Oswald Lutepo’s health deteriorates

Advertisement
Oswald Lutepo

The health of former People’s Party top guru and Malawi’s chief cashgate convict, Oswald Lutepo, continues to deteriorate a development that has forced Mikuyu Prison officials to transfer him to Chichiri Prison in Blantyre.

According to a local online media outlet, on Monday Lutepo was moved to Chichiri Prison following penal complex on medical grounds.

Oswald Lutepo
Lutepo (C) in poor health situation.

Lutepo was convicted of money laundering contrary to Section 35 (1) (c) of Money Laundering, Proceeds of Serious Crimes and Terrorist Financing Act of 2006 and Conspiracy to Defraud contrary to Section 323 of the Penal Code.

Through his lawyer Oswald Mtupila, he initially denied all the charges but later pleaded guilty saying there was much tension on his case and it led to him getting paralyzed.

Throughout his trial, he went to court while in a wheelchair.

He was handed a jail sentence of 11 years imprisonment with hard labour for conspiracy to defraud government and money laundering of K4.2 billion.

Among other properties, Lutepo was the owner of O and G Group, Cotton Ginners, Oil Mill & Refinery, Cotton Cake, and Tele construction.

 

Advertisement

214 Comments

 1. the cup of suffering.kkkk. Mr lutepo you have contributed to low pay to all civil servants.inflation,threat to unemployments. Spirts of old hundreds ancestors yakwiya. . . Watch out !

 2. Mr lutepo wory not mulungu amakhululukira anthu ochimwa ngati atalapa simulungu akukulangani koma ena akhalidweso lakuba akufuna asawonekele tidziti akugwira ntchito painu koma ife tikudziwa zoona zake get wel soon palibe wabwino padziko lapasi

 3. Akuba ndi ambiri koma kusagwidwa ngati mulungu ananena kuti tchimo lingafiire bwanji lidzayeretsedwa ngati kapezi why not tchimo lalutepo osamukhululukira even masiku ano akuba ndiye achuluka m’bomamo come to chipatala mwanza odwala akudya soya pieces daily opanda tomato tinene kuti the whole of dpp govt lilibe ndalama

 4. Sangafe ndithu athu oyipa awa mulungu amawapatsa moyo wawutali ndi cholinga choti azitizuza basitu tiyeni tilimbe nt`ima basi

 5. Zimenezo ndi ntchito za manja ako, nde udzilore zikuchitire umboni. komanso ndikuona ngati anakupatsa sentence yochepa kwambiri anthu ngati inu mukuyenera kulandira “Life inprisonment chifukwa mwamphetso anthu ambiri osalakwa.

 6. Zonsezi siziza sintha kathu ai boma lizayesetsa koma palibe chiza thandize tikukhala mmasiku osiliza pomwe yesu mkhristu akubwera ndye tiye tizingoyana AMEN

 7. Anthu aba ndalama zambiri ndipo boma linawakhululukira olo nkhanzanzo boma lasintha ma Presindenti katatu konse still munthu madakamuzengabe mlandu mupindulapo chani kodi anthu akuba chuma cha dziko alipo ambiri zangochitika kuti munthu tsiku lake linakwana

 8. Ineso ndigwizana ndi T@B kuti aboma mmangotiphimba mmaso cholinga tidziti mkuchitapo kanthu papita miyezi ingati mkukamba nkhani ya lutepo chilungamo mkuchdziwa tiseni tidzvuti inu mkudya ndalama mdzitengelapo maiko ena samasunga munthu woononga

 9. ALL the best,anthu akumudzi amavutika kuposa pamenepo coz of your cachgate,anthu otiu munalemera kale koma osakonda amalawi amnzanu rip

 10. Thats the results of being greedy.He was already rich and well known, why did he stole government money again?.He deserve death.

 11. deteriorates more than more people in hospitals buying themselves medication only lacking specialist to inject them, food shortages in hospitals, education sector on wheel chairs coz 2 to 3 individuals were greedy.ife tinakhululuka koma sinanga muli manja mwa boma,

 12. Ineyo ngati doctor musiyeni andipeza ndim’mariza kokuno inu phee,ngati kumikuyu amusiya kuchichiriso ndi awo asiyeni athera kokuno tisamangoganiza khani imodzmoz yomweyi ndithana nazo

 13. Lutepoyo musieni, inde wadya koma sakwanitsa kubwez, mungomuonetsa lyf yaku cell, then mutulutse pakatha 30dayz, ndikunkhulupirira kuti sazabaso olo mutamusilira ndalama yokwan mk.3billion,

 14. as much as I know that there’s a lot of prisoners that are sick and receive no attention because of their poor status.give this thief the treatment he need,

 15. Kkkkkk Eeee!!! Kodi Cashgat Inali Ya Lutepo Yekha?Bwanji Osangolanda Ndalamazo Iye Ndikumutaya,ife Tikufuna Ndalamazo Omse Amene Anaba Kuwamanga Ife Sitipindula,komamso Milanduyi Ikungotha Ndalama Za Misonkho Yathu,DPP Eeee Kaya Mavuto Alipo,profe Profe Kumangokhalira Pa Bemchi.

 16. Koma Mulungu wathu ndiwachifundo,sawerengera mphulupulu zathu..monga mmene anachitira ndi paulo…sanawerengere kuti wapha akhristu rather He used him to proclaim the gospel and win souls.

 17. Tikati ukaidi ndi zilango kapena kuti chilango choncho kudwala pa ukaidi ndi mbalinso ya chilango, koma pali act imene imavomeleza kuti mkaidi akuyenela kulandila mankhwala akadwala motelo ngati mwai ulipo akuyenela kupita kuchipatala madokotala akagwila nthito yao, ngati sakapeza vuto tiziziwa kuti pali matenda enaake omwe sangakhunze munthu amene sali mkaidi choncho akuyenela kumubwezela mkati kukapitiliza kudwala matenda otchedwa ukaidi. Ndiye apa tisathe mau, chifukwa palibe wabwino ndi mmodzi emwe, awa zawo zaziwika chifukwa choti agwidwa koma pali enanso anachita zoposela izi lelo ifetomwe timawatcha ma bwana.

 18. Nanunso a Boma ndinu opepela kwambiri eti.. Who is Lutepo kuti akupatseni busy mbamva ngati imeneyi? Ndisamve kuti akayidi ena akufa ku Mikuyu komwe mwachotsa galu wakubayo pokhapo muona polekera. Iya daily basi tizimva za bakha Lutepo ife. Ngati akukuvutani ndiyitaneni ine ndizamunyonge mwamva.

 19. Kumanga Osward, adangolakwa chabe chifukwa sadatcholepo malo osungira ndalama. Zimenezija ankapatsidwa. Kodi omwe ankapelekawo alindende zake ziti?

 20. Wawa bwana lutepo. Malipiro a ndale amenewo. Kugulira chipani ma galimoto?? Kkkkkkk

 21. Kulakwa Ndi Uko Koma Ndamva Chisoni With This Gay May The Lord Help Him!Kmano Wanzeru Aphunziripo Yapa Nkazi,ana,abale,akuvutika Because Of One Second Distion Of Stealing Repent And Come Back To God Or Perish Right There In Prison

  1. adavomereza yekha kut iyeyo ndi wakuba.iweyo ukamayankhula kuti m’boma akulimbana naye ukutanthauza chyani? koma nkhaniyo ukumaimvetsa bwinobwino kapena ukufunika xul ya kwacha?

 22. So What ?Devil Amongst Innocent Malawians Thousands Have Lost Lives Others No Employment He Should Go Back To Mikuyu ,

 23. Amalephera kudwra nthawi yomwe amaba ndramazo bwanji….chomwe angaziwe alutepo ndichakuti…ndalama zakuba sizipasa Chimwemwe ayi….adali madolo pazana paja lero ndiwo makape…leave him there and lot in ,jail

 24. We dont Care about U #Lutepo,olo Utafa U dont hav a prblm, mwina Mitima yathu itsika pansi, Musamulore kutuluka kupita ku #Chipatala cha Kunja ameneyo, Aone m’mene #Life imakhalira anthu Akamakudandaula, Shame on U #BigThief!!!

 25. Pardon??? Chisoni kwambri iweo??? Okuba mmaikana kumbuyo…..kodi JB nde alikuti?? Abwera koma?? Mundiyakhe mafunso onsewo pamenepo

 26. Anthu olemera kungomangidwa uwamva BP yavuta, mtima watupa nthawi yomweyo kuwatengera ku chipatala chonsecho ku ndende kuli akayidi ambirimbri omwe akudwalika mwakayakaya koma sakuthandizidwa. Pa dzilo lapansi palibe moyo wopotsa unzake.

  1. man! lutepo adavomera yekha kut adaba ndalama za m’boma and a khothi adamupeza wolakwa.ndiye iweyo ukufuna kunena apa kut nkhani imeneyi sukuidziwa?

 27. Convicts like Lutepo,Mphwiyo, Kasambara are vital if you want to catch big fish….keep them well. Once these guys die ,forget about the big chejumo

 28. Inuyo a news kuli bwino mzitipasila news zabwino osati zamakapewa ai anthu akuzuzidwa ndinjala matenda ndi umphawi, malo moti mtisakile madonas kuzela mnkhani zanu,, basi daily zandale basi ok ndangati ali kundende akukhala bwino?? Chonde nkhani zachitukuko tikuzifunanso abale ndinu atolankhani abwanji ongotola nkhani zapompa pa anthu andalewa inu??

 29. ifeyo sitimafuna zauchitsiru afanawa adaononga ndalama zathu pomwe ndikunena pano ena ali mmanda chifukwa adasowa thandizo lokwanira kuchipatala ndieno zomangodwala zopusa kuthawa prison unya uona…..ingomubayani jackson wapoison tikamupeza,,,,adali madolo amenewa koma zoti anthu akuzuzika samagamiza No mercy today ….mupaneni

 30. Koma yaaah,amavutikad ndianawa eti en deal alipheee,nthw yabingu anamva zowawa ndachina john chikakwiya,humfry mvula,,,,achair alichete lero ndimfulu koma anahasula papakulu ndithu!!

  1. Chitsiru cha munthu iwe macson,umboni ukufunawo ndiye uti? Ameneyi Lutepo olo atafa we dont care,ndi angati amalawi ataya mmiyoyo mzipatala coz of these selfish pple,tili pa moto mmalawi muno chifukwa cha mbuzi zimenezi,asamusiye olo atafika ku intensive unyolobe ukhale omanga mbava iyi

  2. Kkkkkk Maphunziro Ndiye Tsogolo! Onyozera Tizingolira ! Me Singing Joseph Afazema Song. Ok Amackson Mwasonyeza Kuti Chingerezi Simumva Mvayenso Mkalasi, Lutepo Is Already Convict. Pepa Ndinaiwala Kuti Chingetezi Suumva Anapezeka Olakwa Pamlandu Ozembenitsa Ndalama Za Amalawi Ndipo Anamangidwa Moti Mukamatchula Zaumboni Zikumadabwitsa Kuti Mukunena Ziti.

 31. takulandirani ku chichiri przn komatu ndi weel chairyo sorry ma step 47 kuti uwonane ndi abale ako azikabereka ndani uyu ndalamanso zinanthera kale uyu chilango cha dziko lapansi .nanga kumwambanso kuli moto shame lutepo.

  1. we can not judge him on spirital matters coz we never know maybe he repainted,paja tchimo lingafire ngati kapezi koma lidzayera ngati matalala

 32. naoxo andende,,munthu anaba ndalama mkumapitisa kuchipatala,mankhwala akuxowa kamba kaanthu ngati awa…nanga cikha adapeza kopanda mankhwala kuhospako akanakhala moyo ameneu?? finye wenwen!!

 33. Munthu ali pa wheelchair ndiye hardlobour agwila bwanji komaso lero ndi uyu akusunthidwa kokhala pakuti akudwala chosecho ena oba nkhuku akufela momwemo

 34. Matupi a plastic anzao ife olo atatitsekela mu drum zaka4 timatuluka chimodzi modzi ngati ndakhalamo 2minutes yokha basi anthu obadwa ndi miyezi 12 nanga ndi china wamasiku anoyu ndiye munthu udzibadwa ndi miyezi 9 umakhala usanakhwime kaya

 35. Mdala ameneyu zoti amayenda sindikayika! Get well soon boss kuti mubwelere ku Mikuyu. Ulendo wina mukadwala asatiziwitse, nkhani zanu zimatinyasa zedi, onani mmene Malawi alili pano chifukwa cha anthu ngati inu.

  1. asaa, he is not special in any way. Mandela spent years in prison for nothing lethal, and you want this thief to be pardon? mwene, tiyeni tizingolima.

 36. We’re suffering coz of these idiots. ……kodi kumikuyuko odwala ndye yekha?…….. musiyen akhale choncho ameneo watizuzitsa hvy…….#xiew

 37. kma adha!!! Ku chichiri prison nde ndikwabwino??? Munthu akadwala amayenela kupititsidwa kuchipatala iyaaaaa???.

 38. Angophedwa Ameneyo Bax Iyaaah! Tsiku Ndi Tsiku Nkhani Izikhala Ya Iyeyo? Ife Tatopa Kumva Za Lutepo Apa Shiiiiiiit!

Comments are closed.