![Malawian Musician Tuno](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/03/Tuno-Musician-Malawi-276x176.png)
Nkhondo siimanga mudzi: Tuno wapepesa Zani Challe
Potsatira kalata yomwe Zani Challe anatulutsa yodandaula komaso kuopseza kuti apanga chinthu china chomwe sananene pa Tuno kamba komunena kuti iye amagulitsa thupi komaso amachita malonda a mankhwala ozunguza ubongo, oyimbayu wapepesa tsopano. Nkhaniyi inayamba… ...