
Zipani ziwiri zikuluzikulu zinandipempha kuti ndikhale runningmate ine ndidakana – Bushiri
Mtumiki Shepherd Bushiri wati zipani ziwiri zikuluzikulu m'dziko muno zinamupeza ndikumupempha kuti akhale wachiwiri kwa otsogolera zipanizo (running mate), koma iye anakanitsitsa kuti sakufuna kupanga zimenezo. Iwo afotokoza izi mu macheza awo ndi kanema wa… ...