“Hallo! Ndi kumwamba kumeneko…ndilankhuleko ndi Mulungu,” m’busa alankhulana ndi Mulungu pa selefoni
Masiku otsiliza mudzaona zinthu zosiyanasiya zina zoona komanso zina zomusemera Mulungu koma iye asananene kalikonse mkamwa make, malemba amatero mu buku lopatulika. Izi zikupherezera pamene m'busa wina m'dziko la Zimbabwe akuti walumikizana ndi mulungu osati… ...