

At a time when dust is refusing to settle within the Malawi’s opposition party, United Democratic Front (UDF) over who should discharge core duties, the party’s national executive committee (NEC) has obtained an injunction against suspended Vice President Iqbar Omar and two others officials.
The injunction aims at restraining Omar and the other two – Zaituna Yusuf who was expelled while serving as deputy director of women and Dinocius Magombo – from conducting meetings or any other activities using the party’s symbol, slogan or colours.
The injunction was granted by Judge Lloyd Muhara on Monday.
According to UDF’s Publicist, Ken Ndanga, the injunction was obtained after Omar was found conducting activities using party colours even though he is suspended.
Recently, Omar dragged party president Atupele Muluzi to court saying the UDF president should prove claims that the embattled vice president was forming parallel structures and that he once sent thugs to attack Muluzi at his residence.
Pakuganiza kwanga chipani chabwino chikhale motere munthu kapena bale asakhale kuti anayendesapo boma
chipani chathu chimenechi wina alila atupele woyeeeee!!
Atupele sikono lapweteka kkkkkkk. love of money selling our beloved party kwa bubu
Atupele sikono lapweteka kkkkkkk. love of money selling our beloved party kwa bubu
UDF is dead atupele is good for nothing very greedy
UDF is dead atupele is good for nothing very greedy
Amlawi kusachedwa kutengeka kodi munthu ameneyu mukuziwako kwao inu?musankha ngati za kamuzu muona kutha zaka 41 osatha kuyakhura chichewa ,ife ndiongoyan’gana basi muziona mwakula mwatha kaya ndi mavuto usatanic sutha muona
Amlawi kusachedwa kutengeka kodi munthu ameneyu mukuziwako kwao inu?musankha ngati za kamuzu muona kutha zaka 41 osatha kuyakhura chichewa ,ife ndiongoyan’gana basi muziona mwakula mwatha kaya ndi mavuto usatanic sutha muona
Tizipani titha ngati makatani
Eeeee limbanani ndi njalayo izi sizitithandiza olo ata zopanda pake ndiwomwewa amene akupeleka chisokonezo dziko koma bcz kuti enanu ndinu ana simudziwa mukungoyakhulapo zosadziwika ndale si nsima ayi anzathuwa kudya chidyeleni kumwe chimweleni koma ifeyo opanda kathufe tikuti tinge ayani zisiyeni izi mungotaya nazo thawi kapena moyo chimamvetsa chisoni mchoti enafe timango nenapo olo mumbili ya dziko mulibe khala maso owelenga
Ngati Lucius Aliduu!! iwe ndiye uti utani?? tikuwonera.kodi kwanu ndikuti ukuwonekatu ngatiso Waku India utisocheresatu iwe!! nkhala pansi wachepa pa ndale iwe.
I think. evil spirits have attack our beloved parties. The nation must be delivered from these spirits
Lord. have mercy upon us .
Mr omar, warry not about that munthu akamafa amagontha m’makutu. ife tsogolo la UDF with ATUPELE sitikuliona that the end of this party.
UDF imadana ndimunthu amene amaona patali tinaonela pa malewezi ndigulu lwo pankhani ya kusankhidwa kwa bingu sizachilendo ayi amafuna azi panga zimene banja lamuluzi akufuna osati maganizo amunthu wina ayi
aa does this udf still with us
mr omar you are not alone,majority are not benefiting from this coalition and atupele has show to us his type of leader tht he is greedy and he will not see my vote go to the court and remove injunction you are wishing malawians well atupele akhutitse mimba yake
mukambirane chonde chonde, mr omar ndi munthu olimbikira pandale
Atupele ukhale pansi ndi omar ndkukambirana ndizochepa izi ndinu anthu anzeru ndikudziwa kuti mukambirana m’mati m’malo
UDF Idatha kale
Mulimbike ntchito osati kulimbana ndi ndale
Udf ndimaidziwa ineyo siiyi . Vuto ndi chani kwenikweni ?
wawukape iwe utaluza 2014 mesa unawalanda mafumu katundu yemwe unawapatsa mpaka kukazulaso chigayo
Omar panga chako ngati ulinazo, chipani cha UDF chatha ngati Pp ,achigulisa ku Dpp ife zinatinyasa zomwe anapanga bingu
If u were sighted enough,unakaona how strong PP is,right from the Grass root. Wait till 2019 arrives, muzatondiuzaje mapwiya.