The South African government has decided to release some Malawian illegal immigrants from Lindera Repatriation Centre.
Reports indicate that all Malawians who have spent more than 120 days at Lindera in Krugerdorp have been sent back to South African communities.
One of the illegal immigrants who spoke on condition of anonymity said that the South Africa Government has released them because there are no funds for deporting them.
“We have been repatriated back to South African community because we have spent more than 120 days in Lindera which is contrary to the constitution of South Africa,” he said.
According to the source, there are thousands of Malawians and people of other nationalities at the centre.
“We were thousands of Malawians there, it’s just lucky to be released back to South African community. Lets pray for our friends who are still there. The environment is not good for human beings there,” he said.
The released Malawians have been told to go back to Malawi within 17 days failing which they will be sent back to Lindera.
The immigrants released are those arrested in the months of June, July, and August soon after xenophobia.
It is not clear what assistance has been given to first travellers to South Africa who were arrested upon entry into the country.
am hiye. mukunama afana. dakadyabe rand imeneyi
Ndikumva chison hevy nd mmene ndikukhalila kuno bolabetu ku jon konku tsoka kwa omwe amasangalala nzao akamutola ali pa tsoka lolima kwambili but no rain kapena ana ake alipila 3z kupulimale zs y’r
Thanx to God,we missed our innocent friendz,mulungu amaona amalawi timangogwira ntchito basi,no zaupandu,indeed He make way were seemz to b no way
Tathokoza imwe bambo zuma ndi boma lanu potulutsa abale ndi alongo omwe munkawasunga kundende .katikomelenibe mtima kutisunga ku dziko lanu lino mavuto achuluka ku malawi tikulephera kukhalako
Mvula yayamba bwelani tizizalima kuno
Anthu ayamba kutulutsidwa kuyamba dzana ngakhale boma la Malawi akuti litumiza ma bus 17
kamba kakusowa tchito a malawi tikuoneka ngat mbuli maiko ainyakea.
Kusamvetsa man tinathamangira kubwera kuno kuthawa xool .Tidya zakudya zakulindera mpaka kutha kuyamba kutisiya okha eya ana achepa
Winawake akuchita kunenetsa kut kuno sangabwelenso, hehe! #Kukakamira_mtof_waen. Just thank God they have bn released & left freely
A malawi 24 plz check yo post b4 posting becoz your confusing us with yo post hahaha,,,,
u must understand de stoly first b4 comenting bro!
I understand there is no malawian who sent back here that’s liar
Great Baxter Sokalankhuku Mkumba Theu
Hummy Humphreys wana tikumwa nawo wamukakaka kuno
Mufwenge nyifwa yiheni Baxter Sokalankhuku Mkumba Theu
Cc
Silence Banda
Hummy Humphreys
Well done SouthAfrica that’s what we call Ubuntu thanks Mzansi
And now a home affairs sakupereka ma asylum… Even to sm other countries
Praiz de Lord.
Bola Lindera kusiyana ndi Malawi
zithumwa zagwila ntchito ati?
all the best
zili bwino koma vuto lainu mukapita ku jon ko mumaiwa abale ndi family sinthan pliz
Abele tisanyozane kodi amalawi tinakhala bwanji,y r we best on let somebody down tiyeni tialimbikise a Malawi anzanthu they go there for green pasture some of them they have families that they look on them,so z indeed painful,tisasankhane.
Mnyani waku escom waiwala kuthimitsa magwetsi mwina wagwidwa shoko, achule ndi nkhanu aumitsa kale madzi kuli zii kumpop zili ku malawi dzko la malaulo eiiiiish
kwaeni ndi kwaeni! mungazilimbitse mtima maka koma mtendere wamu mtima mulibe inu! coz u r saying that u r now free how? nanga 17 days ikutanthauza chani? onyozanu zinyozani ifetu kuno movutika momwemu nyumba tamanga abaleso tikuwathandiza
Be awake guys South Africa is not a country that u should feel proud of it. Let me decleare this, there is some plans that you cnt see that they are planning, as we speak watch out for the next year what is gonna happen. Dont ever being a dom my brothers and sisters by shouting your home and your home people in Malawi, im also here in SA but home is best indeed. watch out for the next year to come.
I agree with u, they cant just do this and smile… Smthng is gona happen realy, as of now they’ve stoped giving or renewing the asylum @ home affairs even to sm other foreigners..
God is good, lets get back to work.
Mwati awatulutsa ndiye ndichifukwa chaninso akuwapatsa 17 days kuti adzipita ku malawi kodi ndalama akayitenga kuti poti ntchito samagwira?
Koma bola pamenepo tayambaso kuma wamkaka kkkk cremora mfwethu wa33wa
mudala kanjoka achimwene!! ife talimba nawo mavuto ku Mw home is Best coz agogo okalamba omwe munawasiya aja tikusamalira movutika momwemo! mulibwiino ndinu munathawa mavuto!#4evarRealCitizen
Amen Amen
North west home z best eat volosi but fusani muzadyere kwanu next time
Zosangalatsa tilimomuno @ ngiyabonga wamkulumkulu
I think anthu enanu khalidwe mulibe kumalawiko sitingakhale cz kuno tazolowera timalandila ndalama zambira kuposa wa ku unima kkkkkk mbola malawi nditha kulipila aziphunzitsi atatu pamwenzi
Thank ZUMA eye witness ol people from honey dew are here in mikhukhu
Welcome guyz; go en work hard.
All the best guyz kagwileni maganyu anu kuno kuli umphawi anthuwa akunyoza cz paspot yadula sangakwanise kubwera kumeneko pano ndi maforena ziko lathu lomwe all de best
NEVER LET YOUR FAILURES GET TO YOUR HEART AND NEVER LET YOUR SUCCESS GET TO YOUR HEAD (STUPIDITY MIND)
SO PLEASE STOP SAYING YOU WISH START SAYING YOU WILL WHILE YOU ARE FAILUREZ….
Mmmm its truee story?
Yes sir..am the author of this story..
God is good
Good
Am happy asiyeni akhale konko malawi opanda ndalama anthu tingovutika kuno
17 days,they must leave RSA to there homes,the reason is that SOUTH AFRICAN government has no fund for deportation of these illegal immigrants,so confusing.
hahaha funding from where??? point of correction ,it’s not RSA but Malawi doesn’t hav funding 4 it’s pipo 2 come home.
No no my friend,no point of corexiont here,its the host community that is responsible for deportation,RSA gvt has done this coz it has no funds due to economical problems in the country not Malawi unless otherwise.
Am the author of this story Davie Chaula where you dont understand??
Still in South Africa mwene, simukungozuzula boma chifukwa cha umphawi,mukungokanda dairy, mukutuwa kumeneko ndikuma comenter mbwelera zanuzo apa zopusa…
winawe uisova, tinathawa2 ulova ife kumalawiko, kuno2 mwina suziwa tikadya volose ndye kut tadyera masamba, pomwe iweyo uku comenter mopusawe ukungodikila christmas kut uzadye nkhuku, south africa is the best country in the world …
Ndizowona guys,Pali Anyamata Atatu amkhalira ku Durban anawatulusa Monday afta atakhala 108 days ku Lindera
After 120 days komano ntchito akapeza alemba ena koma nkhani yabwino
Kma mwanva chingerezi kuti citi bwanji ife apa tili free tsopano
Good news
Anthony, next is who?
Thats good,i thank for that decision,we are all blacks and we have to fill pity on one another.
Apandiye tamasuka basi kuteleku ndimawopa kupita mtown ya Rusternburg .powopa myezi yazisangalaloyi ndati Azangonditchava kkkkkkk koma ngati Ayamba kumatisiya chochi zilibwino baasi chaka chino ndiyekuti Satchava anthuu kkkkk.
Samala ukakhala 3 months nawe kkkkkkkkkl
kkkkkkk koma ndiyetu ku saver ee!!. Ayi man bolanibeni Awabweza atlist cz Dzikolathu sililibwino ndiye kupita osakozekela iyii!!!Man ndi mavuto osowa kukamba.
Zili bwino pamenepo! Hw much i enjoy to hear that!!
better
woow that’s lucky guys
Bweraniko mutipezaa.
tiwavele chison ndiazibale athu amenewo tiziwapephelela kuti azikhala mwamtendele alikumeneko cholinga chokasokola kuthandizila mabanja ndiabale awo u SA pple and the govrnment ur pple are spleding to all countrs seeking for ajob doing busness ndiye atakhala eni maikowo kapena maikowo azibwezela nkhazazo mungave bwanji sherm on u with ur stupid goverment
zitsilu zimenezi asabwele angakapeleke matenda zowona kumathawa mabanja awo akungochitaso uhule azikazianu mwati mwapita kutchito pdmene muli kokaba ndikuchita uhule
zitsilu zimenezi asabwele angakapeleke matenda zowona kumathawa mabanja awo akungochitaso uhule azikazianu mwati mwapita kutchito pdmene muli kokaba ndikuchita uhule
Kuno bwanzi kuli ngati ku Soth Africa koma vuto atsogoleri athu amafuna kukhala Numb one iwo,Chitsanzo Mchikumbe Num one anali Mtsogoleri wa dziko chfukwa iye anali ndi Matractor tosono if khasu ndiye tikhala othandizika nkoona anawa amangoyenda kuti mwinaor Ninkawa
Njomba Che Yusufu, Tawecheta Mbolembole
iwe wawerenga sukuva kuti abwerara kuno ku south africa iwe innnocent
what about those who have spent less than?
munidye munitafune.kapena munithilire levlon mumpunga..kod kunyachulak ndidayamba ndne?kkkk ko 2mbi lo aimba anzanga….
uuu! mphakana 120 days
Kkkk sowani basi tipezane mu mthembisamu!!
Eishhh,can u re-read from “Reports….
Ena anangobadwa osokonekera basi abale takulandila tiyeni tibwerere kutchito satana achite manyazi
Kkkkkkkkkkkkk
God is good all the time
Shuwa ka
Olakwa ndi admin khani zouza amalawi amalemba nchizungu, ndimenezo akungoti tiwalandila
Kaya bola ndikulandira dzindalama dzanga malipiro kufanana ndi MP Wakumalawi kkk dzinenani mungathere
koma nde alipo eeeee
Understand the story before commenting..they have been sent back to south African communities not to Malawi..eeish koma ku Malawi ziriko..
enanu mwangokula mitu ngat mapapaya ndemanga zanu sizikugwirizana ndi zomwe # admin pliz read carefully n’ understand.
,..
Chawonanzako chapita.ndiumphawi umapangitsa osatikutsata #KCF.we thank #GOD powamasula musinga.
south Africa is a Rainbow Nation
Muzamutambile ndani? Osabwela kumeneko kkkk
Anthu amene anabwela ku Sourth Africa anabwela ndicholinga chochepetsa umphawi kuopa kuba akanakhala ku Malawi kuba mbuzi bwezi mukuwaotcha ndi mateyala, guys ngati akutayanidi ku Lindela ayi takulandilaniso tidyele limodzi a Voloc ndi Anapiyewa atayeni akunyozawa bwelelani maganyu anu azungu akufuna akupatseni ma Bonus anu munawasebezela aja
Enanu muku commenter zawu tsiru kodi ndalama zobwerera kunozo amakatenga kwanu,kapena mumadyetsa ma banja awo zazii
usapye mtima ataye,sakumva English ikt chan,auze awelengenso!
yo
Zonama
Abwere- abwere kuti ngati zocommenter zakusowani kusiya bwanji? African in africa no boarder
Welcome back guyz
Thax South Africa government. Kulinjala kumalawiku
Kumawawuza mazulawo kuti ndinu ochokera ku Kwazulu Natal..ndinu amodzi koma munkathawa apartheid kuolokera ku tsidya la Zambezi & make plan!!!
Alakwisa kuwatulutsa,akanakhala mommo bola coz samamva ayi anthuwo,dzaka dzapitazo adawawotcha ndimateyala,mwapompano apa adawakhapakhapa koma ayi ndithu osadula phazi kujoweniko..
mutu okulawo opanda nzeru!!! mbuzi ya munthu!!
U r fool bustard
You don’t know what you are saying my brother, Mulungu akukhululukire.
Hahahaha,ngati anali azibale anu kapena munali inu nomwe zanu izo,adzingokugwiranibe ngati mukusutsana ndilamulo la boma la RSA..Sindine mmodzi wa ogwira ntchito a Home Affairs koma ndine munthu chabe wokhudzidwa ndimchitidwe womangotengera anzanu poti akupita kujoweni basi nanunso nkumapita nawo pamapeto ake nkumapeleka mavuto kwa mabanja ndi achibale anu akakupangani detain azamalamulo aku RSA..Ndalama yomwe mumaitsatira kujoweniko kunonso iliko olo moyo wabwino womwe mumatsatira kujoweniko kunonso uliko ndipo wopanda chewu chewu!
Mr Gondwe….fundo yanu yomwe mwalankhulayi yandipangisa mwina kukulankhulan mowawa pliz 4dat…..koma mukadaenela kuzifusa kale mafuso ngat awa:akadakhala wachibale wanu wamangidwa fo 120dez ziko laeni mukadamamva bwanji mumtimamo?..2 mukuti kumalawi kuno kuliso ndalama…kod ndiangat omwe amalembedwa ntchito kuno akamaliza xul?…palibe chithu chowawa kwamunthu yemwe wamangidwa in foreign country bra bra
Nzeru ulibe ungofuna potchukilapo iwe zoba
wena mdoda wagula
hahahaha,Guys pali zinthu zina zoti ukayesa kawiri katatu dzikakanika kulibwino kudzisiya…sikutinso mukayankhula kwambiri olo kunditukwana ine zipangitsa azamalamulo aku RSA kusiya kukusakani kapena kuwasaka achibale anu ngati sakukwanitsa malamulo..weza zey lyk it or nt Home Affairs are stil after zem..Am out ooooh!!!
They will come back where? They are already in South Africa in their places.
Other pipo they just coment bt he dont know what happen
Yeah is true
Escape from sobiba!
Enanu zomwe mukucommenter ndi nkhani sizikugwirizana apa
zoona man,umphawi ndi nsanje zimayendera limodzi,utha kuona yakula ndi nsanje apa!
Waitn 4 u ladz. Fortunately most parts have nt yet planted. This is gud tym for u ne!
They have been sent back to SA not Malawi
These guys make me sick bcs without mincing words here, they r in total trouble but luk, wen they av bn deported, they sneak out again. I feel they can b ok here than down south.
nde yake madolo!!!
They Are Like Cociroaches… THEY WILLL COME AGAIN 🙂 #ndanenamunthuapa?
sunamvetse anthu wo awakhululukira ali komweko ku joniko a
yap,kulephera mayeso sikupanda nzeru koma phuma ku mamvedwe kaya!
The Fact Is; SA Can’t Do Anything Lasting To Tek Them Competely Out For Good.. I REPEAT They Are Like Cockroaches. To Those Who Think I’m Of Topic, Think Again Coz Im Jst Expressing My View On AlThis Related Topic. No Where Does It Say Comment Specifically On “Point”. #Ndanenamunthuapa
Choka iwr Real Doublec
Ndatukwana Carpena 🙂
Ndatukwana Carpena 🙂
Shupit
Usova…. shoe pit
Kkkkkk welcome back guyz
sunamvese re-read
Abwere amenewo kumudzi, tidzadye deya akudziwa kulinjala ku malawi
mutu okulawo opanda khalidwe!! mbuzi ya munthu!!
From de passage,they are not coming home,they are to be sent back to RSA communities, ok.
Hahaha #mrjohnphiri express your opinion on the issue :p ……….. thanks for atleast expressing your opinion #innokhonga 🙂
Oh tank God
Sorry guyz sizabwino ambuye aZiwa zomwe apanga monse