Agamulidwa zaka zitatu ndi theka kamba kolemba zabodza pa Facebook
Inu nonse amene mumabwela pa Facebook ndi kulemba zabodza ndi zofuna kuipitsa mbiri ya ena, samalani. Anzanu akumangidwa nazo. Bwalo la majisitireti mu boma la Mchinji lagamula Bambo wina kuti akagwile ukaidi wa kalavula gaga… ...