
Phungu wa Chikwawa West wathokoza boma chifukwa chofuna kumanga nsewu wa Chapananga
Phungu wa mdera la Chikwawa West a Susan Dossi athokoza boma la a Lazarus Chakwera chifukwa chofuna kumanga nsewu wa Chapananga omwe wakhala nthawi yayitali utawonongeka. A Dossi awuza Malawi24 potsatira zomwe adayankhula mtsogoleri wadziko… ...