![Paul Chizetere Osuaha](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/05/Paul-Chizetere-Osuaha-235x176.jpg)
Nzika yaku Nigeria yagwidwa ndi cocaine
Apolisi m'boma wa Lilongwe amanga nzika ya m’dziko la Nigeria yazaka 43 kamba kopezeka ndi timaphukusi 33 ta mankhwala ozunguza ubongo a cocaine. Malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa za polisi mchigawo cha kumadzulo mchigawo chapakati… ...