![Inkosi ya Makosi Mbelwa](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2018/04/Inkosi-Mbelwa-235x176.jpg)
Zako izo, ife timwa mowa ndi kukwatila mmene tingathele: Angoni a ku Mzimba sakuifila CCAP
Inkosi ya Makosi Mmbelwa, imene ndi Mfumu yaikulu ya Angoni, yadzudzula a Livingstonia Synod ndi kuwachenjeza kuti akapanda kusamala athamangitsidwa mu dera lake. Pa mwambo oveka ufumu a T/A Mzukuzuku ku Mzimba, mlembi wamkulu wa… ...