
Boma lipemphedwa kuti lizimanga onse onama pa FACEBOOK
Inu nonse amene mukutchukitsa kuti mtsogoleri wa dziko lino akudwala ndipo akuganiza zotula pansi udindo, akuti muzimangidwa. Anthu ena omenyela ufulu wa anthu wa chibadwidwe ndiwo apempha boma la Malawi kuti liyambe kuunika bwino nkhani… ...