![Wode Maya visited an initiation camp in Malawi](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/09/Screenshot_20230920-2013392-235x176.jpg)
Wode Maya wavula chinyawu; watulutsa kanema ali ku ndagala
Pomwe anthu omwe sizikuwakhudza amaletsedwa kupita ku malo alionse opangira chinamwali cha a yao, ndagala, anthu adzidzimuka kuti mlendo Wode Maya wa ku Ghana anakalowako mpaka kujambula kanema yomwe watulutsa pano. Mlendo odza nkalumo kakuthwayu… ...