Lilongwe man jailed for stealing from a grave

Advertisement
cemetary

cemetaryGift Manison, a 19 year-old Malawian man in Lilongwe city , has been sentenced to 15 months in prison with hard labour by the Dedza first magistrate court after being found guilty for the offence of trespassing on a burial place.

According to state prosecutor Sub-inspector Bauleni Namasani, the convict trespassed on a graveyard in the area of village headman Katsekaminga in Lilongwe where he stole a picture frame belonging to late Steve Chizala’s late mother.

In his judgement, first grade magistrate Symon Mwambo slapped the convict to 15 months in prison as a warning to would-be offenders.

Dedza deputy Police spokesperson Constable Cassim Manda said he is satisfied with the sentence.

“What the convict did was not only a breach of section 129 of the penal code but also a total breach of section 26 in chapter 4 of Malawi’s constitution,” Manda said.

Manison hails from Katsekaminga village, Traditional Authority Kamenyagwaza in Lilongwe.

Advertisement

72 Comments

 1. Sanalakwe manio akufuna akakongolesere tchemba mwao,osamulakwila ai siyeni mu2yo kolesedw ndie kt cani apa anakatengaso mtandao akapange makasu ozalira or mipeni ma batcala ena mpeni tilibe

 2. Akumubakirayo naye akuziwapo kanthu zao ndizimozi,aa bm limangoona kukana zaufiti munthu wazeru akabe kumanda km malawi tichitepo kanthu.

 3. Zakumva kumvetsa mutu mulandu suchepa kukhala munthu osaba mkusagwidwa muliposo m’bomamo mukuti mwabisala koma la 40 lidzafika wakuba a mawa mudzakhala inu. chigwire nyanga kwa wina mawa ndiwe

 4. Mmmmm guys, ndi nkhanitu yaikulu imeneyi. Tisaitenge mopepuka ayi! Amangidwe ndithu. Anthu ngati awa ndi amene amakonda kufukula mitembo ya ana ang’ono aja. 15 months yachepa, zaka zitatu bola.

 5. Katsekaminga Vg, TA Kamenyagwaza in Lilongwe. Really? Malawi 24?

 6. Achewa kutukwana anthu akumpoto kwambiri,ndiye mwazionela,bwelani kukabwafu muzapitilize kutilimila fodya,kumeneko mwachulukana zitsiru zawanthu,fokolo muwuzane osatukwanaso atumbuka

 7. Trespassing mlandu wake.kumanda pamalamulo nkolesedwa kupezekako wamba.zoona guys mukuti wabela ndani olo wadandaula ndani?Are u sure inu koma?shame on u all nzelu ngat mbavayo.

 8. Manison ameneyo am sure naye ndiwakumupoto sichoncho?kunyoza mpoto too much yet kwinako mumachitazodabwisa ngat zimenezo.Zoona mpaka kuba pikicha felemu kumanda eeee….man ulimo!!!

 9. Nanunso apolice mudziona zomangira anthu ku malawi kuno kusowa zochita eti? Pali nkhani yoti munthu ndi kulowa pa OB apa or ma criminals atha ?

 10. Nanunso apolice mudziona zomangira anthu ku malawi kuno kusowa zochita eti? Pali nkhani yoti munthu ndi kulowa pa OB apa or ma criminals atha ?

  1. Kodi court anthu ake m’mesa amakhaka oti anaphunzira bwino, ndie angamagamule milandu yoti m’criminal law mulibemo? Komanso mutafufuza mwapeza kuti amugwira kumandako ndi apolice?Have some questions in your head and ask then judge.

  2. Ulipo mlandu,trespassing kumanda ndikolesedwa n inu mungakondwe restn place ya abale anu yoti munavutikila kukongolesa wina wake wakachochepo jst lyk that?nkhalani ngati anthu oziwa momwe manda ndi malilo timawalemekezela kuno.

 11. T/A Kamenyagwaza its in Dedza…not in Lilongwe…..kaya mwina ena andithandize di we have this TA in Llwe?

Comments are closed.