
Chelsea maso ndi maso ndi Tottenham Spurs usiku uno
Timu ya Chelsea usiku uno yakodola timu ya Tottenham Spurs mu mpikisano wa English Premier League (EPL) kuti agumulane masewelo awo a chi nambala 30 pa bwalo la Stanford Bridge mu mzinda wa London. Chelsea… ...