Ndachimina, watero panza Ichocho

Monga malemu John ‘Izeki' Nyanga ananena kale kuti “zina umangoona waziyamba,” panza Yassin 'Ichocho’ Suwedi wachimina ndipo akuziguguda pachifuwa uku akuyankhula yekha yekha kuti kodi moyowu unkalinda kuteleku? Panzayu apempha anduna kuti amukhululukile. Potsatira zomwe… ...