ACB and Ministry of Education have released a book for primary schools

ACB yakhazikitsa bukhu

Bungwe lothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau lakhazikitsa bukhu la tsopano lotchedwa "Anti-Corruption Source Book" lomwe lidzigwilisidwa ntchito ndi aphunzitsi a kupulaimale. Bukhuli lomwe alikhazikitsa dzulo ku Lilongwe cholinga chake ndi kuphunzitsa chikhalidwe, umunthu komanso… ...