Malawi police in Limbe have arrested two men for robbing a Burundian businessman in Bangwe Township.
According to assistant public relations officer for Limbe police station, Widson Nhlane, the criminals attacked the businessman and stole a Vanette minibus, 87 bags of maize flour weighing 25Kg each, and cash.
”We have identified the suspects as Yusuf Raphael aged 31 and Charles Chilimango aged 44 who connived and robbed the Burundian businessman,” said Nhlane.
He further said that police recovered the minibus and 85 bags of maize flour.
Nhlane also urged Malawians to continue tipping the police whenever they suspect criminals in their areas.
Raphael hails from Mawa village T/A Kadewere in Chiradzulu district and Chilimango hails from Balason village T/A Nkalo in the same district.
The two will appear before court soon to answer charges of robbery with violence.
Ameni.
Malawi ndi dziko looga mulungu ndiye osaliyelekeza ndi ku south africa kuno
Apolice Mwasowa Zochita Mmesa Ndi Ma Elligle Emigrants Azipita Mabrund Ndi Ankhanza Ameneo Azivaya Amasulen Amalawiwo Ndikwao Akupanga Nkhola Mwao
Mani simunaende
In S A stealing from foreigners is not a crime.
Gud job police
Gud job police
stupit police wobwera azilila kumene
Ine nkudabwa ndi m’malawi uzakhala nkulira mpaka liti? Anthuni wake up stop sleeping! We have to work and our dreams will come true. Mabulundi are good examples they work hard sanabwele kwathu kuno kuzatibela koma business. How comes someone all the way from Burundi to Malawi God saw that here is where his safety is. Tisawabele, kuwatukwa or any sort of evil. Malawi is the country God gave them just take a look what is happening in Burundi and if you have the spirit of humanity you’ll never ever want to talk bad about people who enter Malawi for the purpose of seeking refuge. God blesss Malawi God bless Africa.
Mwayamba Xenophobia etiiii?
GERESOMO ,THINK TWICE #MW
Ine sizinandisangalatse. Ite timaberedwa kuno koyenda. Kuti upite ku police amati akuchita bwino. Ngati zakuwawa zipita kwanu. Ndiye inu a Malawi police antende good?
ife tilibe ufa onse anakaoda kuti iyeyo
adzibeledwa bax ndimene dzimakhalira dziko ĺachiledo
Is this linked to poverty ? The president must address this.
Kkkkkkkkk
Nanga paliso nkhani apa its nt malawian national inu tamaganizani apolice.
kkkkkk……..Atsogoleri!
Munthu wa mkulu nanga abela mtundu wathu wakwina amwene dziko la asouth africa manyi amenewa silimalola.
Inu january simukumuona momwe ndalama yavutira
nde owabelao mmati tizikabela ndani. muzitengebwinotu ndikamba ndiinu anyamata a#ZCC#
Achita bwino sanalakwise nanga azitilemelera dziko lokha lathu
Wrong, God said be nice to foreigners one day you will be a foreigner too in another country.
Loud N Clear !
The kill must be arested becoz they dont want to work
The bulundis akulozaniii
Nanga azilemelera kwathu, ife eni nthaka kumatsauka ngati tilibiletu zeru zoyendetsa ndalama?
Of course nzeru za business amatiposa makwangwanyawa kkkkkk
ndinu awulesi.. azilemera kumene.. kachasu too much
kkkkk maluZi anyanya pamalawi!!!!
Chabwino
Including Fuggie Kasipa
eee! mpaka fuggie man
man amenewa nde kt amaba ndi mfuti et?
kikkk ma celeb aku Malawi
Wapezeka ndi EK47 now he is in cell
Aziwona
What kubela anthu olakwika
kkkkk nde mbava kukazisunga mu neti muli serious inuuu? Mapulisa akumalawi simuzatheka