Palibe kuvota pompano, tidikile kaye Bajeti
Bungwe loyendetsa zisankho m'dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) latsindika kuti zisankho za pa dera zomwe zimayembekezeka kuchitika m’ma dera ena a dziko lino zidikira ndondomeko ya za chuma ya boma. Malingana ndi wapampando… ...