Apolisi akhudzidwa ndi ntchito yozembetsa anthu
Pamene thupi la Habtamu Tamirat Suganomo yemwe ndi mzika ya dziko la Ethiopia limafika pachipatala cha Mzimba katangale wa ziphuphu zomwe zidamupha zinali zitayamba kale kufalikira. Imfa ya Tamirat yemwe ndi wazaka 23 zakubadwa yaulura… ...