
Mabungwe oyima pa okha ku Balaka akhumudwa ndi Nkhani yokhudza malo kwa Ng’onga
Mgwirizano wa mabungwe oyima paokha m'boma la Balaka ati ndi okhumudwa ndi mpungwepungwe omwe wabuka pakati pa anthu a m'mudzi mwa Ng'onga, khonsolo ya Balaka komanso kampani ya Portland Cement pa nkhani yokhudza chipukuta misonzi… ...