Police Nkhotakota district are keeping in a Malawi Defence Force (MDF) soldier for being found possessing Indian hemp found in his two travelling bags.
According to Nkhotakota police relations officer, Sub-Inspector, Williams Kaponda, the suspect has been identified as Andrew Matochi, 34 for Kamuzu barracks.
Kaponda said the suspect got nabbed on Monday, 19 October at a Kaombe checking point as he was driving on the Dwanga – Lilongwe road in a Saloon car, registration number IT 6496.
He said police officers who were on duty at this checking point, found the suspect’s two, travelling bags filled to the capacity with the Indian hemp. Upon being asked as to where he got the hemps, Matochi failed to defend himself a development that was followed by his arrest.
Andrew Matochi who hails from Kanyenda village in the district, will soon appear before court to answer charge of possessing Chamba illigally.
shame on you soilder.
Maluzi anyanya titani ifeno
He is a soldier he must use it.ukuiwala kuti nawe ukamakalndera umakhala utasuta.poor policeman
apolice of coz its ur job komabe ndinu amodzi muenera kukambirana rather than kumuyalutsa nzanu choncho. chilinga akutamen anthu ayidi akutaman ndi mavuto omwe mukumane nao.
wachamba iwe, empty head, umafuna angomusiya poti ndi msilikali? akumana ndi mavuto anji? empty brain, i think ur brain is housed in the urinary bladder,
Nkhokwe zimene zimasunga chamba ndi asilikaliwo,osatira ake ndi apolice . Mukuyenera kudziwa zimenezo.
shame
He posessed ….he ddnt smoke …. Let hm mek money pliz
abwera patata muona
agalu osaka mwamanga munthu osalakwa mu$iyeni!
Kupusa kumeneko mmasuleni nsanga simudziwa ndi masamba a tea ku barracks
Ndizimene Amadya Akakhala Ku Training
Za mphwiiiiiiiiii
tiyeni tiwone mathelo ake
Where do the police take the hemp they smoke?why arrest their own boss?they are all hemp users so they had to hold peaceful dialogue.
sry….” no 1 iz above de law” they say bt 2 sy de truth, som avaz are abv de law…msirikali musiyeni pangani za chitetezo….
Plz release him,we soldiers are working 24hrs but are geting paid peanuts,I suport him,as he has got family to care and suport
Wapolisi alibe gawo kumwamba anthu oipa inu sindifuna kukhala ndi nzanga wapolisi alibe chinzako a traffic nonse tikukuonani dzidyengo dzanudzo mwaonjeza time will tell.
chamba should be legalised in Malawi we are losing huge amount of income. The country owns excellent quality chamba simply release the soldier he has committed no sin.
A Police mwaonjeza chifukwa chani mumafuna kukhala ma STAR enanu mwangolowa kumene police simunaiwone opaleshoni bwezani mudzifunsa abale anu amene anali ku MYP zimene anaona inunso ma soldier asamakutoleni ndiana amenewo
Apolice mutayeni Soldier, Police Head quaters ku Area 30 anzanu akulemela akuba magalimoto inu mukuchedwa kumalimbana ndima Soldier. Ma Soldier amasutatu inu simuziwa?
kumeneko ndiye kuputa mavu ali pa chisa ndithu
Apolice r u againest soldiers?mwachepa nazo aphwanga,mwati lamulo ligwire ntchito?soldier mudapha ku zomba uja bwa?lamulo lidagwira ntchito?kupusa eti,mukangodziwa kut galimoto iyi ndi ya soja nayo kuikhawala.komabe munya soja ndi soja basi iknw simumawafunira zabwino masojawa.tazingowaberani aminibus minsewumu.zopusa eti.chamba ndi dill
shaaaaaa kuwonjezera pasalary,
msilikali? kaya muziona!!!
indian hemp ndi deal
Malikisi zero
Lamulo ligwire ntchito kwa wina aliyense olakwira lamulo apolice gwirani ntchito yanu mosachita mantha.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk zosekesa
I can see very well that 3quarters of the comments are against police but one thing you should bear in mind is that nobody is above the law.others are just talking out of anger maybe coz they were once arrested by police for some offences so they police as their enemy.others are saying “alonda” but still more the government gave powers,privileges & immunities of a police officer which includes arresting anybody who violates the law.so to all those who see police as an enemy pliz be civilized for once,coz other comments are coming out of ignorance.And I can also sense from some comments about who is more powerful between police & mdf,but let me tell you these people they work hand in hand bcoz their aim is make sure that malawi should be a better place to be.finally let the law take its course on this soldier for no one is above the law!!! I rest my case.
Wise talk
wish mukanachuluka anthu a nzeru ngati iwe
zoona umbuli ndiwomwee wachuluka pamalawi pano.big up man Malumbo.
Kupha muthu ndikupezeka ndichamba choopsa ndichiti? Inuyo mudapha soja nkhani sikudziwika kuti ilipati musiyeni ndibussines yake inuyo simukuwona kuti ndalama yavuta pamalawi? Soja pitiliza mpamene umapezelapo mtchele bola osatchola nyumba yaweni kapena kubanawo misokho yanthu!
A police mwayamba kugwira asilikali , inuyo mukazalikwisa azakugwilani ndani ? Watch your self thats His #food release him he is an #innocent person
Mukamamva chamba nde chimenecho a polisi mwalozedwa mukuwayambila dala anyamata a kuluakulu
Musiyen buffalo koma ulemu wasowa mpakakumayalutsana chonchi osangokambirana konko ife tisadziwe bwanj adzakutetenitu inu nthawi yankhondo mudziwe inu apolice mungameze bomba nkufera ntundu inu ?
Mangani Chilombo who is he kuti asamangidwe? Lamulo silisankha.
Okay
Asilikali aku malawi manyi eni eni
Asilikali aku malawi manyi eni eni
Kkkk mdf nothing to do no worry yaa its better kumasuta ganja
Not police nkhotakota but police in nkhotakota
Mutayen apeze ndilama mosavuta
Haaaaaaa!
Koma inu akaombe road block mukuwajaila asikali eti ok akuonetsani zakuda mwava mukumanganso mwana wamudzi ai tiona kuti zikuthelani bwanji
A Mdf Tisamatero
Mwati anatenga kanundu wosutidwa ndi igweee ….aaaaa mtayeni ndi zochepa
Palibe kumasulidwa lamulo ligwile tchito poti ndi msilikali zazii akadakhala muthu wamba nde bwezi mukuti chani amangidwe basi nyc job the police
Iwenso siwe mulonda iwe? Dikilani mutikitidwa muona.
Chonde apolice mmasuleni msanga
All am seeing is Stupidity here! why why why I said why? release him before its too late
Masulene inu
chibaba chandpwetka ganja samanana
anatenga leav or retired?
My fellow guys.when you want to comment please make sure you got a point.i know some of you got good brains that can give advises.people can learn from you.when you comment its like you are on air.people do read what you think.if someone does wrong lets criticise by giving better options.also lets appriciate if one does good.if we join our brains we may reach a good option that our readers can benefit..read the following comments and reason whether there is sense.
What?my fellow sodier?eish!!!.
KAMBILANANI NDINU PACHIBALE ,ATENGEPO PANG’ONO AZIKABANDA BASI
YOU SITUPID POLICE PLZ RELEASE THE GUY!!!! KUSOWA CHOCHITA ETI!
kalandeniso ku nkhotakota farm agalu inu
Zazii To All Thoz Who Ur Against Wt Wht Police Hs Done,mind U Nobody Iz Above The Law,u Ur Calling Thm Alonda Wht About Thoz M D F Pipo? Aja Akulondera Nkhalango Yadzalanyama Ndi Chikangawa Aja Ndindani? Bravo Malawi Police For Agood Job!
Awona polekera ana apolice amenewa. Mukazulidwa mapwala musadandaule mwaziyambira dala. Amuna anga amachidya chimenecho ndiye mukuti china akapeze kutiko? Fuck u!
Kulemera basi
dziko lalowa chaina etiiiiiiii
Hahaha mmalo molimbana ndimbava uko mukuti ayi koma Ganja,chamba eti
wen i burn the weed it mi big vission.thats y mi burn it from season to season.#legalise it
Yusufu Tchale Gilbert Marayiti Richerson Francis Kalungu Lameck Raul Chimutu Joyce Sadick Luke Nathaz Daniel M’manja Claisa Jame Bywell Chisi Anold Mavuto Mavuto
Zikungosonyezelatu Kuti Muboma Ndalama Zavuta Mpaka Chamba. Komaso Mukagwila Wachamba Muzikataya Kudzala Bwanji Mmapolic Mulibe Madzala? Mundiuze Ndidzakumbe Ine Khasu Ndimalipha.
Why arresting the man who has the herbs as any type leaf?This doesn’t make any sense ,The Stone that the builders refuse will surely be the head cornerstone,
Release my soldier now….I was a soldier I used to risk my life.
Shupitiiiiiii…why arresting him?dnt they knw that chamba/marijuana stimulates the brain?
Shaaaa!zatelonso?
kukhomelelana bax
Mwazolowera kugwira munthu wamkulu musamale amene mwachita izi game sithera pompo
Ndasilira buznss yabwino
why arresting him..
why arrestin him its food for great men even de data men knowz set him free pliz!
Kkkkkkk ok
amutulutsa m`mamawa omwe eti,tikanakhala enafe mmm
Promotion yavuta pa malawi hahahah mbava zokhazokha kugwirana, ok tiye nazon nde apolice mukamapasidwa ma kofi muzidandaula choncho muxova
Apa ndiye alonda nonse m’waisosha Pachiyambi munanapha nsilikali apa mwagwira m’modzi mwa iwo paja akuti mukagwira msilikali m’modzi iwo azagwira alonda 100 kapena kuti anyama 100 achitetedzo hahahahahaha kikikikiki wanditseketsa dala.
Tiye nazo ayise alondawa ajayila mpaka kumanga boma kkkkkkkk
Police imayima palipose, ndima loweyer pawokha kaya, lamulo liposa mphavu, wa police amakhala owina always no matter what!
Kulimbana ndi police usakuziwa malamulo ndikutaya nthawi, ndi lowyer ekha amene angalimbane ndiwa police, coz police imalanga munthu through laws, then physically!
Kulimbana ndi police usakuziwa malamulo ndikutaya nthawi, ndi lowyer ekha amene angalimbane ndiwa police, coz police imalanga munthu through laws, then physically!
za ma soldiers zimathera mkati chenjerani inu a 24……
Lol
nyau zapondana masamba
Malipilo nd 10000 mwez onse nde nde banja la ana 19 eh….. Amsiye bas boma lavomelezatu za hemp
Inu chakudya chathu chimenecho
Mumusiye ngti mukufuna kuti chamba chithe mukaotche kaye mbeu ya chambayo kmso muononge minda yake
Kkkkk
free him is a soldier please!
Chamba ayi muziti fodya wa mafumu bwanji chinthu chabwino mmachipatsa dzina lonyasa
Aaaaaa!
ths why we Africans r poor tel mii what iz gud selling chamba or selling weapons.to bad guyz
Asamusie apitenae akamuweluze,
police ngafunika makofi bwanji kuseweretsa ndalama
mpaneni ameneyo
Soldiers need to relax too
Legalize chamba pliz tilemere ife iwe malawi government
Apolosi nanu, mukanangomvesetsana ndiwaboma nzatu ameneyo.
Legalise Marianna u u u!
Down here in Malawi, u u u.
No more, criminalising ganja smokers.
Apa nde waliputa boma aise zikuvuta. Police!!! Bweraniso m’zomba mu amapezeka mu ntiyamu zathanenawoni! Fakaaa iweee!!
Pliz jst share those bags of camba,u a police man what is a use of that camba to your self after realise MDF member?
Olo ine mmene ndalama zikundivutilamu,chinyengo kapena kkugulitsa zithu za illigally ndi momwe muli makobili pano
Apolice mwayamba kugwira asilikali akumenyanitu
I dont even understand,Our cntry is Famous for Farming n’we Chamba as an Income”this week our PRZDNT hv Legalize GAY-law which is nt accepted & is a Sin’So why cant you Regalize this Chamba/Indian hemp,as u knw we dnt have Gold n’Mine…BRAVO AS A SOLDIER UNEED 2HAVE CHAMBA ITS UR DUTY NO CRIME”
which is good,amwene galu pampando
parliament needs to draft a law that legalizes marijuana…………. #right #to #use #marijuana #plant 😎 :p
In or on?
both
Zovuta kwabasi
Shashasha!!!!!!! Malawi police in duty nw!