UDF MP rapes daughter of fellow legislator

325

Malawi opposition United Democratic Front Member of Parliament (MP) is facing possible jail time after being caught in the act defiling an underage girl at Annies Lodge in Lilongwe.

The MP, Shaibu Kaliati, who is legislator for Machinga Central, is believed to have lured the 16 year-old girl with K6,000.

Jane Kathewera, an administrator of a Facebook group, posted on the group that the UDF MP had been caught with the daughter of a fellow legislator.

Shaibu Kaliati

Kaliati: In a sex scandal.

According to Kathewera, when he was going to the lodge to meet the Bambino Private School student, Kaliati removed number plates from his vehicle to avoid being identified.

In their discussions, some members of the Facebook group called for the arrest of Kaliati on charges of having sex with a minor while others reasoned that there was consent and Kaliati should be left alone.

The MP reportedly removed a number plate from his vehicle when he was going to the lodge to avoid being identified.

In their discussions, some members of the Facebook group are calling for the arrest of Kaliati for sexual exploitation of a minor.

Others, however, argue that a “sweet 16” girl is mature enough to consent to sex and that she willingly had the intercourse.

Share.

325 Comments

 1. Kkkkkkkk” zomvesa chisoni kwambiri, stupid member kumeneku ndiko timati kutha maplan ndithu.mukumakhala busy kutchetchetera timauthi malo moti nthawi imeneyi muziwayendera anthu akumidzi omwe anakuikani pampando wanuwo.you unfaithful MP zitsankho zikazayandikira, tisazakuonenso mapazi potopoto mmidzimu ndizakulumisa galu kkkkkkk check this out!!

 2. Kaliati, stupid man. Even though concert was there, but the fact that the girl is 16 yrs, surely u MP wathapo. Goat ya munthu!

 3. Khakhakhakhakhakhaaaaaaaaaaaaaa kugwiririra mpaka Ku lodge? Mmmmmmmmmmm achidyamakanda samalakwaaaa amalakwawaaa ndi anawaaa amamuyamba dala kususukira kwacha,(Ku lodge anachita kupangana amenewa palibe zogwiririra apa)

 4. I don’t believe this was rape…..wapalamula zina koma not rape….tsikanayo mesa anapita yekha Ku lodgeko komaso wapatsidwa 6000mk….this is mo ov a prostitution crime than it is of rape

 5. Related development ku KASASIRE Ekwendeni area wina wapangoso zomwezo ndi mtsikana wa 15yrs. ku chipatala anasimikiza. Bamboyo anazemba asana fike ku police. Amene mumazichemelela kt u r fighting 4 girls rights visit Ekwendeni plce unit 4 details.

 6. Munthuyu wafa kwambiri ntayeni 6pin service, nanga ya room nanga mpano aluzanso, anga madam akamva alimmadzi nanga kuchipani kkkk mphuno salota

 7. Am repeating this comment..!¡ wanena izi akuziziwa ndipo ku xul anapitako ndipo nd nzika yodalilika..”May somebody define the word rape?”..!¡

 8. Mawu anga Nda amodzi Kwa Nose Omwe Muli Agaist #mp Kaliat. Ndimwe Vindere/ndinuzitsiru-chifukwani – ndinu zitsiru!! Dikrani Ndikuuze
  (1)munapuza Kaliat Akungwirira?
  (2)mwanayo anakudandaulirani kut amungwirira ah mp kaliat?
  (3)ndi Vuto Lanji Lomwe Mtsikanayu Wapezeka Nalo Afta Having Sex Wit Kaliat?
  (4)mwanayo Anadzidalira Popita Ku Lodge Komaso Sikut Ndikoyamba
  (5)komaso Inu Mukut Kagulu Kapa Facebook Kaya!! Inu Ndee Zitsiru Ntheretu Osakhala Bzy Ndamuna/akaz Anu Bwanji?Amuna/akazi Ndee Hule Theletu, Mwina Anakuchndanipo Ah Mp Kaliat Dats Dats Y Ura Duing This Eeeeeeh,
  (6)akanakhala Munthu Wamba Gat Inee Khani Sikapita Patali Koma Poti Nda Mp Dats Muchita Kutchukitsa Gat Wangwilira Pamene Ayi.
  (7)kodi Mtsikanayu Atamufusa Za Akaliat Anati Chani?Naga In Case Kaya kuKhoti Atanena Kut A Kaliat Nd Chibwezi Chake Mukachan?Uchitsiru Nthooo Sanje Nthoomabodza Kumagokhalira Majerousy Cholinga Mzanu Amuchotse Pa Mpando Warwa Warwa Uheni Pala Warwa Anyoko Kkkkkkkkkkkk In Our Days Chimtsikana Cha 16 Mmmmm Mzimayi Nanga

 9. komanso if they met at d Lodge that was an agreed Plot they both accepted the matter and moved into it mwanayo anavomereza Bull-shit thus not Rape but may probably be Defilement.

 10. Mwanayo amafunanji ku lodge ko? Si rape koma mwanayo kutengeka bwanji samakana? Nkutheka sanampatse ndlama zomwe iye amafuna ndie yasandukano rape

 11. Thats not rape or difilement how ever according to the constitution it is unlawful to sleep with a minor and a minor is anybody at the age of 18 or below. And the writers of this page should learn to use the word allegedly or some one jus might sue you one day jus a piece of advice

 12. Kungoti khani yochitika ndi nkazi mamuna samawina, koma ngati analowa muroom anali ozindikila chomwe akukachita, masiku ano kulibe mwana wa zaka 14, akumabeleka kukhalanso ndi ana, ngati alibe mwana ndiye kuti wataya mimba zambili, komanso mimba zikutayidwazi boma sili mawamanganso.

 13. Machinga Central tagwidwa ndi manyazi former MP E.Maotcha Banda anazengedwa mlandu ndikulandira chilango chokhala mndende pa nkhani yonga yomweyi(about 2 months ago) pano wina ndi uyu yemwe azichose pa mpando kamba konyenga mmalo mochotsedwa ndi section 65.shaaaaa…………

 14. msikanayo ndi wa disable kapena amayenda,amalankhula kapena salankhula?ngiti amalankhula ndiye kuti anagwirizananzo,ngayi amayenda ndiyekuti anafuna chifukwa sanapite kunyumba kwake kukamutenga ayi anayenda yekha,ali ndipakamwa akanatha kumukana nkuluyo.apa palibe mulandu ngati angapite ku jail ndiye ndiye ndizifukwatu zimenezi

 15. The girl is aproblem.ungapite bwanj ku lodge usakuziwana naye munthu bwino bwino.mwinaso zimenezo zimachitika chitika..sikanali koyamba.she needs guidance.cuz ndimwana olowelela

 16. your so funny your saying two things while u know d truth dat its defilement not rape more over its nt a knew thing big pple goes for young nd cheap girl iweso ukuziwa u hv ever been @ d Lodge or Hotels

 17. Tell him that his Constituency is now vacant. We are going to conduct By-Elections in that jurisdiction very soon so that the electorate may elect another development conscious Legislator.

 18. Akumpando ngati amenewa kuyambaso ngati izi amenewa akufuni chilango kt ngati kuli ena amene amaganiza ngati zomwezi atengelepo chitsanzo mp opusa mumaganizo ngati uyu.akanava bwanji iyeyo akanakhala mulongo wake kapena mwana wake mulungu awatsogolele kt ampase chilango chokhwima

 19. That’s bullshit, people like these must rot in jail if found guilty. That’s painting unprecedented foolish picture to our country. Shame on him!

 20. nkhan zinaz amangochita chogwiriza anthuo. Nthawi zina chitsiru chimakhala mkazi, bt de problem iz our law. Nthawi zina atsikanao ndi omwe amayamba dala amuna chifukwa chokonda ndalama.

 21. Kodi kusauka ndithenda? Palibe ndisiku limozi kuti wina azazonda muzake kuti mwazuka bwanji ndikusauko muma komomo kumawala langiza anao.osamaiwaka kuti ndalama ndisatana ndangodusa njila sindinachole kwani

 22. Listen u domo and dealth person no body can take his or her foot puting on top of light fire even could be promised money never.Mkazi wazaka 18 ndiwamkulu amadziwa zomwe anachita,sanamugwilile ulendo wakulodge ndiwawutali , palibe kut anamupseza ndichita mkazi amadziwa chomwe mamuna amafuna ,amakalowa bwanji kulodge mpaka mulumu izi nde zopusa akufuna kumapusitsa anthu even abakakhala mwana wanga or sister wanga anagwilizana.Sangapite komwe sakudziwa anayambilana kale .

 23. haibo what kind of mp you pple of maching central u got? He must be an example for taking care future of young girls But he is a great destroyer. He needs to face laws. To those who u say the girl knows what she was doing, are mad? U dot see that she did because of unmature thinking of mind and because of money. Imagine if it was your fucken daughter or sister. Kaliat u need to jell with ur former mp maotcha banda. What kind of mps u r? Dammit.

 24. Akut rape chifukwa nd mp?… sichithu chachilendo ku malawi ana a size imeneyi kugona ndi azibambo … all rich men they do that amafusila ana ang’onoang’ono

 25. With that nonsense so how do you expect people to change?especialy youths who will give advice to young people?If law is greater than anybody lets wait the results otherwise dont take anybody to court with defilement news.

 26. Is That Rape Case, Or Defilement?
  Anyway, I didnt Know that General Kanene Aliko Ku Malawi!!.. Adzamuchotsa Ameneyo a President Muthalika akangoti Akhoti amu Ngenetsa Mu Jele.

 27. Wekha ukuti rape wekhanso ukuti defilement which is which??..amakatani ku room moreover ku lodge …lets not pre empt until we hear the otherside of the story….

 28. Kodi Madalawa Ali Ndi nkazi Pa Den? Kuthawa Zokambirana Ku Parliament Kukachinda Mwana Wa MP Mzake’ Eish! Koma Ndiye Kuyalukatu’ Ma MP A UDF Ndizimene Amakuphunzitsani A Tcheya? Paja A Tcheya Naonso Kuchinda Sinkhani, Tiona M’mene Zithere, Kuchinda Siwalesa, Manje Manje Kachindidwe Kkkkkk

 29. She wanted to do it,if not she wouldnt have gone to the lodge.
  So marriage age in malawi is 18 yass but shes not getting married she is having sex just like some teenager out there only difference is that its with someone waay older than her

 30. what kind off kumuyipitsila mbiri munthu woti akuononga tsogolo la makolo amawa iye anaphunzira koma akupha ena off caus tikhoza kunena kuti mwanayo amakatani zoona koma zikutengera ndinyengelera komwe waudindo amamuuza mwanayo tikunena izi chifukwa mwana ukamasewera naye mpada samadziwanso kuti uyu ndiwamkulu ndiye apa timati nkhuyu zodya mwana zimapota akulu apatu ndiye zikampotera kundende ukufuna kumpha mwana chifukwa cha k6000 stupit mp

 31. Mau oti RAPE atanthauza kuchita zachiwerewere ndi munthu yemwe sakufuna.DEFILE kuchita chiwerewere ndi munthu yemwe nsinkhu wake ndi waung’ono(zaka zochepa moti mwanayo samaziwa chomwe chikuchitika).Mafuso anga ndi oti nsungwanayu anakakamizidwa kapena titi samaziwa chomwe chimachitika?.Mwanayu ndi Hule anayamba kale khalidwe lakeli koma anali asanagwidwe.Asikana amasiku wano akumaputa dala anthu akuluakulu ndi cholinga choti apeze ndalama zochuluka.Akanakhala kuti sanapezedwe inu mukuganuza yekha akanaulula?

 32. thats defilement not rape. Whether they agreed or not,bt as long as the girl z less than 18 years its an offence. Him being a lawmaker,carrying magnitude behind him as arepresentative must lead by example. He must face the charges koz He z leading by bad motives. Uwo ndimlandu ndithu,ngati amafuna mahule asaizi yake kunalibeko. Inu amene mkuvomeleza zoti anagwirizana ndinu mbuzi zachabechabe,udnt even kno w@ u r arguing. Zidya makanda ngati izi nzomwe zimangofalisa matenda kwa ana ang’ono powapezelera kuti ndiosauka. Uli iwe ukukomenta zambwelerawe kan u alow sambody to infect u jst bkoz of k6,000? Olo hw kan u fil if sam1 has dan it 2 ur beloved sista or dota? Poor minded malawian pipo,no wonder rape/defilement cases r @ an increasing rate. & panopa ma under 18 ndiomwe alindi matenda adzaoneni,mpamene wina akusekerera nkumakomenta mbwerera apa. With such minds we’l neva develop!

 33. uchimo olo tingaupolishe bwanji sumawala apapa munthu wamkulu kuti zochita zake zionekere ng’amba koma mkukhala mp kodi akupeleka picture ya mtundu wanji kwa anthu amdera lake komanso kwa mtundu wa amalawi ayi tichite manyazi atsogoleri inu ndamene mukuonjezera chiophyezo cha matenda kwa ana achichepere foltsek mp

 34. I c no wahala here..the gal knew exactly what she was getting herself into..ngati kuli koti a MP awa akayankha mlandu angosunga ma conversation as evidence basi…

 35. How in the world is that a race case ?? You just don’t know what these 15 year olds or 16 years are capable of … Let me just say any girl over the age of 14 these is capable of anything .. Just because it was a minor it does not mean it was rape .. What kid of rape happens at a lodge ??

 36. Ndikufunanso nkhope yamtsikanayo bwanji mwangoika nkhope yamunthu m’modzi anthuwa anali awili kuyambila lero mukamajambula ndikumatumiza nkhani zanu muzipanga mbali zonse tiziona . Mwina kansikanako nkopyapyalitsa nkale.

 37. Mwanayo ku Lodge anakudziwa bwanji , kuti afike pa size yodziwana ndi Mp ndiye kuti iyeyo anaziona kuti wakula .Akanakhala mwana akanakana. Amumasule Mp yo , kwawo chitukuko chingaime. Msikanayo ndi khalidwe lake iye anamziwa bwanji munthu wankulu. Ku Lodge ankatani mtsikanayo, pamenepo? Apa zikuonetselatu kuti chipanda anthu enawo kuwaona mtsikanayo sakananena it means mtsikanayo anagwirizana nazo.Mwina sikuyamba ku meneko aka nka chi 90 times kameneko Ndiponso munkhaniyi ndawelenga akuti ndi fellow it means mtsikanayo akumudziwa bwino bwino Mp ameneyo bwanji nthawi imene ankamunyenga sana nene kwa makolo ake kuti a Mp aja amati ndi anzawo akumufuna . Amumasule basi mtsikanayo ndiwankulu analora bwanji , Osati pakalowa mbewa nkumafunapo koma poti palowa njoka nkumati ikulumani bodza. Mtsiyileni mtsikanayo wakonda njokayo. M’mene ndikuonela ine pamenepa palowa ndale basi. Mukufuna ma MP Athu azichepa ku parliament ko. Mwanyaaaaaaaaaaaaaaaah!

 38. This just proves the misbehaviour and bad characters of this loose girl who combines school and going to lodge(s) for sexual activities in exchange for her personal needs.A daughter who’s brought with good manners,given,is able to differenciate this is beyond her normal girlish activity.Should you closely find out you’ll hear that may be the girl resides at home where’s lack of parental care due to absence of manhood.Ndiye atsikanawa amangodabha nthawi zina zomwe akuziona poperekera ma drink pakhomo ndi kukazingira chips alendo.

 39. Koma pamenepa ofunika kupaona bwino chifukwa ngati anatengerana ku lodge ndiye kuti mkaziyonso anavomereza ndiye poti munthu ukakhala kuti ndiwe public figure eeish

 40. Mmmmmiiiiii, #Rape sichitikira ku #Lodge,Malawi 24 mwanama,anali atagwirizana kt akakumane,Not kuti dis Guy has Raped,meyb U shuld Correct ur Information,Hahahahahhahahahaa, Rape ku Lodge………

 41. Is this raping or defiling? I know that according to the law, the latter attracts more years as punishment than the former. But lets wait to establish how under aged this woman is that can prove to the court. Otherwise, this wasn’t their first encounter.

 42. ameneyo simwana ndiwamkulu mot amamuhoda boh boh komanso kumumva kukoma mwamunayo. akanakhala kut ndimwana sakanavomera kupita ndiponso anakakuwa kut anthu amuthandize.. aseee bwanj mumakonda kukakamila nkhan zopanda address ndikumasiya nkhani zanzeru?

  • He got the whole story right. She’s under 18 years old so he raped her, intercourse should start at 18 years of age and not earlier or you can be arrested for rape. Even if it was an agreement