kkkkkkkkkkk, ndi njalazi ndani angagule maminawa. Chifukwa chosagudwa anangoganiza zokaba mowao
Kikikikikiki ma broke diva’s lol
Kungoti maludzi achuluka pa tauni
hahaha koma adha si inayache imenei kkk
Akazi monga amenewo komanso ena kuposera apo amovomera kwa magarden boy kutheba nde muziti mamodel kkkkk
koma ndiye malawi wavutadi uyu, mpaka ma model kuba? shaaaaa! economic silibwino pa Malawi
Mwayi Sinoya onakoo
Bola iwo
Sanabe inu koma amatenga
Mmm zopanda umboni zimenezo! Mowa umene anabawo ulikuti? Kungofuna kuipitsirana mbiri basi!
Wambali zaukoyo akukhala ngat xulmate wanga..
kuba ndi thupi kenako mukukabanso mu shop
kuba ndi thupi kenako mukukabanso mu shop
Kkkkkk yah mamodel a fake
Kkkkkk yah mamodel a fake
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ok
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ok
Abale kubako akabe mtonjani? Bwanji osamakagulitsa uko kumabalako.
Abale kubako akabe mtonjani? Bwanji osamakagulitsa uko kumabalako.
I think its because of this hunger here in Malawi.
I think its because of this hunger here in Malawi.
Oh NO. BEER? Shame !!!!!
Oh NO. BEER? Shame !!!!!
mukuti ma model mmmm gold digs
mukuti ma model mmmm gold digs
Hahahahahaha mahule yawaaaaa.
Hahahahahaha mahule yawaaaaa.
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS..

Kkkkkk,baasi ine ndizingowelenga ma comment wo,
Kkkkkk,baasi ine ndizingowelenga ma comment wo,
Mukamati mpaka kuba mowa ….inu mmafuna abe chani? Chomwe dzina lake silikhala kuba ….
Mukamati mpaka kuba mowa ….inu mmafuna abe chani? Chomwe dzina lake silikhala kuba ….
Next time try to steal Juice
Next time try to steal Juice
Chocho ndiy tisamakwatilane tokhatokha loi
Chocho ndiy tisamakwatilane tokhatokha loi
Tingowakwera basi zinthe alikuti?
Tingowakwera basi zinthe alikuti?
Nyasaland wavunda uyu
Kkkk ZInazi zosangalasa kwabasi hahahaha
Kkkk ZInazi zosangalasa kwabasi hahahaha
Kugoti njala ya mowa ndiyo vuta hvy!!!!
Kugoti njala ya mowa ndiyo vuta hvy!!!!
Bail them out
Bail them out
Mmene Akuwonekela Azimaiwa Nkumaba? Kusonyeza Kusowa Ndalama Kapena Nchikhalidwe Chao? Ngat Nchocho Guyz Chabwino Palibe Pa Malawi
Mahule akuno ku Johns ndi ama Land,Osati okuba mowawo..
Iwenso Tazingogwila Ukaidiwo Kumeneko! Kuzolowela Kugona Gulu Mu Mkuku Eti! Osamatinyasa Ndi Theba Yakoyo!

kakakakakakaka koma amenei osekesa bwanji ukuona ngati kukhala Ku jonz ndi udolo? tazingo tchetchani kumeneko mkusamala agaluo

Mbava kutengela Mai angathawa aja kkkkk
Am willing to bail them out if any one who knows them please inbox me
Kkkkkk,ukuseka anzako kuti adzipita ku xul pamene iweso wapalaso,(siliphera mistake)ndekuti chani?
Kkkkk he!hedeee zafika pena mpaka kuba mowa mmmm bola mkanaba ufa kwathu.
Ma Model samaledzera izi ndi zitsiru mahule amu Lilongwe awa.Koditu pamalawi pali anthu ongoziyerekezera kuphunzira ambiri.Ena uphunzitsi womwewu mpaka kumaima nawo pachulu, apolisi mutha kuwanyenga no problem muwaone mkati mwaomo ngatidi muli mwa MODEL.
iwe ndiye ophunzira nkhani yake iti yoti ukanyozere ntchito zanthu ena ukamamva uchitsiru ndiumenewo kuganiza ngati mbuzi nosense!
You’ve gone out of bounds in your commenting Bro. You’re able to read and write today because some teachers did a great job on you. Why should you tear them down now?
You’ve gone out of bounds in your commenting Bro. You’re able to read and write today because some teachers did a great job on you. Why should you tear them down now?
The educated savage
The educated savage
eh eh pupa easy easy pupa
eh eh pupa easy easy pupa
eh eh pupa easy easy pupa
wanena wanena bac
wanena wanena bac
Ha ha ha ha! Anawatuma satana awakhululukile
Mahule awa panonso anatuluka ali ku mogasa.
Inavuta ndi timing, bt d fact remains…mowa timaba, y shud we buy…try to be more careful nxt tym, ladies!
mowa ndiye wofunika kubawo, timing basi lero kujudula mawa kugulako ,kenako kukalowako mu peoples.
Zaziii
Aka save basi
Nkhani iyi ndiya last wk lachinayi mukuchedwa nazo kkkkkk
osakaba thumba la ufa?? ndinu zidakwa eeeh
Steal steal steal they can even steal from their husband mmmmmh shame on u
mavuto simaliro okha ndithu..
mavuto simaliro okha ndithu..
Uhule sunayende ndiye anaona kuti pa line asapite ndi jumbo aoneka kuchipa kkkkkk
mwat mowa? Wandalama zingat?
kuba kulibe kuti uyu ndioneka chonchi uyu chonchi kuba ndikuba basi magulu awa ndiofuna kuoneka kuti ndionjoya koma nthawi yawo isanakwane za zii tazionereni za shit basi osakabadi ma bible bwanji ku claim mabukuko muzilange musanyengelele mwina kulandilako yesu ku ndendeko
Koma ndiye oba moyawo,anatani anakapita ku capital kumakanyengelera ma bwasala kuti aziwapasa mtereshede…bcoz tikanena za cash gate ndikonxo ku ministry kumeneko,koma mpaka mowa ayi mwina akuwanamizira olembayu
Bola mukanaba Maize flour koma Alcoho, amenewa ndi Mahu…
Mmmh nkhani yapita mphepo iyi….tinaidziwa kale kkkkkk
Shameeeee:h!
A Malawi masiku ano manyado mpakana kuba mowa, masiku omalizadi. Where is those respected Malawian ladies. Zokopera maiko akunja zaononga Malawi.
Ukunena zowona #Prisca
Ukunena zowona #Prisca
Psg 2-1 Chelsea
Kkkkk
kkk akongolelenji akaziwa mpaka kuba mowa zamanyaz
Adim uyu amakhala mwa mgona nde angalembe English yomveka manyaka enieni
Ziwanda azimawi owoneka ngati aulemu wawo ngati awa
Ndiye Malawi24 iweyo wachitapo chani pamenepa?
Malawi has very high maternal mortality rates and high unwanted pregnancy rates. This is because many people lack maternal and reproductive health information. Walter Moyo and colleagues developed “Maternitech”, a mobile phone app that: 1) provides complete info on contraceptives (what they are, how they work, side effects etc); 2) provides complete info on pregnancy issues during all the nine months 3) predicts delivery date of pregnant women, enabling them to prepare for delivery. Our app is now in the semifinals of the TNM app challenge. Please vote for our app to win this challenge and to allow our women to have safe pregnancies. Vote by sending an SMS written: SS4 to the number: 575. Voting is FREE of charge, doesn’t use any airtime (although it may warn you of charges). Those without TNM numbers can vote online at: http://smartchallenge.tnm.co.mw/index.php Then select “smart student category” then vote for “Walter Moyo Maternitech”. On SMS you can vote as much as you want per day. Whether 5, 10, 20 or even 100 times. Vote for this app and help women have access to important information right on their phones!
where and how can the app be accessed? what is it’s current success rate? What platform does it work on?
Chipuku ndechani u dont know what proofreading z,shame on u
They say Malawi divas
A Malawiwa wapa joni angabe mowa Mahule anu awa
Kkkkkk malawi 24 wawonekera poyera uchitsiru wako bodza 2 much kkk chipuku
Addiction or what? mpaka kuba mowa
Afufuzeni bwino ndi akumalawidi? Kapena akujoni?
Kkkk chipuku store koma malawi 24 u must go 2 xul every story siliphera mistake
700,000 nkhani yake iti.. Nde bola kupita Ku cell Tu.
read the full story . not the first time
Basi seeking attention! Atchuka basi. Whose next?
Zaziiiiiiiiiiii
Mmmmmm bt y?shame on u ladies.
This story happen @L/city last Wk-end n’publish 2day where were U? Nt Chipuku is CHIPIKU STORES,im sry 4u journalists evry story ubring prblms n’some propaganda’s,Eeeeeeish!
Why cant u kst quit de group? Ngati amakubalalitsa zako,ife timakhutira nayo
nanu ndemumakhutila zilizose,mpaka kukhutila chipuku kkkkkkk!
Kaya2 #MALISEN tafuseni Zonyadira zake Bodzalo ndi ma Wrong spellings nthawi zonse
ife taiwerenga kale mukuibweretsa lero….nawenso ukukhutira nayo mw 24 yabodzayi
#FANNY i’ve already said imy Comment dat this Repetetion,bt pple dnt understand,tasiyeni awa!
Amafuna alezere asiyeni.
Why Not Steal Sanitary Pads… Coz There More Important Than Alcohol 🙂
Chindapusa cha 700000 eesh agwanayo baxi
wat is chipuku?
Unprecedented, shame on these two angels!
mahule opanda cash.
Akongolelenji simungakabe bible ku cleim bookshop koma mowa?kkkkk musovenge
uhule opanda ndalama ndi choncho
Give them long sentence