A Malawi akwiya ndikuletsedwa kwa chakumwa cha Frozy
A Malawi ambiri ati ndiokwiya ndikulesedwa kwa chakumwa chozizilitsa kukhosi cha mdziko la Mozambiki cha Frozy. Kukwiyaku kukutsatira zomwe lanena bungwe lo unika zinthu mdziko muno la Malawi Bureau of Standard (MBS) dzulo pa 25… ...