Malawi Police officers at Dunduzu police unit in Mzuzu purportedly rejected a bribe of about MK80,000 opting instead to apprehend two thieves who were caught with various drugs worth millions of Kwacha.
The two suspects had stolen the drugs from hospitals across the northern region. Sources alleged that before they were caught, the two had already managed to bribe some police officers and cross some roadblocks with the drugs.
When they reached Dunduzu roadblock, they met ethical police officers who nabbed them for being found in possession of the hospital drugs.
In a bid to rescue themselves, they told the officers that they were ready to give them MK80,000. The officers declined the offer and insisted on arresting them now on two counts: one for trying to bribe police officers and the other for being found in possession of drugs without relevant documents.
Northern region police publicist Sergeant Maurice Chapola identified the pair as Chimwemwe Chibankhuni and Simeon Mwenesulu.
He said the two have since been sentenced to six years imprisonment for the offences . In a related development, three medics have been arrested in Chitipa for aiding a drug thief to steal various drugs across health facilities in the district.
The trio have been identified as Owen Mnyenyembe, Fanson Kathonga and Waukile Mkhondya. Police say they managed to arrest them after the drug thief revealed that the three were involved.
“The other dealer identified as Jacob Msiska who is currently behind bars helped us with information leading to the arrest of the three,” said the police.
Meanwhile, the three are expected to appear before court to answer charges of aiding the stealing of drugs.
Records indicate that the practice of stealing drugs is fast becoming rampant in the country despite several government efforts to curb the malpractice.
zay amba liti zokana zinyengozo?
Strongly no!!!
Bravo Police!
iyeyo kutani?aziyelese?nanga wakanapo kangati zinthu ngati izi?to hell
Bravo POLICIA!
Azako akwiya anayipeza iya yomwera wafoyilisa game but mutu wako ukuyendako bwino …… Abwana musakwiye nitchito lero mimba yanu susa palibe…..
Kodi munthu ungalemere ndi 80000 k ndindalamaso masiku anon
Alekeni akagawana abwana awo imeneyo mungomva kuti awatulutsa pa bell usiku omweuno
Very strenge! Malawi’s Police is adicted to coruption! Reazon is simple, these people are paid timachenji. Chitsiru ndi Gvnt of Malawi
Apolice nawo anachulukana lnu ndie oyambisa anasowa kuvomera kulandila ndalama ngat amatheka ndi k5o mmm
Kungoti anamupasa zochepa.
apa nde madolowo atchuka…ofcz sawakwezabe…timalandira chuma chimenecho nanu kkkk
Umangodziwiratu Kuti Ma Big Anali Pafupi,akanapanga Bwanji AKapokola,akana Akuyifuna.
Ineso ndine wa polisi wa chinyengo ekanapeza ine ndikanauza andipase k20 000 ndikanasiya coz boma malipilo siikwana 80 000 wapolisi wamba tiyen tilibeleso boma coz misonkho imadulaso moti bera
Afufuzidwe apolice enawo amene analandira ndalama kuti adutse pa roadblock
Mmmm kaya.anthuwa amagulisa ndi affidavit yomwe
Scono inachepa
Ndalamayo inachepa nkhani sichina osati kufuna kukwezedwa
Apolice oterewo kuxowa
Ngati Pali apolice achinyengo ndi apadunduzu koma izi zatheka bwanji?
Who Z De Police Officer? May God Continue Blessing Him,
Who Z De Police Officer? May God Continue Blessing Him,
He is a true citizen a patriotic man n deserve a promotion
Apolice ake ndiofoila
when there is positive & negative,malawianz choose to be on negative side always
koma ndiye malozatu malawian police denying k80 000.
Ka 80,000 masikuano ndikachani?bola akanaonjezerapo mkunda ndi paketi ya ascort mwina akanatha kulandila
Apolice akumalawi kwathu kuno olo kuwapasa thobwa amalandila kenako iwe nkudusa,so if so well done
Awonetsa good example a police amenewo
Asiyeni ndalama yafertilizer inapezeka mwapanga miskate muthila manyowa muwona kkkkkkkkkkkk
50 kwacha imawakwana sizingatheke kukana 80,000 kwacha
mwagwira ntchito yabwino guyz takunyadilani kuti, nyadu!
Dunduzu Police Officers Not Malawi Police, Gud News.
Kkkkkkkkk guyz munthuyu anangoyiona ndalamayo kuti yachepa as comparing ndi ma drug wo. Nde anaona kuti ndibwino kuwakakamila kuti mwina angapeze promotion.
Kkkkkkkkk guyz munthuyu anangoyiona ndalamayo kuti yachepa as comparing ndi ma drug wo. Nde anaona kuti ndibwino kuwakakamila kuti mwina angapeze promotion.
Maka apolice apa bangwe load broko amaitanisa ma k200 . Upeza magalimoto a kwamkando okutha mateyala opanda ndi misonkho yomwe lamba anadulapo adilaiva amamangila munchuno ati ndi olimba .umawapeza ali mbwe mulimbi .
safuna kukhala olemera!!!! zakeyo 11 vs 5-8
Anaziwa kuti itonyoka , amalandila olo k500
Ukunamiza mwana wakhanda a police apa Dunduzu amenewo
Akufuna kukwera maudindo
great….from belarus…
You are true Sangakane K80,000 nzotsatheka zayamba liti? Mwina apolisiwo analipo ochuluka kuposa ndalamazo.
Amalawi lets learn to thank if things done well tisamangonyoza anthu achita zabwino alakwaso ndinu mtundu wanji wa anthu inu aaaaaa
Kkkkkk ameneyu akuyenera kukhala wapolice amene wangochoka ku training osatikhala kale kkkkkkkkkkk sanajayire
Nkhani zakalekale izi kuyika lero?
thats wat we call professionalism
Mmmmmmmmmm kungoti ndalamayo inachepa. Nanga anthu 5 akanagawana bwanji?
pay dem well,ana akuyigwira ntchito day & 9t.
weldone to Dunduzu police, it looks like u r serious at your work keep on doing that! congraturation to uuuuuuuuu!
okhawo aku dunduzuko lero lero wina walandila k200. 00 pa road block chifukwa minibus ina dzadza kwambiri
Musatayike aMalawi anzanga siapolice onse amalola ziphuphu tinali ndi OC pa masambanjati ku Thyolo amakana amati ndi tchimo .
strange,is’nt it?
Zaboza izi mwina ndalama inali yochepa
kma akanakhala apathupa achina ….
Panali pagulu,anayiwonetsela,amalandila zochepa guys.
Apolisi mwaonetsa khalidwe labwino, a malawi kunyoza ndi kwawo
Apolosi apa Malawi anayamba kuvalanso jersey ya u soldier. Kip it up
Thumps up
Mwaona2 vuto lanu olemba inu…mwagulidwapo kutereko
Ndiye iwo apindura chan bonus awapasa zambiri aiwala kti mwezi ukatha amabweza ngongole
i think they did not understand each other if not the police wanted the dealer top up the amount.Hmmmm apolice athu sangakane ndalama under any.if it tru please promote them
They deserve promotion
wapolisi unkhungu too mch
Medical officers who sold them public drugs also must be charged to balance the equation
zautsiru dont u knw dat mulungu sapatsa pamanj sudzalemera kapee!!
at least its a good news coz malawi is on record that corruption its at 99%.
The money was too short!! Even if it was me, I couldn’t recieve,but lets congratulate them they hv shown their maturity,
wa #police wa ku Malawi ?
Afa osauka makape amenewa kkk
kungot ndalama inachepa k80,000,drugs worth millions akanawapatsa ndalama yochuluka sitikanadziwa,anyway ayesetsa agwira ntchito yotamandika
Akana bwanji?
Gwirani ntchto yanu anyamata
Panaliso madala team
Big up ofcers on duty! Kachama give them 1 step ahead pa rank anuwo they hv shown good xample,but to say reallity ndalamayo anayiona kuchepa compared to v goods ananyamula komanso ndekuti apolisiwo analipo ochuluka.
Anthu Openga Mwachita Bwanji Kukana Ndalama? Ameneyo Siwapolisi Weni Weni
Muwamangenso a polisi anzanu amalandira ziphuphuwo
mbuzi yamunthu imeneyo kukana makwacha zoona azafa osauka
Aaaaaayes Malawi is changing now,is it true Malawi Police men to reject abribe ov K80,000 ngati ndizowona pitilizani
sanagwirizane price
sanagwirizane price
Nice work my officers
Anakana chifukwa ndalamayo yachepa comparing ndi katunduyo.Nkhani ndi yoti sanamvane mtengo basi.Amatheka ndi athu.
akana 80,000 asiyeni, adzafa ali amphawi amenewo anzawo akupakula pakulu in the name of cashgate. mufuse a tcheya .
aaaa i can’t believe this.. zinachitika liti bcoz t seems dat the thieves hv already appeared b4 court. wat a quick move.. malawi yomweyu? mmmm kaya
Kuyamikako Pakachitika Zabwino,nthawi Zonse Basi Kunyanzisa Police.Anthu Apulumutsa Mankhwala Ama Millions Awa
bwanji, zinachepa? Nanga deal ya mamillion inu akupatseni 80! Zachilendo mpaka kukana! Big up our law enforcers
Kkkkkk hope ayamba kuziwa ntchito pano
ndlama inachepa imeyo
akudziwa ntchito yimeneyo
Thumbs up mr policeman
Dunduzu Police Officers #not Malawi Police Officers we know…kkekekekeke thumb up for #DPO
Nangudabwa na kuwenge uku kwa wanyithu uku mmmmm kkkkkk mpha wapoka izo kkkk
Za Ziiiii Muli Poti Paja Amalandira Iliyonse Iyiyinso Alandira.Mwachita Bwino Kuwaminitsa Choncho.Mwano Abuluzi Amenewa.Eee Apolisi Amatibera Eeee They R So Corrupt Yet Mmapisa Mthumba Nokha Mkumapereka Kufupa Nyau Yosavina.Ngati Amaba Kopita Mukaberedwa Simmakudziwa??Wamaliwongo Apanidwe Ndi Chigwenembe Ameneyo.New System In The Block.Thumb Up!!Show Them You Can Do Without Their Money.Asamalalate Ngati Anakulembani Ntchito Adziwe Kuti Anakulembani Ntchito Ndi Wachikhalire.Kugula Njira Ndikufuna Ma Favours Kukuphani.Wasala Ujeni Usamale Khwekhwe Lako Lapotedwa Kale Likupuma Padenga Liphwe Madzi Kaye.STANDBYNtchito Ndiyolumbira Iyi.
Malasia
Obviously apolisiwo anali Ambiri awiri or atatu sangakane
These guys should get promoted and get a raise. They have saved lives by bringing back those drugs and should be rewarded
mumayambisanxo ndiinu
Lets give pamene zithu zayenda tisakhale ndicizolowezi comangoyang’ana zooipz zokhozokha, well done Donduzu Police Officers
Amene Amaberedwa Ndi Apolisiwo Kufuna Kwao.Ngati Amamupisa Munthu Mmatumba.Kopita Mukabeledwa Simmakudziwa.Kugula Njira Ndikufuna Ma Favours Mkumene Anthu Kumawafupitsa Nyau Yosavina.Mukafupa Uko Kumabwera Apa Eeeee Apolisi Andibela Eeee Chinyengo.Changamukani Kunyoza Olo Kunena Apa Sikungabwezere Ndalama Zomwe Munafupa After All Munatulutsa Nokha Mthumba.Thumb Up Officers Achangamutseni Chonchi Ofupawa Adziwe You Can Do Without Cash.Ntchito Ndiyolumbira Iyi!
Mwina salary yawo inali itangolowa kumene,thats why
iwe usatinamize malawi police yake iti? Imayamba yalandila ndikumangani pambuyo
Hahahaha,wonders will never end indeed.A Malawi police officer rejecting a bribe yet his boss is busy receiving it behind the curtains.What an irony?
akanavomela bwenji tisakuziwa,zachamba
Anaikana chifukwa choti inachepa amafuna meter
mK80 000 inachepa mpake kukana
bodza ili there is more to the story
Good example keep it up guys.
Mwachita bwino apolisi,Akhaule agaluwa.
Ameneo nde ma udindo akwezedwa bas mpakan kukan 80 galand eee apolice ake aku malawi? ameneo nd azibusa ma chalich mwao
Mwachita bwino apolisi,Akhaule agaluwa.
Tinamizeni zina mmesa abisa kale.
Ameneo nde ma udindo akwezedwa bas mpakan kukan 80 galand eee apolice ake aku malawi? ameneo nd azibusa ma chalich mwao
I would like to ask the inspector general of police to promote all one step up, kumeneko kuwapasa mangolomela ndi kukopa enaso kukana bribes, azindikireso kuti ngati azathu akwezedwa pa k80,000 ndikupulumusa mankhwara yamunthu wamba wakumuzi bwanji yikanakhara kukana amillion kwachas?? ndiye mwina two steps up, thats the only way to reward and encourage them
Good Job By Plce Ofcers, Kp Up To Save Lves Of Malawians
Thumbs of to The MALAWI POLICE OFFRS on duty for being good examplary by saying NO to corruction to law breakers suspects:Anyanya kuba mankhwala mu zipatala za Boma enawa and that’s is the way to go inorder to reduce such mulpractices. KEEP IT UP WITH YOUR PROFESSIONALISM CATCHING THEM!!!
Drugs worth million…….Bribe worth 80grand.kkkkkkiest.Wise policemen.Deal with these stingy dudes.
amafuna million agwa nayo
kkk nane ndadabwa
Nazoni,cashgate za apolice ndizimenezo,
Ma new recruites eti?mukanaterotu nanga,chapanchombo sichinagwe kkkk
Akunama,koma aziti yinachepa
ndili ine ndingalole . . .sakukondwa nayo salary yaoyo sakukondwa nayo
Chabwino 1 million kwacha…mukuti bwanji pamenepo?….. EEeeee dutsani koma musazabwerenzetso muzatichotsetsa ntchito…..kkkkk
Inamuchepera ndalamayo wangobapo mankhwalawo mmene amaikondela ndalama a police yakumalawiso aaaa
What ? oh my foot !, tel me its a lie thus not possible may be there was a cat hidden in bag, atrap sort of , snare somehow somewhere!!
Apolice opemphera kkkkk
Thre stupid that’s why peter don’t pay them in tym and not putting increase he knws there dull kkkkkk
Ameneyo umphawi sanatope nawo,
Akadakhala a dziko lina not Malalawi
Money goes money comes.dollar ndi satana
Akalandila amanena?
Siwapolisi ameneyo. Amufufuze bwino mwina anangobwereka uniform. Chomwe ndiziwa ine wapolisi wakumalawi sakana ndalama yina iliyonse. Yikakhala yochepa amangolandila monyinyilika koma amalandilabe.
Zitsilu za APOLICE mene zili pa MALAWI kumakana ndalama?
Kukana ndalama ndi tchimo atembereledwa basi amenewo .
Big up to u officers
Anakalandira anakatiuza? zopusa basi! kanangochepa kadorako.
Ndakaika man
Admin!! are you sure are they Malawian police..,no no no thats imposible, maybe we should call them Dunduzu Police Officers(DPO)coz Malawi police is even corrupted with K200.00 yeniyeni
Its not all Police officers who are corrupt
but 97% are corrupt
Nzosatheka Malawi police kukana ndalama ngakhale Petulo Ibu atawamalipila MK100,000 komabe sadzatheka kubela wanthu patsogolo
mmmmm boza onse iwe why they are employed
guys mulibe pa bwino ndi2,,kkkkkkk,,kulandira ziphuphu kumangowanena,,kukana ziphuphu mukuwanenabe,,,,,hahahaha
kkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkk u have made my day
Ah malawi police are 101% corrupt.
alipireni bhoo!
kkkkkkk dunduzu police officers kkkkkkk
Anurse Musanene Anzanu Inuso Mumatitumiza Mutimaprivate Tosadziwika Bwino Pansi Pmtima Mukudziwa Kuti Ku Kaprivateko Mwakagulitsako Timankhwala Tokuba Tikukuonani Kkkkkkkkkkkkkkkkk
ndeti dollayo inachepa. katundu wamamita mfana akapereke 80g?
akutitu zachitika ku mzuzu asati kumalawi!
Nde muzit apolice sakugwira ntchito? Thanx officer 4 rejected bribe.
aaaa kufuna kusauka
analipo ambiri ndiye anakanika kuti agawa bwanji koma mumutima zikuwawa.
apolice amenewo adzafa osauka, amakana ndalama? hahahahaha kupusa! make aplan samayidziwa eti
alibe tyming Dollar mmene yashuphilamu!
Samakana wamba apolisi akumalawi ndikuwadziwa ine,anayiwona kuchepa 80pin yo,nanga deal yama million unkapatse wapolisi 80 pin??? akanawapatsa 500pin or above mukanamva “BASI DUTSANI ABWANA KOMA MUPANGE CHANGU” hahahaha
kkkkkk ndalamayo inangochepadi apolice amayendera yomweyo. moti minibus anthu akwele atatu atatu pampando ife timakwela folofolo. ndiikudutsa pa Lunyangwa bridge bola kugula nsewu
Sukunama Tiwo,nthawi zina apolisiwa amangofuna kukonza reputation yawo ngati akakhala kut kumbuyoku amapanga ma blander pantchito
80 Pin? Hahaah! Yachepa imeneyo ndiyomwe ndimalandila 4rom Monday to Friday
80 grand inachepaa!!
Promote them
80 pin agawana bwanji apolice 10
Malawi 24 chithunzicho tanditumilani. wachibongayo kukhala ngati ndachimwene anga Lol
God Bless
Anayiwona kuchepa kuti agawana bwanji
hahaha kukhulupilika kumeneko?ndimbavabe or zakana chinyengo.
80 pin inachepa kutengela ndi millions
Makape Awo I Think Ndima Recruit Kapena Inachepa Ndalamayo Mene Ndikuwadziwira Apolisi Aku Malawi Sangakane
Makape Awo I Think Ndima Recruit Kapena Inachepa Ndalamayo Mene Ndikuwadziwira Apolisi Aku Malawi Sangakane
Apo ndimulungu akulipile nchimwene usadandaule 80. Gwilatchito yako basi ndalama siyintha koma tchito yimantha!!!!
dollayo inachepa
Apolice analipo angati?
80 kugawana 1pin 1 pin hahahaha! Nkana anakana yachepa. #Macheza
Malawi is full of corruption, apolisi kukana bribe pot month end z approachng
Sukunama maybe thats money was not enough 2 sharing those police
eyetu mwene
is this really how we can reward those gud cops out of the bad ones?
I personally knw that police unit ndanthu achinyengo kwambili amenewo,,,
Nthawi yolima ngati ino,munthu kukana 80 sauzande?wapolice ameneyo amfumu akwao aziziwe
Well done
Ndalama mmene ikuvutiramo kukakana k80 pin??? minyama chan???
Keepitup
Mbava zokhazokha kukanilana kash
chabwino tamva
Aaaa inachepa 80? Katundu wa million? Mbola
I’d better pocked the 80pin