![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/06/Dominant-1-235x176.jpg)
Oyimba hipapu ambiri akumveka ngati Gwamba – watero Dominant 1
...wati nyimbo zambiri ku Malawi ndi mbwelera Oyimba nyimbo zogwira palisani, hipapu (hiphop), Dominant 1 wabweretsa chifwilimbwiti pa masamba amchezo pomwe wang'alura oyimba anzake kuti ambiri akubera mmene amaimbira Gwamba ndipo wati nyimbo zambiri ku… ...