
Tiyesetsa kupanga bajeti yokomera aliyense – boma
Boma lati liyesetsa kuti mu ndondomeko ya zachuma ikubwerayi aikemo zinthu zomwe zikomere anthu ochuluka mdziko muno. Izi ndimalingana ndi nduna yazachuma a Joseph Mwanamvekha omwe amayankhula mu mzinda wa Blantyre pakutha pa mkumano omwe… ...